Emmi Deebo Chani ft JeyDak Official Music Video

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 вер 2024
  • (Verse 1)
    Zaka zikupita
    Miyezi ikudutsa
    Masiku nde akutha awawa (akutha awa)
    I've been waiting waiting waiting
    Kuti tsiku lina uzayankhula
    I've been telling all of my friends, kuti chaka chino titengana
    But you'r not saying anything (ndimangodikila dikilabe iwe ine)
    Nane ndimafuna banjaa (nane ndimunthu ndikufuna ndidziwe)
    (Hook)
    Kodi umafuna chani paineyo?
    Cholinga chako nchani Paine?
    Umaganiza chani zaineyo? Oooo!
    Ndimaoneka opepela
    Pena ngati ndine otengeka
    Amzanga onse amangondiseka inee!
    Nane ndimafuna banja.
    (Verse 2)
    Umaopa kukusiya wekha
    Ndichifukwa ukukana kudekha
    Ine ndikumvetsetsa
    Mbali yako ukuyesesa
    Sikuti zokhala nawe zili kutali
    Vuto ndizikamba kumbali
    Pali amzanga okhaa
    Awa ndakazi anga (ndimawanyadila)
    Tsono lelo udziwe
    Sindingakusiye (ndili nawe plan mamie)
    Kukupangila njilaaa
    Sizothamangila..
    (Hook)
    Kodi umafuna chani paineyo?
    Cholinga chako nchani Paine?
    Umaganiza chani zaineyo? Oooo!
    Ndimaoneka opepela
    Pena ngati ndine otengeka
    Amzanga onse amangondiseka inee!
    Nane ndimafuna banja.
    (Bridge)
    Nane ndimafuna banja!
    But you not saying anything (ndimangodikila dikilabe iwe ine)
    Nane ndimafuna oyela
    Ndiuzeni mwina nane ndingavale Velo!!
    (Hook)
    Kodi umafuna chani paineyo?
    Cholinga chako nchani Paine?
    Umaganiza chani zaineyo? Oooo!
    Ndimaoneka opepela
    Pena ngati ndine otengeka
    Amzanga onse amangondiseka inee!
    Nane ndimafuna banja.
    The end.
    #EmmieDeebo #chani #beke #khumbo #afrobeat #afro #malawi #malawianyoutuber #youngmusician #african #pop #popular #popmusic #new #newrelease #top #topmusic #trending
    Follow Emmie
    web.facebook.c...

КОМЕНТАРІ • 69