Joab you are a good journalist,umafunsa mafunso mosapanga attack munthu komanso mafunso okhwima,osati ena omwe timawaziwawa,omwe amapanga za personal pomufunsa munthu ndikumupanga attack,namangobwelezabweleza mafunso
Amene muti sadziwa chomwe akunena or ndi mbuzi. Munangozorowela kut ma poticians adzikunamizani. What an honest guy he is. We need more leaders like him .... Leaders who can admit pomwe zinthu sizikuyenda bwino
First time seeing a politician who is not political. Composed, humble, honest, remorseful and brilliant. Explaining things like an ordinary person without being pompous. Big up Hon Dimba
Big up to hon Dimba ,he's humble and honest , and when the government arrested opposition politician who concerned with corruption ,the same malawian came to say it's political issue if is not true anthu opusa ife
Hon deputy minister u seem honest though you're deliberately failing to tackle certain crucial questions and it shows that you're hiding or you're protecting ur government that's what I have discovered from this interview but we'll done Mr j chankhaza
I think your the guy 🔥..but am finding some difficulties on water transportation,I don't think government can manage to operate such transportation.palibe chomwe chuyenda with government.
joab ur the best interviewer in malawi i watch alot of interviews but how u ask its comfortable for someone to answer even if he/she doesnt want to answer
Interview iyiyi ili bwino ndi Nduna iyi umunthu ukumutsutsa koma mbali yake yaikulu akudziwa kuti MCP siili bwino. Imagine za Chizuma President anakana kuti sanadziwe yemwe anatuma a polisi kukammanga.Panopa MCP ndiyolemera kuposa mmene inaliri 2019 pomwe imadya ndalama za Mia. MCP ndalama yazitenga kuti?
Bodza, Malawians don't highly regard MCP, it's undemocratic, and u shld provide ur evidence in the court of law that DPP murdered Njaunje, this is a serious allegation and u must prove it. Anyone found guilty shld face the law, why keeping silent?
He avoided certain questions, but from the ones he answered, he comes across as quite honest-a rare quality in politics.
Glad you also noticed
why have written zomwe ndimafuna kuti ndilembe?😂😂
He is smart but ngachibwana akuluwa...the story of Malawi transformation is not a movie neither a book reading.
Dimba will give you back to back.
Joab you are a good journalist,umafunsa mafunso mosapanga attack munthu komanso mafunso okhwima,osati ena omwe timawaziwawa,omwe amapanga za personal pomufunsa munthu ndikumupanga attack,namangobwelezabweleza mafunso
Amene muti sadziwa chomwe akunena or ndi mbuzi. Munangozorowela kut ma poticians adzikunamizani. What an honest guy he is. We need more leaders like him .... Leaders who can admit pomwe zinthu sizikuyenda bwino
Peter Dimba inspires me alot❤ remain blessed boss
Joan!!! You are a genius...... Peter Dimba too is one
First time seeing a politician who is not political. Composed, humble, honest, remorseful and brilliant. Explaining things like an ordinary person without being pompous. Big up Hon Dimba
Also not being biased
Dimba is a straight forward person.
Hon. P Dimba, you always impressing my heart. Keep it up!! MVULA kumudziko akuti ikubwera bwino- Rev. J Dimba.
Big up to hon Dimba ,he's humble and honest , and when the government arrested opposition politician who concerned with corruption ,the same malawian came to say it's political issue if is not true anthu opusa ife
Kmaso Joab mwavala bwino 🔥🔥
Salute Mr Dimba for your Honesty. I hope this is really u
This is guys is very good. I have honestly liked you. Very honest and intelligent MP
I salute this man , humble
Joab Busy making History, big up bro!!
We need to have more honourable like this,I salute you bwana
This Guy is Good n Honest kma Ali mbali yolakwika mwaiye kachilungamo kalimo kma wazungulilidwa ndi ng'ona I feel sorry for him
Politics is not for honest people
Hon Peter Dimba ndi Katswiri !, a very rare kind, I like this guy !👏👍
Joab ndi dolo
Fadawa ma crucial questions angowapondatu🤣🤣🤣
One honest Politician in Hon. Dimba
Hon deputy minister u seem honest though you're deliberately failing to tackle certain crucial questions and it shows that you're hiding or you're protecting ur government that's what I have discovered from this interview but we'll done Mr j chankhaza
Honorable l use to know you through kindness, humbleness
We need to do more in our politics. Our politics from since the so called independence is a scam we need to take the path of Denis Mahata.
Koma Dimba, you remember your lecturers well well... Nthindwa, mwamuna wake wa Ruth wa UCCC kkk
I think your the guy 🔥..but am finding some difficulties on water transportation,I don't think government can manage to operate such transportation.palibe chomwe chuyenda with government.
Koma 😂😂😂 Joab Unabadwa Thawi yakamuzu mot ndiye siukulat ngati Lulu 😅❤
Zimangofunika leader azikhala ndi experience. Angakhala minister of finance awa..? Nice nice kma.
joab ur the best interviewer in malawi i watch alot of interviews but how u ask its comfortable for someone to answer even if he/she doesnt want to answer
He's genius
U have mu vote as my area Mp but on party eeesh prove me well on economy.how can we buying 3700 dollar
Aaah aaaa ma guy😂
The honourable seems to be an honest and intelligent i like that about him
Mbuzi ya munthu iyi amangofuna vote Koma kuthandiza anthu ake ai mnabetsa vote yanga .....Zaka zambiri mbiri koma kulephera kuika Phula nseu kwao, zipatala,madzi aukhondo 😭😭
Ndiwakwanu ku Lilongwe? Ooh oky
Dimba🔥🔥🔥👑
Big up bwana Dimba, muli kachilungamo mwa inuuu!
Paja nthawi imeneyi ntchito accountacy department imachita kutifunsira ... kkk
Ngati ku MCP kuli anthu abwino 5 Mr Dimba muli mommo
Uyuyu saziwa zomwe akunena
Ma biggie munapezanatu macheza abwino awa
Interview iyiyi ili bwino ndi Nduna iyi umunthu ukumutsutsa koma mbali yake yaikulu akudziwa kuti MCP siili bwino.
Imagine za Chizuma President anakana kuti sanadziwe yemwe anatuma a polisi kukammanga.Panopa MCP ndiyolemera kuposa mmene inaliri 2019 pomwe imadya ndalama za Mia.
MCP ndalama yazitenga kuti?
Akakhala pa nkhate.
Ameneyu ndi mbudzi bwanji.
Iwe nde yamano kunsi
Bwanjiso 😅😅😅😅😅
Kikiikiki Thengolose --- ati Then go lose amazuza anthu uyu. kaya ali kuti mkulu ameneyu
Dimba you are amazing
He is a genius but Ali muchipani cholakwika
Joabu wagonjesa nduna ndimafunso, nduna ikukanika kuyakha mafuntso ingozikola
Ikuteteza mpando wake padakalipano sangayakhe chilungamo
2000 14 points za nice..
Joabu umakwana
a classmate anthu, a poly UCC cong rep. mumatiimilira inuyo
Bodza, Malawians don't highly regard MCP, it's undemocratic, and u shld provide ur evidence in the court of law that DPP murdered Njaunje, this is a serious allegation and u must prove it. Anyone found guilty shld face the law, why keeping silent?
Dimba ndi dolo
Zinangowona kuchitika uyu kukhala wa mcp, koma alindinzeru kupotsa chakwera.
Mukulakwitsa muwadulitsa kuchipani anzanu
Mwati awawa ndi deputy minister? Mnyamata wabwino bwino koma zero pa 10.
Achakhaza apa mukucheza ndi bulutu weniweni akuyankha zosemphana ndizomwe mukufunsa
MQT😂 eeeh achina Simulation
License mungopeleka zipepala ku road traffic
But jowabu chakaza umakwana ndipo umafunsadi mafuso abho ndipo adimba akulephela kuyakha komaso tiwayamikile Zina akuvomeleza
Mchifukwa chake Malawi wathu yu sakuyenda bwino munthu wa za Ulimi sangayendetse unduna wa za Maphunziro kumeneko ndy kulakwitsa zinthu
Joab umabebetsa iweyo
Munthu wamoyoo angamapange za MCP koma?
Eti eti, mnyamata wabwino bwinotu kikikiki
Ka Mr Smile Dimba
Muzijambulila panja za showing off
Anzangawa amakonda kuseka😊😅
Phwete basi
Aise iweyo umakwana wandisangarasa usamusiye zaka 5 ndizamber azao amakhra 4 km kukoza zithu
Joabu wagonjesa nduna ndimafunso, nduna ikukanika kuyakha mafuntso ingozikola
Ikuteteza mpando wake padakalipano sangayakhe chilungamo
Ya true