God is good always! Ndine mboni 😢😢 kupita kumudzi its not a solution ndi mmene akunenera kut kwao mkuvitika, since 2012 ntchito tinayamba kugwira 2020,and si ntchito wamba yomwe tinapedza, zosatheka ndife zimatheka ndi Mulungu, pemphero ndi pembedzero limasitha nyengo osafooka, we will help you,but God will help you permanently! God bless you my brother spie pix.tiyakhulane ku wap
@@SleepySakura-qe8un it depends nd tchito yomwe mukugwila. Pamene enafe or mwana wa 2 years sitingamutenge ku tchito working place yake mwana akhoza kudwala
Osataya mtima anthu a Mulungu, 2022 ndi pompano, nyengo Za munthu sizisintha pompopompo, amuna ndi munthu wachikondi kwambiri coz nthawi yomwe anapeza ndalama anakonza dongosolo loti mupite komwe ali cholinga mudzionela limodzi. A Malawi omwe mulikumeneko ndi udindo wanu kutengapo mbali/ chithandizo Kwa family iyi/ ntchito/maganyu kwa amuna awo.
Nyengo iliyose ili ndi malire chachikondi inu mayi Mai ndi amuna Anu mukhale kupemphero isataya mtima nkhuluta I kuti mulungu amasintha nyengo ngakhale zingalibe bwanji lilirani pa dzina lake azakudalitsani. Ambuye akuchitireni chifundo.
Mulungu amakonza njila that's why anapeleka nzakeyu kuti azimuthandiza so Mulungu ali mma plan okhazikika ku family yake Mulungu akudaliseni nonse kumeneko
Coming back home is not a solution. Kunonso anathawa mavuto. Time changes and this shall be history. Mulungu anayambira pamene ife tathodwa ndi kulephera. Be prayerful.
Ndiumboni Mulungu azakusinthiran nyengo ndiy ena akunena zoti akuberekeranji sizikgwilizana ai munthandizen ntchito basi
God is good always! Ndine mboni 😢😢 kupita kumudzi its not a solution ndi mmene akunenera kut kwao mkuvitika, since 2012 ntchito tinayamba kugwira 2020,and si ntchito wamba yomwe tinapedza, zosatheka ndife zimatheka ndi Mulungu, pemphero ndi pembedzero limasitha nyengo osafooka, we will help you,but God will help you permanently! God bless you my brother spie pix.tiyakhulane ku wap
Zangovuta kumudzikonso ndiye ayi bolanso komwekuno Mulungu awasogolera amunawo ntchito azayamba
Ndi bwino ayambe abwelera ku mudzi mayiwo chifukwa pano ndi chipsyinjo kwa ena. Amuna awo akadzapeza ntchito yokhazikika adzapite.
God bless you Mr Spie pix and my blood Sister Sister Edda
Home is home no matter how humble.Watching from Zambia.
anthu ena macoment onyoza ..just imagine iweyo ukugwila ntchito upeza ndalama but supita kumuzi means we know kuti malawi pano salibwino what about munthu oti angokhala ..plus aluti mayi ake ndiopeza movutika ...Mulungu alowelelepo ..kwa omwe mukukamba zoti bwezi akulera osabeleka mwana .mwana amapeleka Mulungu ndicholinga ...
Umenewo ndiye moyo dziko lililonse kulimavuto kungolimbikila basi chauta apasa olimbika
Mawu mawu amphanvu zedi uwu ndie umunthu ❤❤
@@StellaCharmerPenatu anthu amayesetsa komanso amalumbikira komano nthaka ndikumawakanabe Stella mmm
Kusitha Dera sikulemela Koma kusitha kavutikidwe
Akungofunika kuwapezela tchito amuna awo ku South Africa komweko coz mayiwo sangagwile tchito ndimwanayo
Ife tikugwira bwanji mwana Wakhanda
@@SleepySakura-qe8un it depends nd tchito yomwe mukugwila. Pamene enafe or mwana wa 2 years sitingamutenge ku tchito working place yake mwana akhoza kudwala
Mmmm koma Mulungu apanga njila. Zomvesa chison
Nkhan apasiren transport azibwera kumudzi kuno ena kuno akulima moyo ukuyenda
Ndipo mawu abwino kwambili uphawi supha anakula bwanji hiyaaa
Big up Spiepix.. God will provide may God bless you..
Mamvuto Allah bless him
God Bless you Dolo Wakwathu
Chiyambi sichophweka only God knows tomorrow
Osataya mtima anthu a Mulungu, 2022 ndi pompano, nyengo Za munthu sizisintha pompopompo, amuna ndi munthu wachikondi kwambiri coz nthawi yomwe anapeza ndalama anakonza dongosolo loti mupite komwe ali cholinga mudzionela limodzi. A Malawi omwe mulikumeneko ndi udindo wanu kutengapo mbali/ chithandizo Kwa family iyi/ ntchito/maganyu kwa amuna awo.
Yehova osintha nyengo akuyendere m'bale wanga ndipo usadandaule Mulungu akuthandiza ndiwazantheka bwanji,
Azipita ku Malawi not kupanga business kuno ayi, ngati ndalama ipedzeke kungowapasa azikathamanga kumalawi.
Iiiiiii uphawi sumapha bwerelanu ku mudzi kwanu kwanu
Kubwerera kymudzi basi ndipo simudzachi5a manyazi Mukwonago muli penapake
Come back home and start farming... Home is best. The more you stay there, the more you will be suffering
Mulungu NDI mayankho tsiku Lina udzakhala umboni sister wanga nthawi yoyikika ikubwela NGAKHALE nyengo zathina usaiwale kuyamika Mulungu muzonse
Kuopa kupita kumudzi ndimene ziliri kunoku or atayamba business mukuona kuti zingayende bolatu kumudzi umakhala mwaufulu
It's better kuwapezera zochita komko cos kunoso ku Malawi moyo azauva kulimba mix alibe poyambira ndizovutabe akhale komko koma athandizen ntchito
Mulungu ndiwadongosolo umenewo ndi umboni wanu mamie pamawa
Ambuye alowelelepo kwa. Thuthu
Moyo ndi ovuta paliponse kujonz zimavuta pena ziyende km nkhani iyiy yovuta kwambri vuto mwana alima
Nyengo iliyonse imakhala ndi mathero,Mulungu si munthu ayi
Nyengo iliyose ili ndi malire chachikondi inu mayi Mai ndi amuna Anu mukhale kupemphero isataya mtima nkhuluta I kuti mulungu amasintha nyengo ngakhale zingalibe bwanji lilirani pa dzina lake azakudalitsani. Ambuye akuchitireni chifundo.
Koma ndchisilu ameneyi galu bwanji osabwela kumalawi
Koma ndithokoze Mamunayochikondi chomuyitanitsa mkazi wake analinacho
Mwana ndi mphatso sizikugwilizana mwanayo antha kuzawagwila pa mkono komanso mulungu salakwisa alinawo cholinga anthuwo osamaweluza kuweluza ndikwake kwamulungu
She must go home than to say l don't want to go home is best sis
Kwanumkwanu mayiwa akanangopempha thandizo lobwerera kumudzi
Mulungu amakonza njila that's why anapeleka nzakeyu kuti azimuthandiza so Mulungu ali mma plan okhazikika ku family yake Mulungu akudaliseni nonse kumeneko
Amai bwererani kumudzi kwanumkwanu, musafere khunkha ngati nyani okuthandizaniwo kenako atopa.
Coming back home is not a solution. Kunonso anathawa mavuto. Time changes and this shall be history. Mulungu anayambira pamene ife tathodwa ndi kulephera. Be prayerful.
Vuto ndilakuti anthuwo akukhala Ku cape town anakakhala xoti akukhalira mu joberg muno ndiyekuti ndinakawathandiza powapezela chochita ndicholinga asazapemphetso thandizo kwawathuena I mean ineyo kupezela wathu zochita limenelo silikhala vuto bola osasokoneza.ngati mulinawo number abambowo tipaseniko
Number ndikuona Ngati ili pompo pamwambapo.
Mulungu awaone ndithu
May Allah bless them 🙏
Muziona south africa malawi ndiokongolatu
God time is best God knows osataya chikhulupiliro
Ambuye akhale thandizo mmm
Abwelele ku malawi basi than kukhala komko
Nde Akana kumudzi pomwe akuvutika amalawi mwatani kwathu kwathu kovutika indee koma kunoso muvutika the best way kupitq kumudzi mama😊
Sister musataye mtima inenso ndadutsanso muzimene mukudutsamo inumo komano Mulungu wandidalitsa chifukwa chake ndi kuti Mulungu akukumbukireni ameni
Ineso ndadutsa ndithu adziyenda makomo kusaka manganyu ochapa
Osangobwera ku Malawi kuno
Muziphika magwinya
East or west home is the best bwelelani ku mudzi kuno kwa eni kudyetsa mthanga dzungu ukuli wona
Kwambiri big,ine ndimanena kuti kwathu ngakhale kuli kosauka koma ndimalukonda kwambiri ndipo sindingakukane
@@lifredchikumba420 nde bolanso nthanga Za dzungu lakunoli kumalawi maungu onse aoleratu baba🤑
Amuna ake ndi achikondi zithu zikuwamvuta koma anaitanisa mkadzi... Mulungu akuze malire azimayi uyo amagulira ana mapampao.
Mayi, there's no better place like home.just go home and try other things umphawi siupha munthu..
Chakwera waonongerako kuno angabwereko Ndi ndani bro?😢😢😢
@@RiteRoderick tonse tayeserako kumudziko m'bale akuyhawa ma profenals omwe...kumangothandizana ndikumapemphelerana bas zonse ndi mulungu
Akapeza ndlama azibwera ku Malawi Bola azivutikila kwao
Iwe mbuzi bwanji kupepha transport yobwelela
Bwerani pa home mamabefore being stranded and worsy
No where no safe,,,akuKana kubwelela kwawo
Athandizeni awo abwerere kwao
Zoona bola kumudzi kwanu ndi kwanu
Chimen adakachita mayi adakapita kumudzi kae
Mai mubwelele ku Malawi
Osati business koma azipita kumudzi
Just come to Malawi
Mulungu atichitire chifundo
Chiyawo adakonza proud to be a Yao
Mmmm koma ndiye zosayendatu Dunoon mbali yake iti
Koma nyengo Zina abale MMM Mulungu awathandize ndithu
Ndakunyadilani a Spie pix tv pitilizani zomwe mukuchitazi zikutisuntha ndithu
igot her point ....nkhani yolilisa
Kodi ukakhala pa mabvuto ndie kt tisamabeleke chifukwa ndife ovutika
Mmmmm zosayendatu kwambiri
Ndinayesa kukuimbirani phone kuti mubwere muzawatengere zomvala zoti atha kugulisa kutheka zingawathandize koma inuyo simunayankhe call 4 times
Anapanga chiganizo chabwino kutenga banja lake koma pamene zavuta nkazi abwelere kumudzi bamboyo azitolere Kaye. Kwanu sikuyipa akweni!!!
Ingobweran kumudzi
Dzosayenda kwambili tikuyesa koma siikuitan sir
Apaseni ndalama akengi namwi imwi mmmmm mutitinyazisa
Bola mayi akanabwelela kumudzi atsale Amunawo 🤔
Mayiwa asakane kubwerera kumudzi kuno kumalawi,mulungu sanyozeka.zithu zinamulungu amagoona chikhulupiriro chanu. Mulungu azasithira nyengo zanu mwina kokuno kumalawi. Mau anga kwa amalawi tamuoneni mwenye amabwera kuno kumalawi ku chokera ku dziko la kwawo opanda ndarama,koma amakhala kuti wasiyako kazi komwe akuchokerako,koma samamuuza kuti abwere muno m'malawi akayamba ntchito ndi kumalandila ma makwacha amawasitha kumakhara ndarama za kwao kumatumiza ziko lakwao kwa mkazi wake.koma inu amalawi mukapeza ka RAND mumati kaz wanga kumudzi abwereso kuno,kumalawi kuno musakutenge ngati kusauka koma ife tomwe amaliwi sitimaganiza bwino.ndiye ine mawu anga ndioti abalewa abwerere ku mulanje onse monga banja
Koma zangovuta moti mavuto ochitikila ku tali ndi zosiyana ndi kumuzi zitu zikavuta mutu imabwerela ku muzi kumakalima mamunda ndi ambiri sor
Achisiru
Akufunika kuti adzipita kumudzi basi
Inenso ndidavutikako ku capetown koma pano ndikuyendera polo vivo...kumangokankha basi time imafika🤑
Ndipo kunoko aliyese amavutikapo aaa ineso ndinavutikapo
Mmmmmmm. Mamvuto kwambiri
Zokhudza pano pa John kukhala choncho
Vuto la malawi amaganiza kuti kujoni ndikothesela uphawi ndizimenezo anzanu kumalawi kokuno akutukuka khani ndikulimbikila ndi kaganizidwe mumaononga ndalama zambili kupangila passport ndi transport mukapita uko kumakavutikaso
Bola iweyo uli pabwino yamika kumwamba pakuti siwonse angalandile m'dalitso mofanana, enanso kuthebako zikuwayendera mkumathandiza kumudzi kuno, mwayi sufanana....
😢😢😢km zokhuza
Inu mukuona kuti amunaanu sakugwira chito basi mukubereka mwana karera yoseyosimukumuona inu ayi azimai muzitengakarera chonde karera ariko waurere
Eeeeeh!! Zomvesa Chisoni, Ambuye ndithu alowererepo
Just come back home
Aa musatero m.mawa ndi m.bale
Zachisoni😢
Pajatu munachoka mwa mwano
Mmene ndimakanila kupita ku south Africa ineo😂😂😂😂
umakhala mwaimwai
Zofuna zimenezo ife tikuthananga kumalawi komwe kuna kumapusha
Well done my friend
Nde ukakamira kwa eni,osamangobwerako bwanji?sizikusiyana nkukhala kwanu kuno
Zakwawo zimenezo analodza aaa kumulanje umfiti
Tithokoze nzimayi uyu kamba kachikondi chomwe akumuwonesela nzakeyu amalawi tiyeni tichepese kupeleka ma comment onyoza plz kutukwana kumangooneselatu umbuli wathu onse poyera phunzilani umunthu ife zomatibowa zomatukwanazi muzikhala ngati munabadwa mwa kholo😂
....
Malo mopita kumuzdi kukakamila kuno zopuse basi
Chokhalira ndi Mwana ndichani
Nanunso musalankhule choncho😮
😢
Mmmm eeee
Mmmmm zovesa chison km ngat mukuwona kut sizikuyenda zithu chobelekela mwana ndi Chani amalaw
Ndi chilengedwe kulakwa ndikutaya mimbayo bola apopo, mwinaso m'daliso umwela chifukwa cha mwanayo sitinganeneletu akuziwa yekha Mulungu kumwambako
Koma pena pake choonde tiziganiza tisanalankhure Mulungu samalakwisa mwanayo ndi Mphatso akanatayaso mimbayo bweziso mukulankhura zosakhala bwino tisamatero palibe yemwe savutika
Mukuyakhula bwanji kod
Oyamba ndi iyeyo yemwe akuvutika ndikakhala ndi mwana? Pena kumaganiza pofuna kuyankhula, mwana ndi Mphatso ndiye mumafuna ataye mimbayo? Mulungu amachita chilichonse ndi cholinga idzakhala history mmawa imeneyi.
Bwana pix tikuyesa namba koma voice mail
Akuonekaso ndimwana mkaziyu koma zalakwika kuti wabeleka mavuto alitho nyumba mwao
@@EstherZintambira-sq3yy mpatso ya chawuta sitingayike milomo. 👌
Dunoon mbali yiti
Side 29