KOMA MWAMVA? EEH MBOLA AKUTI NKHANI YOLEMBA ANA IJA WINA ALIPIRA 1 MILLION NDIPOSO KU NDENDE ZAKA 5
Вставка
- Опубліковано 14 гру 2024
- HERE...
Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
#MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika
Koma ijayiso yoti ukalembetsa upititse kwa afumu akalembe number yakovotela mubuku mwawo.Kuti Zola ndila landila zisawa phonye
Kd tingalembese bwanji yet pali ulendo wa 5 kilometres kt tikafike kolembeselako??? Tingapite bwanji using transport yet there is no fuel magalimoto sakuyenda.
Kodi zolandira zinthu zikugwirizana bwanji ndi kuti Mafumu azikalowesa nambala yazitupa
Apa zachitika ndi zibwana..ziyambilenso ndipo no smartmatic machine..
Karembera abwerezedwe coz nthawi imene anthu amarembetsa anthu ena anali bzy kogura mafuta agalimoto, pachifukwa ichi karembera abwerezedwe
Mavuto nde alipo akuyenela abwelezeso kuti a Malawi ife tikhutilenazo osati mmene zayendelesedwamu ayi
Kodi inu a Mcp mukuona ngati ndinu mulungu kapena enidziko anthu mukuwaopsweza kuti amangidwa kapena apeleka 1 million for what
NDIYE NAWONSO AMENE AKUITANITSA ZOVOTERA NAONSO AMANGIDWE CHIFUKWA AKULIMBIKITSA UMBANDA
Mavuto ndiatsogolel athuwo Wanda taonako zisakho olo kunoko kusouth Africa
Ineso mwanawanga analembesa 2019 koma ma I'D sanatuluke NRB anayambilatso kurembe mwanawanga anapitatso kut ndipo anamuuza kut nkhope yake siikuoneka ajambulisetso anajambulisatso panadusa miyezi 6 ndinene MEC inayamba kulembesa zisankho atapita kut akalembesetso akumuuzanso kut nkhope siikuoneka komaso zinalake likupezeka ndianthu awili mpaka anabwerera sanarembetse Kodi NRB akumajambula Chan nanga zithuzi zamwanawanga zikumapitakut
Mmene zikuwonekelamu pali chinyengo onse a N R B ndi a MEC akudelera chigamulo cha khoti akudzipo china chake. Anthufe tikufuna manual nde ambiri azavota