Nokha mwati khani izintha lorani chimphwanya abwerele pompanda chimphwanya saname sidzikukoma chifukwatu chimphwanya kungomuwona khope yokha maka makawa sewero limakhala lakwana i miss u mr chimphwanya ine Trevor ku cape town
guys ndimakufilani heavy especially Sasoka ndi Chiphwanya muli massive guys 😀😀 but where is Chiphwanya? watching from South Africa Pretoria. big up Flora and Sasoka hahaha ma director Inuyo mumatha. koma tikuwona kuchedwa combination ya Mfumukazi ndi Mdyangu Comedies 🤣🤣
@@laurynkaunjika8479 akuti samayankha phone , then he was busy kupanga zinthu zina nde samayankha phone , ndeno akuti anamupasa sas, ndeno apapa sizikukoma ada aja amatha koma inde timakonda mdyangu comedies Koma asamangochotsana sizikukoma mlelemba, sasoka, shoko shoko, chiphwanya , queen 👑, mercy , mdyangu big man , ndi ena nonse we love 💕 you guys make sure chiphwanya abwerele otherwise zitibvuta kusata izi guys
Heeheee koma Gani wandikomola ndikuseka kwabasi kkkkkkk kukana Mimba ya mkazi wake yemwe. 😂😂😂 koma mimba ya Queen akasowa osamala ndilela ine imeneyo😀😀😀😀ndawauza kale apongozi ake kuti pena zikayenda bwino tikhala ndi mwana🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Nkhani izitha,chimphanya abwelele basi(miss him)❤
Nokha mwati khani izintha lorani chimphwanya abwerele pompanda chimphwanya saname sidzikukoma chifukwatu chimphwanya kungomuwona khope yokha maka makawa sewero limakhala lakwana i miss u mr chimphwanya ine Trevor ku cape town
Kkkkkkk mr mulelemba ma mdyangu number one inu mumatha 😂😂😂😂
Ya week ino sinasangalase , please ya week yamawa chonde yesesani izakhaleko yobeba, timakukondani💕💖🤩😍
Kwavuta ku mdyangu ena anachosedwa chibelekero ena ayamba kulandila mimba😂😂😂😂😂 koma mumatimvesa kukoma big up
Video yosangalasa kwambili 🔥🔥🔥
Please ojambula musafookese ndithu😂😂
Mumathama gyz keep it up Maka mulelemba mayi favorite actor
😂😂😂mulelemba cyclone munyanyiwa,I think next kubeba,big up guys mmatimvesa kukoma watching from durban
guys ndimakufilani heavy especially Sasoka ndi Chiphwanya muli massive guys 😀😀 but where is Chiphwanya?
watching from South Africa Pretoria.
big up Flora and Sasoka hahaha ma director Inuyo mumatha.
koma tikuwona kuchedwa combination ya Mfumukazi ndi Mdyangu Comedies 🤣🤣
😂 😂 Mlelemba ndichiyabwe ndithu 🤣 🙌
Mukuitha guys koma tamusowa Chiphwanya pliz ❤
Mlelemba akati ayibongetse 🤣👐
❤❤much love from Cape town mdyangu team you are the best osaiwalanso Likiliki ladies keep it up to support Flora Suya Mulungu akudalitseninso
Gani aaaa ofoila kwabasi 😂😂😂😂 keep it up guys
guys chonde chonde tikufuna chiphyanya tamusowa kwambili chiphyanya love you guys ❤❤❤
Achokochoko akuziwapo kathu pa mimba ya queen amenewo nanga bwanji akukana kuti azipita😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkkk mulelemba akuti mumafuna wagalimoto chosecho mwapita kuphili Kodi galimoto ingafike kuphiliko ? Kapena mwina herkopita kkkkkkkk
Ahule awumuwa😅😅😅
Gani 2 double. Watengera bambo ake ameneyo. Team Mlelemba
😂😂😂😂😂mulelemba ndi sycron gan komaso ashokoshoko yakwera bp
Nice gaez,,, koma nde ngat kafupika bwanji kuli kusangalasidwa😂😂😂😂😂 nkhwini queen, moto bas
Kkkk Queen tchula mwini mimba,mapeto ake usokoneza Banja la sister wako 😂😂😂😂😂
A Ganizani akwatila ku Zambia 😆
Koma Mlelelmba ndi number 1
😅😅😅😅😂😂😂😂😂 eshiiiii koma mleremba ayi ndinthu
Shoko shoko kkkkkk
Yemweyoooo man gani 😂😂😂😂
Kd mwasiya kuonesa pa Times Tv
Huuuuuu ndikuonaso kutiso ashokoshoko adalowamo mwakwinimo akudaso nkhawa
We need chiphwanya back ,munthu amalakwitsa , osamakwiyilana ife timaikonda mdyangu comedies, palibe osalakwitsa , amene mwawabweresawo sapanga zachiphwanya , pliz pliz a suya m,bwereseni chiphwanya zinthu zikome izi , ❤❤❤❤❤ mdyangu comedies
What happened
Kodi analakwa chani chiphwanya?
@@laurynkaunjika8479 akuti samayankha phone , then he was busy kupanga zinthu zina nde samayankha phone , ndeno akuti anamupasa sas, ndeno apapa sizikukoma ada aja amatha koma inde timakonda mdyangu comedies Koma asamangochotsana sizikukoma mlelemba, sasoka, shoko shoko, chiphwanya , queen 👑, mercy , mdyangu big man , ndi ena nonse we love 💕 you guys make sure chiphwanya abwerele otherwise zitibvuta kusata izi guys
😂😂😂😂😂 Mimba imeneyo ndiya chokochoko
Nkhani ndi yamimba basi😂
😂😂 Queen di atha kukhala mfiti, aliphee! olo kuyankha kamodzi 😂😂😂 umatha adha
Shokoshoko akuopa 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Shoko sho
Mwanyanyuka tu😂😂😂😂😂 kod pa mudzi pano pali zotani
Mr shoprite from mfumukadzi, wabwera ngt coming atameta m'mbali mix chibwibwi next series kuli zinthu can't wait 🎉🎉🎉😅😅
Heeheee koma Gani wandikomola ndikuseka kwabasi kkkkkkk kukana Mimba ya mkazi wake yemwe. 😂😂😂 koma mimba ya Queen akasowa osamala ndilela ine imeneyo😀😀😀😀ndawauza kale apongozi ake kuti pena zikayenda bwino tikhala ndi mwana🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Cyclone munyanyiwa koma mulelemba🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂 tikudikila mwini wapeleka mimba tizamudziwe kkkkkk nice guys
Mapasa azimayi osiyana eti, kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ai zikomo!
Mumakwana
Flora please tikukupephani mukhululukilen chiphwanya akusowekela ndithu
Kmaso zipangakoni kakataliko pang'ono chonde
Kma kunena zoona mukumuika malawi pa map mukutivesaso kukoma athufe pitilizani ndithu
Chiphwanya anatani kodi
Mdyangu comedy excellent 👍👍
Koma mulelemba mpaka mercy ahule aumuwa kkkk
🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂😂Gani Mmalo mondikalipila mukusangalala
Kkk koma zomwe zitawaonekele achokochoko.tidikile kuti queen amutchula ndani.
Mimba ndi ya Gani
Mlelemba number 1
Kkkkk shokoshoko
Gani waziputa wekha osachulutsa mafunso😂😂😂
Miss chiphwanya , simukubebatu kopanda chiphwanya
Kkkkkkk km mulelemb adakoza
Mlelemba kkkk
Kkkkkk koma zilipo lipo
Best actors shokoshoko, chiphwanya and sasoka landilani Moni guys from Zomba chinamwali mumatha
Mwatichedweselatu, tayamba dzulo mmawa kudikila kkkkkk Queen ali bhoo amandiwaza ndakulu akewo😊
Mulelemba piliiiiiiiizxxxiiiii
Mai chokochoko mwana asachoke uyu
Pasavute.. Eunice bweretsa mimba kuno ku Lilongwe...ndizasunga mimba
kkkkk kod Munthu wamamuna amabooweka eti? kkkkk km Mulelemba mumatokwana
Mlelemba ndi katswiri
Mama Landlady acting yanu yatwa
Bring back Chiphwanya, nkhani yanji yosatha?
Yes tikufuna achiphyanya ❤❤
Mulelemba ni 😂😂😂 number 1
Best of malawi
koma chiphwanya abwerere ndithu tamusowa
Wakoleka Chokochoko
Makolo amasikwano chikondi kwana chinatha moti Muthu azimukalipila kuti wapeleka mimba 😂😂😂😂😂
Mlelemba amasokosa kwambiri mweee😢
Shokoshoko😅😂
Gani ndi dolo,koma ndikuwona kuti mimba ndiyopeka 😂
Mimba zavuta koma Shokoshoko wabalalika
Komanso kwabwera wa chibwibwi kwa Mercy akufuna children of Mkango
MayMdyangu umakwana ,Messe watitengera zotani ,Kodi unapana kapena 😅😅😅😅😅😅😅
Kaya ukuku kuphulika bomba 😅😅😅😅
Ganizani kuganiza kkkkkkkkk 😂
Umakwana 🙏
So funny really🕊📖.........✍
Comedy imene apatu chiyambileni apa nde yayamba kuphuzitsa
Game yavuta queen 😂😂😂
BTS
Queen 😭
❤❤❤❤
Zilikhenge km sindi mumpase moni
Oya babuwe, ukwapi chiphwanya Oya? Tamukumbuka Sana 😢
Koma sasoka umakwana 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chiphwanya abwera please
Cyclone munyanyiwa😅😅
Mulelemba umakwanira
Chipwanya wasowa kwambil
mapasa koma azimayi osiyana
Queen 😂😂😂
Shokoshoko 🤣🤣🤣🤣
Koma mkaxi Shokoshoko puma achepetse...Gani zikuonetsa kuti wagoletsa zigoli ziwiri nthawi imodzi..
A sasoka mwayamba kuseka azanu, mwayiwala inuso munalera ma twins pregnant osiyana azimayi😂😂😂 sikaletu lija hahaha😹
Koma sasoka
Season Yama pregnancy 😂😂😂😂
Kodi chiphyanya ali Kuti?
Ndipo inu