BON KALINDO LERO PA 29 JULY 2024 | MSONKHANO WA UTM MBAMBANDE |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 7 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 31

  • @PetualCheyo
    @PetualCheyo Місяць тому

    My prayer Mulungu awapatse makutu A UTM ndi zipani zonse kuti atsatile zomwe zanenedwa apazi 🙏

  • @GiftMakowa-k9f
    @GiftMakowa-k9f Місяць тому +1

    Mofayaaaa born kalindo 💥💥💥💥 timakunyadilani

  • @AbubakarKalembo
    @AbubakarKalembo Місяць тому +2

    President wa anthu osauka adzagona zinyengozi zikadzachepa eetu kalindo fire ma bomba

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Місяць тому +1

    The DC Bon kalindo number one ❤

  • @LuciaKadango
    @LuciaKadango Місяць тому +2

    Forward ever backwards never aluta continua

  • @PatrickMbenje
    @PatrickMbenje Місяць тому +1

    Mulungu yekha ndi Amene akuziwa mavuto athu ndipo sangalore kuti ana ake akhale akulira mpaka kale one day is day

  • @user-wu8kp7ui5j
    @user-wu8kp7ui5j Місяць тому +1

    The DC 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @HasanMia-g3v
    @HasanMia-g3v Місяць тому

    This is true story

  • @andiwochishadreck3753
    @andiwochishadreck3753 Місяць тому

    True

  • @EdithKamiyala
    @EdithKamiyala Місяць тому

    Ndipo mukunena zoona

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl Місяць тому

    🔥🔥🔥

  • @user-yj5xv4cy8x
    @user-yj5xv4cy8x Місяць тому

    Wamisala wakwathu

  • @HalimaShafie-o7g
    @HalimaShafie-o7g Місяць тому

    ❤❤❤❤❤

  • @AminazJames
    @AminazJames Місяць тому

    Big man the DC like you

  • @GRACIOUSKENAN
    @GRACIOUSKENAN Місяць тому

    WE LOVE YOU SIR

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw Місяць тому

    Zomba chingare kwathu kumeneko the DC

  • @Moses51
    @Moses51 Місяць тому

    The Dc bon kalindo

  • @GeoffreyZuze
    @GeoffreyZuze Місяць тому

    You deserve madala Born

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Місяць тому +1

    Kd ndine ambuye?

  • @GiftMambiya-fh7xb
    @GiftMambiya-fh7xb Місяць тому +4

    We have weak opposition

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope Місяць тому

    Dpp ,utm,, aford,,,udf bwanji osapanga chimodz muchite bailout dziko li

  • @GanieAlidih-gu7no
    @GanieAlidih-gu7no Місяць тому +1

    Bambande

  • @YamikaniTebulo
    @YamikaniTebulo Місяць тому

    ❤🎉

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon Місяць тому

    The deceeee

  • @DevisonHala
    @DevisonHala Місяць тому

    Inuso tithandizeni ku menya nkhondo imeneyi

  • @EllemiaChaduka
    @EllemiaChaduka Місяць тому

    Kod a on kalindo mmesa amati chipani cha UTM ndi cha pa Facebook ineyo abon kalindo sindikuwamvetsa zomwe akufuna kutiuza ife aphawi komaso Ngati president oimila aphawi ifeyo sakutichitila bwino chifukwa iwowo akumaonetsera mbali yazipani zomwe akuzifuna iwowo chomwe ife aphawi tikufuna ndikuthetsa mavuto anthu omwe osaukafe tikukumananawo osati kumayamikila zipani iwowo asakhale Ngati anthu a Dale sawadziwa ndamodzi palibe chomwe chingasithe iwo azitimenyera khondo yoti aphawi adzikhala ndi moyo wabwino ife zazipani sizimatisangalatsa akamaikila kumbuyo zipani iwo azikamba mavuto aphawi osati zimenezo zomaonetsa mbali

  • @LahimuKamwendo-hj9ct
    @LahimuKamwendo-hj9ct Місяць тому

    Koma mukugona akalindo

  • @PRECIOUSMADEYA
    @PRECIOUSMADEYA Місяць тому

    Tiuzeni

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m Місяць тому +1

    Kunena chilungamo DC mumanena dzoona Koma aopodzishoni Ake ogona kwambili akufuna mulamula Koma amatha

  • @WachiyawoWangalusa
    @WachiyawoWangalusa Місяць тому

    Wniko.umanena.zoona.koma.anthu.akususuka.ndi.ndalama.achakwela.akuona.ngati.ncalamari.ziwateteza.kamba.kaumpbhawi.umine.auika.mmalawi.muno.amalawi.tigwilane.manja.pochosa.nyasi.zimenezi

  • @LenardKayange
    @LenardKayange Місяць тому

    🎉❤