thus sulqeman isaud last week that he should be the leader pf opposition in the house..Suleman is like juju the guy who doesnt wznt to tolerate stupid things
Mp wathuwathu uyu si munthu osauka ngati enanu mumadalila ndalama zokuba ......Suleman Ali ndi ma track olo chakwera akunama kwambili .......Suleman woyeeee Mpbwathuwathu ameneyo osati mbuzi za mp .....Suleman kept up mpaka agalu awa azachoke basi
I voted for you to represent us in the parliament... More fire my MP ...this Parliament is not only for mps from the MCP Boma la DPP ndilomwe lidamanganso Parliament yokongola ngati iyi mu Africa muno chitukuko cha malemu Bingu Wa Muntharika..... Suleiman woyeeee, DPP woyeeee, APM woyeeee Ana a DAD onse kuti woyeeeeeeeeee
Proud of you Bakili Muluzi TV. Kunena za bwana Saama Suleman, Dr Kabambe, Denis Mahata, Alexious Kamangira, Dr Mtumbuka, Martha Chizuma ndi Newton Kambala. This can be a powerful government that Malawi can get Rescued.
@@jameskachulu8141mulipamenepo chifukwa cha UDF inakupulumutsani ku ng'ona komaso ku makako omwe mcp imaphelako anthu,,,UDF inakupulumusani ku ma card omwe anthu amazuzika nawo,,,mwaphuzilaso Free primary Education yomwe idayambitsidwa ndi UDF,,,lelo mukunyoza UDF very shamed malawi,,,,onyoza UDF ndi mbuli UDF my support inatichangamutsa kutichotsa mu umbuli wankhaza wa chipani chimodzi cha MCP,,,,
MCP kumera midzu ndi Ku Parliament komwe, now its MCP Parliament eeeeee Koma ana a Njoka inu 🐊🐊 mwalipedzerera Dziko la Malawi. Gotani Hara you think you are there forever as you Said. Your days are numbered ndi Kangaude wanuyo. Anthu Akupha inu, Mkhamza, Tsankho. Koma mudziwe Kuti Ulamuliro wanu wa Ng'ona 🐊🐊 Malawi sitikuufuna Stay safe ✊ Stay blessed 🙏 brother from BAKILI MULUZI TV you are the best teacher ever ✍️
Suleman it's our version and a pillar for us this man once when is speaking truth and painful for government we need people like him plz malawi don't make mistake again because chakwera he just come like a leadership but doesn't know he is position l feel shame to him got full of lies and no action on ground promise for nothing just take people for granted kwinaku nditukwana
SAMEER SURAIMAN IS A LEGEND
We need MP like this guy SAMEER SURAIMAN
Ndipo ameneyi akanakhala leader of Parliament osati chaponda ogona uja, big up Mr suleman
@@AlickMDayi ndipo osat pang'ono
True ❤❤❤❤❤@@besterlumbe4404
Koma Suleman eeee ndikatumdu munthu olimba mtima koopsa.Big man ulemu wanu. Bakili Muluzi TV Historyis a best teacher.❤
thus sulqeman isaud last week that he should be the leader pf opposition in the house..Suleman is like juju the guy who doesnt wznt to tolerate stupid things
AMENE TIKUT TV NDIYOMWEY NDIPO PALIB KUSITHA LET'S GATHER HERE ❤
Live
@@ganizankabango 🖐🏼🖐🏼🖐🏼
Julias malema wa ku malawi mr sulemana very good 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Mp wathuwathu uyu si munthu osauka ngati enanu mumadalila ndalama zokuba ......Suleman Ali ndi ma track olo chakwera akunama kwambili .......Suleman woyeeee Mpbwathuwathu ameneyo osati mbuzi za mp .....Suleman kept up mpaka agalu awa azachoke basi
Bakili muluzi TV and Mr Suleman God bless you all
I voted for you to represent us in the parliament... More fire my MP ...this Parliament is not only for mps from the MCP Boma la DPP ndilomwe lidamanganso Parliament yokongola ngati iyi mu Africa muno chitukuko cha malemu Bingu Wa Muntharika..... Suleiman woyeeee, DPP woyeeee, APM woyeeee Ana a DAD onse kuti woyeeeeeeeeee
Proud of you Bakili Muluzi TV. Kunena za bwana Saama Suleman, Dr Kabambe, Denis Mahata, Alexious Kamangira, Dr Mtumbuka, Martha Chizuma ndi Newton Kambala. This can be a powerful government that Malawi can get Rescued.
I'm a UDF sapota but Sameer suraiman ndiamene tikuufuna kumbali yathu asusa boma very powerful comrade ❤❤❤❤
Wao akopoche yeleyo udf iyichichi
@@jameskachulu8141mulipamenepo chifukwa cha UDF inakupulumutsani ku ng'ona komaso ku makako omwe mcp imaphelako anthu,,,UDF inakupulumusani ku ma card omwe anthu amazuzika nawo,,,mwaphuzilaso Free primary Education yomwe idayambitsidwa ndi UDF,,,lelo mukunyoza UDF very shamed malawi,,,,onyoza UDF ndi mbuli UDF my support inatichangamutsa kutichotsa mu umbuli wankhaza wa chipani chimodzi cha MCP,,,,
❤❤❤❤UDF is my party inatichamutsa kutichotsa mu umbuli omwe amalawi amayikidwa mu chipani chimodzi cha MCP,,,,,
Keep on fire burning brother Bakili muluz tv
History is the best Teacher ❤
Tikadakhala ndi athu ten ngat Suleman Ku opposition bwenzi zithu zitasitha ...big up Suleman..
History is the best teacher indeed brother inuuuuuu 🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤
❤❤❤we need people like this man good work Mr MP 🙏💪
MCP kumera midzu ndi Ku Parliament komwe, now its MCP Parliament eeeeee Koma ana a Njoka inu 🐊🐊 mwalipedzerera Dziko la Malawi.
Gotani Hara you think you are there forever as you Said. Your days are numbered ndi Kangaude wanuyo.
Anthu Akupha inu, Mkhamza, Tsankho. Koma mudziwe Kuti Ulamuliro wanu wa Ng'ona 🐊🐊 Malawi sitikuufuna
Stay safe ✊
Stay blessed 🙏 brother from BAKILI MULUZI TV you are the best teacher ever ✍️
History is the best teacher kkkkkkkkk
Suleman it's our version and a pillar for us this man once when is speaking truth and painful for government we need people like him plz malawi don't make mistake again because chakwera he just come like a leadership but doesn't know he is position l feel shame to him got full of lies and no action on ground promise for nothing just take people for granted kwinaku nditukwana
Honorable Suleman 🎉🎉🎉🎉 bakili muluzi TV you are the best teacher 🎉🎉🎉
God bless you Suleman and protect him
I can watch without comments continue give us update every day my best teacher
History is the best teacher ❤❤❤
Malawian Malema, bravo Mr Suleman.
Best teacher ever ❤
Tiyenazo Suleman much appreciate to bk tv number one
Has reminded me of late Nga Ntafu - mhscrip
Samaar suleman samamphweketsa history is best teacher thanks
Good speech mr suleeman , Tisalole kuti kasongo chakwela anyamuke ,
President opusa ngt uyu ctinamuoneko
Keep it up big 🧢🧢🧢💙 MCP yathapo bs 🐊🐊
Zoona biggy apapa tisalole mcp yatitola muwauze mayiko akunja onse asatipasenso kobili cifukwa tcito zake sidzikuoneka ndicifukwa ndikuti akabambe acita bwino osada bigy suleyimani ife tili pa mbuyo panu dpp oyee!
Following boss and God bless you and protect you ♥️
Lero timati Jumuuah Mubarak kwa asilamu onse Mulungu dalisan aliyense Malawi muno ndpo dalisan Bakili Muluzi TV
Ameen❤
@@imranmposa2788ameen
God protect you Mr Sulaiman ❤
BAKILI MULUZI TV INSPIRING THE NATIONS GOD BLESS YOU SIR
History is the best teacher 🤛
Always with you sir
Seleman is a courageous person
Wake up, thank you our leaders, we pray for Malawi in Jesus name amen.
Tiyenaye mwana owopa mulungu suleman osaopa, osatopa ❤❤❤
We need aman like suleman God bless u
I like his courage❤
❤ 🎉bravo Hon Sameer Suleiman.
Keep the fire burning mr Sulemani
Umakwana fadah ndiwe number one
LONG LIVE BAKILI MULUZI TV 🎉🎉🎉🎉
Sulemani ofunika otsutsa amuthandize asamusiye ekha nkhondo akumenya bho🤜🤛
Suleman ukakhwana.Chakwera akuona ngati ife a Malawi opusa kwambiri.
Big up boss ❤❤❤❤❤❤
Please continue mwatisiya malele zazivomelezi zikuti bwanji kodi😢
History is best teacher bro my best tv
God bless you munthu wathu BMTV
Like from Johannesburg Kempton park
History is the best teacher
😂😂😂😂😂 sulemani #1
Big up bakili muluzi tv my brother
One of the best
Suleman unafunika kukhala opposition leader ku parliament, iweyo ndi mbambande,akanganyawa akufunika akadziotche ngati iweyo
Exactly
Katundu omanga ndima Wire uyu ulemu wanu Bwana🔥
We need more of SAMEER in this country
😂😂😂😂😂😂😂 koma ndaseka bwanji oky
Inuyo man number one bas❤❤❤
Sameer en bakili muluzi tv you r the best owez
Koma zachimwalazo zikutiopsatu 😂
Mposo we are not safe 😂😂😂 ndili ndi mantha iiiii😢
Koma Mr president mmmm dzipatseni ulemu chonde,musanyambite kochepa taninkhidwaka eeeeish 😢
The best TV, Bakili Muluzi.
Akagula mafuta Komatu chakwela ndi fiti ya muthu 😢😢😢
Iweyo Bakili Muluzi TV ndi katundu....
😂😂😂😂
Malawi ofunika anthu ngati awa osatopa osafooka uyu ndiye Julius malema wa Ku Malawi bakili muluzi TV,mtanyuwa boni kalindo ,Sameer seleman kamangira apa kwakwera Dr kabambe anthu munivetsa ukoma mulungu azikutetezelani
My favorite ❤❤❤❤❤❤
Our tv ever in malawi 😮😮😮
Matimilila mfumu bakili muluzi tv ❤
Tili ndi Bakili Muluzi TV Bon Kalindo ndiye kwabweranso Dr Kabambe ndikukupepherelani kuti Mulungu azikutetezani nthawi zonse pamoyo wanu ndikupitiliza kukupasani nzeru zochuluka anthu onse a MCP Mulungu wawapangisa kukhala ndi nzeru zobutha onse Dala kuti wina azindikire kulakwisa kwao koma ayi ndithu akungozitenga ngati anzeru pamene Mulungu wamphamvuzonse anawachokera
Best TV Bakili ❤
All the best Bakili Muluzi Tv 🎉🎉
U still the best ❤❤❤❤
Big up boss ❤
❤❤❤
Ulemu wanu mr suleman
More 🔥🔥 🔥🔥🔥 Mr suly
Big up brother man!!
Suleiman ❤❤❤❤❤
First to comment😂😂😂😂😂😂😂 Mcp yaonjeza kma palibepo ufulu apa❤❤❤❤❤
Big mumakwana
iyeyu akuyankhula chilungamo ine ndlinawo umbani guys pray 🙏🙏🙏🙏 harder
Mesa wanyamuka khale tamuona kuno ku Zimbabwe 😂😂
Salaam alykum bm bm
Kaladi uyu avutika naye a MCP 😅 umakwana iweyo 🔥 keep it up good work 😇
Bakili muluzi tv number one
The pangolin 🫵🫵🫵🫵
History Is The Best Teacher
BMTV lovers Let's Gather Here
Anthu tukufa ndi njala bwanji iyeyo sakugula anthufe chimanga Koma apite kunja mmm ufiti wachinchi muzaona mathero ake
Nde ndimveso wina abuti boma ndlomweli koma guys 😭😭😭😭😭 azuzuleni abambo anuwo kut bweresa MCP sikuthesa mavuto koma kubweresa mavuto 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Big up mlomwe woyela
woyela umatiimilira
More fire big man
My boss
Katundu waboma .... Siza Chaponda mbutuma, dzufunika anthu ngati awa aziwaumisa malobvu ma king of thieves m'bomamu
Best tv ever
Chakwela walephela kulamula athu ambili achoke watikwana sulemani anakoza kkkkk
Dpp munachedwa kusankha Nankhumwa ndi Chaponda munakamuika Suleman koyambilira pa Leader of opposition Mcp inakalamulira bwino
Let's join hands together... Mcp izipitah
Muli mwala inuyo big up
President akutichititsa manyazi kwambili