Chilima Simtsogoleri Wabwino - Bon Kalindo

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 21 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 82

  • @Luxemaven8686
    @Luxemaven8686 4 місяці тому

    Bon Kalindo you have gained a supporter!!!!

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 4 місяці тому +2

    Honest speaking Mr DC Big up

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n 4 місяці тому +2

    booooon kalindo Mo fayaa. keep on to give us truly updates. inu mumalankhula chilungamo chokha chokha

  • @ishmaeldama8906
    @ishmaeldama8906 4 місяці тому +5

    Bon he is talking the truth, but u can see other people they talking sheet, be very careful my fellow Malawian, we must wake up guys, zinazi sizotengela kupita ku school, khalani pansi moganiza bwino, malangizo awuleletu awa,all the way from johannesburg

  • @LoyidKarebe
    @LoyidKarebe 4 місяці тому +1

    Go ahead Mr kalindo we are following you

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO 4 місяці тому +10

    Komatu a Kalindo munthu osamuipitsa choncho. Inu musamunene Chilima kuti oipa lero. Mwagwira naye ntchito limodzi. Kuipa kwa munthu amadziwa ndi Chauta basi. Inunso muli ndi zonyansa zanu.

  • @ellahmwams831
    @ellahmwams831 4 місяці тому +1

    Mr kalindo moto 🔥 🔥🔥

  • @devimatope9980
    @devimatope9980 4 місяці тому

    man of integrate😂😂😂 Bonnnnnnn Kalindooooo mwana oopsa kwambiri from Njeza village ..T/A mabuka, mulanje😊😊😊😊😊

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e 4 місяці тому

    Yes you are really talking

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 4 місяці тому

    Chakwera ndi Chilima wooooyeeee,muwaphe A Malawi onse mukatha mutenge mitemboyo muitafune Mukhute,popeza ndalama mwawa bera Kale,koma muziwe masiku amatha ndikugona adaku voterani wokha samaziwa zoti Chibwenzi chankhwangwa chokoma pokwera, Amalawi mukaza voteranso awa izo ndi zanu wanthuwa ndi aka Nyimbi Anunkhisa Malawi.

  • @AlastairGutt
    @AlastairGutt 4 місяці тому +2

    Kalindo is matured now

  • @FulahaMtafya
    @FulahaMtafya 4 місяці тому

    Chisilu mbuzi 😢😢😢

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 4 місяці тому +2

    Mukunena zoona big, koma mmalawi opusa akuona ngati chilima ndiwabwino

  • @RodwellLupiya
    @RodwellLupiya 4 місяці тому

    Bwana Born Kalindo pqjatu ndinu amene munamukakamiza Chilima kuti avomere kukhala vice president lero mukumunyozaso . Komaso inuyo mumatiuza kuti sindinu wandale koma chosecho mukuwauzaso anthu kuti akqvotere aford , udf kqpenda dpp.

  • @IsihakaAmidu
    @IsihakaAmidu 4 місяці тому

    Mbambande mr presdent bon kalindo kwathu kwa chulu zinthu sizilibwino tikukhalangati tili mkamwa mwa mikango

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu 4 місяці тому +3

    Kodi inu mumkamuuza chilima ngati ndani? Osachita naye msanje. Pangani zanu akulu

  • @georgebalala3048
    @georgebalala3048 4 місяці тому

    Shaaaa this was days ago

  • @CheloyaaChikwatuu-ob2mt
    @CheloyaaChikwatuu-ob2mt 4 місяці тому

    DC ❤❤❤

  • @beakab2378
    @beakab2378 4 місяці тому +1

    Zooona zokhazokha, Chilima wakhala duuuuu a Malawi tikulira, olo one day osalankhulapoyi mmene m"boma mukubedwera ndalamamu, nde atifune pano? Ine ndamitsikatu, he won't get my vote

  • @SibwenzaLevisoni-gm6rv
    @SibwenzaLevisoni-gm6rv 4 місяці тому

    Ndipo nkhaniyi ndioona big up DC

  • @esternguluwe
    @esternguluwe 4 місяці тому

    Bwanji adzangotiimra bon kalindo yomweyo pa u president,akuoneka ali ndi nzeru kwabasi

  • @JonathanKamwetsa
    @JonathanKamwetsa 4 місяці тому

    Ipondeni Fadala........ You're a real son of Malawi........

  • @BrightKuyaka
    @BrightKuyaka 4 місяці тому +2

    Zoyankhula za bon kalindo zatitopetsa tsopano, katakwe ndi bakili muluzi tv

  • @AnnoyedFallingLeaves-zp8dy
    @AnnoyedFallingLeaves-zp8dy 4 місяці тому +6

    The problem with Kalindo is that he wants to be the master minder of Chilima. But he has to understand that Chilima has brains. My instincts also tells me that he is indirectly campaigning for DPP.

    • @Janetjombo-r7k
      @Janetjombo-r7k 4 місяці тому

      This is true. Kalindo is 4 dpp

    • @EvanceSungani-cv9jk
      @EvanceSungani-cv9jk 4 місяці тому +1

      In your minds but he talks vry true posatengera za ndale,,,,,and all of this akuya khula ndizoona,,,, nokha mukuziwa mene adalankhulila chilima mu campaign ya 2019 analankhula zambili mbili zokomera Ife achinyamata koma ndzt wakwanilitsapo,,,,,inuso musamangosutsa zilizonse you supposed to see the true

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 4 місяці тому

      I fully agree with you, Kalindo is taking advantage of illiterate masses.

    • @GRACIOUSKENAN
      @GRACIOUSKENAN 4 місяці тому

      Which brains dear, you talking about??? No he is bad man also,can he preform good speak today how??

  • @macksonkalasa9668
    @macksonkalasa9668 4 місяці тому +2

    Koma kumanidwa udindo kulira mpakana 4 years

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 4 місяці тому +1

    Apadi akunena zoona zaka zonse takhalayi chilima ali.duuuh nde angabwele kwa ife kutiwuza chani ??

  • @SanudiJaymofred
    @SanudiJaymofred 4 місяці тому

    Kalindo to the people

  • @DesmondKanguwe
    @DesmondKanguwe 4 місяці тому

    Kalindo ndiwamisala uyu

  • @PeterPadambo-kk5oh
    @PeterPadambo-kk5oh 4 місяці тому +2

    Chilima sanalakwise kanthu, cholinga akawukira muzimunena kuti amangowukira kulikonse? Apa pokha nde ayi, boma ili tinalivotera chifukwa cha Chilima, nde atulukeko chifukwa? Mesa kuli mavoti ake, musiyeni Chilima akhale, nthawi ikakwana ayankhula

  • @BrianBanda-nn1gt
    @BrianBanda-nn1gt 4 місяці тому

    Ndizoona ndikugwilizana nazo

  • @MavusoNdhlamini
    @MavusoNdhlamini 4 місяці тому

    Nkhanira yakwachulu yokha mwapala. Miyambe mwazimvetsa zinthu mmene zikuchitikora. Bwerani ndi ma demo anuwo tione ngati simuyaluka

  • @Nomsa77
    @Nomsa77 4 місяці тому

    Vchifukwa choti azakhala pa u president ndichifukwa achakwera amuphera.....
    Chifukwa chani mdziko mumalowa anthu osaziwika bwino

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu 4 місяці тому +1

    Musamuipitsile mbiri a chilima inunso simulibwino.

  • @LucasKavala
    @LucasKavala 4 місяці тому +1

    Yes DC akunena zovona

  • @PeterkinsJanuary-fv9wd
    @PeterkinsJanuary-fv9wd 4 місяці тому

    Bon kalindo ulemu wanu

  • @WilliamBanda-un5eg
    @WilliamBanda-un5eg 4 місяці тому

    Dzapangeni nawo compete bwanji because it seems mukudziwa zambiritu

  • @MercyPhiri-nh9jy
    @MercyPhiri-nh9jy 4 місяці тому +1

    Zoona amasankha tsogoleri ndi mulungu. Inu musaweluze

  • @GiftAsirKhwanya-ok2gu
    @GiftAsirKhwanya-ok2gu 4 місяці тому +1

    Akunena zoona kalindo

  • @HakeemJossam
    @HakeemJossam 4 місяці тому

    anatipwetekesa asabweleso

  • @ShabanMajor
    @ShabanMajor 4 місяці тому

    iwe ndikumenya bwanji mulimbana ndi DC wanga

  • @daveskachiphaphi
    @daveskachiphaphi 4 місяці тому

    Tabalirankon aku mwera usabwere ndi mademo Ako pano pakati chita kwanuko

  • @KondwaniMunthali-lx5jc
    @KondwaniMunthali-lx5jc 4 місяці тому

    Ndiye tivotele ndani utiuze kalindo manyi ako

  • @josephchika173
    @josephchika173 4 місяці тому

    Amakomadi akamwalira munthu sure

  • @vitumbikokamanga5869
    @vitumbikokamanga5869 4 місяці тому

    Chilima usogoleli mlibe ose ndi adyera same like chakwera 😅

  • @AnnaPhiri-b8t
    @AnnaPhiri-b8t 4 місяці тому

    Zitsiru ndizomwe zingakhulupilire chilima opusa omwewa ndizomwe zikunamizika chilima zaupresdent alibe nazo ntchito koma iye azingodyelera mimba yakeyo

  • @YohaneFoster-vq7wp
    @YohaneFoster-vq7wp 4 місяці тому

    Kalindo akufuna atibalalise Ali ndi reason behind

  • @NtabaKali
    @NtabaKali 4 місяці тому

    Yaaa

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 4 місяці тому

    Munthu amakondedwa anamwalira Pamalawi

  • @RoseMwasikakata
    @RoseMwasikakata 4 місяці тому

    Impossible ngati munthu akugwira ntchito mmboma sangayankhulepo zotsutsa boma man limenelo nde bodxa

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx 4 місяці тому

    Uyu ndi wamisala chilima ndi otumidwa so sakadaima mkuyankhula mudakati ndi oukira

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 4 місяці тому

    Akutitenga ife uchitsilu pomwe achitsilu ndiyiwowo amalawi asukutsula ngati tinachotsa mbuyawo kamudzi chifukwa chankhadza chakwela nde ndanitso galu kwabasi

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx 4 місяці тому

    Chilima waonetsa kudekha ndipo sadaukire koma kalindo ndale zidakulani

    • @grandwellkatumbi4763
      @grandwellkatumbi4763 4 місяці тому

      Dziko likamaonongeka mtsogoleri wabwino sadekha ....chilima akudekha zichani pamene zinthu zikufoila mdziko muno

  • @ShukuSh-vi1hk
    @ShukuSh-vi1hk 4 місяці тому

    Ndizoona zimene akuankhula karindo chifukwa nthawi yakampeni ndiiyeyo amene amanyamula thumba la 50 kg sichakwera iyayi

  • @SangwaniNkosi
    @SangwaniNkosi 4 місяці тому

    Chilungamo chimawawa,Koma DPP ayi ziko linaliko bwino mnthawi yimeneyo

  • @BazaarShaibu
    @BazaarShaibu 4 місяці тому

    Aka ndi kachilungamo

  • @giftmingo9293
    @giftmingo9293 4 місяці тому

    Uzitiuzanso za DPP ifeyo lero? Moti ukakhala umati aMalawi angamvere ndithu iweyo kkkk

  • @AishaChibwana-b8o
    @AishaChibwana-b8o 4 місяці тому

    Kalindo ngati ndi chamba uzavula galu iwe ukukhale wachilungamo ndiwe mulungu?? Ndiwe galu kwambiri usatibowe uziyankhulira amako ndi anthu akwanuko

  • @francischikaya3146
    @francischikaya3146 4 місяці тому

    Iwe sukuimirira a Malawi koma chipani china chomwe aliyense akuchidziwa. Ukulimbana ndi Chilima nthawi zonse bwanji? Kodi kwinako kulibe zofooka zawo. Usawaike a DPP ngati ndi Angelo lero. Sitinaiwale zomwe amachita padzana paja. Tikudziwa kuti mtunda wa kwanu ndi omweo. Usatinamize ife takana.

  • @giftmingo9293
    @giftmingo9293 4 місяці тому

    Boma la Chakwera silizakhala labwino kwaiwe only if utakhala Minister. Unduna sapatsa zitsiru ngati iwe. Anthu a kwa Chulu akakuthibula bwera uzazione. Kulira 4 years kufuna udindo kkk😂😂😂😂

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 4 місяці тому

    Aaaa chilima angoputsisa MCP tsingapase utsogole chifukwa chakwela akumva kukoma ndibanja lawo lotse nso dzoti chilima akudziwa chilungamo koma manyadzi uchitsilu mutayeni tiwone 2025 dzizatha bwa

  • @GiftNgwira-e8l
    @GiftNgwira-e8l 4 місяці тому

    Zoonadi zianthu zoipa kwambiri 😂😂😂😂😂😂😂

  • @SAIKINGFRIDAY
    @SAIKINGFRIDAY 4 місяці тому

    Eh komatu akulu awa chilima anakulakwilani chani muja munayambila kumunenamuja mpakapano or kukuyankhani osangomusiya bwanji ndiwankulutu ameneuja amadziwa chimene akupanga nde zinazi ife mumatinyasanazo zomalimbana ndimunthu oti samakuyankhani

  • @MalakamMillie
    @MalakamMillie 4 місяці тому

    Chilima ndi witch craft mbuzi mwana wajoka amati tizidya katatu madzi awulere magetsi awulere fetelizer wochipa. chilima ndifiti kwambili

  • @LovelyGalaxy-rb7yl
    @LovelyGalaxy-rb7yl 4 місяці тому

    Zinthu zake

  • @henrykapinga1433
    @henrykapinga1433 4 місяці тому

    Kkkkkk

  • @AlexanderBilliat
    @AlexanderBilliat 4 місяці тому

    The DDCccccccccccc

  • @angelj3771
    @angelj3771 4 місяці тому

    It a better to dellete this video. You have cursed him

    • @josephchika173
      @josephchika173 4 місяці тому

      Lero akuti anali tsogoleri wabwino tooo bad

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 4 місяці тому

    Izi ndi nkhani za amalawi ngakhale a president anayankha nkhani ya America mu chichewa, translate in English nonsense

  • @EmilyBakali
    @EmilyBakali 4 місяці тому

    Kkkkkkkkk