KOMA BOMA ILI ABALE ~NKHANI YAMA ID IJATU YAMUSALIRA CHAPONDA ~ PARLIAMENT YAMUKANILA OPANDA UMBONI

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 91

  • @KestherMkandawire
    @KestherMkandawire 3 дні тому +6

    Ukakhala wakuba umaona ngati aliyese ndiwakuba amalawi saiwala chimanga chomwe unabq chqponda.

  • @GeorgeKaluwa
    @GeorgeKaluwa 2 дні тому +2

    Mcp boma 2030 woooo

  • @DerlinNyirenda
    @DerlinNyirenda 3 дні тому +3

    MCP oyeeeeee

  • @AgnesNjikho
    @AgnesNjikho 3 дні тому +5

    Osafulumila kunena kt muoneke abwino kwa anthu izo rero zikufunika umboni awoneseso kt awonese munthu yomwe anakayikako zinthuzo

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 2 дні тому +1

      Nanu umboni wake utiwo akufuna apa. Ndipo mcp ikutidoda akuchita ku madzi wa kut a Malawi ndi Ma bulutu

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 3 дні тому +2

    Inu adpp udf utm aford mukugona kwambili

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu 3 дні тому +6

    Mwenye uja asakupeperetseni a Chaponda

  • @frankbanda7333
    @frankbanda7333 3 дні тому +2

    Ayi sunamufere mumanja mulungu apeleka umboni

  • @JohnMwale-q8z
    @JohnMwale-q8z 3 дні тому +2

    Fever of elections in opposition

  • @AusteenSumael
    @AusteenSumael 3 дні тому

    Which umbon,?

  • @JohnMwale-q8z
    @JohnMwale-q8z 3 дні тому +2

    Sleeping opposition in Malawi

  • @ChikumbutsoTsalangu
    @ChikumbutsoTsalangu 3 дні тому +2

    Speak sakhala wa chipani

    • @RosinaPatel
      @RosinaPatel 3 дні тому

      Speaker akakhala wa rulling party?

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 3 дні тому

      ​@@RosinaPatelamakondera

    • @ChikumbutsoTsalangu
      @ChikumbutsoTsalangu 3 дні тому

      @@BrightZionga Ndipo live bwedzi aku mapedza anthu o ziwa ma lamulo oyima pa okha

  • @EvansEgra
    @EvansEgra 3 дні тому +2

    Chaponda anaba chimanga uyu, chisiru chamuthu, wosamasewera ndi boma ai

  • @SamuelBotolo
    @SamuelBotolo 3 дні тому +2

    Phuma

  • @BusaGaniza
    @BusaGaniza 3 дні тому +3

    Kodi umboni uponse pa zimene zaonekazo Amalawi dyela lidzatipha mukufuna kusangalatsa ndani akakhala chakwela akupita kukasiya mufune musafune

    • @DesireMoyo-y8x
      @DesireMoyo-y8x 3 дні тому +1

      Vuto lake achisiru unapaka chifukwa mkufuna zomwe mwafuma ndi zomwe zizichitika

    • @GiftBello-v1i
      @GiftBello-v1i 3 години тому

      Aaaa sanaione ndi ndani ?

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani Годину тому

    Sapereka umboni musiyen Chaponda mulimbane ndneyo ndpo ngt kuli kufa ndfe ndineyo case closed

  • @samsonmtumbati4855
    @samsonmtumbati4855 3 дні тому +1

    Zopangana izi kuti awoneke ndiwosalakwa don't worry guys tomorrow is coming

  • @CardoJustin-l7m
    @CardoJustin-l7m 3 дні тому +1

    Umboni wanjinso zinthu zoti dziko lonse laona

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 2 дні тому +1

    anthu osutsa ali ndi vuto boza kwambir fundo alibe km maboza bas guys perekan maomboni muva ukweche achaponda 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 3 дні тому +2

    Opposition yongona iyi tsete

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 2 дні тому

      Koma kukula konseko mungamalembe zimenezi???? Zipatseni ulemu

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 2 дні тому

      @ShamilahSaizi vuto lako ndi chani phone ndi yako

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani Годину тому

      Sister pliz usamalimbane ndi ana asatana pliz ss love u so much dzitalikise kutali ndi asatana nthawi yatha enawa akuona ngt pamanda pawo padzalembedwa MCP ndye kuti akalowa kwa Mulungu​@@ShamilahSaizi

  • @JohnKayila
    @JohnKayila 3 дні тому

    Ndiwe chitsiru which backfire?

  • @StephanoIssah
    @StephanoIssah 3 дні тому +2

    Umbon Ndiokut malo ameneaja ndii osungila chimanga not ma ID n amakatani kkkk manyi amenewo ife ayiii

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 дні тому

    Akufuna umboni wanji agalu wose wooo ngati ndikosungura ma id nanga malaputopu amapanga chani kumenekuja

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 дні тому

    Wumboni ndiwoti NRB yimayani kunyumba yosungira chimanga ndi ma ID

  • @KumbukaniZgambo-xd9tm
    @KumbukaniZgambo-xd9tm День тому

    Komatu mukunama umboni tawuwona kale olo mutapangana

  • @TchumaKanyemba
    @TchumaKanyemba 3 дні тому +1

    Mcp ikunamatu ikupamgazo

  • @chifundochalowa5323
    @chifundochalowa5323 2 дні тому

    Before evidence you supposed to find out what happened there,Mr sikala. nanga atakupatsani evidence yabodza? Mudzadziwa bwanji kuti ndiyoona kapena Ayi. Coz kumaloko simunapiteko kukaona kuti chachitika ndichani? Chimwendo akuti Phuma iyeyo anapitako ?

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 3 дні тому

    A GEORGE CHAPONDA SADZIWA KUPANGA MFUNDO ZOTSUMIKIZA .KOMA ANAKAKHALA DALITSO KABAMBE OLO SAMEER SULEMAN OR NORMAN CHISALE CONVINCINGLY

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani Годину тому

    China chimangolimban ndi opposition ukhalira yomweyo garu iwee umbon wake akufuna utiwo zaziii kukakamira znthu zoti zakukanikan hehehehehehe mukalamul ndikumanda kkmwe

  • @FunnyKalimwayi
    @FunnyKalimwayi 2 дні тому

    panya panu abanda kumene kuja sikosungila ma ID munya

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 дні тому

    Kazombo sikutitu iweyo wchita kutsika kumwambatu umakhala ndiukali ndi opposition bwanji osakhala pa neutral bwanji

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 3 дні тому

    Kodi umboni wake akufuna wamtundu bwanji? Kodi mipando ndima gadget amakapangako chani? Ndazonso zimakasungidwa?

  • @feliciajohn6041
    @feliciajohn6041 3 дні тому

    Dzisilu za MCP agalu

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 3 дні тому

    Umboni ndi woti bwanji a NRB sanauze otsutsa kuti akupanga ma id ku kanengo?

  • @ThomasJohn-d9r
    @ThomasJohn-d9r 3 години тому

    Umboni otani si zamuyayatu izi

  • @SalatiKiddie
    @SalatiKiddie 3 дні тому

    Ndipo ife sitikulola umboni ilipo anthu aziwona ndimaso komaso malo amene anja ndiwosungira chimanga

  • @chifundochalowa5323
    @chifundochalowa5323 2 дні тому

    MCP chikuwakhudzq ndichani zaku NRB? Chimwendo amandibowa, komanso speaker asamakhale wachipani

  • @MorrisMapiri-o4k
    @MorrisMapiri-o4k 3 дні тому

    Anthuwo awapeza ndi ma printing machines, so what kind of evidence does ruling party want?, this is nothing else but intimidation to the rights and democracy.

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  3 дні тому

      No, there were no printing machines. Just computers and scanners. Ndi pamene umboni wavutila, Chifukwa achina Chaponda akuti NRB imachita print, koma printer munalibe, nde nkhani yavuta pamenepo
      Mukanakhala printer zinali za straight forward

  • @JoiceChisambi
    @JoiceChisambi 2 дні тому

    Mukufuna umboni wachi zithu zawoneks ndimaso

  • @GitfIobodo
    @GitfIobodo 2 дні тому

    Komatu munu mmalawi mkhala nkhondo tiphana magazi ku magazi

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 3 дні тому

    Chimwendo kodi phuma la amako?

  • @SebastianSauwa
    @SebastianSauwa 2 дні тому

    Akamati phuma silabwino akutanthauza chani?? Izi sidzamuntthu mmodzi ndi MEC and NRB.Ayiniake ndi aMalawi what ever is happening aMalawi eniake adzidziwa china chilichotse kuti asamutsa office kupita uku.Kuti anthu asamadabwe.Why hidding things? Remember black box ijainasowa bwanji.what evidence are u waiting for????

  • @KennedyKManda
    @KennedyKManda 3 дні тому

    Aboma chikuwakhudza ndichani pamenepo akukakamila NRB yileme office zawo kuti akapangile kobisika?

  • @DumisanPhiri
    @DumisanPhiri 2 дні тому

    😂😂😂😂 chaponda mwapanga mwa panga bwanji apa nde akugwesanisotu

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 3 дні тому

    Mafumu..chimwendo akutenga ma id awanthu ndikumagawa ndalama

  • @ibrahimmumba
    @ibrahimmumba 2 дні тому

    Wakuba ndi wakuba bansi

  • @KelvinBanda-s1s
    @KelvinBanda-s1s 3 дні тому

    President ndi chakwera enanu mukufuna mukabe musiyen mzanu apitilize mission bas

  • @tonnexScott
    @tonnexScott 3 дні тому

    A Chimwendo mumandibowa kwambiri

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 3 дні тому

    I think wina akutamba kumeneko zoona mukanikiranji ma vidio ali paliponse adzulo and u Mr sipikala usamankhale ndi mbali mache.....ako pati

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO 3 дні тому

    Speaker wa MCP uyu!!! Apart from the evidence there is also need of an explanation of what is happening there. Dont rash to evidence yet everyone saw those gadgets for both photographing, printing yet claimed to be for solting 😡😡

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 3 дні тому

    Umboni ndi womwe Uja zinajambulidya zija

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 3 дні тому

    Ukamafuna kulanda nkazi mwaphuma zimakupatsa mavuto adpp phuma kaya ndikukalamba kaya

  • @JoyLuwanika
    @JoyLuwanika 2 дні тому

    Mulungu akudalitseni anthu mukuwadzuzatu

  • @GibsonBankha
    @GibsonBankha 2 дні тому

    Kkkk koma makadeti ya bpp kkkk

  • @EvansEgra
    @EvansEgra 3 дні тому

    Zitsiru mbuli, agalu a opposition, maka Dpp

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 3 дні тому

    Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxidwa pa ifa ya chilima

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 3 дні тому

    Umboni ulipo zija taona zija nde umbonio

  • @MikeMsamalaphiri
    @MikeMsamalaphiri 3 дні тому

    What evidence?
    They say they were using the hall for sorting IDs kodi mesa sorting amapanga ndi manja?
    Nanga ma camera amachitako chani???
    The PRESENCE of cameras is a real evidence of theft period..
    Cameras are supposed to be found in centers where people's faces are captured..
    Why do you want to compromise straight forward things?
    Malawians are not fools.
    We are taking you out mcp

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  3 дні тому

      Kkkkkk zilikotu chaka chino

  • @GiftMuyungu
    @GiftMuyungu 3 дні тому

    Achimwendo ndi nonse amcp mulibe manyazi kwanu mkupha kuba komaso kuwononga ntchito zasatana zagona mwainu koma kumwambaku kuli mulungu muzaziwona

  • @tasmania527
    @tasmania527 3 дні тому

    Akuti DPP ndi system koma system yake yofoiraso, yikugwedezeka. Ma leaders a system akupangaso phuma, akukhala ndi mantha oluza zisankho, nde udolo wake uli pati?kkkkk. Gone are the days when DPP used to steal elections. This is the new era of sanity, VIVA MALAWI!

  • @SalatiKiddie
    @SalatiKiddie 3 дні тому

    agalu amcp awa ndipo tikoma ndipo popano

  • @FunnyKalimwayi
    @FunnyKalimwayi 2 дні тому

    ayalukabe k

  • @KennedyKManda
    @KennedyKManda 3 дні тому

    Chimwendo Mboli yamako

    • @EvansEgra
      @EvansEgra 3 дні тому

      Ukhalira zimenezo

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 3 дні тому

      ​@EvansEgra kodi iwe kape why you are busy attacking others iweyo kwanuko zilibwino mavuto akulilitsa amalawi iweyo zako zilibwino shame on you

    • @EvansEgra
      @EvansEgra 2 дні тому

      @BrightZionga I fight my slf, sindimayang'ana zisiru za ndale ine ai

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 2 дні тому

      Chikangawa son, ngt mukudya nawo za zipereganyo muzingokhala chete osati muziziwonetsa ngt inuo a nzeru apa

    • @GibsonBankha
      @GibsonBankha 2 дні тому +1

      Kazilimbikilancito osamangotukwana azitsogoleli kkk

  • @AmosiChauluka
    @AmosiChauluka 3 дні тому +1

    Koma chimwendo iweyo uzazuzitsa banjalako