Ku UTM Kuli Ana Pa Ndale (Lyton Mangochi Response) - Mzika Yokhudzidwa

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 21 жов 2024
  • On Nyasa VoiceBox, a concerned citizen, in response to Lyton Mangochi's claim that Michael Usi is not a true member of UTM, said that UTM is full of amateurs in politics.
    Ku Nyasa VoiceBox, mzika yokhudzidwayi, poyankha Lyton Mangochi yemwe adanena kuti Michael Usi si membala weniweni wa UTM, adati UTM ndi yodzaza ndi anthu osachita ndale.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 93

  • @thulambale2836
    @thulambale2836 2 місяці тому +1

    Very good speech bwana ziuzeni zitsiru izi zikusokoneza Malawi

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 2 місяці тому

    Aaaaah uyuso ndi Gwape weni weni za Michael Usi nchimodzimodzi Nankumwa

  • @AishaChipande
    @AishaChipande 2 місяці тому +2

    Inuso Pitani uku mapwala anu ndi usi wakoyo nonse

  • @muhaspader3593
    @muhaspader3593 2 місяці тому

    Pitani kù Dowa muzikalimba mbatata
    Zaziiiiiii!

  • @AgnesMatola
    @AgnesMatola 2 місяці тому

    Nthumwi za Dr Chikangawa iziiii😢 Ziphe ndithuf

  • @owenskabazanechiumia3543
    @owenskabazanechiumia3543 2 місяці тому

    Zaziii Lyton Mangochi akukamba zowona, Iwe ndiye wabodza

  • @HannockMesiwni
    @HannockMesiwni 2 місяці тому

    Ndiwe galu kwabasi ndinu amene mukusakisa Malawi

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 місяці тому

    Mumamynyoza ku Tonse alliance panondiye muziyankhula zausiru

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa 2 місяці тому

    Akulu tamva mwayankhulazo za nzeru nzochepa 1 Kyton mangochi sanalakwitse 2 sizikukufunika unboni kuti USI ndi wanu wa MCP 3 mukati mu ku UTM kuli ana pa ndale ndichifukwa chake tinachikonda motsogozedwa ndi malemu inuyo khalani ndichipani cha magogocho 3 president wanuyo alipamenepo chifukwa UTM 4 mwati mumuza manganya njomba zoti agwetse kaliyati tikudziwa kare ndizinene mukuchita simukudziona kupusa nokha 5 paja ndale zanu mumapanga usiku anthu osayamuka basi ndilekere pompa ndingaononge

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 місяці тому

    Iwenso ukuyankhulawe ndi wa Mcp ngati ukumufuna Usiyo ingomutenga ndi chani chomwe chikuonesa Usi kuti ndi wa Utm

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 місяці тому

    Usi chisankhidwire u Vice president sanapangisepo msonkhano ndiliti anapitapo koyasa makandulo umuuze Usi kuti asasokoneze utm

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 2 місяці тому

    Kape iwe ndiwe wa MCP

  • @apatsaphanga9252
    @apatsaphanga9252 2 місяці тому

    Mzika imenei imatha kulankhula mafumu amenewa

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 місяці тому +1

    wopusa kwambili mkunama wovota ngati ndiwe wekha ngati ndife anthu inuyo ndimene mwampha mramu wathu inu wopusa ife zikutiwawatu muribeso ndiuremu poyankhura popanda sauros bwezi mutauwona mpandowo muziyamika ndarama ndiweyo zikupeteketsa ndikuuzatu sitinapusetu

  • @ChimwemweKaonga-tm9ek
    @ChimwemweKaonga-tm9ek 2 місяці тому

    Kabembe akhale VC wa usi

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 місяці тому

    Iwe mchewa aaaaa ukutani apa kalowe kudambwe ukavale 😂😂😂 kadzole manyi uko shaaa

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 2 місяці тому

    Ana ????? Tiyeni tithamangisane tione atawine....

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 місяці тому

    Manganya usiye kusokoneza Utm Usi ndi wa mcp

  • @mdakakachokammanja7510
    @mdakakachokammanja7510 2 місяці тому

    Akuchita kumveka kuti ndi mchewa munthuyu. Kodi anthu a MCP zikukhuzanitu kwambiri kutuluka kwao ku alliance 🤣

  • @chipi892
    @chipi892 2 місяці тому

    Mwalira man

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc 2 місяці тому

    Useless government

  • @FelixRonald-fx9df
    @FelixRonald-fx9df 2 місяці тому

    Nchoka iwe wa MCP mbuz ya munthu🤣🤣

  • @BeatriceProfessor
    @BeatriceProfessor 2 місяці тому

    Tatopa ndi boma la old school

  • @SandramuYonasi
    @SandramuYonasi 2 місяці тому

    Koma ndiwe galu kobasi,ndimaona ngati ukuyankhula zanzelutu koma ndiwe galu mbuziwe ndipo sudziwa kanthu ndi Michael usi wako yemweyo.

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 місяці тому

    Chilima anapanga mistake kusankha usi kukhala vp sanaziwe kuti ndi udasi.ndichimozimozi azibusa wome anasainira mugwirizana wa mcp ndi utm chilima sanaziwe kuti azibusawo akumugulisa pano azibusa wo abisala chilima atafa.usi apange chake chipani asiyire anawo vuto palibe . And iwe usachuluke zeru amene anayamba ndale zolakwika ndi ndani ndimayesa ndinu mcp

  • @cacksygustarf6260
    @cacksygustarf6260 2 місяці тому

    Chigule ichi hiyaa😂😅

  • @smartjilamu8026
    @smartjilamu8026 2 місяці тому

    😂😂😂 kufuna ndalama iwe a usi apanga chani pamaliro achilima lero akale dolo zoona

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому

    Kkkkk Ku utm kuchitika zomwe zinachita Ku DPP ndithu amalawi timaiwala msanga tiyeni tiwaonela akaliyati ndi anjawala

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 2 місяці тому

    Ndipo iwe ulibe zina nyani iwee

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t 2 місяці тому

    Galu iweyo wamva usalimbane ndi Peter muthalika musiyeninso mangochi chilungamo chiziwike mesa

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 місяці тому

    Ngakhale anapiye amadziwa amayawo pakati pankhuku zambiri.

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 2 місяці тому

    Uyu ngwa mcp.uku ndikulira alliance yathapo basi.

  • @hastingschitaniphiri5071
    @hastingschitaniphiri5071 2 місяці тому

    Iwetu ungovutika. Walowerera zakubanja laweni 😂

  • @GilbertKuchipinda
    @GilbertKuchipinda 2 місяці тому

    Tamajamani za ku MCP kwanu konko man.zaugalu eti

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 2 місяці тому

    Iweyo ndiwe chitsiru tsopano palibe chomwe ukunena

  • @CLIFORDZAKARIA
    @CLIFORDZAKARIA 2 місяці тому

    Ife sitili mbali yanu pangani ZANU basi isiyeni UTM yomwe inawinisa MCP ndipo ikuchoka final. Umva mmbebe iwe.

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 2 місяці тому

    Ati bungwe la agra 😅😅😅😅😅

  • @CLIFORDZAKARIA
    @CLIFORDZAKARIA 2 місяці тому

    Dzingodyani ndalama za blood zo

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 2 місяці тому

    Manganya siwa utm ndiwa mcp we all know about that

  • @ElisyIweni
    @ElisyIweni 2 місяці тому

    Mcp imadziwatso mulungu

  • @ebenezerkamanga6016
    @ebenezerkamanga6016 2 місяці тому

    Iwe mbuzi iwe machende ako PA umunthu wake uti iwe zoti usi ndamene amanena maboza ukuona ngat sitikudzea

  • @AishaChibwana-b8o
    @AishaChibwana-b8o 2 місяці тому

    Kagwere iwe ingodya banzai umwere basi zatha

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira 2 місяці тому

    Iwe ndiwe opepera kwambiri. Anthu akudziwa kuti utm ndiyiti

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki 2 місяці тому

    Ukuziwa chani pandale iwe wa nyau! Chomene umaziwa ndi kuwunika mbewa

  • @anifoiuene6301
    @anifoiuene6301 2 місяці тому

    Iwenso ndi kape machende ako ndi abambo ako

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 2 місяці тому

    Mani manyi anu ndi layton wanuyo mulila simunati khaya mwachita kupangana mulila fwiiiiiijnyooooooooo

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 місяці тому

    Machende Ako ndi Chakwera wakoyo

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 2 місяці тому

    Mutu wankhani muziyika ogwilizana ndizomwe munthu akufotokoza,sono apa sindinamvepo zoti a utm ndi anatu

  • @IsaacMumba-er5hu
    @IsaacMumba-er5hu 2 місяці тому

    Usi ndi chisilu iwe nawe iwe

  • @LucianoKapepuza-sy9wx
    @LucianoKapepuza-sy9wx 2 місяці тому

    Iwe nfichisilu kwambili nofu a MCP ndi utm anapasa zake nofu ndindani galu iwe

    • @lungsTug
      @lungsTug 2 місяці тому

      Nyasa Box mukutiyimilira

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 2 місяці тому

    Gulu iwe Chikangawa wa MCP choka lwe

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell 2 місяці тому

    Aaaa palibe zimene ukuyankhula iwe

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 місяці тому

    Kodi mwadya zingati?

  • @peterkinsLekera
    @peterkinsLekera 2 місяці тому

    Tikutsikani mukapitiliza kuponya izizi

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 2 місяці тому

    Iwe NDIwe chikangawa galu wamunthu

  • @RonaldGama-gz9ug
    @RonaldGama-gz9ug 2 місяці тому

    Inu omdala mukumveka ngati ochewa okulilongwe ..mukudziwa kuti game yagona apa kuti kuturuka kwa UTM chanu kulibepo mCp agalu inu

  • @bensonbwanamili2926
    @bensonbwanamili2926 2 місяці тому

    Golu

  • @senaherbo3714
    @senaherbo3714 2 місяці тому

    MCP member usatinyanse kagwereko

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 місяці тому

    Fisi iwe garu kwabasi

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 2 місяці тому

    Osewo sangamake kwa usi angozivuta usi ali ndikuthekera kopanga chilichose ndipo ali ndi sapoti

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo 2 місяці тому

    Mawu

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 місяці тому

    Yooo uyakhuluma lo bhuti

  • @IsaacMumba-er5hu
    @IsaacMumba-er5hu 2 місяці тому

    Iwe ukuyankhulawe uli chisiluso kwambili wamva

  • @bensonbwanamili2926
    @bensonbwanamili2926 2 місяці тому

    Achewa okumba

  • @JamesMaduka-wk8xi
    @JamesMaduka-wk8xi 2 місяці тому

    Ndichitsiluchamunthu chosadziwakulankhula chilimawanzuzidwakwambili mu mcp ndindaniemwesakudziwazoti mcp yaphawanthu 10 kuyambilalelo abamboinu nzimuwa mulungukuloweni mutilankhulitsapambali ufunakunenakuti potianthu ambiliamamwalila imfayachilima tisaiganizile pepa mkuluwanga masomphenyaakulankhulaulibe uchepetse kutamikila mcp please

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 2 місяці тому

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 місяці тому

    ankakhara kuti ndimunthu wachikondi usi bwezi anawonesa mphavu pamariro azake anapangapo chani kufera ndarama zo unena chani wopenga iwe usiyo ndiwanu ife wathu ndi mayi kariat wamenya nkhondo yayikuru kwaife takubanja or kuchipani mkungo rubwa rubwatu muzayakatu tikazayamba kuwurura zose dikira mzawona anthu wopusa inu

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 місяці тому

    And kangati utm ngati yabalalika iwe chikukhuza chani mutenge usiyo akhale kumbali yako vuto palibe ndi anthu amene ali kutigeranji ko apa tikupanga za utm osati tikuferanji.

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 2 місяці тому

    Iweyo wunena apaxi ndi za satanic kuyenda njomba yake yiti zakupha anthuzo ngati momwe munayedzekera Chilima?

  • @SALIMASSAN-vr8ld
    @SALIMASSAN-vr8ld 2 місяці тому

    Inus nde palibes bwanj pamenep nde mwat mwakambap chan zikuvutan tangodikilan

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому

    Bvuto kumalawi ndiumbuli umbuli sizinthu ai chipani chimakhala ndi malamulo koma amalawi umbuli umabvuta kwambili

  • @wittinessnkhokwe
    @wittinessnkhokwe 2 місяці тому

    Achitsiru awa angopanga phokoso basi,sukuona kuti mbuzi yako chakwela ndiye akuzuza Malawi ndi chipani chake chokupha ichi

  • @RabsonSauti
    @RabsonSauti 2 місяці тому

    Ndwe galu wa munthu.munthu wakupha iwe.Njomba imene ikuenayo ndye it? Njomba yakupha,chipani chanu MCP chakupha.mulungu azakulangani inu.

  • @lenzophiri
    @lenzophiri 2 місяці тому

    Kape wa mcp

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 місяці тому

    Mwana wa chikangawa usatinyaseso apa mumamudziwaso mulungu inuyo Ana oyipa inu.

    • @NelsonMataka-d1w
      @NelsonMataka-d1w 2 місяці тому +1

      Tudikira convention kuti manganya abwere kwao kwa Dr. Chikangawa

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 місяці тому

    marlllll

  • @innocentnjoka7014
    @innocentnjoka7014 2 місяці тому

    Iwe ndi MCP yakoyo kagwere uko madevils

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 місяці тому

    kodi iwe wawonekeratu kuti wakupasa ndarama zambiritu wosiya moyo sakuziwika ifeyo tikurira mariro ukunama iwe murungu simunthu ariyese ndiwakufa basi ukuyankhura mopusa kwambili

  • @BensonPiasi
    @BensonPiasi 2 місяці тому

    Iwe mapwara anu abambo inu usi anga gwese ndani garu iwe

  • @RonaldGama-gz9ug
    @RonaldGama-gz9ug 2 місяці тому

    Iwenso ndiye galu wa munthu ulibe mzeru chakwera ndi emwe anapha chilima kaliati sakufuna u pulezidenti muliradi muonadi

  • @victormaluwa6710
    @victormaluwa6710 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy 2 місяці тому

    Aaaaaaaaa iweeee chitsiru iweeee mpatse masamuwo tione amneyo sangawine amneyo iwee opatsidwa ndalama uzingodya ndalamazo

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 місяці тому

    Mwayamba chibwibwi litilo?

  • @jackmambo2638
    @jackmambo2638 2 місяці тому

    Tandipaseni number yake uyu

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 2 місяці тому

    usiyo anapangapo chani pamariro athu amangodikira u vp basi pari zeru apo munthu wachikondi sasowa mwasewera game yopusa mzayaruka tiyeni nazon

  • @Margaret-t7m
    @Margaret-t7m 2 місяці тому

    Chokani apa mukudya nawo ndrama za boma inu, ngati mukuti SK anawalako nofu chifukwa cha chakwela iyeyo chakwelayo waima kangati payekha osawina? Agalu inu kagweleni uko

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому

    Uneyo ndikupempha autm kuti mukamatukwana ausi mukuyenela muzisuzumila malamulo achipani chanu kuti kodi akuti bwanji ndipo musamale patsogolapa usi akhoza kukhala bwana wanu manyazi adzakugwilani ndiye samalani anjalwala komaso akaliyati

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi 2 місяці тому

    Iwe mcp inawina khamba ka chilima what are you talking about

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 2 місяці тому

    Galu iwe wa nyau panga zako za mcp mbuzi zikukhuzani ndi chani machende