EVANCE watsopano MELEKA UFUMU OLEPHERA MALAWI OFFICIAL VIDEO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 жов 2024
  • EVANCE watsopano MELEKA UFUMU OLEPHERA MALAWI OFFICIAL VIDEO
    Find out more: / @malawimusictv

КОМЕНТАРІ • 24

  • @paulnkhama3621
    @paulnkhama3621 2 роки тому +1

    Nyimboyi muyimbeso chakwera Nayeso wafoyila

  • @EsnartChiundila
    @EsnartChiundila 8 місяців тому

    Pitilizani kuwelenga mau ndipo mu mau muli mphamvu, kulimbikitsa zabwino zonse 🙏

  • @lowrancekayona3081
    @lowrancekayona3081 4 роки тому +1

    Malawi akubowoleza mawu Basi Achina mtambo Trapenz anasankha kusagwadila fano ngati Daus ndi anzake mpaka mulungu ananva kuti akukana kugwadila fano lelo ndizo.

  • @kassimyatolayatola8394
    @kassimyatolayatola8394 4 роки тому +2

    Iwe ndioyimba sizokakamiza just keep it up

  • @domingosportimao6622
    @domingosportimao6622 4 роки тому +1

    Kuno ku mizambique tilinawe meleka.umatisagakatsa.Portimao ,zumbu

  • @lowrancekayona3081
    @lowrancekayona3081 4 роки тому +1

    Mdima kudana ndikuwunika, lankhulani Mr meleka siyinu koma It was written in a Bible

  • @Lloyd-gd6pu
    @Lloyd-gd6pu 19 днів тому

    Komatu ntengo wake ukufunika chainsaw coz zikwanjezi ndiye utha kudzagwa mochedwa

  • @selemannyirongo5360
    @selemannyirongo5360 4 роки тому +1

    Sono Nebugadineza aliku malawi sazamva ayi peter muthalika

  • @eltonmaseya6511
    @eltonmaseya6511 4 роки тому +1

    Meleka uli fire u are my best

  • @moyo77777
    @moyo77777 4 роки тому +2

    ndimakukonda bro

  • @lowrancekayona3081
    @lowrancekayona3081 4 роки тому +1

    Madala?🗣️🗣️ Kodi coronayu mungomusiya choncho tikudikilatu 🏋️

  • @wilsonlowore5140
    @wilsonlowore5140 4 роки тому +1

    Nice Guys

  • @priscainnocent7197
    @priscainnocent7197 4 роки тому +1

    chulungamo ndichofunikadi

  • @stanleydamalekani7113
    @stanleydamalekani7113 4 роки тому +1

    Absolutely brother:)

  • @baldwinmunkhondya4070
    @baldwinmunkhondya4070 4 роки тому +1

    Zimbabwe

  • @memorymbepula3772
    @memorymbepula3772 4 роки тому +1

    Chilungamo chimamasula