5. Ndipo mipingo isanu ndi iwiri iyo inali ndi chikhalidwe chosiyana. Ndipo kuchokera kutsanulira kwa Mzimu Woyera mpaka Mkwatulo, Mpingo wa kwa amitundu udutsa mu nyengo zisanu ndi ziwiri, ndipo ine ndikukhumba kuti ndiyankhule za izo m’mawa uno. Ndipo pa nyengo iliyonse, Ambuye Yesu Khristu adzatumiza padziko lapansi imodzi mwa nyenyezi zisanu ndi ziwiri zomwe Iye wagwira m'dzanja lake lamanja kuti amenyana ndi mzimu wolakwika. Ndipo nyenyezi iyi, ndiko kunena m’ngelo wakumwamba, kutumizidwa pa dziko lapansi, idzagwira munthu woti imugwiritse ntchito kulimbana ndi mzimu wolakwika. Ndiye choncho, malingana ngati nyengo siyinathe, nyenyezi iyi ikhoza kugwiritsa ntchito anthu ambiri. Inu mwawona? [Mkonzi: Osonkhana ati, "Ameni!"]. 6. Nyengo yoyamba ndi Mpingo wa Aefeso: Chivumbulutso 2:1-7. Ndipo izo zinachitika padziko lapansi kuyambira chaka cha 53 mpaka chaka cha 170 pambuyo pa Yesu Khristu. Ndipo mipingo ya dziko lonse inali mbali ya Mpingo uwu. Ndipo mtumiki woyamba wa m'badwo uwu anali Mtumwi Paulo. Ndipo pambuyo pa Paulo, Mulungu anaukitsa aneneri angapo m’modzi mwa iwo anali Ignatius wa ku Antioch ndi Polycarp wa ku Smyna. Mpingo wa kwa amitundu ukuvutitsidwa ndi antchito onyenga a Mulungu. Chiphunzitso chonyenga chabadwa, Chogonjetsa anthu wamba: munthu akufuna malo a Mulungu. Cholengedwa chamoyo chimene icho chinatuluka chili mkango. Malinga ndi Chivumbulutso 4:7, mukudziwa kuti pali zamoyo zinayi zozungulira mpando wachifumu: Mkango, mwana wa ng'ombe, cholengedwa chamoyo cha nkhope ya munthu ndi mphungu. Ndipo kwa m'badwo woyamba, cholengedwa chamoyo chimene chinatuluka kukamenyana ndi chiwanda chimenecho ndicho mkango. PKPCHANELTV
12. Ndipo ngati Mulungu apulumutsa Mkatolika, wa Chiprotesitanti, wa chievangeliko, wa chiBranham, kapena membala m’modzi wa mamishoni ndi mautumiki amenewo, Mulungu ayenera kuchotsa gehena ndipo aliyense adzapite ku Paradaiso, ngakhale Satana. [Mkonzi: Osonkhana akuti, "Ameni!"]. Kodi munthu angakane bwanji m’neneri wamoyo wa nthawi yake ndikupita ku Paradaiso? Kodi munthu angapulumutsidwe bwanji ku Chigumula pamene atakana Nowa? Pamene Ambuye Yesu Khristu anali pa dziko lapansi, zikanatheka bwanji kumukana iye ndi kupulumuka? Dziko lonse lapansi liri ku mphompho chifukwa cha mipingo iyi.
Akufuna kunamiza ndani ome cosmetic sikuti ndi product yawo....iwowo analembedwa ntchito kugulisa ku Malawi....komanso Aliponso ena amene akugulisa ku Zambia
#ProjetKacouPhilippe Mawu Achiheberi kwa m’neneri ndi nabi, mawu awa akuyimira: “woyankhula”, osati ochita zozizwitsa kapena wonyamula kudzodza koma wolankhula. Inu mukuwona? Mneneri wam’thenga ndi chikhumbo ndi chiwonetsero cha Mawu a Mulungu mu kam'badwo Kake.
Ziwanda zomwe nthawi yakale zinayima kumbuyo kwa mpingo wa Chikatolika ziri zofanana ndi zomwe zimayima kuseri kwa mipingo ya Chiprotesitanti, Chievangeliko ndi Chibranham yomwe inu mukuiwona lero. Mu bukhu la Chikatolika mudzawona rozari, makandulo, zofukiza, mtanda ... ziwanda zomwezo zomwe zimayimirira kuseri kwa zinthu izi ziri chimodzimodzi ziwanda zomwe zimayima kumbuyo kwa sitolo ya mabuku a Chikhristu cha Chievangeliko. Chimodzi ndi chithunzi cha chimzake komano mu choonadi chotsalira, Baibulo ndi lolemera koposa mabuku onse ogulitsidwa ku masitolo awa kuphatikizidwa. Ziwanda zomwezo zomwe zimayima kuseri kwa wailesi ya Chikatolika ndi ziwanda zomwezo zomwe zimayima kumbuyo kwa mauthenga a Chievangeliko. Mabaibulo a Chievangeliko ndiwo maonekedwe a Mabaibulo Achikatolika. Pologalamu yovomerezeka ya Mneneri Kacou Philippe ya Android: play.google.com/store/apps/details?id=com.matth25.prophetekacou
11. Pamene mtumiki wam’thenga akutumizidwa kudziko lapansi, ndichifukwa chakuti palibe choonadi padziko lapansi ndipo uthenga wake ndiwo wokhawo woona wa nthawi yake. Iye ndiye choyimira cha choonadi. Iye ndi woweruza wa Mawu a Mulungu mu nthawi yake. Inu mukuwona? Pamene Nowa ankalalikira, palibe amene akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Nowa. Pamene Yeremiya ankalalikira, palibe amene akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Yeremiya. Pamene Eliya ankalalikira, palibe amene akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Eliya. Pamene Ambuye Yesu Khristu ankalalikira kumeneko m'misewu ya Yerusalemu, palibe amene akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Ambuye Yesu. Iye anati, "Palibe amene amabwera kwa Atate koma kupyolera mwa Ine." Inu mukuwona? Pamene Martin Luther anali kulalikira mu Germany, palibe yemwe akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Martin Luther. Pamene John Wesley ankalalikira, palibe yemwe akanakhoza kupulumutsidwa pa nkhope yonse ya dziko kupatula mwa Uthenga wa John Wesley. Pamene William Branham ankalalikira mu Amerika, palibe yemwe akanakhoza kupulumutsidwa pa nkhope yonse ya dziko kupatula mwa Uthenga wa William Branham. Ndipo lero inu simungathe kupulumutsidwa koma kupyolera mu uthenga wa m’neneri Kacou Philippe. Ngati inu munali mwana wa Mulungu m'nthawi yawo, inu mukanakhulupirira mwa iwo ndipo ndi zofanana lero.[mkonzi: wosonkhana anena, “Ameni! "].
18. Zabwino! Mateyu 25:6 ...Ife tikukhala mu nyengo ina ya mbiri ya chipulumutso. Si nthawi yakukweza nyumba zachipembedzo zazikulu ndi zapamwamba ndi za mabo, mikeka yapamwamba, mipweya yokonzedwa ndi zidazoyimbira zamphamvu. Iyi si nthawi yokuti munthu wa Mulungu adzilota za nyumba, magalimoto ndi zina. Koma khama lililonse, zopereka zonse zachuma zizipita molunjika kupititsa mtsogolo choonadi ichi chifukwa cha kudzutsa. 19. Ndipo palibe yemwe angakhoze kumutumikira Mulungu pa nkhope yonse ya dziko lapansi pokha-pokha ngati iye ali mawu obwerezedwa pa zomwe Mulungu akuchita pano. Ichi ndicho chifukwa ine ndikutsutsana ndi a Chievangeliko, a Chibapitisiti, a chi Foursquare, ndi ena otero ... Ndipo ine ndikuchenjezani inu motsutsana ndi iwo! Ife tilibe gawo ndi iwo! Musakhale achinyengo ndipo musatikhazikitsire ife tsogolo lina motsutsana ndi ife! Iwo ndi akhwangwala. Ndipo pamene mphungu zifuula, lolani akhwangwala akhale chete. [Mawu a Mkonzi: Msonkhano unati, "Ameni! "]. Ngati inu mumlalikira wa Chisilamu kapena wa Chikatolika kuti mumtumize ku mpingo wa Chibaptisiti kapena Pentekosti, kodi ndiye kuti mwapangapo chiyani? Inu mwangosintha selo ya wa mndende. Ili ndi khola lomwe-lomwelo la Satana. Ndipo ndiwe liwu losokoneza motsutsa pa zomwe Mulungu akuchita pano! #PKPCHANNELTV
4. Ife tikudziwa lero kuti a Chibranham ndi ofwifwa ndipo ena mwa alevi a William Branham siwovomerezedwa lero mu Mpingo! William Branham amatha kupita ndi kukalalikira mu mipingo pa mfundo zofanana ndi kumalumikizana nawo, ndi osonkhana ake ndipo m’nyumba yake mbusa wa Chibapitisiti amakhoza kuwawelutsa omvera ndi mawu a chilimbikitso ndi pemphero. Izi sizinali zoipa madzulo, koma lero ndikukuuzani kuti ngati ndinu Mkhristu ndiye kuti mulibe ufulu wokhala m'chipembedzo cha Chikatolika, Chipurotesitanti, Chievangeliko kapena Chibranham kapena mapemphero a aneneri awo. [Mawu a Mkonzi: Msonkhano unati, "Ameni! "]. Awa ndiwo maguwa a zonyansa zonse zomwe Mulungu sangazisiye kuti zisalandire chilango. Ngakhale ngati inu mutakhala pa ulendo, inu musapite kumeneko! Kodi inu mudzafuna chiyani pakati pawo? Kodi iwe udzayang'ana chiyani mu mpingo wa Chikatolika, wa Chipurotesitanti, Chievangeliko kapena wa Chibranham, pamene iwe uli mwana wa Mulungu? Malo anu siali kumeneko! Inu mukuwona? 5. Ndipo inu Achibranham, mtundu wa achule! Wamoyo, ine sindidzasiya kukhala kwa inu chimene mkango umakhala kwa mtundu wa mbawala, ndipo ndikadzafa ine sindidzakhala wochepera. Inu mukudziwa ine ndi khansara yomwe ingakuwonongeni inu. Ola lanu la chiweruzo cha Mulungu lafika ndipo inu simuthawa. Mawu ayesa chilichonse ndipo kuwala kwachititsa zintchito zanu kudziwika ...
Koma television channel imeneyi aaaaaa pa chabe , koma Brain asamale cos tikumamuona , adzagodzuka ku mawa tv station yake kulibeko komanso mwai kuti adzakhala kulibeko , akanazapitira limodzi
41. Kubwerera ku vesi 10, yemwe alipo ndiye Kaisara, amene amabwera ndi Mfumu Nero yemwe wakhala ndi miyezi isanu ndi umodzi ya ulamuliro wankhanza. Ndipo iwo mu mipingo iyi adzadabwa, koma ife tikudziwa kuti iwo apita ku gehena. Wachisanu ndi chitatu ndikutsatana kwa apapa. Mu vesi 12: Mafumu osakanizidwa awa ali pazidindo limodzi: Hitler, Stalin, Mussolini, ndi zina zotero. Ndipo mbali inayo, atsogoleri a mpingo uliwonse kupatulapo mneneri wamoyo wa m'badwo. Iwo ali ndi mapangidwe omwewo ndi Tchalitchi cha Katolika; mmodzi anapha Akhristu, winayo anapha Ayuda. Ndipo mu Tchalitchi cha Katolika ndi chithunzi cha Tchalitchi cha Katolika chomwe chikutanthauza mipingo ya Chiprotestanti, Evangelical ndi Branhamist kuphatikizapo mautumiki ndi mautumiki. Ndipo mzinda wawung'ono umene uli ndi ufumu pamwamba pa okhala padziko lapansi ndi Mzinda wa Vatican. Amen!Www.philippekacou.org
9. Mdierekezi wapanga dziko lapansi kukhala Edeni wake ndipo mkaziyo kukhala chinthu chake chofalitsira.
10. Mdierekezi wawapatsa amuna zizindikiro zina za kukongola. Kodi ndithudi malingana ndi Baibulo, chizindikiro cha kukongola chili nkhope. Tikuwona nkhani ya Rebecca mu Genesis 24:16, nkhani ya Sarah, mkazi wa Abrahamu mu Genesis 12:11, nkhani ya Rachel mu Genesis 29:17, nkhani ya Abigayeli mu 1 Samueli 25:3, Nkhani ya Tamara 2 Samuele 14:27 ... Koma mdierekezi anapanga zizindikiro zina: matako, kenaka mchombo, kenako mawonekedwe a khungu ndi makongoletsedwe okonzedwa modzipaka, ndi zina zotero. Uku ndiko kutchalenja ungwiro waumulungu: njira yofuna kunena kuti "Mulungu amayenera kuchita zinthu mwanjira iyi." Tsogolo la Yezebeli likusungidwa kwa inu. Dzanja la Mulungu linagwira agalu kuti adye agogo anu aakazi a Yezebeli. Ndipo chimene chinachitika ndi Yezebeli m’chiyani? Agalu sanakhudze chigaza, mapazi ndi manja ake chifukwa cha kuzikongoletsa ndi zopaka ndi zikhadabo zopakidwa. Alongo anga okondeka kwambiri, Mulungu akufuna kukuonani inu monga Iye adakulengerani inu. Khalani monga chonchi! [Mk: Msonkhano unati, "Ameni! "].
#ProphetKacouPhilippe
#PKPCHANNELTV
www.PhilippeKacou.org
Amen
2018 pamenepo koma lero 2023 August 09 ndi malemu eish koma ziko ili shaaaaaa
Continue resting in peace Omega NANKHUNI
5. Ndipo mipingo isanu ndi iwiri iyo inali ndi chikhalidwe chosiyana. Ndipo kuchokera kutsanulira kwa Mzimu Woyera mpaka Mkwatulo, Mpingo wa kwa amitundu udutsa mu nyengo zisanu ndi ziwiri, ndipo ine ndikukhumba kuti ndiyankhule za izo m’mawa uno. Ndipo pa nyengo iliyonse, Ambuye Yesu Khristu adzatumiza padziko lapansi imodzi mwa nyenyezi zisanu ndi ziwiri zomwe Iye wagwira m'dzanja lake lamanja kuti amenyana ndi mzimu wolakwika. Ndipo nyenyezi iyi, ndiko kunena m’ngelo wakumwamba, kutumizidwa pa dziko lapansi, idzagwira munthu woti imugwiritse ntchito kulimbana ndi mzimu wolakwika. Ndiye choncho, malingana ngati nyengo siyinathe, nyenyezi iyi ikhoza kugwiritsa ntchito anthu ambiri. Inu mwawona? [Mkonzi: Osonkhana ati, "Ameni!"].
6. Nyengo yoyamba ndi Mpingo wa Aefeso: Chivumbulutso 2:1-7. Ndipo izo zinachitika padziko lapansi kuyambira chaka cha 53 mpaka chaka cha 170 pambuyo pa Yesu Khristu. Ndipo mipingo ya dziko lonse inali mbali ya Mpingo uwu. Ndipo mtumiki woyamba wa m'badwo uwu anali Mtumwi Paulo. Ndipo pambuyo pa Paulo, Mulungu anaukitsa aneneri angapo m’modzi mwa iwo anali Ignatius wa ku Antioch ndi Polycarp wa ku Smyna. Mpingo wa kwa amitundu ukuvutitsidwa ndi antchito onyenga a Mulungu. Chiphunzitso chonyenga chabadwa, Chogonjetsa anthu wamba: munthu akufuna malo a Mulungu. Cholengedwa chamoyo chimene icho chinatuluka chili mkango. Malinga ndi Chivumbulutso 4:7, mukudziwa kuti pali zamoyo zinayi zozungulira mpando wachifumu: Mkango, mwana wa ng'ombe, cholengedwa chamoyo cha nkhope ya munthu ndi mphungu. Ndipo kwa m'badwo woyamba, cholengedwa chamoyo chimene chinatuluka kukamenyana ndi chiwanda chimenecho ndicho mkango.
PKPCHANELTV
12. Ndipo ngati Mulungu apulumutsa Mkatolika, wa Chiprotesitanti, wa chievangeliko, wa chiBranham, kapena membala m’modzi wa mamishoni ndi mautumiki amenewo, Mulungu ayenera kuchotsa gehena ndipo aliyense adzapite ku Paradaiso, ngakhale Satana. [Mkonzi: Osonkhana akuti, "Ameni!"]. Kodi munthu angakane bwanji m’neneri wamoyo wa nthawi yake ndikupita ku Paradaiso? Kodi munthu angapulumutsidwe bwanji ku Chigumula pamene atakana Nowa? Pamene Ambuye Yesu Khristu anali pa dziko lapansi, zikanatheka bwanji kumukana iye ndi kupulumuka? Dziko lonse lapansi liri ku mphompho chifukwa cha mipingo iyi.
Akufuna kunamiza ndani ome cosmetic sikuti ndi product yawo....iwowo analembedwa ntchito kugulisa ku Malawi....komanso Aliponso ena amene akugulisa ku Zambia
Brain kkkk koma mayiwo akunama lipstick 💄 24 hours nde uli single.
Mama Nankhuni mukumbukirabe chichewa nzabwino.
#ProjetKacouPhilippe
Mawu Achiheberi kwa m’neneri ndi nabi, mawu awa akuyimira: “woyankhula”, osati ochita zozizwitsa kapena wonyamula kudzodza koma wolankhula. Inu mukuwona? Mneneri wam’thenga ndi chikhumbo ndi chiwonetsero cha Mawu a Mulungu mu kam'badwo Kake.
Home is always...best.....Mmmmmmmmmmm.Interesting.......From cape town
The only true prophet of God in this generation is Kacou Philippe.
Ziwanda zomwe nthawi yakale zinayima kumbuyo kwa mpingo wa Chikatolika ziri zofanana ndi zomwe zimayima kuseri kwa mipingo ya Chiprotesitanti, Chievangeliko ndi Chibranham yomwe inu mukuiwona lero. Mu bukhu la Chikatolika mudzawona rozari, makandulo, zofukiza, mtanda ... ziwanda zomwezo zomwe zimayimirira kuseri kwa zinthu izi ziri chimodzimodzi ziwanda zomwe zimayima kumbuyo kwa sitolo ya mabuku a Chikhristu cha Chievangeliko. Chimodzi ndi chithunzi cha chimzake komano mu choonadi chotsalira, Baibulo ndi lolemera koposa mabuku onse ogulitsidwa ku masitolo awa kuphatikizidwa. Ziwanda zomwezo zomwe zimayima kuseri kwa wailesi ya Chikatolika ndi ziwanda zomwezo zomwe zimayima kumbuyo kwa mauthenga a Chievangeliko. Mabaibulo a Chievangeliko ndiwo maonekedwe a Mabaibulo Achikatolika.
Pologalamu yovomerezeka ya Mneneri Kacou Philippe ya Android:
play.google.com/store/apps/details?id=com.matth25.prophetekacou
11. Pamene mtumiki wam’thenga akutumizidwa kudziko lapansi, ndichifukwa chakuti palibe choonadi padziko lapansi ndipo uthenga wake ndiwo wokhawo woona wa nthawi yake. Iye ndiye choyimira cha choonadi. Iye ndi woweruza wa Mawu a Mulungu mu nthawi yake. Inu mukuwona? Pamene Nowa ankalalikira, palibe amene akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Nowa. Pamene Yeremiya ankalalikira, palibe amene akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Yeremiya. Pamene Eliya ankalalikira, palibe amene akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Eliya. Pamene Ambuye Yesu Khristu ankalalikira kumeneko m'misewu ya Yerusalemu, palibe amene akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Ambuye Yesu. Iye anati, "Palibe amene amabwera kwa Atate koma kupyolera mwa Ine." Inu mukuwona? Pamene Martin Luther anali kulalikira mu Germany, palibe yemwe akanakhoza kupulumutsidwa kupatula mwa Uthenga wa Martin Luther. Pamene John Wesley ankalalikira, palibe yemwe akanakhoza kupulumutsidwa pa nkhope yonse ya dziko kupatula mwa Uthenga wa John Wesley. Pamene William Branham ankalalikira mu Amerika, palibe yemwe akanakhoza kupulumutsidwa pa nkhope yonse ya dziko kupatula mwa Uthenga wa William Branham. Ndipo lero inu simungathe kupulumutsidwa koma kupyolera mu uthenga wa m’neneri Kacou Philippe. Ngati inu munali mwana wa Mulungu m'nthawi yawo, inu mukanakhulupirira mwa iwo ndipo ndi zofanana lero.[mkonzi: wosonkhana anena, “Ameni! "].
6. Chabwino! Ife tikudziwa kuti aneneri a m’thenga onse adalandira uthenga wawo kuchokera Kumwamba ndipo tsopano tiyeni tiwone Uthenga uwu kuchokera pa vesi 6 ndi 7. Uwu ndi uthenga woyamba umene ukunena ndi wachiAfrica kuti mwachitsanzo, apembedze Mulungu woona amene anapanga kumwamba: Nyenyezi, dzuwa, mwezi komanso ngakhale angelo akugwa amene amagwiritsa ntchito horoscope, malamulo a chinsinsi ndi zipembedzo. Mulungu sanakhalepo mu chipembedzo. Chikhristu chowona si chipembedzo koma moyo. Mngelo uyu akufunsa achi Haiti ndi achi Benin kuti aleke vudu, unsupa, miyambo ndi mitundu yonse ya mapembedzero ndi kupembedzera ... Mulungu adalenga malo adziko lapansi kuti likhale la moyo wathu ndipo sitiyenera kulisandutsa kukhala nkhalango kapena mitengo yopatulika, ziboliboli ndi zigoba ndi kuzipembedza izo ... Uwu ndiwo Uthenga wa mngelo woyamba. Ndipo mngelo woyamba uyu ndi Mtumwi Paulo. Nyanja ndi akasupe a madzi sanalengedwe kuti azipembedzedwa koma ndi Mulungu yemwe tiyenera kumupembedza; Ndi Mulungu yemwe ali Mlengi. Inu mukuwona?
bwana Brian muzipitaso ku midzi muzikamva mavuto awo from cape town
18. Zabwino! Mateyu 25:6 ...Ife tikukhala mu nyengo ina ya mbiri ya chipulumutso. Si nthawi yakukweza nyumba zachipembedzo zazikulu ndi zapamwamba ndi za mabo, mikeka yapamwamba, mipweya yokonzedwa ndi zidazoyimbira zamphamvu. Iyi si nthawi yokuti munthu wa Mulungu adzilota za nyumba, magalimoto ndi zina. Koma khama lililonse, zopereka zonse zachuma zizipita molunjika kupititsa mtsogolo choonadi ichi chifukwa cha kudzutsa.
19. Ndipo palibe yemwe angakhoze kumutumikira Mulungu pa nkhope yonse ya dziko lapansi pokha-pokha ngati iye ali mawu obwerezedwa pa zomwe Mulungu akuchita pano. Ichi ndicho chifukwa ine ndikutsutsana ndi a Chievangeliko, a Chibapitisiti, a chi Foursquare, ndi ena otero ... Ndipo ine ndikuchenjezani inu motsutsana ndi iwo! Ife tilibe gawo ndi iwo! Musakhale achinyengo ndipo musatikhazikitsire ife tsogolo lina motsutsana ndi ife! Iwo ndi akhwangwala. Ndipo pamene mphungu zifuula, lolani akhwangwala akhale chete. [Mawu a Mkonzi: Msonkhano unati, "Ameni! "]. Ngati inu mumlalikira wa Chisilamu kapena wa Chikatolika kuti mumtumize ku mpingo wa Chibaptisiti kapena Pentekosti, kodi ndiye kuti mwapangapo chiyani? Inu mwangosintha selo ya wa mndende. Ili ndi khola lomwe-lomwelo la Satana. Ndipo ndiwe liwu losokoneza motsutsa pa zomwe Mulungu akuchita pano!
#PKPCHANNELTV
4. Ife tikudziwa lero kuti a Chibranham ndi ofwifwa ndipo ena mwa alevi a William Branham siwovomerezedwa lero mu Mpingo! William Branham amatha kupita ndi kukalalikira mu mipingo pa mfundo zofanana ndi kumalumikizana nawo, ndi osonkhana ake ndipo m’nyumba yake mbusa wa Chibapitisiti amakhoza kuwawelutsa omvera ndi mawu a chilimbikitso ndi pemphero. Izi sizinali zoipa madzulo, koma lero ndikukuuzani kuti ngati ndinu Mkhristu ndiye kuti mulibe ufulu wokhala m'chipembedzo cha Chikatolika, Chipurotesitanti, Chievangeliko kapena Chibranham kapena mapemphero a aneneri awo. [Mawu a Mkonzi: Msonkhano unati, "Ameni! "]. Awa ndiwo maguwa a zonyansa zonse zomwe Mulungu sangazisiye kuti zisalandire chilango. Ngakhale ngati inu mutakhala pa ulendo, inu musapite kumeneko! Kodi inu mudzafuna chiyani pakati pawo? Kodi iwe udzayang'ana chiyani mu mpingo wa Chikatolika, wa Chipurotesitanti, Chievangeliko kapena wa Chibranham, pamene iwe uli mwana wa Mulungu? Malo anu siali kumeneko! Inu mukuwona?
5. Ndipo inu Achibranham, mtundu wa achule! Wamoyo, ine sindidzasiya kukhala kwa inu chimene mkango umakhala kwa mtundu wa mbawala, ndipo ndikadzafa ine sindidzakhala wochepera. Inu mukudziwa ine ndi khansara yomwe ingakuwonongeni inu. Ola lanu la chiweruzo cha Mulungu lafika ndipo inu simuthawa. Mawu ayesa chilichonse ndipo kuwala kwachititsa zintchito zanu kudziwika ...
Yao dje cyrille
Home is the best, kkkkkk akunena zoona kunjakutu sometimes kuli Racism especially USA mmm
Chimwemwe Chimwaza 12. Ndipo ngati Mulungu apulumutsa Mkatolika, wa Chiprotesitanti, wa chievangeliko, wa chiBranham, kapena membala m’modzi wa mamishoni ndi mautumiki amenewo, Mulungu ayenera kuchotsa gehena ndipo aliyense adzapite ku Paradaiso, ngakhale Satana. [Mkonzi: Osonkhana akuti, "Ameni!"]. Kodi munthu angakane bwanji m’neneri wamoyo wa nthawi yake ndikupita ku Paradaiso? Kodi munthu angapulumutsidwe bwanji ku Chigumula pamene atakana Nowa? Pamene Ambuye Yesu Khristu anali pa dziko lapansi, zikanatheka bwanji kumukana iye ndi kupulumuka? Dziko lonse lapansi liri ku mphompho chifukwa cha mipingo iyi.
Chimwemwe Chimwaza
12. Ndipo ngati Mulungu apulumutsa Mkatolika, wa Chiprotesitanti, wa chievangeliko, wa chiBranham, kapena membala m’modzi wa mamishoni ndi mautumiki amenewo, Mulungu ayenera kuchotsa gehena ndipo aliyense adzapite ku Paradaiso, ngakhale Satana. [Mkonzi: Osonkhana akuti, "Ameni!"]. Kodi munthu angakane bwanji m’neneri wamoyo wa nthawi yake ndikupita ku Paradaiso? Kodi munthu angapulumutsidwe bwanji ku Chigumula pamene atakana Nowa? Pamene Ambuye Yesu Khristu anali pa dziko lapansi, zikanatheka bwanji kumukana iye ndi kupulumuka? Dziko lonse lapansi liri ku mphompho chifukwa cha mipingo iyi.
PKPCHANNELTV
Asakunamize ifeso tilikokuno tikufuna tiziva zimene zikuzitika kumalawi Brian and we like you Brian zitaye zimenezo plz
Koma television channel imeneyi aaaaaa pa chabe , koma Brain asamale cos tikumamuona , adzagodzuka ku mawa tv station yake kulibeko komanso mwai kuti adzakhala kulibeko , akanazapitira limodzi
41. Kubwerera ku vesi 10, yemwe alipo ndiye Kaisara, amene amabwera ndi Mfumu Nero yemwe wakhala ndi miyezi isanu ndi umodzi ya ulamuliro wankhanza. Ndipo iwo mu mipingo iyi adzadabwa, koma ife tikudziwa kuti iwo apita ku gehena. Wachisanu ndi chitatu ndikutsatana kwa apapa. Mu vesi 12: Mafumu osakanizidwa awa ali pazidindo limodzi: Hitler, Stalin, Mussolini, ndi zina zotero. Ndipo mbali inayo, atsogoleri a mpingo uliwonse kupatulapo mneneri wamoyo wa m'badwo. Iwo ali ndi mapangidwe omwewo ndi Tchalitchi cha Katolika; mmodzi anapha Akhristu, winayo anapha Ayuda. Ndipo mu Tchalitchi cha Katolika ndi chithunzi cha Tchalitchi cha Katolika chomwe chikutanthauza mipingo ya Chiprotestanti, Evangelical ndi Branhamist kuphatikizapo mautumiki ndi mautumiki. Ndipo mzinda wawung'ono umene uli ndi ufumu pamwamba pa okhala padziko lapansi ndi Mzinda wa Vatican. Amen!Www.philippekacou.org
12. Ndipo ngati Mulungu apulumutsa Mkatolika, wa Chiprotesitanti, wa chievangeliko, wa chiBranham, kapena membala m’modzi wa mamishoni ndi mautumiki amenewo, Mulungu ayenera kuchotsa gehena ndipo aliyense adzapite ku Paradaiso, ngakhale Satana. [Mkonzi: Osonkhana akuti, "Ameni!"]. Kodi munthu angakane bwanji m’neneri wamoyo wa nthawi yake ndikupita ku Paradaiso? Kodi munthu angapulumutsidwe bwanji ku Chigumula pamene atakana Nowa? Pamene Ambuye Yesu Khristu anali pa dziko lapansi, zikanatheka bwanji kumukana iye ndi kupulumuka? Dziko lonse lapansi liri ku mphompho chifukwa cha mipingo iyi.
PKPCHANNELTV
Brian asakusokanize ameneyo ndioenda enda usalibane nae tikufuna tiziva zenizeni osati zauhulezo ife sitikufuna Brian ok
Koma Brian mpaka kuseka kwa Indiana police umakwana brian
Koma Inu mafuso kkkkkkk😂😂
Uhmmm interesting.
Davie Wilson Themu , 8. Inu mukuti: "Chiukitsiro chinachitika kale!" Iwe ukhale wotembereredwa! "Ife sitimataya chipulumutso kotero kuti ine ndikhoza kuchimwa, ichi chilimphotho yomwe sindidzakhala nayo padziko pano koma ine ndapulumutsidwa!" Wotembereredwa akhale munthu amene pakamwa pake patha kutuluka mawu otere! [Mkonzi: Msonkhano unena, "Ameni!"] Ndipo popeza inu simukuyenera kukhala ndi mphoto padziko lapansi monganso kuli Kumwamba, ndiye muloreni iye amene amakupatsani chakhumi, chopereka kapena mphatso iliyonse akhale wotembereredwa kwamuyaya. [Mkonzi: Wsonkhano unena, "Ameni!"] Inu mukuti, "Ine ndinabatizidwa mu dzina la William Branham" iwe ukhale wotembereredwa! Iwe ukuti, "Ine ndine wa Bapitisiti," iwe ukhale wotembereredwa! Iwe ukuti: "Ine ndine wa assemblies of gods", iwe ukhale wotembereredwa! Iwe ukuti, "Ine ndine Mkatolika", iwe ukhale wotembereredwa! Inu mwawona? "Mulungu adalitsidwe, ine ndinatsatira maphunziro a zamulungu ...", iwe ukhale wotembereredwa!