BAKILI MULUZI TV, LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA amanena chilungamo kuulula zonse mumabisa a MCP. Mchifukwa chake mukusegula nawo mmimba ndipo osawasiya anthu Oyipa Adyerawa Kuwayika poyera. Keep it up BMTV Keep it LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA You are loved ❤❤❤ever
@@FaysonChimbalanga Eya ndine kape Koma wa Smart opanda magazi mmanja. Ma Stroke ayamba kukubandulaniwo mudziwe Kuti Mulungu sakukondwera Mwazi wa anthu Munapha Ku Chikangawa 👹⚒️🔨🐊🐊👹 Judgement day is near,👹
Mbuzi za wanthu izi ife timakhulupilila bakili muluzi TV palibenso amene timakhulupilila kuposa bakili muluzi TV we love brother we're with you all the time or mukamaponya mavedio usiku timatsekula kuti timve basi boma lopusa limeneli
Bakili Muluzi TV is the best technical maniac kinda of a person that is why mbuli like Kumkuyu, Chimwendo, Chakwera Zikhale they won't understood him, he's a genius if they evens know what genius means
Ndipo ndikakhala ine nde ndaonjezela gear yokonda BKTV coz anatiuza za condition ya chakwera wanuyo with pure evidence nkono waku left uli weak zenizeni zija za munthu wa stroke. Ine nde sindikugwedezeka pa BKTV ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Akamathigidi mitu yodzadza ndi maminayo Don't back down brother you've ALMIGHTY watching your sincerely to your family and friends who mistreated by this so called chipiku guy Big up this is our TV whether they like it or not
Ubwino wake timaziwa chifukwa chimene amakudelan but b m tv we love you lot of people brother don't stop what you u did here Allah ndi amene azakupatse mtendele chifukwa mukuwachotsa amalawi pa mavut we know that
Ndipo ife tizikhulupilila bakili muludzi TV ndi Ena onse omwe kulankhula chilungamo ngt mukugona kuti anthu wa akumanama bwanji inu Osama bwela ndi chilungamo Cho bwanji kkkkk km gyz mwayaljka serious
MBUZI ZA NDUNA ANTHU OPUSA INU MUKUONANGATI MWAFIKAPO MUMVAKUWAWA , CHAKA CHA MAWA TORI NANU , SIMUNGAWAPEZE ANTHUWA MUDZAFERA KONKUNO AGALU INU MANYI ANU KONZANI DZIKO ANTHU AKUVUTIKA KATUNDU KUKWERA MWA DZINA LAKE
Ngat amakamba za boza inu nde zkukuwawan chan???
Nduna zompusa kwambiri,,,!!!
Malawi uyuyu si ujau wa ambuyanu uja👊👊 BKM TV... Forever!!!!!
Bakili Muluzi fans let's gather here 💯 💥
As malawi wa kumuzi I have added my trust on bakili mulizi tv because its where we finds the truth ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Kumkuyu ndiye mwakwanitsa kumugwira bakili muluzi tv yo😂😂😂😂😂 muchedwa nazo
Ife a mcp simungakwanitse kutichotsa chinkhulipiliro chathu pa Bakili Muluzi tv ndipo ife tili nga- nga-nga!! Pa mbuyo pa Bakili Muluzi tv ❤❤
History is the best teacher Aken zikhare Ng, oma muzuzika Nd kupanda dzelu kwanuko
I like this TV. Keep it up
I love Bakili muluzi tv
Bakili TV number one ❤
We need a 20 minute video boss
Ndipo izitalikadi
Ubwino wake nduna zonsezi nd ma top fan ako 🔥🔥🔥
Ndi omwe amawonela mwansanga enafe tisanafike
BAKILI MULUZI TV, LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA amanena chilungamo kuulula zonse mumabisa a MCP. Mchifukwa chake mukusegula nawo mmimba ndipo osawasiya anthu Oyipa Adyerawa Kuwayika poyera.
Keep it up BMTV
Keep it LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA
You are loved ❤❤❤ever
Ndiwe kape umakhulupirira mabodza awowo amati chakwela wamwalira zimenezo nzoona koma anthu inu mupepela naye bakili muluzi tv ndi mtanyiwa wanuyo
@@FaysonChimbalanga Eya ndine kape Koma wa Smart opanda magazi mmanja.
Ma Stroke ayamba kukubandulaniwo mudziwe Kuti Mulungu sakukondwera Mwazi wa anthu Munapha Ku Chikangawa
👹⚒️🔨🐊🐊👹
Judgement day is near,👹
Bodza lanu lomwe likukutsutsani
@@FaysonChimbalanga bakili sananenepo kut wadula aaaa mwagula lit phone kodo
Tamalembani zoti tiziwelenga bwino no sense
Bakili Muluzi Tv is the biggest television in Malawi for its accuracy
Bakili Muluzi Tv he's the best.❤❤❤
Zaziii zigawenga za a Malawi Mulungu achita nanu
Long live B.M tv❤
The history is the best teacher
Keep it up brothers bakili muluzi TV
Bakili muluziyooo ..sangawapezenso😂😂😂😂 mukachoka m'bomamo mumuona bakili muluzi TV pa msonkhano wa atolankhani😂😂❤❤
Respect to you bakil muluzi tv anaa achepa awaa sanawonere last video kt munakqmba kt chn pankhn yakufa kapen kudwal kwa chakwera ❤🎉
Inu ndi one big muthu samalimbana ndi muthu yemwe akunena zabodza 💪
Bakhili mulizi tv is forever is not go anywhere ❤
Bakili muluzi TV, it's where truth exists,,,mukhaula Inu a achikangawa party😂😂😂😂😂,, uyu akusasulani upto September 2025🎉😂😂😂😂😂
i love you bakili muluzi tv ulingat balle ukasowa nimadwala
First comment... Nduna zopepera / Zitsiru za nduna agalu eni eni ( Long Live BMTV❤️)
Bakili muluzi tv the best❤❤❤
Inu ndi one best tv ever
More love BMTV will continue love it.....
Mbuzi za wanthu izi ife timakhulupilila bakili muluzi TV palibenso amene timakhulupilila kuposa bakili muluzi TV we love brother we're with you all the time or mukamaponya mavedio usiku timatsekula kuti timve basi boma lopusa limeneli
Ana Anjoka amenewa kuposa fiti zazikaz
We are believe on your speech bro kp it up💪💪
Bakili Muluzi TV is the best technical maniac kinda of a person that is why mbuli like Kumkuyu, Chimwendo, Chakwera Zikhale they won't understood him, he's a genius if they evens know what genius means
History is the best teacher, inuyo ngat ndinu achilungamo tulutsani black box komwe ili??
ngakhale athu oyipa atachuluka motani mulungu amapeleke anthu ena opanda dyela kuti adzawayimilile basi so we prod of you never give up 🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤
Ndipo ndikakhala ine nde ndaonjezela gear yokonda BKTV coz anatiuza za condition ya chakwera wanuyo with pure evidence nkono waku left uli weak zenizeni zija za munthu wa stroke. Ine nde sindikugwedezeka pa BKTV ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Tiyen nawo tigwetsa mbuz zimenezo 🔥
Brother man keep it up!!
We love you bra, please why we can't find the old history like for osama and other did you delete boss
Akamathigidi mitu yodzadza ndi maminayo
Don't back down brother you've ALMIGHTY watching your sincerely to your family and friends who mistreated by this so called chipiku guy
Big up this is our TV whether they like it or not
History is the best teacher
Bakili muluzi TV 💯 umakwana palibesowina amene ndi ngamukhulupilire ndi bakili muluzi TV bas AMALAWI osofowoka
As Zambian I added my comment on bakili muluzi tv because is where we find the whole truth
Big up bosss❤❤❤
Bakili muluzi ndi mbambande😂😂😂❤
Mmalo mochita zinthu zopindulira amalawi akufuna kulimabana ndi bakili TV 😢 ....ulesi anthuwa alibe
Zitsilu izi za MCP zidazowela nkhanza, kupha basi. Brother mulungu akufungatile, zoona zokha zokha zomwe mukunena.
Kkkkkkkkkk koma inuy gys aaaaaaaa ndinu mbambande gys
Iyeso kunkuyu ndi chimwendo naoso ali busy
Ndi bakili mz tv
Ilibooooooo bakili muluzi tv
Ndasangalala poti nawoso amavela bakili muluzi TV 😂😂😂😂😂😂aziziwa kuti zitsitsi zawo athu amaziziwa
The best TV in Malawi
Bakili muluzi amayakhula chilungamo ifeyo sitisiya kuvela bakili muluzi tv amatisekula munthu
Ubwino wake timaziwa chifukwa chimene amakudelan but b m tv we love you lot of people brother don't stop what you u did here Allah ndi amene azakupatse mtendele chifukwa mukuwachotsa amalawi pa mavut we know that
anali ndi cholinga chothetsa bakili tv km ife sizinatigwedeze chilungamo chili bm tv we you forever❤❤❤❤❤❤❤
Bmuluzitv that man is not alier (siwabodza) I will be with him always and pray with him (mdima umadana nikuunika )
MCP Chipani Chakupha Chazifwamba, Moses Kunkuyu anapha Allan witika, Chakwera Anapha Chilima
Zisilu izi mbuzi za anthu awa ...ifeyo bakili muluzi tv ndiye timaikonda koopsa
Best TV madhala
I love bakili muluzi tv inuyo mumalìzè nkhani ya chilima ija mwayiwaĺa kodi
We love you bakili muluzi tv no one can stop me to follow you
It's only best TV bakili muluzi TV idabwela kunzankhala mbava nzamcp
BAKILI MULUZI TV INSPIRING THE NATIONS
More fire wa BK TV
The best tv in Malawi my God protect you my brother
Ndipo ndavomereza Nduna nazo zimatchera Bakili Muluzi tv new video....amavera ndithu
True 😂😂😂😂
Straight kkkkkk kunkuyu ndi chimwendo kkkkkkk bakili muluzi tv kkkkkkk this is for real
😢Bakili muluzi tv ❤❤❤❤❤💯💯💯💯💯💯💢💛
We are always with you
Zandisangalatsa kwambiri achina chimwendo ndi team yawo nawo akumamvelanso TV yathu yapamwambayi BMT kuti wooow
Kunkuyu chimwendo Banda pamtumbo pamanu😂😂
Bakili Muluzi Tv the eye opener, I used to hate History in school
😂😂 Bakili Muluzi Tv forever 🤝✊✊
Apa pamene akupangila bakili tv kutchuka coz athu akumudzi ena samadziwa nw ayamba kufufuza kuti ayambe kuva zambiri kuti amanena zotani 😂😂😂
Osafooka 😂let's go we can do it together
Ndipo ife tizikhulupilila bakili muludzi TV ndi Ena onse omwe kulankhula chilungamo ngt mukugona kuti anthu wa akumanama bwanji inu Osama bwela ndi chilungamo Cho bwanji kkkkk km gyz mwayaljka serious
Koma abale malawi dziko lovesa chison b m tv my best tv❤❤❤
Kod ana anja afa njala ndiboza zoona tiyeni tinene zoona amalawi awatu mukuwasekerelawa alemera kare oro utafa alibe nawe ntchito mwamuona joyce banda mtima wachikondi ndi anthu kugawa chimanga mwaonako kumene kunja Mr banda akupangq akolobqtiki amalawi amalawi amalawi ndanena kangati nonse qmene zikukusangalasani mulungu akukhulukire kod fetereza wa 4 pin unja alikwa ndinenq inu muoba manja inu
Keep informing us our real comrades though ifeyo sitikupangapo kanthu olo titamva dandawuro langa pokhapo ine zimandikhuza 😔😔😔
MBAMBANDE BAKILI MULUZI tv true
Zikundisangalasa kuti amanvela, Bm TV
Ndipo Apa apangisa kuti osatila Bm TV achuluka
Timadziwa kuti mtengo omwe uli ndizipatso ndiumene umagendedwa chilungamo chimabaya MCP ikupumila mkhwapa chifukwa cha BMT 😅😅😅😅
Power bro
Inu Bakili Muluzu amapanga zonvekaa. Bwanji Witika uja unamupweteka ujayo 😢😅
I'm with bakili TV
NGAKHALE NDUNA ZA BOMA ZIMANYADILA ZIKAMAMVELA BAKILI MULUZI TV
PAMBUYO PANU BIG MAN
Bakili tv stay blessed where ever you are,we love you 💜 all the time ❤❤❤
Bakili TV Comrade Ntanyiwa born kalindo akukhaulisani a mcp cz ndima advocate a anthufe cz amakuuzani chilungamo ndipo sasiya aii
More fire big man
We love you BKLTV
Umakwana brother samagona nawe tulo komaso ndizoona zomwe umakamba komaso amamvera
Apule tulutsani mau😂😂😂😂😂,sitisiya ife bundle timagula tokha fonnso ndizathu palibe kutipangila zochita
Bakili more fire 🔥🔥🔥 wina alila ndima Jackson akewo bm tv timayikonda
Anthu sitingasiye kukukhurupirila asy keep it up
Kani ndunazi zimadikiranso update ya Bakili Muluzi TV?, kkk
Viva BMTV, we love you nigga,and no one will pluck from us the trust we have on. You
Nd u na zimenezi ndie zitsiru...the whole government body kulimbana ndi BM TV ..Kupusa
Tiripano tcheru kunverainu BMT❤❤
Ngati a bro bakili muluzi muli aboza tiwonera myenda njira samantha five days asanayende mukamva ziiii kwa five days mungoziwa kuti mavuto alipo
Up big 😊
Watching from KATETE ZAMBIA
❤❤BAKILI❤❤MULUZI❤❤TV❤❤
Ife tikufuna umboni ndithu kod ife tidzinamizidwa ndi mcp mmmm kwa wo ndi Kuba ndi kupha
Bakili Muluzi tv exposes your crimes
MBUZI ZA NDUNA ANTHU OPUSA INU MUKUONANGATI MWAFIKAPO MUMVAKUWAWA , CHAKA CHA MAWA TORI NANU , SIMUNGAWAPEZE ANTHUWA MUDZAFERA KONKUNO AGALU INU MANYI ANU KONZANI DZIKO ANTHU AKUVUTIKA KATUNDU KUKWERA MWA DZINA LAKE
Ndinu nokha big man
Big man ndinu bakili muluzi TV