KOMA CHAKA CHINO TILIMA? ~~ BRIAN BANDA NDI SAM KAWALE ~ MINISTER OF AGRICULTURE ~ KUNACHEMA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 66

  • @DeborahGeorge-g3i
    @DeborahGeorge-g3i 12 годин тому +3

    Km group ya anthu kubwereka 1,000,000 nde ndchimodzimodzi nd matumba awiri a AIP😅😅😅😅

  • @HamzahTwaib
    @HamzahTwaib 16 годин тому +5

    Ingomvomelezani kt mwalephela kugaila anthu fertilizer musati mango masamba zija ndizowona zomwe anthu alankhulala zija kt muli be fertilizer zija ndinu zisilu bwanji kd mukumatitenga ngat ife ndi anthu ogona kt muzingotinamiza et mbamvaaa

  • @robertharawa9203
    @robertharawa9203 9 годин тому +1

    Alomwe agundika kutukwana

  • @RazackSongiso-y6s
    @RazackSongiso-y6s 15 годин тому +8

    Nde pakusiyana pati pa mathumba awiri out of 200 thausand ndiwe garu kwabasi ukuona ngt anthu alibe masamu

  • @siliyapatrick8932
    @siliyapatrick8932 15 годин тому +1

    Nzeru zanuzo a minister ndi zopoila coz ,1 million devide by 5 it's = 2 bags of fertiliser per person. Of which is expensive than AIP.

  • @ElizabethMwale-z3s
    @ElizabethMwale-z3s 15 годин тому +3

    Koma ndalama zonsezo mwatchula Mr kawale ife osauka sizikutipezabetu tili mbuu mmidzi muno akutidyera ndalama zathu ndi ndani? And this is October kuli AIP sikukudziwika. Kummwera kuno tangotsala ndi 2 to 3 weeks kt mvula igwe. Manyazi bwanji kunamiza dziko.

    • @DeveliousMasinja
      @DeveliousMasinja 13 годин тому

      You must do action kuti zikupeze ,, kuteloko chakachino anthu ena azipexa

  • @LuciousRhodrick
    @LuciousRhodrick 9 годин тому +1

    Kod ndiazizake ndiaja anagula fertilizer ku butchery aja??

  • @LawrenceNdala
    @LawrenceNdala 11 годин тому

    Nice articulation, Minister.

  • @takondwajamesdickson7917
    @takondwajamesdickson7917 Годину тому

    Mbamva inu kwanu kwatha basi muchoke tione zina mukungoyankhura mfundo zopepera basi ndalama zamisonkho yanthu mukungoba basi amphawi kumawanamiza . Achakwerawo aiwala zomwe ankatilonjeza zija eti.

  • @Dan44-x5b
    @Dan44-x5b 5 годин тому

    Just want to know if these are loans or grants to Malawi?

  • @AllanKqminga
    @AllanKqminga 7 годин тому

    Ambuye tithandizeni wakumuzi uja wafa ndinjala bas

  • @MacfelsonMunthali
    @MacfelsonMunthali 16 годин тому +2

    Well said Mr minister, however my question, do we have the market

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 16 годин тому +1

    A Minster Kawale, mukuti forex yikusowa nanga zoyendela maulendo zimapezeka kuti

  • @saulbipa6882
    @saulbipa6882 16 годин тому +1

    Anthu 5 agwirizane kukatenga 1 million, , meaning 200 tau per person, amenewo si matumba awiri?
    Ndale zanuzi nzaboza a MCP and neef.

  • @RodrickBonongwe
    @RodrickBonongwe 13 годин тому +1

    Brian ukumvesera zopusazo ziitana anthu amene azikamba zothandiza Zimene akukambazo ife sitikuziwona

  • @LeonMaluwa
    @LeonMaluwa 9 годин тому

    Agricultural sector has registered tremendous positive impacts yet the country is still languishing and starving are you sure Mr Minister?

  • @SaulZefinat
    @SaulZefinat 14 годин тому +2

    Ndie mukuibwereza dala malo amodzi modzi video. Timadziwa kuti mumafuna kumuipisa munthu. Koma amalawi ozindikila pano sadalila AIP chifukwa or anthu alandile zimenezi amatha mkugulisa. So kwa ife amane focus yathu ili ku ulimi. Timadalilaso manure aziweto zomwe tili nazo.mpaka timakolola phwamwamwa chosecho AIP sinatikhudze.
    Boma ndilomweli tikupasan mpata mu 2045.

  • @patesnkajenda4258
    @patesnkajenda4258 4 години тому

    Soka kwaine sinapiteko ku sukulu kamba kaumbwawi kom ngat mister of agriculture sakiganiza zongotsitsa mtengo wa feteleza kut mulimi azitha kugula bobho alibbusy kumangokamba zandalama ife tilibe😅

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 7 годин тому

    Uyu ndi galu kwambasi

  • @VigourNasangwe
    @VigourNasangwe 4 години тому

    Nduna yakuba iyi palibenso chomwe akunena apa nzautsiru basi

  • @stevendaluni
    @stevendaluni 16 годин тому

    Kuti dzisiru kokatenga ndalamadzo instead Kuti inu mukagulire fertilizer kapena kukapereka kumakapani a fertilizer Kuti asike
    62 billion
    70 billion
    Ndiye Kuti chani😢

  • @IshmaelNgeyani
    @IshmaelNgeyani 8 годин тому

    Aaaaaaa umati Anthu asabereke mukungodya ndalama agalu inu

  • @mphatsomalenga
    @mphatsomalenga 14 годин тому

    From the interview zaonetsa kuti fertiliser kulibe plus mavuto Ku AIP ngochulukaso

  • @richardmasina5454
    @richardmasina5454 7 годин тому

    Anthu opusa awa anenazi zosanveka wht not take that money kupititsa kokagura fertilizer then nkumutsitsa with 50% kuti aliyese athe kufikira than ngongole zoti sionse omwe angapatsidwe

  • @FiskaniLungu
    @FiskaniLungu 4 години тому

    Koma minister uyu mabatile ake akuyankhula ngatii position iyi wayitenga zulo

  • @timothymhone2340
    @timothymhone2340 2 години тому

    Anthu ali busy kutukwana azawo akutenga ndalama kumapangira business

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 14 годин тому

    Ngati pali unduna umene kuli bodza lochuluka komaso umbava ndi umeneu ndipo nduna imene ndi imene yabweletsa njala ku malawi

  • @patesnkajenda4258
    @patesnkajenda4258 4 години тому

    😂😂😂😂 Mr tell us how many people did get that money chomwe chilipo ndikudya ziteze bassss

  • @andreabanda7838
    @andreabanda7838 11 годин тому

    Mmmm kukometsa pa kamwa abale. Nthawi ndi ka mnyamata. Zioneka.

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso 10 годин тому

    Fotsek! 4500 amanena uja ndameneyu

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 13 годин тому

    Mwakanika kukwanitsa kukhala ndi chakudya in four years do you think u can manage in less than a year 😢😢???

  • @stevendaluni
    @stevendaluni 16 годин тому

    Alp is Alp don't change where to get those money

  • @EdwinZiwa-x2g
    @EdwinZiwa-x2g 13 годин тому

    Wakuba uyo ndi chakwela wakeyo

  • @RazackSongiso-y6s
    @RazackSongiso-y6s 15 годин тому +1

    Kd akati munthu azikhala ndi fetereza okwanira akutanthauza chani

    • @DeveliousMasinja
      @DeveliousMasinja 13 годин тому

      Akuti fertilizer uja matumba awiri mutha kuwapanga kukhala ten ndiekuti mulima malo ochuluka

    • @ShakiraJackson-x8w
      @ShakiraJackson-x8w 7 годин тому

      Kkkkkkkk am confused ​@DeveliousMasinja

  • @MakhandaSandikonda
    @MakhandaSandikonda 13 годин тому

    Mpumarang

  • @ShameemChimenya
    @ShameemChimenya 15 годин тому

    vuto bomali ndilosamva zomwe amalawi eni akufuna tinati zopereka zaulelezo zisiike tangotengani ndalamayo mukapereke kwa Admarc anthu azigula motchipha basi njala yatha

  • @PhonexDaniel-t5v
    @PhonexDaniel-t5v 15 годин тому

    Awa apapa akuonjezela njala osat kuthesa mbuz athu imoz ithandiza chani. iii tafa basi

  • @AdamuKasimu-x5o
    @AdamuKasimu-x5o 13 годин тому

    Patumbo pamako phwokophwoko pamaphwisipo

  • @DanielDoctor-t3p
    @DanielDoctor-t3p 15 годин тому

    Iiiiiiii dziko lathu boma ili ayi or mukati boma lomwero za manyazi kwambiri

  • @HamzahTwaib
    @HamzahTwaib 16 годин тому

    Ndiwe galu kwabasi

  • @BraviousPhiri
    @BraviousPhiri 16 годин тому

    From AIP to Katapira . Neef izakulanda nyumba kkkkk

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 16 годин тому

    Greedy ndiyomwe ikupangisa malawi azikhala ndi njala anthu oyipa inu

  • @HassanSaid-q8q
    @HassanSaid-q8q 16 годин тому

    Agalulu inu opanda chifundo

  • @GeorgeKambwiri-xr9ri
    @GeorgeKambwiri-xr9ri 15 годин тому

    Zakumbolo basi

  • @stevendaluni
    @stevendaluni 16 годин тому

    Mufuna kuchosa subseed thus points
    Anthu oipa

  • @MagretPhiri-z3b
    @MagretPhiri-z3b 15 годин тому

    Bodza likuchita kutuluka kamwa malo mwa million mukuti thousands ai xikm 😅😅😂 tinamizeni km mau anuwa tawasunga

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 16 годин тому

    Chitsiru iwe mbamva yachabe chabe ulibe choyankhula galu iwe

    • @GreshamKadzembe-tn8cq
      @GreshamKadzembe-tn8cq 12 годин тому

      Eeeee munayambana naye chani a bwana, ngati muli awuletsi olo at akukupatsani zawurere dzaka teni simungapindure

  • @HassanSaid-q8q
    @HassanSaid-q8q 16 годин тому

    Iwe utilakwisa

  • @PgodfreyBanderouss
    @PgodfreyBanderouss 15 годин тому

    Kodi mwati awawa ndi nduna ya ulimi kapena wankulu wa neef??akanangofotokoza za ulimi ifetu zoti anthu akulandira ngongole sitikudzidziwa nde tikuchosa Chanel yi mwina tingonverako nyimbo

  • @YusufJames-f5f
    @YusufJames-f5f 17 годин тому

    Zachamba

  • @stevendaluni
    @stevendaluni 16 годин тому

    Koma mbudzi idzi you have still talking about covid koma kungoti mumabera alimi afodya pobwedza ngongole dzanuzo

  • @JalitahKatumbu
    @JalitahKatumbu 15 годин тому

    A bag of money it won't heal poverty on your statement you only talk about money money teach people to discover them self.

  • @RencoMandah-vd2yp
    @RencoMandah-vd2yp 7 годин тому

    Palibe company ya kunja ingalole ma kwacha zimenezo ndizaboza

  • @stevendaluni
    @stevendaluni 16 годин тому

    Kuti dzisiru kokatenga ndalamadzo instead Kuti inu mukagulire fertilizer kapena kukapereka kumakapani a fertilizer Kuti asike
    62 billion
    70 billion
    Ndiye Kuti chani😢