Tikumphunzirapo zambiri izi ndithu mmidzimundiye zikuchitika ndendende ..mmaitha good acting osaonetsera kuti ndi sewero.keep it up Director , script writer ,actors. & producer
Honestly kumalawi tili ndi luso kuthekela ndithu kochita bwino ku zisunzo tili nazo koma timasowa upangili wina wake maka sponsor ship. Tiyeni tiyambepo kuwaponya pa sogolo anthuwa
😂😂😂😂😂 Tonde akudandaula ati koma pano tidya Kkkk nice guys pitilizani mumatimvetsa kukoma
Tikumphunzirapo zambiri izi ndithu mmidzimundiye zikuchitika ndendende ..mmaitha good acting osaonetsera kuti ndi sewero.keep it up Director , script writer ,actors. & producer
😂😂😂kkkk km ndaseka tonde kudandaula kumeneko ati km lero tidyapo pano
Nice guys mumakwana❤
Ikumachedwa😅😅😅😅zakuqwima amayi yako okalamba❤❤❤❤❤
Eee cicilia alibe mantha guys kkkkkkk
Muli phunziro umu😂😂😂Ayi zikomo pitilizani
amake dollar anyangala 😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤
Kuwonera mwa pheee course mumativetsa kukoma kwambili 😂❤❤ .much love you guys big up ❤❤❤❤❤
Ikumachedwa bwanji kutuluka tonde❤❤❤
Kkkkkkk u r making it guyz. Km2 kuvuta ma dola nd anagumbo mchbale?
Good guys..mukuitha
Kupilinga palibe mwaotcha tchalitchi😂
Ndikubwela konko ndizakwatile ma Doral sangamazuzike mamuna wabwino osanyenganyenga ndilipo iyaaa
Kk😂😂 Zakhwima nd bro wake
The best actors yet in Malawi 🇲🇼 ❤
Waiting patiently for the next episode 😊😉
Mayi zimveka mukuwalatu mama
Ndaseka nkutopa ,,,keep on bringing laughter 🤗 my people mumayitha 👍🇲🇼we have talent in Malawi
Ikumachedwa kutuluka tonde
Tonde iwe ndi katundu ase
Honestly kumalawi tili ndi luso kuthekela ndithu kochita bwino ku zisunzo tili nazo koma timasowa upangili wina wake maka sponsor ship. Tiyeni tiyambepo kuwaponya pa sogolo anthuwa
First one ❤
Zimakoma kuwonela weekend koma timakunyadilani koma tamayesetsani tiziwomela Saturday or Sunday night please guys
Zakhwima umatha..ma dolla mumandiwaza
Koma zakhwima ndi bale wake 😂😂
Maaa dola makina wane❤❤❤❤
Nice ❤
Beautiful ❤️❤️❤️
Ndende yaku Nsanje
Zakhima ndi zakoyo simulatheka ndithu
Ineyo nimaconda kwanbiri mau amene amachokela pakamua pa chifunilo iye ndi wani
Koma tsiku lomwe mumatulusa ndilachingati
Keep it up people
Where is Gaga in this episode nayeso ndi katundu payekha keep it up
Ana ovuta kulela zakhwima ni makwale
Keep it up guys
Mumakwana inuyo
Zilibwino keep on
Tonde palibe kudya lero
usamalowe nokha
Dola
Zakhwima ndi nzake
Ma dola angokwatilana ndi tonde basi just because he can make good husband
Mli bho
TONDE😂
Makwale😂😂
🤣🤣🤣
Zilibwino ❤❤❤
Makwale suzatheka
Zilibwino
Mumaitha tinakusowani
Farao wabwera basi
Klkk
Umakwana
koma athu inuyo ayi mumatha inuyo
Makwale
Koma zakhwima ndi bale wake 😂😂