NOTE A'ba.le okonda nyimbo za mapwando zodumpha ma speaker this is your song promote it kwanuko mpaka ma speaker ang'ambike, yifakeni pa repeat weekend yonseyi mpaka neba awone ngati ndakulipirani kuti muzingovina PUPUPU yokhayi, please yimwazeni Pali ponse,🙏😅 enjoy your song
NOTE
A'ba.le okonda nyimbo za mapwando zodumpha ma speaker this is your song promote it kwanuko mpaka ma speaker ang'ambike, yifakeni pa repeat weekend yonseyi mpaka neba awone ngati ndakulipirani kuti muzingovina PUPUPU yokhayi, please yimwazeni Pali ponse,🙏😅 enjoy your song
Ife pano 🥰🥰🥰
abare tiripano
I'm inside IB ENTERTAINMENT studio right now listening to it 🔥🔥🔥
Neba wanga alimmadzi lero asokoselidwa
Moto wake braza 🥳@@mosesmilinyu8414
Chinyimbo cha vibe brooo....mukajambura video muxatenge ma dancer abholl
Okonda abusa ndinyimbo zao tonse tabwelan pano🔥🔥🔥
Mumatha abusaa 😂❤pupupu inde fadaah wikise inuyo munavayaaa kale
Habusa ❤❤❤
Ichichi chipweteka anthu ku Malawi 🇲🇼 big up wikise muzik wakoka
Mumakwana fadah
🔥🔥🔥
𝗣𝘂𝗽𝘂𝗽𝘂 𝗲𝗲𝗲𝗲 🏄🏄🏄
Ukali wako 🔥🔥🍒
I didn't know kuti pupupu yu ndi vibe chonchi 🔥🔥
Big up @wikise1992
You're very talented 😍😍😍
❤🔥🔥🔥
Nice
Mwapha abusa
Your growing in music...km l think it's high time musiye KUIKA za abusa zija 😂😂
My Trade mark is bigger than me..singasiye ngati ufuna siya kumvela iweyo
🔥
Ndli nkat mweni mweni hit after 🔥 🔥 hit
Nyimbo ilimwala 🔥 🔥 🔥
Ukanangodikila Kaye wezi ikamakhala track of the month koma eeeeeeh tikumvela Kaye Eli simpo..❤❤❤ nice tune bro
Abale omvela ndi ochuluka ndipo it's different audience, inuyo kazimvelani iyoyo ife tumvela iyi basi.
@@Wikise1992😂😂
@@Wikise1992 inu tikukumvelanibeni apa koma timangoyenera pa mawa musazatipanikize chochi😂
Ntimboyi mwachatatu bwino mwaitulutsa tym ya maluzi ! Sured ikanatithera ndalama nyimbo imeneyi in the month of July !
More fire umatha iweyo Wikise
Ikumveka bwino
Iyiyi ndi hit 🔥🎯
Kkkkk nyimbotu aaaa
Awa ndimadala amatha ndapapata naneso
More fire mesaa,,,,tidyeraa.wozaaa
Tidyera mu zinjoyi ichi 🔥🔥🔥🔥
Confidence ya pu pu pu 🔥🔥🔥🔥
Kuteloku yakwanila kudyelaa town muno
Nyimbo ili mwala🔥🔥👌
My brother wikise💥💥💥💥💥💥🙌🙌🙌love from🇹🇿🇹🇿
Osapeza Zina zochita bwanj nd luso lanu lokakamizali
Singakondedwe ndi aliyese Chule iwe iya 😂😂
Koma abusa kkkkk
Ili mwala nyimboyiii🎉🎉🎉
Ili khenge
Amandiwaza
Fire 🙌🙌💪
Umakwana
😍😍😍😍
🥳🥳
Mwapha baba🎤🔥
Hit of the month
Iwe simunthu wamba
Nyimbo yatha itangoyamba😭
Iyi ndiye moto🔥🔥
Iyiyi nde yadda🔥🔥🔥
Koma amapiano uyu bwanji aaaaah
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉iyi indithers money
Continue pushing bro
Finally the song is out🤗🥳🥳🥳🥳🥰
Kodi mukuti chani
mumakwana 🔥🔥
Komatu ma speaker aphulika nacho ichi🙌🙌🙌🙌🙌🙌
Keep pushing bro....
🔥 this is fire aise 🎉🎉🎉🎉
Kumaimba zoti anthu akanvera nyimboyo azipezamo uthenga ndikuwugwirisa ntchito osati izi pupupu ndiye chani nyimbo zakuti izi ndiye kumati ndatulusa nyimbo ikukamba zachani nyimboyi
Kod zauthenga mpaka liti iiiiii muzingolira daily ?
Uthenga wachani apa
🔥tichezera imeneyi
Garu iwe hit after hit mmmh napatapata
Hit 🔥🔥🔥
Ma speaker aja tadumphatso🎊🎊🎊🎊
This is hit 🔥
Iyi ndi ya weekend 🔥🔥🔥
Waiting
Fire 🔥
Aaaaaaaa ndey zichan izi madala ine ndimaona ngat chividio chazithuzi
Pachidwa kulembedwa Bwino bwino kuti mp3 basi muziti zichani ? Mukufuna kublockedwa kapena ?
@@Wikise1992asakupangeni demotivate bro track ili bho 🔥🔥🔥🔥
Apa wafika 🔥 🔥 🔥
Sure
Muchedwatu aaaah tizingodikira😂😂
Zili nice napapats
Trek Music ... Timzy I See You
Pupupu 😌🔥
Wahala to Malawi since song of the year is out 😂❤
Ma judge aku Malawi agundika😆# agulu😄
Iwe umati🤣
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥♥️🎹🎶 GhettoPiano
Dolo kwambiri 😁☺️
Waiting malume wikise
We are here abusa
Mabomba 💥💥
Chi hit cha bho
odi ukooo💥💥💥
Nyc ❤️
pupupupupu
Nice one
Pupupu🔥🔥🔥🔥
Koma ndiyedi ndi pupupu ine palibe ndikunvamo Sir wikise
Chili bhooo
Tikudkla yomweyo 🔥🔥🔥🔥
Hit🔥
🥰
This is a great...
Dis😅
We are waiting hoza
Dolo kwambiri eeeh ulemu wako Gettoh product 😁
Hard
Tikudikila video man
Koma abusa aja mmmmmm anachimwa basi😢😮
😂😂😂
Mwabwera
kodi tittle yachokeraa pa kamene kakulila pupupupu ko😀 iwe ndi shasha
Yes bros 😄😁
Ine kukonda zinthu video kulibe😂
Ndapapata
Kd nyimboyi ikut chan😂😂😂😂😂😂
Pupupu basi nothing much ngati baby crying song 😅
Big up @wikise