Nkhani Masana | 3 JANUARY 2025

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 13

  • @JafarWiati
    @JafarWiati День тому +1

    Kulela wachani muzidyesa anawo ndiinu zopusa basi anawo mulungu alinawo zochita inuyo muzibeleka enawo azipha ana awo aaaa

  • @CharliePaulelic
    @CharliePaulelic День тому +1

    Achakwera ndi galu kwabasi

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms День тому +2

    Ngakhale wasakha nduna zimenezi aluzabe chakwe palibe

    • @FranksonKennethChipande
      @FranksonKennethChipande День тому

      Osaneneratu Chakwera Sali yekha ziwani zimenezo.Winning election is about numbers.The one who get more numbers will carry the day

  • @MphatsoLuka-gn3lr
    @MphatsoLuka-gn3lr День тому

    Umafuna azipha anawo

  • @OsmanPatrick
    @OsmanPatrick День тому

    Kulera wa chani Mene akuvutikira anthumo akuwapasa chakudya ndi ndani mulungu yekha ndi amene amasala Moyo wa anthu

  • @MphatsoLuka-gn3lr
    @MphatsoLuka-gn3lr День тому

    UkanabadwA anakakhala mayi ako kuti amwe makwala akurela

  • @RafickAlie-i5m
    @RafickAlie-i5m День тому

    Amayi anu bwanji sanatenge kulela kut inuyo musabadwe pasana pako

  • @AlicksonMakata
    @AlicksonMakata День тому

    Amuthalika akunama akunena zimenezi chifukwa alikunja kwa boma.

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u День тому

      Galu wa nchira nde iweyo, kudali kuti 2014-2020?zinthu zidafika apa??? Achakwera chidebe chopanda nzeru ngati iweyo mboli yakonso ndi a Chakwera akowo galu

    • @AlicksonMakata
      @AlicksonMakata День тому

      Nthawi ya Dpp maunivesity amapanga ma strike koma lero ayi ,magesi amathima thima albino amasowa ndipo ndi chipani cha kochi chikagwere uko sitikuchifuna ife chathu ndi mcp boma ufune usafune mcp ndi boma basi

    • @AlicksonMakata
      @AlicksonMakata День тому

      @LastonMmanga-r2u ufune usafune mcp ndi boma la bwino munthawi ya dpp timamwa zithaphwi kunalibe cĥitetezo malbino amasowa maunivesity amapanga mastrike koma lero kulibe..

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u День тому

      @@AlicksonMakata boma la MCP???? 🤔 Amalawi sakulora zopusa izi anthu akupha chilima cz kufuna udindo ozunza anthu, lero chitetezo chili kutiko adzikwanje mpaka kunyumba ya MA sisiteli?? Sindine obwera kuti wina angandinamize za Chakwera and inuyo mufune musafune Adad akubwelera ku state house, thumba la chimanga mu mbiri ya dziko sichinafikepo k20, 000 koma lero ngati amalima ndi ku America k60.000 mmmmmm ngakhale inu mumakhuta nthawi ya Peter koma lero mulu ndi njala ndichifukwa chake mitu yanu yabalalika Iya!!!!