Inde Norman chisale ayenera kulandidwa katundu chifukwa sanapeze munjira yoyenera zoona munthu woti alibe even msce kulemera chonchi ,nanunso penapake mzikhala ndi manyaz kaputabuya iwe ungalimbane ndi boma olo khot
Amwalira pophano andu a mcp ndioipha kwambili nde zomwe aziona ndi izi azimwalira modzi modzi na a mcp aziona ena ayamba kufa khale kwasala akuluakulu aboma
Chisale ndi mmalawi ndalamayo ziri Ku Malawi satar ndi obwera ndalama amaganizridwazo ziri kunja kodi ACB mmene amapanga Kaya mmati freez acc yake kodi inali mu dzina la ndani ndipo chinawapangisa kuti uku kwalowa ndalama za ku Army ndi chani awo mafunso ochokera kwa Mwalimu kachisi from Malaysia he is a Malawian amalankhulanso chichewa zomveka bwino kwambiri
Big up mr Game changers,,mokupemphani ndithu plz plz Mr Game changer zaonetsetseni ndithu kuti a chipani cholamula asazabere zisankho ndithu.. achotsedwepo ndithu pa mpando
❤❤❤❤❤ fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 agalu a mcp awa tatopa nawo madrmo basi ayambike
Mr game changer nice♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️
Hon Dalutso Kabambe A Visionary Leader For Malawi 🇲🇼
Amusiye norman chisale , norman is strongest man ❤❤
Akufun agulise agulire mafuta ngongole akuwakaniza zavutapo znthu apa God almighty forgive us all we r all sinners
❤❤❤ u brother
Ndichocho Mr game changer mkwana
Tiwaphurese mitu aise
Noorman chisale danampeze ndi mlandu ndiye tikudabwa kuti akulanfa katundu wake chifukwa chiyani?
Welldone mr game changer ❤❤❤
Ife tatopadi ndi ulamuliro opanda nzeru, Police ndi army dziwani kuti mukuthandizira mcp kuzunza abale anu. Mulungu akulangeni pamodzi ndi mabanja anuwo komanso mabwana anu. Ifensotu tiri ndi mizimu , ndalama akumakupatsanizo eni ake ndi ifeyo
Finsi ndi finsi MCP ndi MCP ndipo sizasitha koma agogo akanena koma kusava lelo tikulika
Zoona
Koma Chisale anawalakwila chani anthuwa 💔🙌 koma munthu uja amusuza mokwana abale 😢
Chakwera tigomutumizira mphedzi watikwana.
❤❤❤❤❤❤
Enough is enough indeed. Si boma limeneli koma ndi gulu la zigawenga
Mbambande game changer
🎉🎉🎉
Paja ya smartmatic mwayisiya et mwavomeleza mukanatani boma ndi boma tazingobwebwetani anzanu Ali busy pa ground
Mau amenewo mr game changer Zikomo kwambiri
Mulibe nzeru a chisale ndalamazo adangwira ntchito yanji, mulonda ngati ine
Ndiye kuyankhula kokonda dziko uko..
Keep it up Mr Game changer..
Kodi iwo sadziwa kuti anthu ena ake anafa chifukwa cha Democracy???
Mumakwana mr game changer
Dziko likufunika anthu olingalira bho ngati inu Mr Game Changer
Chisary anayamba kugwila ntchito kare chakwera zakusiwika kut ndindani sizingateke kurandidwa ayi usalore nomar
Etini?
Umakwana game changer
kuyankula kwa nzeru anthu a mcp alibe zeru iwowa akuba kwambili ndipo chisale anayamba kalekare kugwira nchito
❤❤
Malawi adaola changamukani amalawi dziko ndi lanu.
Koditu khani zinazi tisalowetsepo ndale ngati anaba alandidwe basi
Zaziiii, kapolo uli mbuuu pamene ulipo. Waganyu iwe
Amadya kwanu. Iwe nde ndaninso
Inde Norman chisale ayenera kulandidwa katundu chifukwa sanapeze munjira yoyenera zoona munthu woti alibe even msce kulemera chonchi ,nanunso penapake mzikhala ndi manyaz kaputabuya iwe ungalimbane ndi boma olo khot
Uyu bola Habakuku amanena za zeru
Agalu ena akubawo sakulandidwa bwanji
Katundu wa chisale akodza dziko?
mcp ikufuna moyo wa boss Norman chisale basi bwanji osangomupheratu lusiyana kumadula chala kenako nkono nkhutu diso
Akungonama paja ena anamena kut matpaty ndi nkhondo
So anthu amangopeka zinthu kut wina awoneke oipa
Ndipo agalu awa atikwana mulungu achitapokanthu
Zamisarazo ndezitiso izi
Malamulo atsatilidwe
Kuba kowonekera and kopanda nako manyazi, MCP tsiku Lili mkudza Ana anu adzazunzika sure...
Dizoonazake amasuleni zintu zavutadi atizuza kwakwana ndipo mulungu awakate
No vote for MCP, Awa atiwonongela dziko lathu agalu ,Ang'ona a MCP. MICLE USI Stay away FROM UTM
Ttikungodikira alone Lilongwe t tikatenge chikwanje chodulira tombola wakuda ku ME c
Koma ndie kulintchito
Chisale amene ati agwire katundu wako ndikutenga alowe manda modzi modzi utenge number yanga ndikuuza koti upite ndipo akatenga usalimbane nawo ungosunga maina awo basi azasatana azayamba kubweretsa katunduyo okha kenako kupita modzi modzi manda enough is enough
Komadi abale zipindula chani zimenezo
Tikasintha boma tim'bwezela coz mukumulanda bcause of ndale but any way is the way how chikangawa doing
Boma lopusa Ili akhakhakha okha okha
Mungozipwetekesa kukhosi nonse ndinu anthu akuba nokha nokha tonend uko dzitsilu inu mcp 2025 boma
Akulu musowa chochita zolakhula zanu palibe chomwe tikuvapo,manganya adampatsa udindo wa u vice president ndi malemu chilima osati izi mulakhula zopanda nzeru.
Koma sizoona izi zopatsana katundu?
Kuyakhula kwabwino
Amwalira pophano andu a mcp ndioipha kwambili nde zomwe aziona ndi izi azimwalira modzi modzi na a mcp aziona ena ayamba kufa khale kwasala akuluakulu aboma
Chisale ndi mmalawi ndalamayo ziri Ku Malawi satar ndi obwera ndalama amaganizridwazo ziri kunja kodi ACB mmene amapanga Kaya mmati freez acc yake kodi inali mu dzina la ndani ndipo chinawapangisa kuti uku kwalowa ndalama za ku Army ndi chani awo mafunso ochokera kwa Mwalimu kachisi from Malaysia he is a Malawian amalankhulanso chichewa zomveka bwino kwambiri
Amulande ifeso tidzamulanda akadza ludza osadandaulula man chimwendo chityola chakwela nose paka nyumba dzanu ku aria 44 kuja tidzalanda
Ndiwe wasankho mlomwe iwe
Game changer afunseni kuti kod kapeni wawo azanamiza amalawi chani poti 2020 munanamiza amalawi olo chimodzi mwapanga ndiye lero game changer chikhuni cha usi wakufunsani achakwela achimwendo akunkuyu 😂😂😂😂😂😂😂😂 za manyazi
Big up mr Game changers,,mokupemphani ndithu plz plz Mr Game changer zaonetsetseni ndithu kuti a chipani cholamula asazabere zisankho ndithu.. achotsedwepo ndithu pa mpando
Lamuro lipotsadi mphamvu
😂
Aaaaaaa useless thinking