INE NDINE SAPOTA OSAMUVOTERA AUSI KOMASO PASAPEZEKE WINA ABWERETSE WACHITETEZO KOMA NOSE AMENE WARANDIRA NDALAMA KWA AUSI ZILANDILENI NDITHU NDIZANU ZAMITSONKHO YA MALAWI ZIMENE MCP YA PEREKA NDALAMA IMENEYO NDI BONASI NDALAMA MUZIDYE NDALAMA ZA AUSI KOMA OSAMUVOTERA
Zoonadi comrade azathu ena ma passport yawo ilibe number kumapeto and amafuna kukatsegula account yakana chifukwa ilibe number kumapeto koma oti analipilira limodzi yake ili ndi number what a shame of Malawi Passport
Yes ofunikad akapanda kupitako kukachotsako zinthu zawo za expire mupitekodi nokha boss Comrade Mtanyiwa coz ndizinthu zoika pa chiopsezo miyoyo yathu . & I support you all amene mungapiteso ku queens ko kuti mukawagwireso nokha anthu achinyengowo coz kukapita anthu ena akapezeka kuti sakafikako... Moto kuti buuuuuuuuuu Mr Comrade Mtanyiwa 🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤
Umakwanaa boss ❤❤❤❤❤
Chipulumutso ndi iwe mwini Nyirenda ndi azibusa onse a seventh day sichipulumutso werengani chibvumbulutso 22 v 12 azibusa ambiri ndi achinyengo.
Amene avotere manganya ndi chitsiru
Ntanyiwa pena pake umachulutsatu bodza zinazi umangopeka kufuna kupatsa nkhawa ma sapota a UTM iwe uzikhara serious ngati the DC Bon Kalindo
Siyani kunvera muzidwara mutu amwene sizambari yanu izi zisiyne
Ntanyiwa Kodi unapita ku sukulu yamaboza koma watitopesa mene unyambila muja palibe chosintha
Mulungu alowelelepo zimenezo zisatheke mudzina la Yesu
INE NDINE SAPOTA OSAMUVOTERA AUSI KOMASO PASAPEZEKE WINA ABWERETSE WACHITETEZO KOMA NOSE AMENE WARANDIRA NDALAMA KWA AUSI ZILANDILENI NDITHU NDIZANU ZAMITSONKHO YA MALAWI ZIMENE MCP YA PEREKA NDALAMA IMENEYO NDI BONASI NDALAMA MUZIDYE NDALAMA ZA AUSI KOMA OSAMUVOTERA
Inutu mukuchulusano bodza penapake idont support any political party but this hiruos mtanyuwa
Zoona comrade katundu wambiri amagulitsa za expire especially a Kapani even ogwila nchitho komweko akuvhutika
Kwaine ndimaona kt kusankha Manganya as UTM president kukhala ngat mwagulisa chipani chanu Ku MCP
Zoonadi comrade azathu ena ma passport yawo ilibe number kumapeto and amafuna kukatsegula account yakana chifukwa ilibe number kumapeto koma oti analipilira limodzi yake ili ndi number what a shame of Malawi Passport
Eesh
Lichokendikoma
Sangawine manganya aiiiiiiiii betchi a mcp samava aiiiiiiiii niki nayeso njala yonse iri ziko muno zoona kuononga ndalama
IWEYO ULIBE NDA MALAMA !?
Manganya ndi Mcp, be careful
Ofunika ovotao chonde akasankhe mwa nzeru chonde chonde
Busa ameneyo siwasevesiday ai tamukana
Kodi aBon kalindo adya chibanz bwanji sakupezekanso tifufuzilen Kut Kod kapena is under arrest?😂😂
Kkkkk wasowadi mkulu ameneyu
OK
Later spray
Waboza ndilo wosokoneza iwe
Ausi ndi njoka ku utm bilimankhwe Ausi
Zovuta kwambiri
Ndalamazo kadyeni koma osakamuvoter