koma inu mukuti uyu ndi busa 😂😂😂😂😂 chilima Ali kuti nanga miya Ali kuti 😂😂😂 busa amakhala ndi nkhope ngati ya chakwela komatu mupite ku church mukalape
Kwatu ku zomb ndikunenapano anthu ochuluk kuphatikizap azigogo athu anatengel ma ID number ao kwauza kt fertirizer yemwe amafuna kugul ma ID awo sakupang scan ndy akuyenel kutenga ma ID awo akaunik bwno ndp anthu ochuluk anapelek pofuna kut apez fertirizer
The DC CHITSANKHO ICHI ANTHU OTSALEMBETSA NDE VUTE YANJI OTSUSA AKULEKELE KWAMBILU CHISADZO ANTHU AKUGULA MA ID AKADZIWIKA KUMANGOWAGENDA AFELE POPO BASI CHIFUKWA ATIYIKA MAMVUTOSO 2025 MCP IPHA ANTHU
Iam following boss the DC, imeneyi ndi kugwa kwa MCP mpaka next generation
Kaswiri kwambili DC woyeeeeeee ❤❤❤❤❤🎉😂❤
The DC preach the gospel 🎉
DC ur amazing guy keep it up
Kwachanso ikugwa friday
I proud of you mr dc
Chakwera is worse but APM of DPP is the worst due to his age .
Words 😄
Aid from china miseu yopatsidwa ndiponso nthawi ya peter wamutharika chakwela munthu omvetsa chisoni
Mumatiimilira Big up
Big Big thanks awuzeni agalu amenewa
Zikanakhala bwino atamugendanso Usi.
Wanditopetsa ameneuja
Wawa DC timakufilani❤❤❤
koma inu mukuti uyu ndi busa 😂😂😂😂😂 chilima Ali kuti nanga miya Ali kuti 😂😂😂 busa amakhala ndi nkhope ngati ya chakwela komatu mupite ku church mukalape
Big up biggy🎉🎉🎉
Amalawi chonde asatipusise chikangawa azachoka ndikupita kundende uyu ndigaru kwabasi
😂😂😂 fada chilungamo chawawa
Osafooka,osatopa kabambe boma nyamata odziwa ,ife nganganga pambuyo pa kabambe ndi machine
Ulemu wanu bwana DC. Yemwe ali ndi makutu akumva, amve
😂😂😂😂kanaolera pansalu kanga kanga😅😅😅inuyo anakonza
Go deeper!! Mr DC
anthu atopa ndikunamizidwa inu andale ndi anthu oyipa kwambili kunamidza mtundu wa amalawi mukunama kwambili pano anthu anazindikila musatione ngati ife tili mtulo ayi muyiwale
Kwatu ku zomb ndikunenapano anthu ochuluk kuphatikizap azigogo athu anatengel ma ID number ao kwauza kt fertirizer yemwe amafuna kugul ma ID awo sakupang scan ndy akuyenel kutenga ma ID awo akaunik bwno ndp anthu ochuluk anapelek pofuna kut apez fertirizer
😂😂😂😂😂che ndani? Koma winiko usandiseketse😂
The DC
Mmatiimira bwana mulungu akupaseni Moyo wautali osawopa osafooka
The DC CHITSANKHO ICHI ANTHU OTSALEMBETSA NDE VUTE YANJI OTSUSA AKULEKELE KWAMBILU CHISADZO ANTHU AKUGULA MA ID AKADZIWIKA KUMANGOWAGENDA AFELE POPO BASI CHIFUKWA ATIYIKA MAMVUTOSO 2025 MCP IPHA ANTHU
Mwati instinki???🤣🤣🤣
Kkkkk ulemu wanu Dc
More fire bon
Mumakwanira amoya kung'alula mopanda chigamba.
Kom mwakalembesa??
Umakwana😊
Koma mr Chikangawa eeeeish
😂kwavutaaa
Mulungu wathu chonde kodi dziko la Malawi 🇲🇼 likupita kut chonde ngat kuli kutiweruza plz tikhululukireni
Nifuna niiimenekha😂😂
Kalindo is on DPP payroll- all perks including ganja.
amuchita bwino
@ hahahaha
Abwana zikafa apa zavuta
Ulemu wanu boss
Kkkkkk ipatse fire
Awuzeni kuti ndi Aid ya china chifukwa mbulizina sidzikudziwa
Mulomwe uyu amakwana awuzen avese
Umskwana bon kalindo
DC followers
Boooon Kalindo mwana ooopsya kwambiri
Mumakhwana kwambiri big
Following
Mbambande inuo ndi 1🫡🫡🫡💞💞💞
Zoonadi sitikukufuna chikangawa iweyo udzingopitatu kudambwe galu kwa basi kkkk
Thanks so much for your help Malawias Mr president kalindo
Mwati bwanji apa mwatipindatu man
The dc ndifuseko kodi kafukufuku wandege aripati
Akuti ali kati kufufuza
Mbambande 💯
Mulungu dalisan dziko la Malawi
Umakwana bro
Smartmatic ichoke basi
Musatinamize Wawa zitukuko zambiri zimene zimachitika mdziko lino zimakhala aided ndiye ngati Malawi akulandira zithandizo zambiri nchifukwa Cha utsogoleri wabwino wa Dr Chakwera.Inu kapepheni kwa bodyguard uja billionaire amene ndalama zake adabera agogo Iwo akugona chifukwa Cha ukalamba
Nanu chakwera wake uti mukufuna kumvesa nzimu chison eti
Iwe Garu kwabasi,tamuthamangisa dzulo kuno kwa chinsapo
Inu ndinu opusa, ndinu amozi ofuna kugwesa dziko lathu,satana akusekani maso
Km munthu wazeru zake angavotereso DPP?????
Foolish you
Akhalise
Machine mumakwana big
Mumakwana
instinki 😅😅😅😅
I believe it is instinct .
The Dc✊✊❤
Tiuzeni zambiri.
Komatu umayankhula zooonaa zokhazokha
Muchedwa nazo izi mzanu wama drama akudya ndalama.Mufune musafune 2025 Dr Chakwera boma
Kwanu komko
Akalindo manyazi mulibe,mesa inu mudalipo muboma la Dpp,mudachitapo chiani?or za aid mudalandilapo mudachitapo chiani?anthu atopa nanu chifukwa zomwe mulakhula ndizopanda nzeru, nchifukwa chake sizikuyendelani,kagwilani ganyu amenewu,ndipo ntchito muitha yopanda tsogolo.
You are not serious Mr . You mean kuti dziko likuyenda bwino?
The dc
Zoonad kunoks.akungt mubwerb mafom.atha zambr.zikuctk.anthu.akungobwerl km.ulend.ndie.achoka.bas
Kutiko
anthu atopa ndikunamizidwa inu andale ndi anthu oyipa kwambili kunamidza mtundu wa amalawi mukunama kwambili pano anthu anazindikila musatione ngati ife tili mtulo ayi muyiwale
The DC