Apa mwaoneka opusa kwambiri!!! Pepa pitaso ku school! Language ya ma bantu ndi yofananafanana, ife tonse ma Bantus timafanana chifukwa tinachokera madera ozungulirana! Ndipo za Anabel ndi chilankhulo zagwirizana pati nyungwi iwe!!! Ndipo ambrera ndi mwafuli osati sumbulera ukunenayo!
Akatundu Bambo !!!!!! Mzwanya pa History ✍️✍️ we learn a lot thru this best TV. Ulemu upite kwa Makolo Onse abereka ndi kulera inu Brother from BAKILI MULUZI TV. Stay safe ✊ Stay blessed 🙏and protected.
wa bakili muludzi tv ine munthu uyu ndimalakalaka nditazamuona ndithu chifukwa amandigomesa..... kwambiri program iliyose yomwe amabwelesa ndimapezeka kuti ndaphudzila china chake akulu amenewa mulungu aziwadalisa ndithu🎉🎉🎉🎉ulemu wanu
Poyamba ndmaganiza ngat ndiwe dolo koma panopa ndazindikira kuti ndiwe mbuzi. Zoti bantu people are related moti sukudziwa? So if the people are related, it means their languages should be related as well. Ndiwe mbuzi, amene amakutsatirawo mbuziso. Muzinamizana mbuzi zokhazokha!
Experience is the best teacher. And like to hear it also when you say "history is the best teacher". BIG UP BOSS MAN 💪💪💪💪💪💪NUCLEAR WEAPON 🚀🚀🚀 IN THE WORLD HISTORY AND EVENTS. BAKILI MULUZI FOLLOWERS COME HERE 👍👍👍👆👆👆👆
@@MadalitsoEvanceMatemba-e4c Ya, ayamba kuonera kusazindikira. There is no relationship between language and the elections officers. Aziyankhula sensible things ngati palibe aziyankhula best way is to be quiet kkkkkk
Sir, I just want to thank you for the excellent work you put on by teaching us every time you post on this platform. You are very intelligent and well informed. Keep up the good work.
Gyz Muno mu Africa timalankhula zinthu zofanafana uyu amakamba chilungamo Koma Iz wabwera nazo lero palibepo phuziro Muno ndimu Africa 🌍 ndi Malo amodzi that's why timalankhula zofanafana
Eu acompanho vos apartir de Moçambique, Línguas africanas tem origem Bantu, por ser da mesma origem, tem algumas palavras em comum, isso não torna uma língua falsa à outra. Mesmo na Europa tem algumas línguas de origem latim como o caso de língua portuguesa, espanhol, francês, alemã,.tem algumas palavras em comum.
Zoona koma osayiwala kuti achewa anachita kubwera kuchokera Ku Zaire komwe ndi kwawo Kwa Chiswahili. Komanso chilankhulo chimasintha malinga ndi kusakanikilana Kwa anthu. Palibe ntundu omwe umaposa unzake ndi iko komwe poyamba anthu ankalankhula chilankhulo chimodzi. Bali Muluzi TV yomweyi inaphunzitsa zimenezo
Kodi tsopano mwayamba kudana ndi chilakhulo koma zikuvutani dziko lapasi mau ambiri amafanana izi ndi za ziiiiiiii mdani wako palibe zomwe anapange ndi kukhala chabwino
Aaah topic iyiyi nde ndiyozizila. Zilankhulo zimapangidwa choncho kumene ka
Boma ndilomweli basi. Bg up BM tv. British Oversea Military Attachee (BOMA) APA nde mwandithetsa nzeru hevy
Kkkkk
Apa mwaoneka opusa kwambiri!!! Pepa pitaso ku school! Language ya ma bantu ndi yofananafanana, ife tonse ma Bantus timafanana chifukwa tinachokera madera ozungulirana! Ndipo za Anabel ndi chilankhulo zagwirizana pati nyungwi iwe!!! Ndipo ambrera ndi mwafuli osati sumbulera ukunenayo!
Akatundu Bambo !!!!!!
Mzwanya pa History ✍️✍️ we learn a lot thru this best TV.
Ulemu upite kwa Makolo Onse abereka ndi kulera inu Brother from BAKILI MULUZI TV.
Stay safe ✊
Stay blessed 🙏and protected.
Chewa wadana naye ASE,,,tatiuzeko history ya Lomwe
@@MandalaChaona kkkkkkkk nosenu mburi zoti chiyankhulo chinapangidwa kuchoka ku chiyankhulo chizake simudziwa kkkkkk mburi zakum'mwera
@@halordbwato mburi iyi osatangwanika nayo
Ameen
Koma tv imeneyi Allah akudaliseni big mn❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
History is the best teacher indeed 👏
Bakili Muluzi tv is the best forever ❤
Nkulu Uyuu Amatiphuzitsa Zambiri Ndipo Apitilize ❤❤❤❤
Mbwerela zinamuchulukira nkuluyi.
wa bakili muludzi tv ine munthu uyu ndimalakalaka nditazamuona ndithu chifukwa amandigomesa..... kwambiri program iliyose yomwe amabwelesa ndimapezeka kuti ndaphudzila china chake akulu amenewa mulungu aziwadalisa ndithu🎉🎉🎉🎉ulemu wanu
The guy knows history abwana
Akamuna
Thanks boss
Uyu katundu
Poyamba ndmaganiza ngat ndiwe dolo koma panopa ndazindikira kuti ndiwe mbuzi. Zoti bantu people are related moti sukudziwa? So if the people are related, it means their languages should be related as well. Ndiwe mbuzi, amene amakutsatirawo mbuziso. Muzinamizana mbuzi zokhazokha!
Kupatula kumutukwanako kmano wamuuza bwino zilakhulo zonse za ku African zinachokela kwama bantu
Today i believe that u are owner of history GOD BLESS YOU MORE
He is the best Malawian Historical teacher, your the best Bakili Muluzi TV God bless you.
All the best Bakili Muluzi Tv 🎉🎉
Experience is the best teacher. And like to hear it also when you say "history is the best teacher". BIG UP BOSS MAN 💪💪💪💪💪💪NUCLEAR WEAPON 🚀🚀🚀 IN THE WORLD HISTORY AND EVENTS.
BAKILI MULUZI FOLLOWERS COME HERE 👍👍👍👆👆👆👆
Nthawi zinazake ndibwino kumva chimene mzathu akuchidziwa, enafe zimene zukambidwadz tinamvapo ndithu mot kwa amzathu amene timateng history ku secondary kujah tichitila umboni ndithu✌🏼✌🏼✌🏼✌🏼
Zopanda ntchito
Aaah Kumayenda...Muno Mu Africa ziyankhula zambiri zili ndi Mawu ofanana ambiri ndipo izi sizitanthauza kuti chiyankhulo China ndicha Fake Ayi...Ndale Zisationetse Uchitsilu bwana.
Ndiponsotu chiyankhulo chalakwa chiyani osangonena point bwanji😂
Adawa mfundo zatha 😂😂😂😅
@@MadalitsoEvanceMatemba-e4c Ya, ayamba kuonera kusazindikira. There is no relationship between language and the elections officers. Aziyankhula sensible things ngati palibe aziyankhula best way is to be quiet kkkkkk
Mesa akufuna tiziwe
@@tiyachisale9075 Ndiye iye akuyankhuka Chichewa chomwecho kwinaku akuchilotsa ndale. Amatero kuphunzitsako? Kkkkk
U are a Best teacher ever
Bwana bakili muluzi TV inu ndi mwala wa gold ❤
Kkkkkkkk zayamba ukusowa zoyankhula, ndwe mbuli iwe
Mbuli ndiiwe..
Ukumupanga follow ngat Ali Mbuli bwanji, locate your own page aise
@@mbirimalowandipo anzeru atsatira bwanji mbuli, osampanga unfollow
Mwana wanga wa zaka 10 akukuseka kuno.....😂😂😂😂😂 history yambani kuitsana ndi BMTV....ife nyumba mwathu history ndikudya kwathu
Osangogona ndi misala yako wachila week yatha usaiwale
ngakhale bambo ako history ya bakili muluzi tv sangaikwanitse
Sir, I just want to thank you for the excellent work you put on by teaching us every time you post on this platform.
You are very intelligent and well informed.
Keep up the good work.
❤❤❤❤ ziyakhulo ndichoncho,poyamba chinali chimodzi paja osaiwala
That's why I follow you ,Bakili Muluzi tv,Yu are the best,,,,,, history is the best teacher
Watching from Venezuela in Caracas 🇻🇪
Mkuluyu palibenso indeed history is the best teacher keep it up good work never give up timakunyadirani Bakili Muluzi TV stay safe ❤❤❤❤
Ulemu wanu bwana olo mutamatulutsa 100 audios pa tsiku titha kumangomvesera the whole day until end😂😂😂😂❤❤❤
Ndimalakalaka ndri first comment km ndimachedwa history is the best teacher 🔥🔥❤️
❤😂
Taphunzila zambili mau okut boma british overseas military attachee
😂😂@@ibraheemkala7581
Nde pa Malawi congress party mwaikapo chani 😂😆
Ndaseka kale😂😂😂..Logo yawo nding'ona😂
BKM TV os the Best Teacher 😊😊
Home of history Bakili Muluz today,..... Live from Lichinga Mozambique 🇲🇿
Home 😭
Hero ov the heroes history is the best teacher big up BM TV❤❤❤
God bless you comrade wathu wa Bakili muluzi TV ❤❤
Best teacher 🔥🔥
Akuku Akuku atuluka ABakili Muluzi TV❤🎉❤
Kkkkkk bakili Muluzi TV big up!!
Gyz Muno mu Africa timalankhula zinthu zofanafana uyu amakamba chilungamo Koma Iz wabwera nazo lero palibepo phuziro Muno ndimu Africa 🌍 ndi Malo amodzi that's why timalankhula zofanafana
History is the best teacher you're the best ever❤
History iyiyi 😂😂😂😂😂Aaaaa African yonse ino mawu amodzi amodzi amafanana
Lets help this channel financially, since we dont have any account details we can watch it even 100 times to keep our brothers going
Our best tv
Ziyankhuro zambiri stem from many other languages, even komwe zikuchokerako nawoso ziyankhuro zawozo ma words amachokeraso ku ziyankhuro Zina.
Ndimbuli munth uyu
Ndale zakumalawi kkkkk apa sapano fight against achewa you can not make a heaven 😂😂😂😂
Koma tiva zambili akhalitse bakili muluzi tv ❤❤ tathaunzo ra boma 😂😂😂 osazandinamiza ndimamutsatila history is the best teacher ❤
Baklil Muluzi TV zikomo ❤❤❤❤❤👍👍👍
Pangolin wen wen 🔥
History is the best teacher sir
Timakudalira brother Koma inu muli ngat mngelo wanthu🔥🔥
Kkkkk KMA nkulu iwe anakonza boma ili lichoke tidzakuone
Iweyo wa bakili tv umadziwa dziyankhulo zingati pakuti umangodziwa chichewa chokha basi
Umatha ntchana Watiuza tanthauzo la Bomba 😂😂😂 olo Chakwera sangadye mwaiwe pa History 🎉🎉
BMTV 🔥🔥 always love you ❤
Ndaziwa Leno tanthauzo last boma kp it up bro
We don't have our own things 😂🤣😅everything we're having isn't for us 😂
Khani yosautsa 😂😂😂😂😂
LONG LIVE BAKILI MULUZI TV 🎉🎉🎉🎉
Following boss and God bless you and protect you
sikomo kwambiri big brother ife ayawo tinabwela ndisindu ku malawi koma achakwera amasitenga ngati dolo 😮 kwambiri 😊
Inu ndachitsilu akulu ndakuonani zelu mulibe
Uyuyu ndi shasha big up
Bola tikumvana .... John Tembo ndi Genius 😂
This is pure history....... ulemu wanu boss ✊
You're most welcome brother man!!
Will still love you bakili muluzi TV 📺 go forward big mn
My best TV forever 💗💗🎉🎉
Keep it up good work Mr ❤
Eu acompanho vos apartir de Moçambique, Línguas africanas tem origem Bantu, por ser da mesma origem, tem algumas palavras em comum, isso não torna uma língua falsa à outra. Mesmo na Europa tem algumas línguas de origem latim como o caso de língua portuguesa, espanhol, francês, alemã,.tem algumas palavras em comum.
History is the best teacher ever 😂
Bakili Muluzi wooooooooyeeeeee ❤
Zoona koma osayiwala kuti achewa anachita kubwera kuchokera Ku Zaire komwe ndi kwawo Kwa Chiswahili. Komanso chilankhulo chimasintha malinga ndi kusakanikilana Kwa anthu. Palibe ntundu omwe umaposa unzake ndi iko komwe poyamba anthu ankalankhula chilankhulo chimodzi. Bali Muluzi TV yomweyi inaphunzitsa zimenezo
😂😅 Better I knew B. O. M. A when I was at secondary school 😂
😂😂😂Eti komanso it was in standard 8 iwe ku social studies first b4 secondary school
History is a best teacher
Let's gathering here
I love your story bakili muluzi TV
😢😢💯 Mbutula,,,,kabudula
We're from Tz indeed 😅😅
Pa dziko lapansi, chiyankhulo chirichonse chiri ndi mau obwerekera. Even in English, some of the words were borrowed from Latin, French and German.
@@petertengani ndipo zoooonadi
History is the best teacher Ngakhare chikangawa akuziwa za idzi
katundu omanga ndimawaya bakili muluzi tv
history is the best teacher
History I the best teacher
Chonsecho ukulankhula chichewa chomwrcho 😂😂😂
Ng,oma yolankhulitsa yang,ambika
Zina amangozindikira wayankhula. I don't see any problem with the language. Ngati mfundo zatha timakhalakaye chete
The best teacher my Tv
Uyu nde mphunzisi wankulu❤❤
History is the best teacher 👊
Vuto la umbuli that's bantu language,iwe osasitha bwanji
Best TV Bakili ❤
Continue educating us pls
Iweno ukufuna uzitinamiza ndiye chichewa ndichiticho ziyakhulo zimafanana kumene osati anabera ayi
Inuso ndale mwafika nazo pochiitsilu,,,,sizikuthandizani izi
HISTORY IS THE BEST TEACHER!!!!!!! UMAKWANA IWEYO USAZAFE
Your respect sir💪👌👊❤️🔥🔥🔥💯
😂😂😂😂😂😂😂😂 muwawunse anthu zakaziwa zaimzii
Km iweyooo ndakatundu 😂😂😂
*Open our fckin eyes king🎉🎉* mmalawi munthu ovetsa chisoni
Almighty God is all_knowing God bless u broh
Lero ndadziwa kuti History is the best teacher di
❤❤❤😂😂😂 big Up brother
Well come back comrade bakili muluzi TV osaopa osatopa osafooka comrade
❤❤❤❤❤ Iwe ndikatundu
History is the best teacher 🎉🎉🎉🎉
Kkkkkkk kkkkkkk kkkk😂😂😂😂 ndawona kuti ndale za kusokoneza zelu akulu zilakhulo ambili zimafana musatinamizepo apa ayi
Big osayiwala tag me next year need to have a cup of coffee with you ❤❤❤🎉🎉🎉
Apandiye mwanama bro zilakhulo zimangofanana basi
Number one b❤❤❤❤
Our teacher the best teacher than zikhale
Ine zikomo Wambuye kundapanda ankulu awa bwezi tisakuziwa zomwe timayakhula
Kodi tsopano mwayamba kudana ndi chilakhulo koma zikuvutani dziko lapasi mau ambiri amafanana izi ndi za ziiiiiiii mdani wako palibe zomwe anapange ndi kukhala chabwino