Skefa, Nkuwo umenewu wamvekera kutali amwene. Keep on doing great things for humanity. Inuyo anakonza. May you be blessed in your work. Band yanu ijanso ndi mwala, achina Yesaya and Cossam Bowa.
If this song has reached Zambia am sure it has already reach the higher authorities of Malawi please hear people's cry through this song 🇿🇲 love you skeffa
Akatelo akufunaso ayambe ndale...please Malawians do what you are best suited for osangoti mukatchuka kujoina ndale basi..tikuononga dziko chifukwa chongofuna kudzikhutilitsa ndi Chuma...komabe this is a very good song to awaken the govt.
Skeffa the Jamming Machine Chimoto. Big man receive your flowers🎉🎉🎉 whilst alive, may Allah continue brighten your music career Boss. I love you and your music. ❤❤
Kuyamba kumva Skeffa kuimba something political apapa something is not going well pa Malawi. MCP must revive what Kamuzu used to do to make Malawi great again in development osati nkhanza
Sorry my big brother😢 for political motivated I really crying for u... A good example look at Billy Kaunda 😅 ankatekesa zikolonse as u r now but politics now he is just a history
The true Malawian son with great artistically song and powerful message. Here is your flowers🎉🎉❤🇲🇼🔥
Uku nde Timati Kukuwa Mwanzeru 🔥🔥🔥
Loving you Mr 🎉🎉🎉🎉🎉🎉 Inu ndinu katundu mwakuwa big love your voice ndibwela kudzavota ndikalephela mapemphello afika muwina
Shaaa ma units nga chipongwe. Luso ili nlochokeradi Kwa Namalenga. Keep it up!
True son of the soil. Apa ndiye watikuwira ambiri
Skefa, Nkuwo umenewu wamvekera kutali amwene. Keep on doing great things for humanity. Inuyo anakonza. May you be blessed in your work. Band yanu ijanso ndi mwala, achina Yesaya and Cossam Bowa.
If this song has reached Zambia am sure it has already reach the higher authorities of Malawi please hear people's cry through this song 🇿🇲 love you skeffa
❤❤❤ Inuyo big mumatha ndipo nyimbo zanu zimapeleka chilimbikitso ulemu wanu ❤
❤ lunso lina eeee ayi skefa uthenga wapelekedwa ,always be blessed and win forever,
😄😄😄😄 202... aimila u MP akuluwa, akatumikire anthu akwao.
Good composition.
Koma maunitsi ashhh...pamenepo mungodziwa kuti akunena za 2025 coz kulibeso 202..... wina kutsogoloku afta 25 kuli 203.....Pitani mukaimire basi anthu akudalirani💯
Skeffa ndimunthu wamkulu he knows how to articulate words
Direct message to the president!! Ngati amamva amva ndithu.... skeffa my vote...
This is great song,Skeffa apa nde mwakuwa zanzeru and ngat mungayime u Mp tidzakuvotelani ndithu.Unabwera kudzakhala
Born talented n blessed guy
This song got tangible n legit infor
Akatelo akufunaso ayambe ndale...please Malawians do what you are best suited for osangoti mukatchuka kujoina ndale basi..tikuononga dziko chifukwa chongofuna kudzikhutilitsa ndi Chuma...komabe this is a very good song to awaken the govt.
True
Father of real music
Kuilowa bwino kampeni bwana shadow. I hope ndizomwe mudzawachitire anthu aku Nkhotakota south West
These emotions shud stay awake.if he feels that way everyday ,He will deliver.Wishing him all the best
True definition of citizenship 😊
🎉🎉🎉🎉 beautiful song by skeffa ❤❤
Skeffa the Jamming Machine Chimoto. Big man receive your flowers🎉🎉🎉 whilst alive, may Allah continue brighten your music career Boss. I love you and your music. ❤❤
A shadow mwatiyimilira🔥🔥🇲🇼
Skeffa sumakhumudwisa,muli uthenga 🔥🔥🔥🔥
You are really good musician with massage of people of Malawi thanks 🙏🙏👍 yr music God bless you and continue for yr love 💕
Koma ichichi boiz eeh respect
God bless you skefa umatiimilila kip on fire 🔥
Kumwamba kulandire ulemu,Bwana uthenga I'm sure wawapeza,so touching yoooo
Mulungu azipitilizabe kukudalitsani bwana ... This is not just a song it's also a savior anthem to the people in the country 🙏🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mumatha kwambiri inuyo ndi Katswiriiii popeka nyimbo
Skeffa si munthu wamba 😅.
Ati kuli vimachani 😅😅😅🔥✌️
Mumatha inuyo 🔥🔥
Receive your frowers🎉Skeffa
continue doing the needful for us great work man
we are proud to have u
Thumbs up our own musician
The king of Malawi
Big up Mr mwakuwa
Mwawina kale.... Nkhotakota south east mwatenga basi
202.... Ma units anathera pompo
An encouraging song Big up Skeffa
Nice songs am following you up Skeffa keep it up watching from Zambia
Nyimbo iyi ndiyakwathu...Big up Skeffa ..Mawu amveka
Great work Skeffa, welcome back home🔥🔥🔥🔥
I like the creativity 🤙
Mnyimbo ya bwino..muli uthenga umu
Kuyamba kumva Skeffa kuimba something political apapa something is not going well pa Malawi.
MCP must revive what Kamuzu used to do to make Malawi great again in development osati nkhanza
Kukuwa mwachiukulu❤
Great man❤
Powerful skeffa
Powerful message 🎉
Original talent❤
🔥🔥🔥🔥🔥
Munthu uyu amafila mlaka maliro
Campaign yatheka basi. Contest against Skeffa at your own risk..
I will comment mosaonetsa kutopa.... most talented ♥️♥️🔥🔥🔥
Chaka cha 2020 faaaah😂😂😂❤❤❤
Uthenga uwemi nadi, but mwachedwa 💔
Abwana uthenga wawapeza
🔥🔥
Malawi imeneyo, kuli ntchito
Mukukamba monyengerela mukanangosiya
Nyimbo zanu ndimazipeza
🎉my big skeffa nice song
Real music 💣
Big kwambiri Skeffa himself 🔥🔥
Luso losachita kukakamiza , inuyo ndi 1
Mwalankhura bwino fadah🔥🔥
Hahahahahah koma chaka cha 2025 kayimeni mwavomera basi kkkkk
Ndava chisoni ndi uthenga uli umu ,mavuto alipo ambiri
Nice message , inuyo mumatha , mwatuimila Ku nkhotakota keep up
Eeeh madala inuyo
Legend🎉
Skeffa umatha,
The message is clear, bwana aimila awa
Akulu nyimbo iyi muli uthenga wa mizimu yambili.mkuwowu awapeze ndthu bwanawo😢
Sorry my big brother😢 for political motivated
I really crying for u...
A good example look at Billy Kaunda 😅 ankatekesa zikolonse as u r now but politics now he is just a history
Nice madala
It's true my legend even here in Zambia things are not okay
Imwe mesa zambia said you are better
Mabvuto siyaona nkhope m'bale wanga@@hamiltonlemilton7322
@@hamiltonlemilton7322things are worse than before but better than Malawi😢😢
That's what we expected
Skeffa nice mmmmm apa mwamenya eeeshi
Machine that never disappoints
Skefa kuyambira kale amatchuka ndi nyimbo zaudzimu zachikondi za chilimbikiso ndipo aka ndikoyamba kuyimba nyimbo yodandaulira president.ndipo nfundo ziri munyimboyi palibe kuonjedzera kapena kupungula koma chomwe tingakambe ndi CHOTI mavuto amenewa Ali dziko lonse chofunika iweyo chakwera umvese komanso uchite kanthu iweyo longwe ndi munlo sizoona momwe liliri dziko lamalawi nkumati kuli chimanga ukuganidza bwanji sibwino chakwera kumubisira mawu koma kumuudza chirungamo kuti akulu siziri bwino aziziwa 😂😂😂😂😂.
Koditu uthenga ulim'menemu ndiongofuna kukuuzani kuti àkuyamba ndale ndipo 2025 akaimira kudera lakwaoko .....
@@talimilejosephmakawa4967 ok
202.....Boma!!!!!
Nice but us artist you need include all district there pass sutiation..
Skefa , mmmm amatha, osati zokakamiza
Owoo 2025 mukuimila et
Powerful 🔥🔥🔥
👏👏🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Word....
Koma skeffa chimoto mmmmm mbambande heve
Wakulu mumatha bambande
Eeeeeeeeee km skeffa iweyo chonena ndilibe ndiyambira pati
Tapangen tag izizi zingofunika Avere changu
❤❤❤
Big up🔥🔥🔥
Kunyadila kwa amalawi
Sizongogweramo izi koma zomati akubadwa lusoso nalo linali litabadwa kale umandiwaza skefa
Koma skeffa guys🎉🎉🎉🎉
Manifesto machine
Born a genius
Tikuvotelani yimani nawo
Anabadwa ndi luso palibeso kuchitira mwina amwenewa ndi dolo ulemu wanu kaka
#Skeffa Mitunda 🔥🔥
Hahaha sir mwatiyimirira pa neef Po km kwinako kayimeni boss zabwino zooonse kuno ku BT😅😅😅😅😅