Mau oti dambwe meaning yake si chewa ai koma kt ndimalo ovalira gule kaya ndi angoni ,nsena ,muyawo,ndi ena otero antha kugwiritsa ntchito,choncho chihana sadalakwitse sanatchule mtundu wa achewa kuno Ku kanjedza Ku chileka ndabwe ilipo
@patrickisaacimbe mbuzi ndiwe chikukukomera ndichn with MCP mupanga support zinthu zot palibe kamene mwapezapo since adalowa kumangodandaura then u come ndiwe mbuz zoba 🤣🤣🤣🤣
Thus why timati mafumu azikhala a school, 14 million ayipeza kuti?? Akuthandauza kuti mitundu ina yonse ikugawana 6 million yosalayo??? Pitani kaye ku school komaso a Chihana sapepesa ok.
Chihana ameneyu ndi chindere. Iyeyu si Mtsogoleri wa chipani china chilichonse m'Dziko MUNO. Uyu ndi chabe MWANA wa munthu amene anali wa ndale, koma iyeyu sadziwa ndale zirizonse. Chimene amadziwa iyeyu ndi kunamiza azimayi ambirimbiri pa nkhani ya ukwati.
Achihana okhala Mtsogoleli sakuenela kulankhula mawu ogawanitsa ngati chonchi coz sionse omwe Ali mtundu wa Achewa alindi Mbali imodzi ya zipani please respect n no tribe attack
Amene mukuzitcha kuti ndi mafumu khalani kutali ndi zandale.Dambwe sintundu wa acchewa kodi mumachita matama bwanji?
Inenso ndi mchewa, koma sindili nawo mgulu lokhumudwitsidwalo, tionana pa 16 next year September
Kulibe mchewa angasangalare ndi mawu onyasa otere iwe sinchewa
Zazii what is that now?? Kumwamba kuli be zimenezo za chewa or tumbuka mkapsya nazo Kusatila zazii koma baible simukusatila mulungu akulangani
Kod mukufuna kuyambisa mikangano coz aliyense amayakhula zokhuza matribe onse bwanj enawo akanenedwa samakasuma bwanj? Alomwe samanenedwa musayambe zopusa apa aliyense akumva kuwawa
Mau oti dambwe meaning yake si chewa ai koma kt ndimalo ovalira gule kaya ndi angoni ,nsena ,muyawo,ndi ena otero antha kugwiritsa ntchito,choncho chihana sadalakwitse sanatchule mtundu wa achewa kuno Ku kanjedza Ku chileka ndabwe ilipo
Tell them my brother we are tired of mcp enough is enough
Aaaaaah Ife ndachewa sitidakhumudwe nao 💔💔. Zopusa izi
Ndiwe mbuzi
@patrickisaacimbe mbuzi ndiwe chikukukomera ndichn with MCP mupanga support zinthu zot palibe kamene mwapezapo since adalowa kumangodandaura then u come ndiwe mbuz zoba 🤣🤣🤣🤣
@JohnBandawe Uzilimbikira ntchito osati zolandira mchewa wabodza iwe
Osapepesa akapanga zopusa mitundu yose tikamenyane ndi achewa
Munamukhumba kale chihanayo, Inu si inu Mulungu ayi komaso mukunena chiwerengero chaboza
Anock chihana woyeee .......Enoch don't apologise please .....we are behind you my leader
Apepesa bwanji pamene anyamata aja anavala za Gule
Asatinamize zoti alipo 14 million amenewo
Achewa ndiwozikonda akufuna anthu tizaopa Malawi muno zisilu zawanthu
Zoonadi ayao timanyozedwa,so how special iwowo za zii
Chihana sadarakwe mwazitenga ngati dziko ndiranu kupepesa satumana
Uziwona apepesa ameneyo
Nkhumba Allah akupase chilango komaso azikupasa
That is nonsense achewa don't give up mr president chahana be strong 💪
Achewa alipo 14million anawauza ndani zimenezi
Inutu Achewa ngati mukuzitama tikwapuranapo ifeso Ayao timanyodzedwa but we are always strong like ONG, BACK
Inu musatinamize mwayiwala kt achita Rute ndi anthu ena akhala akukupepesan
Aaah za ziii. Akusowa poyambisira nkangano awaa!!
Tiyeni tiphane
Ife ndi achewa bwanji sitinakhumudwe😂😂😂😂 achewa ake onse ati
Mpaka mkutukana mtundu onse wachewa mphunzi choncho ndimtendere uu
Fokofu achewa atukwanidwa pati
Sapepesa achewawo ngati mulungu iwo adapepesapo ndani
Dr chihana mulungu akunva kuwawa kwamtima wanu musiyen mulungu akhale mulungu bas zotapana mkamwazo ife sizikutisangalatsa or pang'ono and mcp ndayamba kuitsatila tsopano pokhapa ndakutulukan zafika panyasi tsopano
Ineyo ndine mchewa koma nditankhala chihana sundigapepese zopusazo
Ngati ungafike 2025 O Allah m,pase chilango chakwela azafe
Watching from Mozambique
Aaaaaa apepese chiyani Dambwe ndye chyani zaziiii
Anaweremga ndani 14 million
Osapepesa aaaaaaa ....kodi ndabwe ndi ndabwe basi athu oipa awa timenya khondo basi
Ndawona Kuti achewanu mukufuna kuyambitsa khondo komanso mukufuna kumupha chihana eeeee mulekeletu zadbwe NDI ndale sizikugwirizana musiyeni Muthu ndiye poti ndinu athu oziwa kukhetsa mwazi chepetsani abale
Kk😂😂😂kkkk😂😂😂😂😂
Kudabwe ikhale khani 14 million achewa school yake yakuti
Achewa achewa achewa achewa Kodi ini mimazitenga ngati ziko mukulakwisa mvuto sogoleli wanu chakwela akukuyang-anilani koma ili ndiziko ichi chiwembu mukuyambachi
zachamba kupepesa kwachani 14 million ndiye kuti ku Malawi kulibe anthu
Dziko ramalawi zirazirombotu
Ine simnakhumudwe nawo mundichotsemo mu 14 million mo
Nawo achewawo alibe nzeru kusiya kumutenga nyani wawoyo amene akulephela kuyendesa dziko lino zoona akalimbane ndi munthu oti akudandaula ndi dzikoli likuyendela bwanji osadandaula za mavuto omwe ali dziko muno ashianah palibe chifukwa chopepesela pamenepo
Aaaaaa zopusa apepese chani zaiii
Nanga amene tili makaladife??
Thus why timati mafumu azikhala a school, 14 million ayipeza kuti?? Akuthandauza kuti mitundu ina yonse ikugawana 6 million yosalayo??? Pitani kaye ku school komaso a Chihana sapepesa ok.
This backlash will cost the opposition a lot of votes in the central region, mark my words.
Koma achewa musaname Kuti mulipo 14 million boza la nkhunkhuniza
Ndipo sanalakwise chihana akapangiled kudambwe asatiopye zachambabaaaasi
Komanso dziko lamawi pomwe likufikapa amalawi timanyozana mukati munyoze mtumbuka apa mumanyoza chikhalidwe chilichonse muno mmalawi chimanyozedwa ndiye dabwe likhale lopatulika kudusa onse? Koma chipepeso adye ndi angati mukunama tu, mukudziwa kuti dzina olo limenelo ndilogalukira mulungu kenako mukupitilizabe kumukhumudwisa mulungu popereka chilango chifukwa chazithu zomugalukira mulunguxo mkumazitama ndizimenezo kodi bwanji achihana ayime nji monga shadrick misheck and abedinego anayimira pamaso pa mulungu tione chomwe chicchitike
Chihana ameneyu ndi chindere. Iyeyu si Mtsogoleri wa chipani china chilichonse m'Dziko MUNO.
Uyu ndi chabe MWANA wa munthu amene anali wa ndale, koma iyeyu sadziwa ndale zirizonse. Chimene amadziwa iyeyu ndi kunamiza azimayi ambirimbiri pa nkhani ya ukwati.
Palibe achihana sangapepese ayi
.....achihana alakwa chiyani .....achewa ndi anthu opusa kwambili .....mwasowa choyankhulaveti
....ine ndikuti achihana asapepese ayi
..
Statistics ya 14meter akutenga kuti?
Achwea mukufuna kuyambisa nkhondo ngati malawi ndi wanu muona polekera
Apepese achewa Ngati ndani Mesa amecwo NDI achewa onse machende awo amenewo
Sakunama achihanao
Apepese nding'ombe cholinga amwere tiyi paja achewa amakonda tiyi,akumutola chihanayo chifukwa ndi ntumbuka akanakhala wachiyawo sakanapanga zimenezi olo kupereka matsiku
😂😂😂😂😂😂 koma ndaseka achewa aziwa zichita
Which means achewa onse amapita kudwambwe
Bodza palibe kupepesa,, enafe ndi achewa koma chakwera ndiye mwini
Ndipo ndizioon smatmatic agwilitse ntchito kudabwe ndipo asapepese
Kd achewa akudzimva kt dziko lino ndi lawo?
Ineso ndine mchewa koma zafikapa akutichititsa manyaz olamulawa
Pakuyankhapo ife palakwika mayankhulibwe koma basi kupepesa sikupusa tonse ndife amalawi
Ngati achewa ali 24million ndiye kuti mitundu yina yilipo yingati
Kodi akamati achewa alipo 14 million amatanthauza chani
Ine ndikuti kudambbwe komweko kumene
Iwo kuzimva kuopseza
Dambwe nchimodzimodzi mulungu wa barra.
Alipo 14 million onse akumalawi, Zambia kmso Mozambique
Aaa chihana apepetse Chyani adziiiii inu a MCP MUTSATIKWANE MWAMVA KUDZOLOWELA ULAMULILO WACHIPANI CHIMODZI BASI
Zaziiii.... Mmalo momathana ndi mavuto Tili nawo gule anali kale zauchitsilu😂😂😂
Aaaaaa zakuba basi cholinga mufuna mukamugumulile nyumba mukatelo ine ndi mchewa koma nyasi zomwe mmapanga agulenu msaname zimandinyasa mukatelo mwatumidwa cholinga anthu aziopa kupanga ma demo Kodi dzikoli ndilanu lokha anyau Inu umbuli simunasukusulebe kodi
Manyi amenewo palibe choti apepese pamenepo chakwera akuzuza mitundu ingat malawi muno bwanji sakupepesa
Ufulu watha kumalawi,malo oti dambwee is everywhere here in Malawi
Sanalakwose kodi anthu àmatamagisa ndi zikwaje ndimayesa ndi achewa omwewo
Mapwala anu achewa 😂😂😂😂😂😂 zisilu za anthu
Ndiwe otembeleredwa mwana wa mdelekezi mbamba
Kudambweko Kodi ndikumwamba? Achewa bwanji mukukulemekeza choncho?mpaka kumkwenya choncho Kuti apepese
Ndikuona ngati zopanda pake chifukwa anthuwa amanenana ngakhale mulhakho wakhala ukunenedwa palibe anatutumuka nanga awa bwanji munthu kungotchula ku dambwe basi zakalekale nthawi ya kamuzu zimenezo ya chipani chimozi mungoononga chabe mbili yanu pamenepo
Achihana okhala Mtsogoleli sakuenela kulankhula mawu ogawanitsa ngati chonchi coz sionse omwe Ali mtundu wa Achewa alindi Mbali imodzi ya zipani please respect n no tribe attack
Inu achewa mwakhala mukupanga zimenezo ndi mlako,lero poti chili kwa Inu.
Inuyo kudzimva chani??
Chihana more fire
It was a big mistake kuika MCP m'boma ndipo ikatuluka sizalowanso mpaka kale...... believe me
Hoooo zankutu,akapepesa nde aona kusintha chan? Zauchitsilu mwasowa choyankhura ndithu
Zausilu bas achewa iwo ndimulungu?
Apepese ndithu achihana ayiwala kuti kumalawi ndi dziko laathu amitundu yosiyanasiyana
Wachita bwino apepese zopusa anthu 14 million achoka kt ife tazikonda zomwe wayankhula chihanazo asamatubwe amenewa
Ndie chavuta ndichani akapepese zichani?
Ndekungodzudzula sizinakwane mpaka ngombe hiyaaaa Kodi dzikoli ndilaachewa lokha koma.achewa mwafikapo
Ineso Ndine mchewa Koma chihana sanalakwe anyawu akuwonjeza kwambili
❤🙏
Aaaaah 😂😂😂 kupepesachani
Sanayankhule bwino achihanawo
14 Marion achewa okha, Mfumu imeyo PAthako pake
Chihana ndiwe mtumbuka usagwiritsidwe ndi dpp more over ku northern region ulibe support
Ponda fadala ,, usamupase ndimupasa 😂😂😂😂
Palibe zimenezo m'busa wakumvamaujaso apepese tinazono achewa sangatipusise ife atumbuka achewatu tikhapanadi zezen chakachake nchino
Kumeneko ndkufuna kusokoneza mtundu wa aMalawi pogwiritsa ntchto mitundu nd ndale,zosafunika pa Malawi pano,izi.
achewa asipita kwawo ziamalawi ayi dambwedambwe ndichani zopuza
Pamtumbo panu achewa akupepesani nda manu
Palibe kupepesa, mudziwe kuti mwana otumbwa amatukwanisa makolo, ndiyeno khalani pansi ndi mwana wanu kapena ana anu alangizeni pa khalidwe loyipa
Akapepese chiani ndipo kuzikonda Kwa mtundu wanji kumeneku ndipo atumbukawotu sikuti sakukuvani kuzolowera kudya zaulele bwanji inunso mumatinyoza Ifeyo alomwe ndiye inuyo zakuwawani bwanji
Palibe zopepesa guys kudambwe kulibe gulu akuyenda ndiiiiii chakwera kumisokhano zopusa achewa kugona basses kuvala zibiya
Koma achewawa akufunadi Nkhondo ndaona
Mboliyake chakwera ndi achewa apepeze ndani
Ulamuliro wa nyawu sopano
Mudziwe malawi 🇲🇼 siwa ku Lilongwe
Nangaaaaa mufumu ijaaa inatiiii achewaa azavotereee muchewaaaa bwanjiiii
Smartmatic sikufunidwa full stop...
Zazi ineso ndine mchewa koma sindikuonapo nkhani apa ndipo sinakhumudwepo
Achewa panyo pamanu agalu inu kuzolowela kupembeza ziwanda bas
Aaaa zopusa bas apepese chan asapepese iiiyaaa zafodya bas