Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Amen my brother may God bless you all the time
Look sharp kuganiza bhoo
Cadet ali pachintchito kkkkkkkk
Zabodza izi sindinu wa mcp ndimbava ija yakuchitipi iyi
Mfana wotsogora uyu ,,,( wwdulidwe)😅
Well done God bless you.
Mafana a sharp ndi amenewa Kumaziwa kuti deal mbola yiAli Smart nfanayu....
Very good
Kumeneko ndiye kubwera anyamata anzanga. Let's not be used by politicians guys.
Mau ali mu uthengau akunga ulaliki. Kuwatsata ngobweretsa mtendere. Zitengera kwa okachita ziwawao mmene awalandilire pakuti chisankho nchamunthu payekha.
Amwene ulemu wanu afana oganiza bhoo, amangokugwiritsani ntchito koma akakupwetekani samaonekapo
Ndiweyo mwana oganiza bhooo kwambiri tizakulembe ntchito Ndife a DPP ZIKOMO KWAMBIRI MULUNGU AKUDALITSENI CHIMWENE
Zamanyi ndizabodza uyu mbuli yachambechabe
Mwamudziwa bwanji kuti ndi wa mcp mabodza amenewo .zauchitsilu mukupangaapazi palibepo.wa dpp ameneyo ifeyo ngati akusalima sitipanga zosokoneza
Osamalora zopusazi azipanga yekha chimwendo chimunthu choyipa
Thx for informationGod z not James,,
Kumwamba kuli Mulungu, ziululan tiyen nazo, anthu ot mukut boma ndi lomwelo chomalimbana ndi osutsa nchan,
Koma ndipo Inu mulungu atipulumutsa mulungu si Lazaro
Ndichisunga moyo ichi chapachitipi akungoufuna kutchuka zaziiii
Ukatumidwa kuzoyipa ndibwino akakudule mwendo uve kuwawa
Ma witness akumangidwa kwakwe chimwendo ndiomwea nkhani yake sitizachedwa nayoso.....Will just be playing these audios 😅😅😅😅😅
Iweyo ndiwe nyamata woganiza bwino kwambiri pitiriza maganizo amenewo ndikukuthokoza kuchokela pansi pa mtima wanga komaso pansi pa mitima ya amalawi onse ambuye mulungu apitize kukuonjezela maganizo ndi mphamvu zoganiza mpaka moyo wako onse
Ameneyo ndi oganiza boooo.
Waganiza mofwasa Pala ukuneneska , think twice before you do.
Ndipo. zoona,.. nchimwene,..,mulungu.... akudalitse
Uzigenda agogo ngati amenewa kufuna Kupata tsokatu
Mukusowa zo look ankhula eti ndinu zitsilu kwambiri panganibpost zinthu zothandiza komaso zazeru
Ok
Anyamata inu mwaganiza bwino kwambili .Milandutu sogonela mukhonza kupanga ziwawa lelo koma milandu imakhalapo pangatalike bwanji
Emeni.mulungu.ndiwabwino..amapanga.zimenezo.akudalise.mulungu,,,,,,,,nyamata
Kuteloko omwe akuti zabodzawa naoso anali gulu limwelo munya muona mukamuze masita wanu wakulu mutu chimwendo kuti mulungu akusakazani nose athu oipa inu
Wabodza uyu chindere
Chimwendo banda mimba yaikuluyo .Abwana ako achokapo iwe wasala ukufuna usokomeze ziko ili
Asamalole ayi ziwayipisila mbili anyamatao azipitayekha chimwendo kunseuko
Sure
Amen
Akanakhala kuti anyamata onse ndioganoza bhooo chonchi bwenzi enawa atasiya zaupandu
Mwayamba ku poster zabodza tikutsikanitu pantumbo panu a nyasa box
Iweso nde ndi mbunzi ya munthu
😂😂😂😂mabodza,
Ku opposition nkowawadi... Leilani ndpo smunat
Anyamata pepani tisegende atsogoleli zamawa sizidziwika
MCP lero munganene chani
Wabodza iwe chifukwa chani osampanikiza kuti awulule watuma kuti ndindani wabodza uyu
Amen my brother may God bless you all the time
Look sharp kuganiza bhoo
Cadet ali pachintchito kkkkkkkk
Zabodza izi sindinu wa mcp ndimbava ija yakuchitipi iyi
Mfana wotsogora uyu ,,,( wwdulidwe)😅
Well done God bless you.
Mafana a sharp ndi amenewa
Kumaziwa kuti deal mbola yi
Ali Smart nfanayu....
Very good
Kumeneko ndiye kubwera anyamata anzanga. Let's not be used by politicians guys.
Mau ali mu uthengau akunga ulaliki. Kuwatsata ngobweretsa mtendere. Zitengera kwa okachita ziwawao mmene awalandilire pakuti chisankho nchamunthu payekha.
Amwene ulemu wanu afana oganiza bhoo, amangokugwiritsani ntchito koma akakupwetekani samaonekapo
Ndiweyo mwana oganiza bhooo kwambiri tizakulembe ntchito Ndife a DPP ZIKOMO KWAMBIRI MULUNGU AKUDALITSENI CHIMWENE
Zamanyi ndizabodza uyu mbuli yachambechabe
Mwamudziwa bwanji kuti ndi wa mcp mabodza amenewo .zauchitsilu mukupangaapazi palibepo.wa dpp ameneyo ifeyo ngati akusalima sitipanga zosokoneza
Osamalora zopusazi azipanga yekha chimwendo chimunthu choyipa
Thx for information
God z not James,,
Kumwamba kuli Mulungu, ziululan tiyen nazo, anthu ot mukut boma ndi lomwelo chomalimbana ndi osutsa nchan,
Koma ndipo Inu mulungu atipulumutsa mulungu si Lazaro
Ndichisunga moyo ichi chapachitipi akungoufuna kutchuka zaziiii
Ukatumidwa kuzoyipa ndibwino akakudule mwendo uve kuwawa
Ma witness akumangidwa kwakwe chimwendo ndiomwea nkhani yake sitizachedwa nayoso.....
Will just be playing these audios 😅😅😅😅😅
Iweyo ndiwe nyamata woganiza bwino kwambiri pitiriza maganizo amenewo ndikukuthokoza kuchokela pansi pa mtima wanga komaso pansi pa mitima ya amalawi onse ambuye mulungu apitize kukuonjezela maganizo ndi mphamvu zoganiza mpaka moyo wako onse
Ameneyo ndi oganiza boooo.
Waganiza mofwasa Pala ukuneneska , think twice before you do.
Ndipo. zoona,.. nchimwene,..,mulungu.... akudalitse
Uzigenda agogo ngati amenewa kufuna Kupata tsokatu
Mukusowa zo look ankhula eti ndinu zitsilu kwambiri panganibpost zinthu zothandiza komaso zazeru
Ok
Anyamata inu mwaganiza bwino kwambili
.
Milandutu sogonela mukhonza kupanga ziwawa lelo koma milandu imakhalapo pangatalike bwanji
Emeni.mulungu.ndiwabwino..amapanga.zimenezo.akudalise.mulungu,,,,,,,,nyamata
Kuteloko omwe akuti zabodzawa naoso anali gulu limwelo munya muona mukamuze masita wanu wakulu mutu chimwendo kuti mulungu akusakazani nose athu oipa inu
Wabodza uyu chindere
Chimwendo banda mimba yaikuluyo .
Abwana ako achokapo iwe wasala ukufuna usokomeze ziko ili