IFE A MALAWI PANO ZÀTHU NDI KULAPA KWA AMBUYE YESU KUTI ATIKHÙLULUKIRE MACHIMO.ATHU CHIFUKWA CHILIMA ANATIPITITSA KWA CĤKWERAYU .PANO TIKUVUTIKA..AMBUYE YESU. TIOMBOLENE AMEN..
Mau koma amenewo. Ndalama zikudyedwa ngati masuku ndi anyani mankhwala mzipatala mulibe misewu yonyansa . A small country easy to maintain koma kulephera. Zachisoni
TIYENI NAZO ZOMWEZO A COMRADE LUFEY9 PHIRI KUTI.TICHOTSE MISSION OF INQUIRY YABODZA IMENE .CHAKWERA ACHITA NDI YA NYENGO .AMEN..TITHANDIZENI A COMRADE PHIRI..IFE ANTHU TIKHALA PAMBUYO PANU.AMEN. KOMA MADEMO. ASATSOGOLERE A MAMIWA NDI BONI KALINDO KOMA MARETIRED A ARMY NDI APOLISI..MUYAMBITSE IFE TIKHALA PAMBUYO PANU CHONDE X2 MALAWI AKUFA AKUONA..AMALAWI.KUMAZUNZANA OKHAOKHA
A malawi panopatu zafika pokwana ,angakhale ma Activists athu ndi a nkhambakamwa ; olo ine ndimadzifunsa kuti ,kodi wochenjera anali Timmothy Mtambo yekha basi. Kodi a AP M ndiye analakwa chani?
No sense madermo akulu mkulembetsa mkaundula wa vote nthawi yathera kale mmalawi weniweni ndi amene akut voti yanga ilindimphamvu because alindi Masa akuona pomwe malawi wafika tiyeni tialimbikitse anthu kuzavota osati ziwawa ayi
ndimomo ife amalawi ogona ziko tangolisiya anyaniwa akuononga bass apa chabwino palibe
IFE A MALAWI PANO ZÀTHU NDI KULAPA KWA AMBUYE YESU KUTI ATIKHÙLULUKIRE MACHIMO.ATHU CHIFUKWA CHILIMA ANATIPITITSA KWA CĤKWERAYU .PANO TIKUVUTIKA..AMBUYE YESU. TIOMBOLENE AMEN..
Mau koma amenewo. Ndalama zikudyedwa ngati masuku ndi anyani mankhwala mzipatala mulibe misewu yonyansa . A small country easy to maintain koma kulephera. Zachisoni
TIYENI NAZO ZOMWEZO A COMRADE LUFEY9 PHIRI KUTI.TICHOTSE MISSION OF INQUIRY YABODZA IMENE .CHAKWERA ACHITA NDI YA NYENGO .AMEN..TITHANDIZENI A COMRADE PHIRI..IFE ANTHU TIKHALA PAMBUYO PANU.AMEN.
KOMA MADEMO.
ASATSOGOLERE A MAMIWA NDI BONI KALINDO KOMA MARETIRED A ARMY NDI APOLISI..MUYAMBITSE IFE TIKHALA PAMBUYO PANU CHONDE X2 MALAWI AKUFA AKUONA..AMALAWI.KUMAZUNZANA OKHAOKHA
Ndipo khaniyo ndiyoona amalawi tinagona kumangoyang,anira mavuto kataoni kasundwe kovesa chisoni koma matama
I don't know zomwe timapangadi amalawi 😮
A malawi panopatu zafika pokwana ,angakhale ma Activists athu ndi a nkhambakamwa ; olo ine ndimadzifunsa kuti ,kodi wochenjera anali Timmothy Mtambo yekha basi. Kodi a AP M ndiye analakwa chani?
Ndipo mmene kulili kumalawi kukhala ku SA bwenzi kuli mademo oopsa
Eti. eti tikungonkhala bas. Kuzankhala pa line akudikila mafuta kma osachitapo kanthu kumangokhala bas. ayi ayi amalawi. Tatiyeni. Tidzike. Pano. Pali zambiri zoti tikwiye nazo. amalawi. Tatiyeni. Tikwiye patonkha. Mosatsatilaso adale or aboma tonkha tiyeni
😂😂😂😂😂😂 koma aisey wandiseketsa koopsya ine si wa mcp koma apapa ndieee mmmm zambiri ndi ukupala
Koma kumbwambwana komweko😂😂