😂😂😂😂😂 zitheka bwanj bwanj kut mphavu yamagetsi ikhale yochepa ? Kod mesa mumat MCP inabwela kudzakonza mavuto including magetsi? So what is this? MCP pa 4 years palibe chimene yachita chanzeru chabe enanu mumangolankhula nkumayamikla MCP chifukwa chongotengela komwe mukichokera koma this is stupid party
Palibei chikuenda dziko muno,😊😊 tikungopempha Mulungu kt atipatse mvula yabwino kuti tzakolole zochuluka bs
🙏🙏🙏 ndipo zoonadi
my vote UDF mamuna asamandalile
kulu ai ❤ 🙏 🗳
UDF singawineso DPP ndiyimene itenge boma
Iwe kodi ukumaika mutu wa nkhani yoti mulibe mu video yako chifukwa chani ifetu si Ana ako wamva??
Migod imatipindulila chani Anthu Akuda opusa obeledwa masana
Kodi mukuti UDF izawina Kodi Atupere alipo ? Kapena muzasankha msogoleri wina?
Iwo a boma samadziwa kuti ku Malawi kulibe magetsi oti nkugwiritsa ntchito pa za migodi!, so ministry yimeneyi ikukungowononga ndalama gor nothing.
Dpp ikunyengererani kuti akuberekeni.
UDF matama ai pitani kumgwirisano plz painu nokha simusawins
Mwala imeneyo imapititsidwa,kunjako osati,kokayedza ayi,koma pa makhala nduna imaba mu njila imeneyo.boma,lililonse lalamulilapo malawi limaba mu njila imeneyi.
UDF yafotokoza bwino kwambiri gwilizano ulibe phidu kumangokhala kugwilisana ntchito basi Dpp idaononga chipani ichi
UDF sizalamulilaso dziko la Malawi
Za,katundu,muzingotseka ma shop basi.
madzi mokuti muyamba za chakudya munthu angakkhute madzi madzi alipo kale ambili
😂😂😂😂😂 zitheka bwanj bwanj kut mphavu yamagetsi ikhale yochepa ? Kod mesa mumat MCP inabwela kudzakonza mavuto including magetsi? So what is this? MCP pa 4 years palibe chimene yachita chanzeru chabe enanu mumangolankhula nkumayamikla MCP chifukwa chongotengela komwe mukichokera koma this is stupid party
Boma lolephela ili,chilichonse chasokonekera