Oh the blood of Abel cried to God and God heard the voice of Abel's blood,surely the blood of nine innocent lives,can not speak to the same God who does not change,surely the same God will hear them.
Bon pankhani ya ku MBC yo I support you 100 percent ndipo anandinyasa kwambiri moti ndinakalipira GOtv ndisakufuna chifukwa cha program achibwana ngati imene ija
Timakunyadilani bwana Born Kalindo Mumayankhula mosanyengelela ndipo Mumayankhula chilungamo chonkhachonkha Pitilizani bwana DC ntchito ya bwinoyi ife nde tili pa mbuyo panu bwana👍
Choyamba amange aja anaphwanya magalimoto aanthu a DPP aja , bwanji anthu ameneaja sanamangidwe mpakana pano, koma anthu aku Ntcheu anamangidwa same day, zompusa ,dzikoli silawo lokhatu
Manganya maguy .... dzina liziyamba ndi title Dr, professor etc ... ine i choose to listen from people whose their name starts with Dr, or Prof 🎉..... enawa mbola
I concur with you Bon,I was bored with kasakura and Mvula since they are the same people who were doing cheap propaganda on times TV.... Please citizens of Malawi what kalindo has said is very right be neutral coz it will follow u
Amalavi ndiwokhwiya zedi kwambiri ndi inu aBon kalindo chifukwa ndinu wodziwika kuti ndi wodzindikira koma mukungoyankhulira kwanu,mukutipusisa kasumen/panseu basi osatikutipasa zochita ife amafoni basi
If have knowledge Mr . Bon come with the trueth. Zongosokosa mwayamba kale , we had people like Kamulepo, Chekufwa Chihana, .Koma inuyo mungosokosa apa .come to International court of of justice to assist Malawians. You are now coming up with confusion and you are not president of Malawians.
Kkkk kung'alula basi achakwela musaope ndege bwelani kuno South Africa kuno muzalumbilitse namaphosa tikulembelani anganyu tionengati mudzabwelele amoyo ndi iwe galu kwabasi
Moni a Malawi amnzanga ndati ndikudziwitseni Mulungu ndiye amatisungira madalitso ,mtendere ndi ufulu Pali chinthu china chimene ndikudziwitseni mbendera yathu ili ndi tanthauzo nyimbo ya fuko lathu ilinso ndi tanthauzo chonde chonde abale anga tikhonza kutenga tembelero lalikulu, tsoka lalikulu loospya King David anavutidwa ndi mwana wake Absalom koma linali tsoka kwa Absalom anthu inu mukunyoza mtsogoleri yemwe analumbitsidwa ku dzera baibulo akalira mtsogoleri ameneyo ndi tsoka lalikulu kwambiri Pali anthu omwe akulipempherera dzikoli china choti pulezidenti wa anthu osauka mudziwe kuti umphawi ndi chiwanda ndiye mukuveka dziko ndipo ife tikuchimmanga chimzimu chimenecho mudzina la Yesu ndipo Malawi ndi womasulidwa ku chimzimu chaumphawi.
Timakudyadirani DC osamanyengerela amenewa, anthu oipa a kumkuyu musaiwale witika mulungu akukuonani
Oh the blood of Abel cried to God and God heard the voice of Abel's blood,surely the blood of nine innocent lives,can not speak to the same God who does not change,surely the same God will hear them.
Amen
Komano pempho langa kwa Inu a president a anthu osauka a BON KALINDO, musazamalize ngati agalatia opusa, tiimilireni nyengo zonse,
Kunkuyu akuyankhula ngati akuyankhulila kumachende
Ur a real man DC .B. kalindo and GOD must give long life and protection and don't stop am from south Africa port Elizabeth
Palibe amene angasekelele chipani chokupha ngati McPherson.
Bon kalindo umayankhulira bwino kwambiri mopanda mantha,coz polakwika sumasekelerapo,always we proud of you BON
God protect Malawi
❤❤❤😂😂 kalindoyo athawitsa sthu chakachino
Boma ili likuenera kutura pansi udindo
@@ChisomoSpacer11111111111111811111111
❤
A Bon Kalindo mwalankhula za mphanvu kwambiri, George Kasakula akupanga campaign ya chakwera, zomwe akupanga akulakwa.
Nyengo ino ndiyoyikano m'manda mcp. This is the fall of mcp.
Bon pankhani ya ku MBC yo I support you 100 percent ndipo anandinyasa kwambiri moti ndinakalipira GOtv ndisakufuna chifukwa cha program achibwana ngati imene ija
God protect you Mr president Bon kalindo
Eti ayamba kuopa Ndege kkkkkk asaope naonso awachotsele zipangizo zina mu Ndegemo ikagwe iwo akaphyere momo akuopa Im'fa??? Anzao anaifuna?? Ameneyu ndi galu kwabasi ..azipita kolumbilitsako mbuzi yamunthu
Keep standing for malawian mr kalindo,big up
The DC, inuyo simusekelera zopusa.
Timakunyadilani bwana Born Kalindo Mumayankhula mosanyengelela ndipo Mumayankhula chilungamo chonkhachonkha Pitilizani bwana DC ntchito ya bwinoyi ife nde tili pa mbuyo panu bwana👍
Iwe ndi kuktunda iyaaaaaa mumatiimira ndinu zonse mu zonse ❤❤❤❤
From south Africa great words
Tili mu nyengo yong'alura bas ,ing'alulidwe🔥🔥🔥🔥🔥😛😛🔥😛
Achewa Muzilimbikila Sukulu Osati Muzipha anzanu kamba kofuna udindo kapena chuma, zitsilu inu
Take back your words
Makwana bwana DC matiimilila anthu osaukafe
Koma anawaputsitsa ndani koma nde asewera yachabe aaaa mpaka zawo moyo kupita ndinthu mmmmm Mr DC mwayakhula chilungamo
MCP chipani cha kupha chamagazi ...... Kodi a chakwela analidi Abusa????
Mr DC agogo anga ati akufuna akupaseni n ,gombe chifukwa ndinu Muthu olimba mtima
Apaseni basi
I wish we should wait until investigation has been completed successfully then we wanna see way forward😢😢
Which investigation
This mission must not die in VPs Voice😢
Anthu ake atiwo anthu safa pangozi ,tiyeninazo uko,anthu apandenge,amapangira ngozi pandege,pagalimoto amapanga ngozi pagalimoto,apanyanja amapangira ngozi panyanja.panjinga yamoto amapanga ngozi panjinga yamoto.mulungu akati lero silidutsa oro utakabisala kuphanga iwe umapita ndithu,zokulazo umuwuze peter.nkhondo yake iti bambo asikono nhkondo mumayidziwa kapena mukunena yamumkanema.
Mumakwana kwambiri the DC you the best
You are definition of a real man
Bon kalindo pachilichonse chomwe umapanga umalakhula sungapindule kanthu kalikonse
Kumwamba kukhale Nanu a kalindo keep on speake the truth
Salute Mr DC
Pheeeee kumastand kumvera bon kalindo 💪 the DC
Respect to you Mr winiko bon kalindo, our president of poor people
Mumakwana boss
awa ndachotsiru ngati kuli kufuna kuti apange mbiri mudziko yankhanani zina ndikuchokela ku south Africa Port Elizabeth p e
Wowopwa sadzichemelera,azkoso amkatero anazima ndiana
Inu nzeru mulibemo even kuti iwine DPP akakumanani udindo mutukwanaso. UTM munainyozaso. Bwererani ku uphunzitsi.
Choyamba amange aja anaphwanya magalimoto aanthu a DPP aja , bwanji anthu ameneaja sanamangidwe mpakana pano, koma anthu aku Ntcheu anamangidwa same day, zompusa ,dzikoli silawo lokhatu
The great man Bon kalindo❤❤
😂😂kkkkk panja ndiwokonda dege kare😂😂😂😂😂
Yes dc mumalankhura chilungamo chimkuyu analankhura monyoza kuti ku maliro ena apitira ndale kuti ayimbilidwe m'manja omwe uli mtopora wapadera peter salimbana munthu akulakwisa chabe
Ati munyengo Yong,alula
We follow you King big up
Chilungamo chimenechi ,Born Kalindo more fire
Ndipo awuuze osawanyengelera anthu oipa umatiimilira dziko lamalawi😊
Ndiye kuyankhulatu kumeneko mwauze
Nanga ndichifukwa chani mu ndege muja munalibe aliyense wa MCP
Dangerous child has spoken 😂😂😂😂
😂😂😂😂 at sazasisa pweyaa
Ndipo amalawi takwiya kwambiri,mayankho ndiomwe tikufuna basi
Koma ndiye takwiya kukwiya,moti Wanthu sakukwanisa kugona Ndipo kunkuyuu Lero akuyankhula,koma zikaza mufikira azalira ngati Nkhumba, Chakwera ndi gulu láke azaona tsiku Lina apha Wanthu, koma nthawi ina Yehova mwini azati pasira ngati m'mene adamu perekera Goliath m'manja mwa David.amenewo akuti agula zida zankhondo koma tsiku Lina tizazi tenga ndifenso Ana obadwira komweko
Umatiimiliza DC
Zoona akumalankhula ngati a Malawi ndi mbuli saganiza. Ayenera kuziwa kuti anapangitsa okha a Malawi kukwiya mene anapangira handle
Mukufuna maudindo chabe inu,tiyeni uko.
Mwana oooopsaah kwambiri from Njeza vg bx 76
Ulemu wanu akalindo mumatimilira osaopa ayi mcp yathapo bs
Wakhuta thelere ndiwe wakumudziwe iwe ife sitimalidziwa kkkk kwerani ndege mupite ku south osatuma munthu isaaaa
Manganya maguy .... dzina liziyamba ndi title Dr, professor etc ... ine i choose to listen from people whose their name starts with Dr, or Prof 🎉..... enawa mbola
🔥🔥🔥🔥♥️♥️♥️♥️🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼 Bon kalindo mbambande
Kalindo wakhuta thelele
Power a DC
God blesss u born k
I concur with you Bon,I was bored with kasakura and Mvula since they are the same people who were doing cheap propaganda on times TV.... Please citizens of Malawi what kalindo has said is very right be neutral coz it will follow u
mumakwanira atsogo
Amalavi ndiwokhwiya zedi kwambiri ndi inu aBon kalindo chifukwa ndinu wodziwika kuti ndi wodzindikira koma mukungoyankhulira kwanu,mukutipusisa kasumen/panseu basi osatikutipasa zochita ife amafoni basi
Ndipo Mr DC munena zona pa MBC aaaah
Ambuye azikudaritsani mumatirimirira
Manyazi akuwagwira mene anachitira anthu aku ntcheu anawakhaulitsa a masewera ndi angoni awaliza tu koma angoni
😅
Mr DC Muthu olimba mtima kwambili
Nama ndege kkkk
Perfect boss
paja ndinu mkayidi kale sangakumangeni
Nthawi yong'aluradi eeee kkkkk
If have knowledge Mr . Bon come with the trueth. Zongosokosa mwayamba kale , we had people like Kamulepo, Chekufwa Chihana, .Koma inuyo mungosokosa apa .come to International court of of justice to assist Malawians. You are now coming up with confusion and you are not president of Malawians.
Fuseck wena
Step down babylon your old by evison matafale
OSAOPA
OSAFOOKA
DZIKO NDI LATHU .MCP MA CRIMINALS
Big up our brother Bon kalindo
Nyengo yakuswa bon kalindo😂
Mawu mawu bwana DC,,,athu awa abomawa atikwana ife,Chakwera akudzikumbira dzenje lokuya kwambiri koma wagontha makutu
Zikomo kwambiri a DC nimau akulu,ine nili ku Uganda
inu ndi amfumu. kunkuyu akulankhula Mo pusa kwambili. anthu amenewa atikwana
Simbi sakuyenela kusankhidwa kuti akhale vice president ai. chifukwa nayenso akukhudzidwa pangozi imeneyi. ndipo ndizoona zokha zokha.
Kkkk kung'alula basi achakwela musaope ndege bwelani kuno South Africa kuno muzalumbilitse namaphosa tikulembelani anganyu tionengati mudzabwelele amoyo ndi iwe galu kwabasi
Dc ndikatundu kwambili
Big up
tiye nawo born kalindo akuzolowela amenewa Kwambili amalawi amukhuta muthu ameneyi kwambili.
kkk namadege emweyoooo
mumanja mwanu a Bon kalindo ndiye kunkuyu akanakhala kuti alikuno ku south Africa bwenzi tina kamchita ka zenofobiya
Ichichi ichiii👏👏👏
Zoona Mr Bon Kalindo mukunena zoona maka program ya pa MBC yochedwa kuti Timvense ya Kasakula, ithe. Kuno ku Kasungu.
Moni a Malawi amnzanga ndati ndikudziwitseni Mulungu ndiye amatisungira madalitso ,mtendere ndi ufulu Pali chinthu china chimene ndikudziwitseni mbendera yathu ili ndi tanthauzo nyimbo ya fuko lathu ilinso ndi tanthauzo chonde chonde abale anga tikhonza kutenga tembelero lalikulu, tsoka lalikulu loospya King David anavutidwa ndi mwana wake Absalom koma linali tsoka kwa Absalom anthu inu mukunyoza mtsogoleri yemwe analumbitsidwa ku dzera baibulo akalira mtsogoleri ameneyo ndi tsoka lalikulu kwambiri Pali anthu omwe akulipempherera dzikoli china choti pulezidenti wa anthu osauka mudziwe kuti umphawi ndi chiwanda ndiye mukuveka dziko ndipo ife tikuchimmanga chimzimu chimenecho mudzina la Yesu ndipo Malawi ndi womasulidwa ku chimzimu chaumphawi.
nano mumapanga kaupeni palibe chezelu inu
Wise and courageous words
Namandege wayamba kuopa kukwera ndege😂😂.. tamakweranitu
Chilungamo chozpweteka 🙏
Ulemu kwa DC
Ndipo inu eti 10am mpaka 5 vice president ngati munthu wamba mmmm ife timadalira kuti chaka chamawa tiona kusitha
Zikuonetsaso kuti even iyeyu alibe umboni
Dccccc machine our president wa amphawi
Dzikoli si lanu koma la a Malawi tithanano munomo
tamudulani mutu chakwera kumeneko amalawi plz