BRIAN BANDA INTERVIEW WITH NOMANI CHISALE AT DPP CONVENTION IN BLANTYRE ZIKUCHITIKA POMPANO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 25 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 282

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 місяці тому +46

    ❤❤❤ mr chisale mwandiwazatu kwámbili ifeyotu tikuya'ng'ánaso inuyo mónga big man áchitetezo

  • @MrAhmidu
    @MrAhmidu 2 місяці тому +6

    Man Chisalewatu zikukhala ngati udindo wa Director of Youth-wu akuwumva ngati Director of Security.

  • @DavieMaloya
    @DavieMaloya 2 місяці тому +12

    Auzeni mcikulile tili pambuyo ife APM my vote 🎉🎉

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 2 місяці тому +1

    Comrade Norman Chisale 💙💙🔥 Ntcheu Central constituency tikudikira inu bwana Ndi DPP 💙

  • @mphatsobwanali5981
    @mphatsobwanali5981 2 місяці тому +14

    Dpp, woyeee, APM MY VOTE 2025 MOTO KUTI BUUUIU ❤, 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @LoudonPhiri
    @LoudonPhiri 2 місяці тому +1

    Inu a Brian, this is your vocation, not just a profession. Iwetu Brian umandidalitsa kwambili. Ku Comesa ko tikukuonelani Kuno ku Lilongwe, Loudon Mallingamoyo

  • @jeneziochisonga2819
    @jeneziochisonga2819 2 місяці тому +3

    I like this man Norman Chisale for his loyalty to Peter Mutharika.

  • @lemanissa1125
    @lemanissa1125 2 місяці тому +25

    Kod mulikuti ma fans amadala Norman chisale like basi kwina tikudikirila kuti big ku winner basi ❤🔥🔥DPP woyeeee 🔥🔥🔥

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 місяці тому +8

    ❤❤ DPP ndi chipani chokhacho cha ufulu

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 2 місяці тому +13

    Tikufuna strong man ngati chisale yo umakwana bigy nthawi yakwana yokha.

  • @nobertmartinnkhoma-vg3lk
    @nobertmartinnkhoma-vg3lk 2 місяці тому +16

    Katundu WA boma Mr Noman Chisale ❤❤❤❤❤❤

  • @johnchitenji4
    @johnchitenji4 2 місяці тому +3

    DPP woyeeee kma nkhani mkanyamata eeeeeee decoration ayipanga bwino ❤

  • @TryMoo-c1e
    @TryMoo-c1e 2 місяці тому +2

    Chisale can't forget his Password.. The legend

  • @UmaliDaili-nd6uu
    @UmaliDaili-nd6uu 2 місяці тому +15

    My vote 🎉 DPP ❤

  • @CedricSpy
    @CedricSpy 2 місяці тому

    Norman chisale vote yanga.. All the best sir.... Gwilani ntchito angaphweketse

  • @Mpondapromise9
    @Mpondapromise9 2 місяці тому +7

    Am proud of you Norman chisale.only the strong will survive

  • @Rometcma
    @Rometcma 2 місяці тому +3

    Guys DPP Kuli mayaza and chhisale is one of them 🎉🎉🎉🎉

  • @GiftFrancesco
    @GiftFrancesco 2 місяці тому +5

    Tilipambuyo pano Mr chisary more fire 🔥🔥🔥🔥

  • @luciamkumbwa4829
    @luciamkumbwa4829 2 місяці тому +1

    Musathe mau😂😂 a Norman..mukagwa tizakufusaninsoni loi

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 2 місяці тому +4

    Kokakoka Norman Chisale .A MCP.AKUONJEZA NKHANZA NDI MA DEVALUATION AWOWA IFE TATOPA NAZO .FERTILISER NKUKHALA K120.000.00 ANTHU OSAGWIRA NTCHITO ATENGA KUTI NDALAMA ZA FERTILSERYO

  • @EvanceSungani-cv9jk
    @EvanceSungani-cv9jk 2 місяці тому +2

    Am always with chisale in DPP🎉❤

  • @papelariareis.e.
    @papelariareis.e. 2 місяці тому +4

    I will vote for apm

  • @ChimwemweBottomani-hc5ju
    @ChimwemweBottomani-hc5ju 2 місяці тому +2

    My vote Norman chisale

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 2 місяці тому +6

    Auze aguluwa zenizeni
    ...chakwera ndi munthu woyipa kwambili

  • @JamesOsman-cz9cw
    @JamesOsman-cz9cw 2 місяці тому +5

    Mawu ndiwenso msilikali okwqnila❤

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 2 місяці тому +4

    My vote 💙💙💙

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 2 місяці тому +5

    Zoona mr ❤❤❤ chisale
    its true

  • @RitaBan-t7c
    @RitaBan-t7c 2 місяці тому +2

    Vote yanga Mr Chisale kuchokera ku UK mumandibvetsa kukoma zedi kutakhala azibambo atatu amphamvu ngati inuyo bwenzi tikuyenda osabvala dziko muno 😂😂😂😂😂

  • @MaryndauNdau
    @MaryndauNdau 2 місяці тому +1

    Eeee kma chinachina deco very nice zadongosolo heavy😊

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 місяці тому +1

    Mr chisale mulungu akudaliseni 🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @rittakawiriza
    @rittakawiriza 2 місяці тому +1

    DPP 2024 Boma awuzeni zoona,,asamafunse chinyezi Ku bafa 🔥🔥🔥

  • @NewtonTembo-q4t
    @NewtonTembo-q4t 2 місяці тому +2

    Captain Norman chisale woyeeeeeeeeeee katundu waboma

  • @RuthLynda
    @RuthLynda 2 місяці тому +1

    Eeeeee koma nchi decoration cha nyooooooooooooo DPP my vote kkkkkkkkk koma Cathy ati kwina kuja agwaaa😂😂😂😂

  • @blessingmnomanda
    @blessingmnomanda 2 місяці тому +3

    My vote 😊

  • @Yoxym
    @Yoxym 2 місяці тому +2

    Apm 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙 my vote

  • @PRECIOUSMKUTE
    @PRECIOUSMKUTE 2 місяці тому +2

    Legend in the building ❤❤

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 2 місяці тому +2

    I am proud of you mr chisale

  • @SolomonShaibuh
    @SolomonShaibuh 2 місяці тому +2

    Apm my vote

  • @ruthmulewa6603
    @ruthmulewa6603 2 місяці тому +4

    Deco very beautiful

  • @RachelEmmirahNamate
    @RachelEmmirahNamate 2 місяці тому +9

    Dpp woyeee vote yanga kwa adad omwewo ,,,i love you dad 2025 woooooooooooooooh

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 2 місяці тому +6

    NDIPO DPP IWINA MWA NYOOOOOO!!!

  • @IbrahimJackson-i8h
    @IbrahimJackson-i8h 2 місяці тому +5

    I love you bro 💙

  • @Ghama-k4i
    @Ghama-k4i 2 місяці тому +1

    My vote strong youngman

  • @EvelynMapiki
    @EvelynMapiki 2 місяці тому +1

    Dpp my vote❤

  • @eunicemacdonaldkaipsa9705
    @eunicemacdonaldkaipsa9705 2 місяці тому +2

    Chisale woyeeee❤❤❤❤

  • @KefasiJonathan
    @KefasiJonathan 2 місяці тому +1

    Apa mpamene ndaziwa kuti chikangawa bas waku jahena

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja 2 місяці тому +2

    Zoonadi brother chisale ulemu wanu ifetimakunyadilani heavy osaopa osafooka osatopa

  • @DerickDillah
    @DerickDillah 2 місяці тому +4

    My vote

  • @PatriciaMwawa
    @PatriciaMwawa 2 місяці тому +2

    My vote❤

  • @BrunoMbewe-xj1yy
    @BrunoMbewe-xj1yy 2 місяці тому

    Times ndinu number 1 pa radio station onse pa Malawi.

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 10 днів тому

    ONSE ATOLA NKHANI MALOYA OPEPERA TIKUFUNA ADZAWONE KUTI KODI LIFE IMATANI MWATUMIKILA MCP ZOLAKWIKA MUDZIKO MUNO NTHAWI YANU IKUBWERA NONSE MUNAPHA MR CHILIMA MUDZAFUNIKA

  • @elizamaster2168
    @elizamaster2168 2 місяці тому +2

    DPP my vote 💙

  • @PatrickMangochi
    @PatrickMangochi 2 місяці тому +1

    Kodi paja chisankho cha Makhansala chija zinakhala bwanji?

  • @MrMagombo
    @MrMagombo 2 місяці тому

    A Chisale pangani Nsundwe yanu ife tilowa. Ntendere vs ntendere. Kuphana vs kuphana.

  • @MustaphaChimangeni
    @MustaphaChimangeni 2 місяці тому +2

    Basi ziii yenseuja mmadikila kuti times ikajambure then muziponya Kodi tima station tanuti mulibe atolankhani?

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 2 місяці тому

      The son of snake 🐍 mwana wake weni weni wasata m'dyelekezi iwe

    • @MustaphaChimangeni
      @MustaphaChimangeni 2 місяці тому

      @@joebrown1158 reality talkingz is what we believe as far as I concerned the truth hurts

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 2 місяці тому

      @@MustaphaChimangeni why do you hurt yourself

    • @AlihIbrahim-s7v
      @AlihIbrahim-s7v 2 місяці тому

      Yawawatu ya DPP bwanji ya MCP ija mumawonela umfiti bwanji😂😂😂😂munyelabe

  • @petermsamariamapira8933
    @petermsamariamapira8933 2 місяці тому +1

    Dpp ilowe boma bas ,ulemu wanu bwana ,❤

  • @GodfreyMphaya
    @GodfreyMphaya 2 місяці тому

    More respect to you mr chisale

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 2 місяці тому

    More power Norman heavy weight Chisale

  • @samuelsergio5343
    @samuelsergio5343 2 місяці тому +1

    Achisalewa ndi Muthu wabwino.ola Muthu sakomera wonse koma muli fundo zabwino

  • @BashiruIshumael
    @BashiruIshumael 2 місяці тому

    Katundu waboma chisale ❤❤❤❤❤❤

  • @RICHMANCHIMWAZA
    @RICHMANCHIMWAZA 2 місяці тому +3

    Chisale go ahead l loved your speech

  • @MeriaMasinga
    @MeriaMasinga 2 місяці тому +1

    Chisale umakwana upitilize kumukonda Peter 2025 boma

  • @SamboRuphan
    @SamboRuphan 2 місяці тому

    Am with you chisale❤❤❤

  • @AishaChibwana-b8o
    @AishaChibwana-b8o 2 місяці тому +1

    Chisale ndi munthu wabwino kutengera ntchito zake koma vuto chipani chomwe alicho nganga zokhazokhatu 😂😂😂😂😂😂😂

  • @MalikiAlex-wn8jc
    @MalikiAlex-wn8jc 2 місяці тому

    Mongatu ineyo madala King cobra 🐍 ndikuyipatsa Moto DPP BOMA 2025 😂❤ ndikukufunilani zabwino zonse inutu mukupikisana pikisana mipando yosiyana siyana amen 🙏

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 2 місяці тому

    Koma zot payokha ingawinezo nde ayi pajatu ndi 50+1 don't forget 😂😂😂😂

  • @BenidictoGondwe
    @BenidictoGondwe 2 місяці тому +1

    Okuvoterani inuyo ndiosalongosoka I quess chipani choipisitsa chimenechi

    • @TiyanjaneMkwate-we8gu
      @TiyanjaneMkwate-we8gu 2 місяці тому

      Among all the comments, you are the only one who criticize the party. Shame on you.

  • @ChrisjuZiyaya
    @ChrisjuZiyaya 2 місяці тому

    Uthenga wanu Inu mukangoti mwalowa m'boma choyambirila kafukufuku wa report ya ngozi ya ndege mchikangawa please tatopa ndi mbwerelazi

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 2 місяці тому +1

    Agalu chisale ndi Peter muthalika

  • @MacDonaldkachala-cm5gc
    @MacDonaldkachala-cm5gc 2 місяці тому +2

    A lot of people seem to like expired things,

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 2 місяці тому

      😂😂😂😂 olo nyemba zotaidwa zimakamela kudzala konko

    • @MacDonaldkachala-cm5gc
      @MacDonaldkachala-cm5gc 2 місяці тому

      Loma khwanyawake smartass chisoni, simungadye

  • @manzunzochicafa4889
    @manzunzochicafa4889 2 місяці тому +1

    Kkkkkk koma abanda mwano sudzakutherani!! Brain you deserve some respect

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 2 місяці тому +1

    Mbava chisale ndi Peter muthalika

  • @VincentNyabanga-dw9uj
    @VincentNyabanga-dw9uj 2 місяці тому

    Wozaa Dr Chisale

  • @duncankhofi
    @duncankhofi 2 місяці тому

    APM my vote

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 2 місяці тому

    Awa nkhuku tagura osatimaparts ahhh 10 pin osakwana. Ahhh ahhhh

  • @PRISCAMAKHANGA
    @PRISCAMAKHANGA 2 місяці тому +1

    Dpp my vote

  • @JumashukranDyson
    @JumashukranDyson 2 місяці тому

    Chitsilu chakubachi,amalawi mwayiwala?

  • @CelphaStephanSilungwe
    @CelphaStephanSilungwe 2 місяці тому +1

    Ulibho

  • @ChisomoMpeketula
    @ChisomoMpeketula 2 місяці тому

    My vote 💙

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 2 місяці тому

    I pray izawine DPP bas

  • @EnetChiomba
    @EnetChiomba Місяць тому

    Moni kuti buuuu🥰🥰🥰

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 2 місяці тому

    Zoonad zimenezo Umakwana Norman Chisale

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 2 місяці тому +2

    More fire chisale😂😂😂

  • @AbrahamManyenga-v1g
    @AbrahamManyenga-v1g 2 місяці тому

    Norman Chisale afunanso kut adzidzalowetsanso katundu mu dziko muno opanda misonkho kachikena? Ndakaika

  • @AllanWilsonbanda
    @AllanWilsonbanda 2 місяці тому

    Ndamva chisoni kwambili DPP idatha ngati bodza rest in peace bingu wamuthalika 🙏

    • @TakondwaStima
      @TakondwaStima 2 місяці тому

      Inu ndiye ati .sumazimvera chisoni hahahaaa.

    • @AllanWilsonbanda
      @AllanWilsonbanda 2 місяці тому

      @@TakondwaStima ineyo ndiineyo iweyo ndindani komaso iweyo umadzivela chisonicho kapena ayi mwina iwe ulinacho chifukwa chodzivela chisoni koma ine ndilibe or pan'gono

  • @rexjuwa
    @rexjuwa 2 місяці тому

    Wawa Angoni, Tiyeni nayo, tiponyere kwakuya

  • @ChifuniroMedson
    @ChifuniroMedson 2 місяці тому +1

    Idzawina pakamwa pokha koma Dpp singalamuleso

  • @jonaslabisonnthyola8036
    @jonaslabisonnthyola8036 2 місяці тому +3

    Am watching from South Africa Cape town Doo boma 2025 woyee

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 2 місяці тому +4

    Wawa Angoni

  • @LukaThawe
    @LukaThawe 2 місяці тому

    Mbuzi chisale wakuba uyu

  • @patrickscott9086
    @patrickscott9086 2 місяці тому

    Ndipo azikwanje aja uwakwapule amuziwe msilikali 😅😅😅😅😅

  • @vytwistthelion98
    @vytwistthelion98 2 місяці тому

    A Chisale ndi akatundu

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 2 місяці тому +1

    True brother

  • @DannieldenilsonGhambi
    @DannieldenilsonGhambi 2 місяці тому

    Chisale amatiwaza

  • @vitumbikocobysinyiza-5116
    @vitumbikocobysinyiza-5116 2 місяці тому

    Koma chisale eee😂😂😂 ndikatundu

  • @THOMASMCHOKOCHO
    @THOMASMCHOKOCHO 2 місяці тому

    exactly soldier

  • @YoungKissbeatz
    @YoungKissbeatz 2 місяці тому

    Corporation already okha okha 😂😂😂 ndi ana anga

  • @GladysNgongole
    @GladysNgongole 2 місяці тому

    Chisale ali ndi morale yachabe eish😂🤣😂

  • @EllardHolla
    @EllardHolla 2 місяці тому

    My vote DPP Moto kuti buuuu.....

  • @EdwardRichman-zs5pl
    @EdwardRichman-zs5pl 2 місяці тому

    Wapengatu chisale iwala zodzabaso