Aaaaa iwe zoti chilima ana phedwa ndi chakwera simudziwa athu opusa inu malawi oganiza ndiowona patali chilungamo tinachiona the some day yagwa ndege a malawi tisanamizidwe chilima anaphedwa ndi chakwera
Kodi lowoneka pa ngozi Kuti tikuuzidwa zabodza..? Andale Adayamba anenako chilungamo? Bwanji osanena za aja ankati if not change everything for 90 days I will rising. Asinthapo chiyani ..Kuti akakamile pampando. If ya chilima inenedwe Anthu ave. Inu muli NDI umboni wanji KUT ndibodza.?
chakwela ulape thawi yantha uzaziona wasala ndi zaka zochepa zokhala pa dziko ngati sulapa Yehova Ali nawe pamodzi ndi atumiki ako amene umawatuma zoyipa
We Malawians donot know how to solve problems.That's why we lag behind times of development and modern transformation. SOLUTION A)Define the term problem. B)Find the Root Causes. C)Strategize and plan to Peter out/eradicate the Root Cause(s)Most of the times we solve the results and not problems.
Kodi anthu akwaseka pa kamwa kuti asalire Ngozi imene ija tinakuuza kuti Kampeni inuyo Achakwera munatimenyela kale chifukwa cha ngozi ya ku Chikangawa
I think anthuwo ngopenga are you sure Mr siza you are comfortable with that koma ndiwe obeleka , are you sure akanakhala abale Ako ukanat bwanji with all that contradiction in that report inuso mukhale chete Chifukwa you will be also answerable it's not far from now
Zaziii zokha zokha. Chomwe ndimaziwa anthu anja..munachita kuwampha...😢😢😢😢mcp ma vote anu ndiomwe anja....anthu munawapha anja...
Black box ituluke apa zonse zitha
Kubisa kwa Black box komaso kutseka anthu pakamwa, chifukwa chiani? Zikudabwitsa, kafukufuku akunika 100%,🙏
Zithuzi tilinazo zambiri ndipo mukamati analibe magaz ndimomwe mwendo uja unakhapidwira timadabwa nanu kwambiri 😢😢
@@EsetaGerate ndipo anthu amenewo ndi afiti kwambiri mwendo amachita kuwaza ngati akuwaza nkhuni km mcp mulungu alowelerepo mmmm magazi analibe?nthawi ikakwana akachoka tizaponya zilipooooo asaname.
💙💙💙💙DPP 16TH SEPTEMBER 2025 APM/ADAD MY VOTE ✅✅✅
Osangotumiza ndege bwanj kukatenge fertiliser yo
Boma layamba kunamizila ziwawa zaku Mozambique kuti ndizomwe zikupangisa kuti fertilizer asowe .
Funso mkumati , chiloweleni mcp m'boma ndichamzelu chanji chomwe angatiuze chomwe achita pazaka 5 .
Yankho ndiloti = 0 / 100
Inu amipingo maso anu ali pa ndalama koma muzamva kuwawa kwenikweni akazakhala mb, bale kapena mwanawanu ndizowawa zomwe zinachitikazija
Makosana Boma latikwana ili kod ndilambuyawo kapena bwanji aaaaa zopusa zomwe chakwera akuchita
Kod chovutikila mnchan mmalo mongobweretsa black box yo
Zimene mukukambazo ndi zankutu
Iweso ndiopanda nzeru ndiwe wa mcp
Ameneu pantumbopake galu ameneu pantumbopake
Aaaaa zaziiiiiiii mulungu salakwitsa kalikose aliyese wokhudxiwa ndi ifa ya chilima
Aaaaa iwe zoti chilima ana phedwa ndi chakwera simudziwa athu opusa inu malawi oganiza ndiowona patali chilungamo tinachiona the some day yagwa ndege a malawi tisanamizidwe chilima anaphedwa ndi chakwera
Kodi lowoneka pa ngozi Kuti tikuuzidwa zabodza..?
Andale Adayamba anenako chilungamo?
Bwanji osanena za aja ankati if not change everything for 90 days I will rising.
Asinthapo chiyani
..Kuti akakamile pampando.
If ya chilima inenedwe Anthu ave.
Inu muli NDI umboni wanji KUT ndibodza.?
chakwela ulape thawi yantha uzaziona wasala ndi zaka zochepa zokhala pa dziko ngati sulapa Yehova Ali nawe pamodzi ndi atumiki ako amene umawatuma zoyipa
Ndipo ndi chisilu chazimbambo achipasa ndalama eti zopusa achoke asamatinyase atikwa iyaaaa ,athu oipa akupha awa panyapawo
Zamanyi etiiiiiii kodi mesa SKC ada chita kumpedwa kodi muku tiwona ngati amawi ogona
Zako zimenezo . Bungwe ndi lako sili kudikudza . Anthu akuulu koma opsa mayangulidwe.
Pamene pali bodza pamakhalaso chilungamo,ife sitisiya kulankhula za denge mpaka choona chitadziwika
Mboli zamanu nwalephela kumufunsa kukuyu kuti black box ilikuti ndiye muzilimbana ndikufuza zachithunzi nachende amanu ndithu
We Malawians donot know how to solve problems.That's why we lag behind times of development and modern transformation. SOLUTION
A)Define the term problem.
B)Find the Root Causes.
C)Strategize and plan to Peter out/eradicate the Root
Cause(s)Most of the times we solve the results and not problems.
Angosowa chochita.
Afufuze kuti ngozi kuti ichitike chinachitika ndi chiyani
Nosenu ndinu zitsilu kd kose kunagwa dege kuja anakagwetsaso ku mayiko enaw ? Osatsimikiza bwanji kt anafa bas kd anati adzakhala wamuyaya ?
Kuyankhula kopusa koma akanakhala m'bale wanu,ndiye adindowo bwanji sanawachose ntchito
Bungwe lake liti zaziiiiii zopusa basi kuwatengera kuntoso basi musatinyasepo apa
Smkunama guys 😢😮😮akuyenera arape kd chakwerat watkwana chidebe 😊😮😮
Zabodza zanj chitsilu iwe nkhan ndya straight SKC anachita kuphedwa
Kodi Black box sitinauuzidwe kumene inapitatu, tikufuna black box basi tiona kuti titani nayo tikayiona
Iwe ceazer ndimaona ngati ndiye wamzeru tu ukulorera azikugwirisa ntchito a mcp mugwera limozi
Chokan ana anjoka inu zithunz tidakali nazo,Dpp ikangolowa 😮😮😮tizakumangani chilima munamukhapa miyendo ndi manja...ndpo zikuchita kuoneka agaru inu mwayiwala kt mnalowa muboma chifukwa cha chilima zitsiru inu, zosayamika
Adya ndalama za Congress awa musatipitsitse amalawi si ana
Anthu kumalawi akufuna black box funso kumati black box ilikuti??
Agalu mukuba ndara ma smusthay mrungu wakkwiya nanu mucchite masuti otuwawo😊
The Truth will be known.
What is wrong is wrong. God knows what happened.
Kodi anthu akwaseka pa kamwa kuti asalire
Ngozi imene ija tinakuuza kuti
Kampeni inuyo Achakwera munatimenyela kale chifukwa cha ngozi ya ku Chikangawa
Tikhulupilira kumene anthu Aja anachita kuphedwa ndani sakuziwa zithuzi tilinazo
Zithuzi za kukhapidwa kwa chilima ndilinazo km mmm zomvetsa chison ndipo galu kamagalasi ndi nzakoyo m ulekeretu😢😢😢
Share to me ndione nawo
Ndimafuna nditumize voice note koma space ndilibe anyway mkulu ameneyi ndichitsiru kwambir ngat alidolo akatuluse black box deal done
Dr kabambe zoonadi zomwe wanena big dziko laola anthuni
Mumuuze amene akunena zoti asiye kulankhula za imfa mbolo yake
Inu zisilu kwambili asakabwanji otumiza zithuzi zangozi pamene amene anapangisangozi asanamangidwe apa zikuwonekelatu kuti nose amabungwe amene muluti athu agwilise chito uthenga wamalupoto mukudyanawo ndalama zamwazi wachilima ndiathuenaja pamomozi ndi akasambala munyela mulungu simuthu ngati chikangawa wanuyo zakutu basi
Anyanii awiriwa Iwo angotiudza Kuti Iwo atiudze Kuti ndichani osangosaina mudye nawo.kukula mutuu?
Za zii za kuti muli ndi nzeru namalira simutseka pa kamwa
Aliyense akuziwa kuti chilima adathandizira mcp kulowa m'boma nde kuwaletsa kuankhula pa imfa ya chilima sizingatheke adachita kuphedwa chilima ndindani adachita campaign kulinganiza ndimomwe amachitira malemu chilima kukafikira akumidzi
Izi nzogulidwa asowa zochita. Magulu opusa awa palibe akunamizidwa za ngozi aliyense akuiona momwe nkhani inayendera. Za fertilizer musatipusitsenso siife zitsiru
Mabugwe Ake ATI mukati Ife baziyo muisaza imeneyo
Kodi ndalama mukusowanazo zochita osagura chakudya bwaji kugawa kwa anthu ovutika bwaji khalani serious guys
munya Amalawi ake siapanowa we know
Mapwala anu, anthu sangasiye kuyankhula mmisonkhano kuyankhula zangoz yandege
Tigodikila kampeni kuti azalongosole ndichimene akufuna kuti akumudzi amve azawauza onkha satelo zokhuza ndenge
Best way is just to bring black box out that's end of story
Koma apolisiwa , pena sangathe kugwiritsa ntchito nzeru zawo? zinazi akungowaonesa ngati osazindikira kapena ntchito yawo sanakaphunzire momwe angagwilire
Musamati ngozi yandege ayi.nkhani ndiya straight.muziti.Anafa pachiwemmbu.cha ndege .Aliyese akudziwa .nthawi inotu ndiya social media.osati 2001.fb utube.tisanamudziwe ayi..
Mwadya ma banzi inu.....nkhani ndi black box...
Komatu akulu muli ndi mphuno yoopsa kwambiri mphuno imeneyo ana anu akazi apeza banja koma?
Tiziwawa ta Mocambique tazulozuloli mwapezaso ponamila pokanika kuwapasa zipangizo zaulimi munthw yake? A mcp
Tizasiya kukamba za ndenge mukazabwelesa black box
Awa nde manyaka ankhani, palibe amene saziwa kuti a chilima anaphedwa ndi chakwera. Ndipo za fertilizer mkunena apazi ndiboza lokhalokha boma lakuba la chakwera palibe chabwino
Mwinanso ngatu akufuna a mcp onse mma social media accounts mwao tidziwapanga tag ndi zithunzizo
End zisilu Zina zikuti zikuchita kafukufuku Wina ..zimenezo zilekeke zizachitikanso tikachotsa bomalii
Chakwera anapha achilima monga anthu simukumudziwa?
Ziwawa za ku Mozambique zayamba liti kuti munamizireko poyamba mumati ndi nkhondo ya ku Rasha ndi Ukraine eee koma ndi inu okwana bwanji🤔🤔
Iweso ndi galu kobasi mumfuna umboni wa mtundu wanji kodi amfiti inu... Ifetu angoni zimatiwawa..
Zisiru zaathu ndiye mugwira munthu chifukwa chani ineso ndinatumiza nawo mbuzi zaathu
Kkkkkk koma chikangawa party mpakana kunamidzila dziwawa dzaku Mozambique kuti fetelazi sakupedzeka
Akunamadi ameneyo
Atitankhure akubanja plzzz
Za ziiiiii can u leave saulos chilima spilit to rest pleaseeeeeeeeeeeeeee
Aone madzi anthu ameneyo
Nthawi yoseyija munalikut munachokapo mwaba mwamaliza matumba mwanu mwadzadza et palibe chanzeru mungawauze a Malawi mwatilephera inu
Zophyezana amabungwe a mcp ayi ngozi imeneyi oloko mwana akhoza kufotokozera,kafukufuku wanu ndiwabodza
Chimene mwapangana ndi A police ndi MDF ife A malawi tikudxiwa kti mufuna muopsye anthu mudxiko muno .kma ife tikhala tikukamba kmaso kutulutsa xithuxi xaku chikangawa .......
Chakwela unazi panga di campaign wekha pamene unapha Dr Chilima
Black box ndiye nkhani apo ndye kuti itha
Black box first
Mapwanu nonse mukufufuza zimenezo. Makape achabe chabe
Bring black box first,,, then we will stop
Zaziiii!
Zangozi simungawaletse anthu kusiya kulankhulapo, mcp ikukutumani tikudziwa
Osafufuxa black box koma zinthunzi??? Mulungu tithandizeni
Chikangawa united trying so hard to defend
Kupha chilima ndi misiteki kowopsa
Malipoti ake ati zausilu agalu kwabass iweso chisilu kwabass Ana afti
Pewani kupha anzanu kuti khalidwe ngati limeneli lisazachitikenso komaso kuti anthu azikukhulupilirani
Nkhondo ya Ukraine yaima sopano apa ayamba kunamizira zaku Mozambique, a chakwera auzeni anthu anu achepese bodza kuvometeza zinthu kuti zakuvutani ndibwino, kusiyana ndi daily boza lokha lokha
Poti mufufuze za black box mukupanga za zithudzi koma boma la mcp likunganiza bwanji
I think anthuwo ngopenga are you sure Mr siza you are comfortable with that koma ndiwe obeleka , are you sure akanakhala abale Ako ukanat bwanji with all that contradiction in that report inuso mukhale chete Chifukwa you will be also answerable it's not far from now
Zaziiii mukubisapo chani pamalo angozio zaugalu basi
Sizaboza ndizowona zokhazoka anachita kuphedwa
Mukudziwanai u ndi chakwera inu cheteee
Tipatseni black box
Kodi awa awatengaso kuti Koma manyazi mulibe
Zingoyenera kulowa ndale nayeso anali wandale
Chilima sanafeletu ubusa anafela ndale ndezisalowe ndale bwanji?? Munapha chilima kapeni yazipani zotsutsa ndimeneyo kumene munaphaa chilima ,, a chakwera ndi kunkhuyu,, chimwendo,, wakulu wasilikali,, wakulu wa police,,, kama jacket ndiena ambili, munaphaa chilima
Ndale nd boza ndpo honourable anat ku MCP ndale sapanga masana nde nthawi zina osatitola pakamwa
Athu akupha inu mwawatha amalawi oyimba ndiye chipele lelo mukutenga oyimba kut akathandize komaso oimba ena alibe nzele mawatu ndinuyo akupha inu a mcp ndipo ine mmandinyasa chifukwa chipani Cha mcp choline mulungu mmitimayawo
Anthutu akufuna black box basi. Why you're hiding black box? Zimatiwawatu and sitidzaiwala mpaka kalekale
Nkhani ndiyoti palibe aliyese azadziwe za report ya ndenge ndi mulungu yekha adziwa zonse let's pray for God 🙏
Chikangawa akudziwA
Iweyo ndi amene ufuna kutchukaa
Chitsilu bambo uyu::aliyense akuziwa chomwe chinachitika
Mvula udzabwera black box ikapezeka
Kuyakhulatu uku