Atsogoleri ozikonda nde ali kuMalawi choyankhulira chingerezi chikhale chani ? Inu nkhani yoopsa ngati yoti dziko likufuna kudziwa ndikumva chilungamo momveka bwino basi busy busy ndi English ya form 4yo 😮 inu ndi anthu osaganiiza report tizalimva 2025 osati zopusazi
Ozopusa basi rest well SKC😭😭😭😭
2025 September 16 lipotr lisatuluka libwino nosenuutamangidwa chakwera chimwendo maiko usi
Kod makape inu pali ena samava chizungu wy osalankhula mchichewa
Chokambira chizungu chili chani ngati amalawi ndi azungu mukuona ngati ndi onse omwe angamve zomwe mukuyankhurazi Mmmmm ayi zikomo
Imfa ya Bishop Mkasa Zuza inapangitsa kuti PAC ikhale ilibe mano. Bishop Thawale mbusa kukhala mu gulu ngati ili mhuuuuu!!! Mulungu akhudzeni anthu awa achimve ndithu mu mitima yawo.
@@TonyMhone exactly 💯 pakanakhara zuza apa bwezi ndizina apa
Report tizapanga 2025 not limenero ayi iro ndilanu a mcp not Malawian fake report
Ziko ili likuyendesedwa ndi chisilu cha munthu .....chakwera sakufunidwa ndi anthu ochukuluka.......apapa report mukunamiza anthu omwe mukufuna kuti akuvoteleni .
Komatu zimene mukuganizazo sizitheka .......achakwera awononga Malawi .....tangoganizani katundu akukwera tsiku ndi tsiku malipilo ndi omweo akale ......anthu akumuzi ndiye Ali pamavuto azaoneni .......chakwera azipita basi sakufunikanso ayi
Inu ziwanthu zoipa inu bwanji simukulankhula zichewa?
Mukundinyasa mutasiyanso kulankhulako
Zitichitila ubwino,
mukutiphyesa mitima
Ngati mukutinamiza mukayankha nokha kwa Mulungu popeza tonse tikudikila imfa
Yachabe yakutesya chanasa achalume walunda lwawo iisyene lunduwa kupikanila adisinjo
Noseni Mulungu akuyendeleni ndipo mumanyumba mwanumo ndinu oyipa mitima palibe za report apo muzawona Chaka cha mawa Chakwela adzamangidwadi
MULUNGU onse amaboza ndi mabanja awo omwe this yr before 2025
anthu nonse mwapanga kafukufuku nthawi ikubwela muzayakha kwa Yehova ubwino wake mwakalamba kale muzaziona
KOMA NDALAMA ZABOMA NDIZOKOMA MPAKANA KUIWALA CHILUNGAMO EEEE PAKUT ATHUENA MUMAT KUMWAMBA KULIBE MULUNGU ZIKHALE MOMO MUZADZIWA CHIKUMBUMTIMA CHIZAKUPEZANI ZIKOMO
Koma kayini ndiabeli anaphana pachibale ndipo mulungu ana tembelela wakupha azalima sazakolola samalani ana anjoka inu
Koma ndalama, anthu ophunzira bwinobwino kulepheranso ku mitulusa a credible report. Kulephera kuyankha mafunso ufunikila.
Atsogoleri ozikonda nde ali kuMalawi choyankhulira chingerezi chikhale chani ? Inu nkhani yoopsa ngati yoti dziko likufuna kudziwa ndikumva chilungamo momveka bwino basi busy busy ndi English ya form 4yo 😮 inu ndi anthu osaganiiza report tizalimva 2025 osati zopusazi
Kunama koyamba kufotokoza mu English language cholinga asamve ambiri palibe apa 0%
Witches
Pamkholo panu ndi liport lanu labozalo zausiru afiti inu
No sence