Am a secondary school teacher because I used to listen to this track, thanks to all the above
Nyimbo inapanga dzina iyi
Ndakumbuka ndili standard 4 nthawi imeneyo 🙌
Nyimbo iyi kumaikumbukiranso ngati national anthem yamaphunziro ku malawi kuno❤
Wow kkkkkk these were the songs we used to listen on Sunday top 20 back then. What for bringing back old good memories
Rest well Mr Clement Kajumba mthali from Hewe, sang this song for me. Now am at college
Underrated Malawian song. Nthawi imeneyo kuli mbc radio 1 yokha
My mom's favorite song.... ♥️♥️♥️♥️If i go home i will play this song for her to dance. I hope she has good memories 🥰
Nyimbo iyi munapha boss. Reminds me of my childhood days
One of the few songs bearing undescribable thrilling meaning 🤩
Ukuziwa kale osamayiwala kale
This song aah yes, yikuyenela kuonjezeledwa kumapeto kwa national anthem 👏 🙌
Back in those days nyimbo panali kudekha nkhani ya composition apa bwana alfazzema iyi mukapeza nthawi ikufunika remix
Very true. Education matters .
naupenda sana huu wimbo
Nyimboyi imalimbikitsa anyamata ndi atsikana kuti azilimbikila sisulu komanso ikufunika mwina kumaseweredwa mawailesi pafupipafupi cholinga mibadwo tiliko panopa tizikhala ndi chidwi chophunzila...komanso nyimbo imeneyi imandikumbutsa pa graduation yanga nthawi imeneyo ...ndie panopa imandisangalatsabe ndikamaimvera nthawi anaimba bwino kwambili Dr Joseph Alfazema munagwila ntchito Popeka ndikutulusa nyimbo imeneyi .
Dr. 2024 tumverabe
Reminds me chilimba Mr Alfazema
Do you remember that fateful night
kusatheka okumba nsewu kulandira ndalama kuposa bwana who is with me 2022 song
i remember my parents used to play me this song before going to schjool everday
now am at college
Nyimbo yolimbikitsa iyi Kwambiri
Songs of good old days,, Lunzu yonse nyimbo inali imeneyi
Nice one❤
Kodi ija amati chonena ine ndilibe munaimba ndinu nomwe eti?? Moreee love bro
Nyimbo iyi imandipasa chilimbikiso
Kalelanga abale wow
Apatu malume munandifikapo.nyimbo imeneyi imandikumbutsa pa lunzu mmmmm kale likati lidzibwerela
Dr Alfazema nyimbo idanyamula uthenga Wa phindu Ku ntundu Wa Malawi
+Joseph “Doctor” Alfazema tiponyereni Zafika mochedwa' komanso Goez magwira chisale monga mmene munaliri NTHAWI imene IJA achina Mc Miye
munandiphuzitsa kuyimba inu
I still like this song up to date , eeeee inaimbidwa bwino proud of you always
My memories🥰🥰🥰
Nyimboyi mnachedwapo achimwene ndinayamba kuimva ndili Std 2 Kalanga Primary (Chitipa)
Ndalimbikitsidwa iney...
Kale likati lizibwerela ndithu
Nice song live from Pretoria
Nyimbo iyi ikufunika ka amapiano remix ndi zeze
🎉🎉🎉award winning song
Powerful song ..new video yifunika
Nice one eeish
Muimbeso ina palibe nyimbo ya phindu ngat iyi since pomwe inatuluka
those days,l still like this song.
Aaaaa kale langa
Long tym ago koma malangizo sazakalamba mpaka kale
Wawo this song inspire me alot
Bringing back the memories
Recordo os aconselhamento do meu tio, quando dizia (Estudar é a lanterna da vida futura de cada menino) obrigado tio RIP my uncle Afonso
Keep it up
❤❤❤❤doctor
This is beautiful song
ndagarazo ndiye zinalipodi kuposa masukulu kkkkkk
Who's with me 2023
Good song
Timeless music. Music that makes sense
this video has taken me back in time
One of the good song's in my life
Kaphuka's Signature
A song with a deep meaning.....
please joseph can you upload all those old song,
I love this song being an artist I want to cover this song❤️❤️
Nyimbo tikufuna ndi izi za uthenga
Kale lidali lokoma osati Za ana anatsiku ano ogwila pamachende you akuimba
❤❤❤
Dziko Lili dziko
Kuno mukutiva ndiku radio1 fm ndithawi yazamaphuzoro
Remind me of this year, was it 1998?
Nyimbo inkakoma pa graduation party in early 2000.
Big nyimbo ya chonena ine ndilibe ija bwanji pliz
Haa miss
Ndiwe dolo ase
Good old days
My old good friend
Where is this regend
Joseph pano muli kuti? Ife omvera takusowani pa Malawi music industry ndi nyimbo zanu zamalangizo.
I used to listen to it when iwz a todler up until i finished college and landed a good job, but now i feel like i stil need to improve myself....so we are here again fueling for the next phase😂...respect to u boss for this timeless gift.
Why should I stop listening to this good music, 2024