BISHOP ZAKARIYA MTUKULA vs SH.MUSTAFA DAILESI

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 21 жов 2024
  • Ndi mwana uti yemwe anaperekedwa nsembe part 1

КОМЕНТАРІ • 32

  • @MarianoAly
    @MarianoAly 3 місяці тому

    Ambuye 😂😂😂😂😂 ndakondwa zedi yesu ndi fumudi yo chokera kwa ino.

  • @Amidu-g6c
    @Amidu-g6c 8 місяців тому +1

    Amen mustafa

  • @SaidiKaliyapa
    @SaidiKaliyapa 3 місяці тому

    Abusa kulongorora ndikumene akuziwa nanga zomwezi pakhatukhuta😂😂😂😂😂

  • @samsonmtumbati4855
    @samsonmtumbati4855 Рік тому +1

    From originally mwana woyamba ndi isake chifulkwa Ismail adabwadwira kwamkazi wantchito

  • @MarianoAly
    @MarianoAly 3 місяці тому

    Ndine osangalala kukhala mcristo 😂😂😂😂😂 amen.

  • @afritouch4660
    @afritouch4660 10 місяців тому

    Where’s part 2. Congratulations Bishop for proving Islam wrong. RIP

  • @yahyaabbie9795
    @yahyaabbie9795 4 роки тому +3

    Kodi pankhani yoti anapelekedwa nsembe ndi Isake kapena Ishmael muliphindu lanji kwa ife anthu?
    Funso limeneli atsogoleri athuwo sadatiyankhile

  • @adambakali1172
    @adambakali1172 Рік тому +2

    😂😂😂abusa kubisala mbatata ssana panja😂😂😂😂😂🤕

  • @SaidiKaliyapa
    @SaidiKaliyapa 3 місяці тому

    Chirungamosungabise abuzza kkkkkkkkkkkkk samanyazi

  • @SaidiKaliyapa
    @SaidiKaliyapa 3 місяці тому

    Ndineosangarala kukhala musilimuu

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 9 місяців тому

    Ishumael ndioyamba coz abrahmu anakagona ndi mzakazi cz sara anamakanika kubala.

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 10 місяців тому

    Abusa aboza amenewo mulungu awakang'anthe manda mene alimo pamozi ndiowasatila onse amene ali moyo ndikutanthawuza kuti akhristu nonse

  • @PaKayaEntertainment
    @PaKayaEntertainment Рік тому

    Kkkkkkkk proudly Christian

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 Рік тому +1

    ABUSA makani ngati mwatumidwa ndi SATANA.

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure Рік тому

      Mmmmm koma Abraham mumalakwira chifukwa sanali osutsana ndi mulungu

  • @AnthonyLushu
    @AnthonyLushu Місяць тому

    Amustafa mukuchulusa bozatu apa

  • @NoahKalima
    @NoahKalima Рік тому

    Abraham sanapemphe ismaeli ayi,pempho la Abraham linali kwankazi wake sara

  • @NoahKalima
    @NoahKalima Рік тому +1

    Koma asilamu paboza alibe manyazi

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd Рік тому

    Ntukula unali big....rest in internal peace.....

    • @AndersonBishop-i2t
      @AndersonBishop-i2t 10 місяців тому

      Pali chimene anayakha pamenepo mukuti ntukula wanuo mmmmm

  • @markbanda7434
    @markbanda7434 Рік тому

    Abusa a mtukula Rip mumatha kulalikila mawu a mulungu

    • @AndersonBishop-i2t
      @AndersonBishop-i2t 10 місяців тому

      Pamenepo analalikila akukanika kuyakhawo kod inu mumakacheza ku church ⛪kujatu et

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd Рік тому

    Malibe Zina la Ishmael mu verse imeneyi...Dayilesi akunama........

  • @MarianoAly
    @MarianoAly 3 місяці тому

    Chi islam ndi kusochela 😂😂😂😂ndi onamaso anthu ake zigololoso thopo mpaka ndawi yofunga mukalangidwa.

  • @Bobby265i4k
    @Bobby265i4k Рік тому +1

    abusawo sakuziwa chimene kurani ikunena

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure Рік тому

      Inu mulungu mum udziwe musanizidwe mulungu anadalitsa sarah ndi mbuye yake

  • @NoahKalima
    @NoahKalima Рік тому

    Koma kuchisilam kuli nkhungu losayamba,

  • @ishmaelamadu6425
    @ishmaelamadu6425 Рік тому

    Abusa akanika kuvomeleza kuti ishimaili ndi mwana weni weni wa Abraham abusa akukana Pati akanakhala kuti Mwana okaikitsa Mulungu sakanapelekako utumiki mbali yakumtundu wake abusa mwatani kodi

    • @GabrielJacintoRamussaneR-cp1kd
      @GabrielJacintoRamussaneR-cp1kd Рік тому

      Khani yakuku ndi Zina lanu?

    • @calebghama3213
      @calebghama3213 Рік тому +1

      Mwana wa lonjezo ndi Issac not Ishmael
      Ndichifukwa Mulungu sanatsutsana ndikuthamangitsidwa Kwa hagala chifukwa hagala sanali mkazi waubwana wa Abraham

  • @HashimKazembe-eq4yi
    @HashimKazembe-eq4yi Рік тому

    Ismail odetsedwa tigayile lemba

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd Рік тому

    Without doubt Islam is false.....