NDIKONDA MULUNGU - THOKO SUYA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 201

  • @RocianG.ksankhulani
    @RocianG.ksankhulani 4 місяці тому +3

    Mulungu wanga ndiye wachifundo basi ndipo ndimkonda iye andichotsere tchimo ine Mulungu 😭 popeza ndilibe chomwe ndizabweze 🧎

  • @margretzimba8730
    @margretzimba8730 20 днів тому +1

    1 Ndikonda Mlungu pomva Mbuye
    wanga
    Amva pemphero ndi kulira kwanga,
    Namatchereza khutu nditapfuula,
    Andithandiza, nandipulumutsa.
    2 Mulungu wanga ndiye wachifundo
    Ndiwolungama mtima ndi wabwino;
    Apulumutsa anthu akufoka,
    Akathandiza nkhawa imachoka.
    3 Mtimanga, bwera kuti upumule,
    Wakuchitiranso zokoma Mbuye,
    Wakuchotsera imfa ndi misozi,
    Ndingakhumudwe asungira phazi.
    4 Nditani ine kubwezera Mbuye
    Zokoma zonse anandichitira?
    Chipulumutso chake ndidzatama,
    Ndinalumbira zija ndidzapatsa.
    5 Imfa ya anthu ake imkomera,
    Awalandira m'nyumba zokonzeka,
    Mbuye, kapolo wanu ndipereka
    Nsembeyi yonga yanu, ndine
    ndekha.
    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤my favorite 🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @RuthEverson-lp8sr
    @RuthEverson-lp8sr 12 днів тому +1

    Ndili pano ndili ndingongole za anthu zoti ndufunika ndipereke i dont know kut ndizitenga kut but my God in faithful , kiss my comment i will back with a big testimony

  • @rabeccanchocholo6545
    @rabeccanchocholo6545 2 роки тому +34

    Inuyo ndi Mayi busa🙌...keep on blessing us. There is a certain life and anointing that is added to the hymns when you sing them...hits differently and ushers me into worship. Thank you a hundred times

  • @EllenChimwaza
    @EllenChimwaza 4 місяці тому +3

    Nyimbo iyi ndichakudya changa chauzimu usiku uliwonse ndisanagone

  • @ellenngalande2963
    @ellenngalande2963 Рік тому +2

    Nditani ine kumubwezera kwake Ambuye pazokoma zomwe amandichitira tsiku ndi tsiku

  • @user-dw9hx3vo9y
    @user-dw9hx3vo9y 7 місяців тому +2

    Today ndalota nyimbo iyi❤ wat a message 😭😭Ambuye mukule ine ndichepe

  • @salvationministries745
    @salvationministries745 Рік тому +2

    Ifa ya anthu ake imkomera wow !!!!apapa ineyo pamandikhuza

  • @piliratembo9626
    @piliratembo9626 Рік тому +27

    I have been coming here everyday for 2 months now and each time l listen to this song, I get a new interpretation. I have come to appreciate what God has done in my life. Indeed, God is always with us regardless of what we are going through. May God bless everyone praising and thanking Him for everything He keeps doing for His children.

  • @ruthnangwale
    @ruthnangwale Рік тому +2

    Mulungu wanga ndinu wa chifundodi💯 Mukathandiza nkhawa zimachoka

  • @raphaelpilolo3904
    @raphaelpilolo3904 Рік тому +2

    Mai busa mulungu aonjere phabvu Zina mwainu 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌ineo ndinu mdalitso

  • @user-li3ok4pq9b
    @user-li3ok4pq9b 8 місяців тому +1

    Nditani Ine kubwezera mbuye pa zokoma zonse wandichitira....wandisungabe ndi moyo🙏

  • @alicenankhuni9887
    @alicenankhuni9887 Рік тому +3

    Nditani ine kum'bwezera mbuye🥺🙏🙌

  • @norahmchenga1412
    @norahmchenga1412 3 місяці тому +1

    Ndikamamva nyimbo iyi imandikumbutsa my late father amakonda ngakhale abusa pa maliro awo ananena kt ankakonda nyimbo iyi pitilizani mum kutitsitsimutsa

  • @rosephiri5531
    @rosephiri5531 Рік тому +3

    Ndikamamva nyimbo zanu mama ndimachilitsidwa muzambiri, muli utumiki wamphamvu

  • @GraceSamson96
    @GraceSamson96 Рік тому +1

    Oh yes Lord🙌
    Nditani ine kum'bwenzera mbuye 😭😭

  • @user-yi7sp4hz1j
    @user-yi7sp4hz1j 6 місяців тому +1

    I love this song. Ndipo mu mtima mwanga mumakhala bataa. Indeed mtimanga bwera kuti upumulee.

  • @FellineMbowe-qw3lw
    @FellineMbowe-qw3lw 4 місяці тому +1

    Ndizabweza chani kwa Yehova ine😢

  • @mervisgondwe
    @mervisgondwe Рік тому +3

    Thoko Suya umatha kuimba.. mmmm umandisangalatsa

  • @festerchinula7806
    @festerchinula7806 Рік тому +2

    Zabweza chani kwa yehova zabwino zonse mundichitira.

  • @franciscomedson2759
    @franciscomedson2759 3 місяці тому +1

    All long day have been watching this beautiful song. Watching from sunninghill jhb.. so powerful. sound yabwino ,ma vocals..our brother vocal team i respect him as well from 5:20mns to 6:27mns mawu ake anaveka bwino kwambiri .. i respect him.. God bless you and the team large.. words of encouragement ,you are doing good keep it up..

  • @chifunirochitseko2612
    @chifunirochitseko2612 8 місяців тому +2

    I love you Thoko Suya.. You are a woman Of God indeed

  • @ChrissyGwemba
    @ChrissyGwemba 5 місяців тому +1

    I love this song so much may the good Lord continue blessing u mayi busa....

  • @RocianG.ksankhulani
    @RocianG.ksankhulani 4 місяці тому +1

    kukhara mwa MULUNGU ndikokomad zooona

  • @user-sn5ih8ld2s
    @user-sn5ih8ld2s 6 місяців тому +1

    Nyimboyi imasuntha moyo wanga ndimnkonda ambuye wandichitila zambili ndilibe,

  • @doreenmkandawire1672
    @doreenmkandawire1672 Рік тому +3

    Iam blessed

  • @user-pi3oc6fc9w
    @user-pi3oc6fc9w 3 місяці тому +1

    I am really blessed through this song, I really appreciate the Lord for my life. From Zambia 🇿🇲

  • @agnesschilinda7468
    @agnesschilinda7468 3 місяці тому +1

    Ndinalumbira zija ndizampatsa by grace

  • @salvationministries745
    @salvationministries745 Рік тому +2

    Amen i like this song

  • @RocianG.ksankhulani
    @RocianG.ksankhulani 4 місяці тому

    kukhara mwa MULUNGU ndikokomad zooona ndipo ndizatan kubwezera Ambuye ine

  • @EmmaKaliati
    @EmmaKaliati 11 місяців тому +1

    I just love you Ma and ur ministry, more life in abandant

  • @ritachiluzi6353
    @ritachiluzi6353 Рік тому +5

    Zisomo zochuluka mayi busa

  • @user-zd6ei4xb4m
    @user-zd6ei4xb4m 3 місяці тому

    Mulungu wanga ndiye wachifundo❤Nditani ine kumbwezera Mbuye

  • @QueenBanda-gl7mb
    @QueenBanda-gl7mb 10 місяців тому +1

    This song remind me of my let daddy MHSRIP, it's encouraging my soul to God all the glory

  • @blandinacanaan1305
    @blandinacanaan1305 Рік тому +3

    Indeed apulumutsa anthu ofoka ndipo nkhawa zimachokadi 🙌🙌🙌 wat an inspiration in this song🙏🙏🙏

  • @sarahsakala8066
    @sarahsakala8066 Рік тому +2

    Powerful song and very touching

  • @catherinephiri5091
    @catherinephiri5091 Рік тому +2

    Ndizamubwezera chani mulungu wanga pa zokoma anandichitila? Vry powerfull question to me and am so touched🙏🙏🥳🙏🙏

  • @chikuchimwaza8142
    @chikuchimwaza8142 Рік тому +3

    I have just discovered you but you are blessing.

  • @danielchimpanzi1590
    @danielchimpanzi1590 11 місяців тому +1

    Highly anointed. I am blessed 🙌

  • @rejoicemulenga6091
    @rejoicemulenga6091 3 місяці тому

    This song ama🙏🔥.. Ambuye apitilizebe kuvumbulutsa mavumbulutso ochuluka pa inu

  • @BwalyaAaron-mf3ph
    @BwalyaAaron-mf3ph 2 місяці тому

    enjoying this beautifull n touching song from lusaka,zambia

  • @GilbertMsowoya-bk5nk
    @GilbertMsowoya-bk5nk Рік тому +1

    This song mmmmm touched my heart thinking what can I offer to God for all good things that He has done,He does He will do mmmmmm

  • @aaronprophet
    @aaronprophet Рік тому +4

    Thank you the Song is touching.
    God bless you and the team.

  • @morcyb4513
    @morcyb4513 2 роки тому +3

    Oh huuu Praise the Lord...apulumutsa anthu akufooka

  • @yawosowoya2463
    @yawosowoya2463 2 роки тому +3

    Ndimatsisimuka ndi mayimbidwe anu🙌

  • @chiumiandagha9493
    @chiumiandagha9493 2 роки тому +3

    Mulungu akudaliseni
    Mayimbidwe okoma

  • @giftchimphepo770
    @giftchimphepo770 9 місяців тому +1

    This hymn speaks a lot in my life.... This is my national anthem and i play it everyday on repeat mode...
    You're the blessing in my life

  • @eltonbusiness7649
    @eltonbusiness7649 2 роки тому +3

    Ndikumva kukoma pa nyimbo za munthu odalitsikayu

  • @jabinchipeta1052
    @jabinchipeta1052 Рік тому +6

    Am blessed with your songs thoko, sometimes I even cry nkakumbukira what God doing on our everyday life

    • @user-jq1cu5eh3l
      @user-jq1cu5eh3l 5 місяців тому

      God bless you mama Busa you r ablessing to us this song eeeh

  • @fannymsumba1662
    @fannymsumba1662 10 місяців тому +1

    Andithandiza na ndipulumutsa❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @michellekaphinde5457
    @michellekaphinde5457 Рік тому +9

    I never get tired of listening to this song it revives my soul God bless you Mai Busa keep on preaching to us thru music , your music comes with an annointing

  • @chifuniroskeva
    @chifuniroskeva Рік тому +2

    I love this song million times

  • @MaryChikhosi
    @MaryChikhosi 4 місяці тому

    Ndimadalitsika nazo nyimbo zanu Mama mulungu apitilize kukupatsani mavumbulutso ochuluka

  • @joanathamiemagola4006
    @joanathamiemagola4006 2 роки тому +5

    The is power in worship

  • @jemimasibale-xw4vh
    @jemimasibale-xw4vh Рік тому +1

    Mumandidalitsa mayi wanga.. Ambuye akudze malire anu

  • @richardmwanza9526
    @richardmwanza9526 Рік тому +2

    what a song. what a message. what an artist. blessed to have listened ti this wonderful song

  • @traceyelbynanyumbu4502
    @traceyelbynanyumbu4502 2 роки тому +4

    This song oohh yes amen

  • @smartchiotcha2558
    @smartchiotcha2558 Рік тому +3

    Big up Mayi busa athu

  • @MelinaNyirenda-q1y
    @MelinaNyirenda-q1y 13 днів тому

    Thoko you're an amazing lady.keep on serving God.. You're an inspiration...you're loved dear cc

  • @anniemwale6688
    @anniemwale6688 6 місяців тому

    A day can't pass without coming here and listening to this song ...this one heals my heart ...keep up the good work mama your a blessing to many🙏

  • @aggiemarcolus7489
    @aggiemarcolus7489 Рік тому +1

    Ndimasunthika ndi nyimbo iyi. When I feel down I listen to this song it really strengthen me , coz it says amva pemphero ndi kulila kwanga. To God be the glory it sooth my soul AMEN

  • @user-fu7pe9th9e
    @user-fu7pe9th9e 25 днів тому

    This is powerful message i will return glory to his name, you are indeed a blessing to many souls

  • @francisnjerekeza32
    @francisnjerekeza32 Рік тому +1

    this song comfort me when i recal the souls who left me years ago , mom , brothers ,

  • @doricazimba104
    @doricazimba104 2 роки тому +3

    Zikomo Ambuye. May God bless you Suya and the ministry

  • @lestongeza8093
    @lestongeza8093 2 роки тому +4

    feeling more blessed. Mulungu aliko azakhalako kuthawa zonse and who sees us in lowest and high moments. when we feel so low he uplift our souls .

  • @catherinekatherere6949
    @catherinekatherere6949 3 місяці тому

    Akathandiza nkhawa imachokadi Amen and Amen

  • @damalesinguni8019
    @damalesinguni8019 Рік тому +2

    ....waku chosera imfa ndi misodzi...it gave me hope that mum would recover but after her death, this song meant totally different from my earlier understanding.." God's saints go to rest, He delivers them from earthly sufferings!" ...so much to praise Him for.

  • @marymwakawana4140
    @marymwakawana4140 2 роки тому +3

    Wow! Ur just amazing. Keep blessing

  • @NeliaDaudi
    @NeliaDaudi 3 місяці тому

    Mumandivetsa kukoma kwambili mai busa muma ndilimbitsa mtima mama

  • @Maryjuma-eg4rw
    @Maryjuma-eg4rw 2 місяці тому

    I am blessed abandantly because this song,, keep on blessing us u r so talented artist

  • @BernaBanda-hw4eu
    @BernaBanda-hw4eu 3 місяці тому

    Amen ndizampasa chani ine mulungu wanga😢

  • @MphatsoBanda-9193
    @MphatsoBanda-9193 16 днів тому

    Your songs are a blessing to our soul. Zimatilimbikitsa

  • @BossMwafulirwa
    @BossMwafulirwa Рік тому +2

    blessed beyond measure, Thank you Mai Busa

  • @KennethMchenga-j9c
    @KennethMchenga-j9c Місяць тому

    Mama you bles me every day may God bles u mama

  • @AnnieYasin-ti8zf
    @AnnieYasin-ti8zf 5 місяців тому

    I love this song so much imatsitsimutsa moyo wanga chipulumutso chake ndidzamtama ndinali ndani lne kupanda mwazi wa YESU ndidzatani kubwenzera zokoma zonse amandichitira

  • @elizabethmaz827
    @elizabethmaz827 Рік тому +1

    Indeed this song is powerful 💪💪💪 may God bless both the singer and us listeners ❤❤❤

  • @angelbakaimani8994
    @angelbakaimani8994 Рік тому +3

    I love this song

  • @gkaipa
    @gkaipa Рік тому +4

    You have blessed me. May the glory of God never depart from you in the mighty name of Jesus. Amen.

  • @lotticechinula946
    @lotticechinula946 Рік тому +3

    This is a great song.

  • @audreyplaighnnie
    @audreyplaighnnie Рік тому +3

    God as we are coming to the end of this year may you see me through and remember me just the way did with job....glory to God for answering my prayers and blessings in Jesus name 🙏

  • @alickdyna8228
    @alickdyna8228 Рік тому +3

    Powerful God bless you , true worship

  • @user-zl2lq5jz2m
    @user-zl2lq5jz2m 8 місяців тому

    Nditani ine kubwezera mbuye wanga🙌

  • @ellennyirenda3050
    @ellennyirenda3050 9 місяців тому

    God please I need your hand on the documents,today is the final day, manifest yourself ooh God

  • @patricknzima
    @patricknzima Рік тому +2

    This is really a powerful song.

  • @SarahBchikuni-pz9lw
    @SarahBchikuni-pz9lw Рік тому +1

    I have alot to thank Jehovah.....this song kips me going

  • @franklinbanda-jk8vr
    @franklinbanda-jk8vr 10 днів тому

    2024 and still being blessed here

  • @hellenngwane8265
    @hellenngwane8265 Рік тому

    Ndidzabweza chiani kwambuye ine he has done uncomfortable things in my life and it reminds me of my late amama banga MHSRP

  • @magretuloloo1307
    @magretuloloo1307 Рік тому +1

    This is beautiful 😭😭 nyimbo iyii yandisuntha

  • @kumbumunthali3112
    @kumbumunthali3112 2 роки тому +3

    Amen Amen powerful song am blessed . God bless you pastor Siya

  • @willammahala4481
    @willammahala4481 Рік тому +2

    Amen

  • @PempheroMpute
    @PempheroMpute 9 місяців тому

    Powerful worship song

  • @denisgalileya1202
    @denisgalileya1202 2 роки тому +4

    This song again is superb

  • @ellenngalande2963
    @ellenngalande2963 2 роки тому +3

    Beautiful song I just love everything about it the msg so powerful

  • @ronicangoma245
    @ronicangoma245 2 роки тому +3

    Beautiful song nadalitsika

  • @cathyjoseph1576
    @cathyjoseph1576 5 місяців тому

    I❤this song May God b Glory

  • @chixo-gz7pw
    @chixo-gz7pw Рік тому

    she sings and attaches herself to the message of the song. the listener is then drawn close to the message in the song and begins to understand the greatness of Almighty God. To cap it all the song is full of God's anointing

  • @berthamikundi330
    @berthamikundi330 2 роки тому +3

    Amen praise the Lord

  • @lungusalatiel1890
    @lungusalatiel1890 Рік тому +2

    The whole week , month , I am listening to this powerful worship song. Singing it understanding the words meaning and powerful message. The lyrics ! Beautiful ! Giving thanks and praises. Ndikonda mulungu wanga

  • @nyasongimhango6337
    @nyasongimhango6337 2 роки тому +2

    Beautiful song so touching

  • @florakuyere912
    @florakuyere912 2 роки тому +6

    The more I listen the more I feel blessed.I can't get tired of listening to this hymn