Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Ndimayikonda serie ya Mdyangu ndi Mfumukazi I don't miss from Buckinghamshire UK.
Chiphwanya analakwadi monga mwamalamulo anu....but bring him back...sitingakulamuleni koma ngati ife oonera tikumfuna ndithu in his position ❤❤❤
Bring chiphwanya back. Tizikhululukirana amalawi. Chiphwanya is one of the main best characters. Please Please 😊
Oooooh koma pachimphwanya po ganizasoni dyangu ikuperewera iyi....... Mi love abusa sasoka and big chimphwanya
Koma guys mumayitha keep it up
it's me E,J, BANDA FROM South African
Ai mai zamveka za achipwanya mumaithanso munyanyiwanso alibhoo zikuthekanso bhobho mdyangu ndi mfumakhadzi yatisisa kuonera mafilimu ena im proud of you.....
Mai shokoshoko , Mercy , Queen and Mulelemba i love more guys as well as the whole team
Ndipo or mutatani chipwanya and sasoka ndi one mwa mdyangumo❤❤❤ ndipo musasanamizidwe wallay guy's
Please bring back chipwanya
Florah suya bg up to you Imandivetsa kukoma ndpo you're doing the great job Just keep it up plz msathile mnjira ngat momwe zimachitikila zinazi
Chimphwanyaa akukasaka mano Ku zambiya 😂😂😂😂 best wangaaa
Mumakwana nonse ndimakunyadirani mumandichotsa nkhawa heavy big up
I like you all guys mumandinvetsa sugar kuno ku south Africa🎉
More fire 🔥🔥🔥 mureremba
Chipwanya ndye best comedian yo
alright but chiphwanya is best of best kumdyanguko ndie pangani zoti abwelele please please
Mnyanyiwa is a good actor ..anabebesa kubwela kwake
Mai shokoshoko
Mnyanyiwa akuitha tisaname ndidolo....
Mlelemba bwera tizadye zapa John 😂😂
Lamulo liposa zonse but bring chipwanya back please please please we need chipwanya back
Chiphwanya ndi die hard,abwelere💪
Please bring back chiphyanya
Ngati chiphwanya sabwelela m'malo mwake, ndiye zosakhala bwino. Kapena ndibwele komko ndidzamupepeselee?
Frola iweyo ndi one and umativesa kukoma koma ma minutes akuchepa please
Mumakwana Maka mercy yo ma hope anga
❤❤❤ timamukhonda chipwanya ndi Queen
Ofcoz zachitika and walqkwisa mnyangu comedy timaifila koma without chiphwanya chinachakebe chikuperewera bring him back
Ine nowe ku south Africa chipwamya tikumufunaso amatinamiza kuti ndi siramu
Please bring back Chiphwanya tamusowa kwambiri
Kwiniumandisangalasagirl more fire 🔥🔥
Kod episode ya week ino siinatuluke..?
We love you more 🔥🔥🔥
Dyangu is without chimphwanya sikukoma we need him back
izitha khani ndijoyine nawo ine mumaro mwachikwanya 😂😂😂 ayi chikwanya tamusowa
Chiphwanya abwerele please ngakhare analakwisa koma please please bring him back
Frola ndiwe galu kwambiri muchoseni kwin chipwanya ndi sasoka muone
Nkhani yamveka ya achimphwanya palipose pamakhala malamulo❤❤❤
Flora suya we know kut anthu amatha kulakwitsa but pa chiphwanya pokhapo please taganizaninso kachikena
Bring back chiphwanya madam i beg
How can we get the whole film?
mm makwnila nose kumeneko nosee mulibwanji ♥️♥️
A Flora mumakwana mumatisangalatsa ndi ma series anuwa
Kwini umakwana kom fn isiyen kaye 😂😂
Mesa queen and mlelemba sasoka plz I love ❤
We need chiphwanya pamenepo please
Hy program iyi ndimayisatha koma imandipeza mochedwa
Qween mimba ndiyanda bora yisakhale ya alamu
Nkhani izitha Chiphwanya abwelere
Akazi akumalawi koma kuyela 😂😂😂
please bring him back chimphwanya
Nkhani izitha inu km na pa chiphwanyayo nde mkhan siitha
Chipwanya out it's fine Munyanyauwa emwewo.Queen umatha Ayise,undipezere khani izitha imodzi yokha basi.
Koma mukhuluklukileni chiphwanya amakomesa sewelo please
Kkkkkkk komadi chiphwanya anaphonya
Chiphwsnya tamdandaula mnyanyiwa abwerere kundende 😂😂😂😂😂😂
Queen nd mercy amandvetsa kukoma Kod munthu wakulu kwambr alikuti chiphwanya
Zaziiiii nkhani Mesa mwati izitha ndiye osamuvetsa bwanji
Moni moni guys, mumatimvetsa kukoma ❤
Koma ndiye pa Achiphwanyapo sipakubeba abwerere basi
Queen ukunikondwesa chomene lutizga machelo nizamukupa 50 pin
Please chiphwanya abwerere .muluza mafaz chiphwanya ndi moreee!!!
Chiphwanya ndi dolo be ownest we will miss him
Ine Baby Rasta from Namiyango tishetiyo yandiwaza khani izitha
Mulelemba umandiwaza thawi unali kutikuferanji😂
Ilove you my m,dyangu
Khwiniiii sakubwezaso moto Kwa ccta wake wanyulaaa ,,,,ndimaona ngt anena kut asisi ayambilaso misala Lol
Kwini ndimakukonda kwambir usabwere kwathu udzadye mpunga kumachinga ine lanjesi maida
Zamanyi zanuso ndiye Ife ayi chipwanya tikuti abwerere
Chipwanya ndi Dolo,, ka mdyangu kose mulibe angamake😏😏😏
Pliz forgive Chiphwanya and bring him back again, besides Munyanyiwa nayenso it's another nkhani eeee kkkk
Koma macy❤🎉Umakwana
Kodi a jangu sabwelelanso?
Queen mpakana chizungu mphepo iyi mmm kkk
Basi musiyeni timubweletsa mu zalo ku Durban kuno kkkkkkkkkkkk timphuzitsa chizula
Ndiye mwati chiphwanya analakwanji???? Am lufeyo walufeyo sa
Koma Gaga/mnyanyiwa nd character mbambande eeeeish
😂 ndikupasa yafata chikwanya afike
queen umakwana umandimvesa kukoma ponya number yo . mercy yellow born uli bhoo
Timakunyadirani amon
We miss chiphwanya amativetsa kukoma kwambili
My favour chimphwanya
Mulelemba umakwana❤
Kwa a Shokoshoko mipandonso eeeh
Gani ndi mai ake mai dyangu mumandiwaza
Nkhani izitha mmhKulongolola
Queen perekani nambalayo😂😂 mmm koma nkhani izitha chiphwanya tamusowa and he left infinished part ndi mkazi uja mzukulu wa mdyangu
Nkhani izitha😂, osamapsa mtima mwachangu Flora you are my idol🎉 kupepesa kwamveka❤🌹
Koma chipwanya amatisangalasa
@@maliyadaitoni kwambiritu, tamusowa Chiphwanya😍😍😍
Nonse mumandiwaza ine Mai Banda ku Soche ku Kwale
koma mnyanyuwa can't perform like Chiphwanya,
Abwere chipwanya za ma Jerasi basi Ndiye munyanyiwq angafanane ndi munthu wa mkulu amene uja,.mukambirane osati za chibwana mukuyakhurazo
Hello morning morning
sister timamukonda kwambili munyang'anya
🤣🤣🤣🤣🤣 achiphwanya kufuntha
Queen umanditsangalatsa
Komanso Chiphwanya asamajaire🏌️♂️
Mwanena nokha kuti.nkhani izithaBwanji osamukhululukira chiphwanyayo
Ma triphonia timakunyadila musasiye kuipatsa fire
Koma we need him back
Chipwanya amatisangalasa
Ndimayikonda serie ya Mdyangu ndi Mfumukazi I don't miss from Buckinghamshire UK.
Chiphwanya analakwadi monga mwamalamulo anu....but bring him back...sitingakulamuleni koma ngati ife oonera tikumfuna ndithu in his position ❤❤❤
Bring chiphwanya back. Tizikhululukirana amalawi. Chiphwanya is one of the main best characters. Please Please 😊
Oooooh koma pachimphwanya po ganizasoni dyangu ikuperewera iyi....... Mi love abusa sasoka and big chimphwanya
Koma guys mumayitha keep it up
it's me E,J, BANDA FROM South African
Ai mai zamveka za achipwanya mumaithanso munyanyiwanso alibhoo zikuthekanso bhobho mdyangu ndi mfumakhadzi yatisisa kuonera mafilimu ena im proud of you.....
Mai shokoshoko , Mercy , Queen and Mulelemba i love more guys as well as the whole team
Ndipo or mutatani chipwanya and sasoka ndi one mwa mdyangumo❤❤❤ ndipo musasanamizidwe wallay guy's
Please bring back chipwanya
Florah suya bg up to you
Imandivetsa kukoma ndpo you're doing the great job
Just keep it up plz msathile mnjira ngat momwe zimachitikila zinazi
Chimphwanyaa akukasaka mano Ku zambiya 😂😂😂😂 best wangaaa
Mumakwana nonse ndimakunyadirani mumandichotsa nkhawa heavy big up
I like you all guys mumandinvetsa sugar kuno ku south Africa🎉
More fire 🔥🔥🔥 mureremba
Chipwanya ndye best comedian yo
alright but chiphwanya is best of best kumdyanguko ndie pangani zoti abwelele please please
Mnyanyiwa is a good actor ..anabebesa kubwela kwake
Mai shokoshoko
Mnyanyiwa akuitha tisaname ndidolo....
Mlelemba bwera tizadye zapa John 😂😂
Lamulo liposa zonse but bring chipwanya back please please please we need chipwanya back
Chiphwanya ndi die hard,abwelere💪
Please bring back chiphyanya
Ngati chiphwanya sabwelela m'malo mwake, ndiye zosakhala bwino. Kapena ndibwele komko ndidzamupepeselee?
Frola iweyo ndi one and umativesa kukoma koma ma minutes akuchepa please
Mumakwana Maka mercy yo ma hope anga
❤❤❤ timamukhonda chipwanya ndi Queen
Ofcoz zachitika and walqkwisa mnyangu comedy timaifila koma without chiphwanya chinachakebe chikuperewera bring him back
Ine nowe ku south Africa chipwamya tikumufunaso amatinamiza kuti ndi siramu
Please bring back Chiphwanya tamusowa kwambiri
Kwiniumandisangalasagirl more fire 🔥🔥
Kod episode ya week ino siinatuluke..?
We love you more 🔥🔥🔥
Dyangu is without chimphwanya sikukoma we need him back
izitha khani ndijoyine nawo ine mumaro mwachikwanya 😂😂😂 ayi chikwanya tamusowa
Chiphwanya abwerele please ngakhare analakwisa koma please please bring him back
Frola ndiwe galu kwambiri muchoseni kwin chipwanya ndi sasoka muone
Nkhani yamveka ya achimphwanya palipose pamakhala malamulo❤❤❤
Flora suya we know kut anthu amatha kulakwitsa but pa chiphwanya pokhapo please taganizaninso kachikena
Bring back chiphwanya madam i beg
How can we get the whole film?
mm makwnila nose kumeneko nosee mulibwanji ♥️♥️
A Flora mumakwana mumatisangalatsa ndi ma series anuwa
Kwini umakwana kom fn isiyen kaye 😂😂
Mesa queen and mlelemba sasoka plz I love ❤
We need chiphwanya pamenepo please
Hy program iyi ndimayisatha koma imandipeza mochedwa
Qween mimba ndiyanda bora yisakhale ya alamu
Nkhani izitha Chiphwanya abwelere
Akazi akumalawi koma kuyela 😂😂😂
please bring him back chimphwanya
Nkhani izitha inu km na pa chiphwanyayo nde mkhan siitha
Chipwanya out it's fine Munyanyauwa emwewo.Queen umatha Ayise,undipezere khani izitha imodzi yokha basi.
Koma mukhuluklukileni chiphwanya amakomesa sewelo please
Kkkkkkk komadi chiphwanya anaphonya
Chiphwsnya tamdandaula mnyanyiwa abwerere kundende 😂😂😂😂😂😂
Queen nd mercy amandvetsa kukoma
Kod munthu wakulu kwambr alikuti chiphwanya
Zaziiiii nkhani Mesa mwati izitha ndiye osamuvetsa bwanji
Moni moni guys, mumatimvetsa kukoma ❤
Koma ndiye pa Achiphwanyapo sipakubeba abwerere basi
Queen ukunikondwesa chomene lutizga machelo nizamukupa 50 pin
Please chiphwanya abwerere .muluza mafaz chiphwanya ndi moreee!!!
Chiphwanya ndi dolo be ownest we will miss him
Ine Baby Rasta from Namiyango tishetiyo yandiwaza khani izitha
Mulelemba umandiwaza thawi unali kutikuferanji😂
Ilove you my m,dyangu
Khwiniiii sakubwezaso moto Kwa ccta wake wanyulaaa ,,,,ndimaona ngt anena kut asisi ayambilaso misala Lol
Kwini ndimakukonda kwambir usabwere kwathu udzadye mpunga kumachinga ine lanjesi maida
Zamanyi zanuso ndiye Ife ayi chipwanya tikuti abwerere
Chipwanya ndi Dolo,, ka mdyangu kose mulibe angamake😏😏😏
Pliz forgive Chiphwanya and bring him back again, besides Munyanyiwa nayenso it's another nkhani eeee kkkk
Koma macy❤🎉Umakwana
Kodi a jangu sabwelelanso?
Queen mpakana chizungu mphepo iyi mmm kkk
Basi musiyeni timubweletsa mu zalo ku Durban kuno kkkkkkkkkkkk timphuzitsa chizula
Ndiye mwati chiphwanya analakwanji???? Am lufeyo walufeyo sa
Koma Gaga/mnyanyiwa nd character mbambande eeeeish
😂 ndikupasa yafata chikwanya afike
queen umakwana umandimvesa kukoma ponya number yo . mercy yellow born uli bhoo
Timakunyadirani amon
We miss chiphwanya amativetsa kukoma kwambili
My favour chimphwanya
Mulelemba umakwana❤
Kwa a Shokoshoko mipandonso eeeh
Gani ndi mai ake mai dyangu mumandiwaza
Nkhani izitha mmh
Kulongolola
Queen perekani nambalayo😂😂 mmm koma nkhani izitha chiphwanya tamusowa and he left infinished part ndi mkazi uja mzukulu wa mdyangu
Nkhani izitha😂, osamapsa mtima mwachangu Flora you are my idol🎉 kupepesa kwamveka❤🌹
Koma chipwanya amatisangalasa
@@maliyadaitoni kwambiritu, tamusowa Chiphwanya😍😍😍
Nonse mumandiwaza ine Mai Banda ku Soche ku Kwale
koma mnyanyuwa can't perform like Chiphwanya,
Abwere chipwanya za ma Jerasi basi
Ndiye munyanyiwq angafanane ndi munthu wa mkulu amene uja,.mukambirane osati za chibwana mukuyakhurazo
Hello morning morning
sister timamukonda kwambili munyang'anya
🤣🤣🤣🤣🤣 achiphwanya kufuntha
Queen umanditsangalatsa
Komanso Chiphwanya asamajaire🏌️♂️
Mwanena nokha kuti.nkhani izitha
Bwanji osamukhululukira chiphwanyayo