AYAMBAPO KU UTM__26 November 2024

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 28 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 59

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 3 дні тому +2

    Namiwayo pa thako pake amupwetekesa akumutumawo

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 3 дні тому +12

    MAGANIZO ANGA NDIKUOMA KUTI CHAKWERA AKHALE PRESIDENT WA CHIGAO CHAPAKATI ,KUMWERA KOMASO KUMPOTO ASAZAPITEKONSO CHIFUKWA ZOMWE AKUPANGA AKUYAMBITSA KUGAWANIKA MITUNDU .IWOWO AKAMATI MADEMO MUZIKAPANGIRA KUMWERA KWANU KONKO NDIYE KUTI SAKUFUNA KUTI ANTHU ACHIGAWO CHAKUMWERA AZIPITA PAKATI, NDIYE CHIDULE CHAKWERA ASAKHALE PRESIDENT WADZIKOLONSE AKHALE PRESIDENT WA A CHEWA ,KUMWERA KUMPOTO TIKHALA NAWO ATHU CHIFUKWA AKUCHITA CHAKWERA NDI NDUNAZAKE NDI UCHITSIRU

    • @DavidPhiri-o6w
      @DavidPhiri-o6w 3 дні тому

      Panthawi yomwe chilima anagendedwa ku mwera nthawi ya albinos killer Peter muthalika, petera wano he stopped to go other side of malawi foolish talk don't forget what you did before

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon 3 дні тому

      @DavidPhiri-o6w IWEYO UKATI foolish what do you mean? Ndi chani chomwe ndalankhula cholakwika ? Kapena ukupanga coment utaledzera ? SAMALANI ndi kayankhulidwe cause timachezapo apa koma sitimadziwana ndiye osazitenga kuzindikira CHONSECHO amene kuyankhula naye sukumuziwa ndife isiyana kabadwidwe , kakhalidwe please

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon 3 дні тому

      @DavidPhiri-o6w utapanga check ma message anga ndiye undiuze kuti ndipati pamene ndanyoza kapena kulakwitsa kuti ukafike potulutsa chichewa choti foolish

    • @JosephyChithope
      @JosephyChithope 3 дні тому +2

      Wosati president wachewa ifeso sitikumufuna chakwerayoo ndiwakhaza akhoza kuyambitsa nkhondo

    • @philimonstepe4795
      @philimonstepe4795 3 дні тому

      Anthufe tilibwino kuyankhula zinazi

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 дні тому +4

    Tigawane dzikoli , nyau zikhale ndi mbaliyawo zizilamulana nyau zokha zokha ,
    Zimenezi zichitike ndipo zisalepheleke

    • @philimonstepe4795
      @philimonstepe4795 3 дні тому

      Pangani zogawanazo koma kumbukiran kut kupatula president zigawo zonse za Malawi zimadalirana mwachitsazo timalandira mvula yosiyana zokolola zosiyana ndiye tisanayankhule tiziyamba taganiza bwino

    • @rashidadan2533
      @rashidadan2533 3 дні тому

      @philimonstepe4795 zikativuta zokolola tizipita ku Mozambique

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 3 дні тому +4

    KOMASO A POLICE NDI MBUZI ZA ANTHU NTCHITO YAWO SAIDZIWA KOMASO A SILIKALI ATHU MBUZI ZA ANTHU SAKUDZIWA NTCHITO ZAO BWANJI AKUNGOYANG'ANIRA ZAUCHITSIRU ZA MCP

  • @PeterKambuzi
    @PeterKambuzi 2 дні тому

    Iwe ngati wadya ndarama za ku mcp nawenso panyeropako namiwayotu sakurakwa

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 3 дні тому +2

    Manganya akulakwa auze anthu kuti iye si President wa UTM si member ayi ndi munthu ngati Ineyo

  • @MathewsChawanje
    @MathewsChawanje 2 дні тому

    Kuyambira pano mukafuna kuchita mademo mu lilongwe, ngati palibe. Chilolezo chokwanira mmmm

  • @JosephGama-v7r
    @JosephGama-v7r 3 дні тому +2

    Palibe chisankho chomwe chidzayende bwino ngati zipani zotsutsa zikupondelezevdwa

  • @BonongweRobbie
    @BonongweRobbie 3 дні тому

    I don't think people from Ndix can do that Am from Ndix . Anthu ndiwokwiya ndi munthu ameneyi kuno .Ayesere ku bwera kuno azawone ngati Ali olandiridwa

  • @Tophillpvtsecondary-x7l
    @Tophillpvtsecondary-x7l 3 дні тому +1

    God is watching whatever is happening one day freedom will be revealed

  • @MathewsChawanje
    @MathewsChawanje 2 дні тому

    Or mutabwela komabe chazeru ndi kukumana NDI ando

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 3 дні тому +1

    Aaaa mcp nde imeneyo no DEMOCRACY KOMA IYE ANALOWA BOMA NDI MADEMO NAWO ARMY ALI DZIIIII ADYA NDALAMA ZA MCP KOMA MALAWI TOLI PAMOTO NDI CHAKWELA UYU

  • @Martinchikwakwa-j9l
    @Martinchikwakwa-j9l 3 дні тому

    Anthu sakukufunani Mai mukukakamila chani inuyo Mai sitikukufunani muchoke

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 3 дні тому

    Usi kufupika koma dzimachende dzazikulu

  • @chimwemwedulla6760
    @chimwemwedulla6760 3 дні тому

    Manganya ndiosokoneza kufipika kwake uku ndiuchitsiru chabe ameneyu

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 3 дні тому +2

    I don't think MCP izapitanso ku Southern Region,
    Munthu akavala cha MCP ku Southern Region aziphedwa

    • @philimonstepe4795
      @philimonstepe4795 3 дні тому

      @@Homeofpeace321maganizo olakwika amenewo CHOTI mudziwe ku central region kuli anthu ambiri aku southern region

    • @PetrusTlhokwane
      @PetrusTlhokwane 2 дні тому

      Or ku Northern Region Singabwere Chakwelayo azikhala komweko asayelekeze kubwela kwathu kuno tidzamuloza ife azafa uyo ndipo ife sitimadalira pulezideti

    • @Debbie2004-x9q
      @Debbie2004-x9q День тому

      Nde you call this democratic country pamene it’s rotten from the top to the bottom?? Malawi kunvetsa chisoni

  • @YoweliChipapaChipapa
    @YoweliChipapaChipapa 3 дні тому

    Bomba lake liti loyenjezera nseulo

  • @MarvinChilombo.flourish
    @MarvinChilombo.flourish 3 дні тому

    Usi akusokoneza chipani cha UTM. Akuzimvaso kukula kuposa amzake onse poti akuyendera MG2. Mbali inayi awa anapita kunyumba kwakewo akungowonetsa kusazindikira komanso ndi ma fortune seekers. Zikuvuta kuvomereza kuti ineyo basi kwanga kwatha?

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 3 дні тому +1

    NDIYE KUPANDA NZERU KUONJEZA MISEU CHONSECHO FERTILIZER KULIBE , MAFUTA KULIBE CHAKUDYA KULIBE ANTHU AKUFA NDI NJALA ZAUTSIRU

  • @chimwemwedulla6760
    @chimwemwedulla6760 3 дні тому

    Anthu amenewa ndinakumana nawo akuti akungopita kukadya nawo

  • @stanleymabuku9749
    @stanleymabuku9749 3 дні тому

    Ine ndikuona kuti anthu akumwera komanso aku mpoto onse akasokhane ku central region kukapanga ma demonstration

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 дні тому

    Ma million aanthu kukhalira kumudandaul munthu modzi iiii minyama Chakwera ndwe otembeleledwa msaname lero ndwe ochenjera koma siku lidzafika udzatuluka mamina maso

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 дні тому

    Chakwera angokhala president wa ku Lilongwe basi zikuoneka kuti ali ndi tsankho

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 3 дні тому +1

    Ausi akupwanya malamu

  • @julietsaeed8647
    @julietsaeed8647 3 дні тому

    Magetsi anazima zaka 6, koma nduna yazamagetsi sinatule pansi udindo. nduna yabodza ngat iyo, ayi nyani anakola magetsi mpaka kuzimitsa.

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 3 дні тому

    NKHAZA AKUCHITA CHAKWERA ZI MAI SAKUWONA MATAKO YAKO MAI CHAKWERA MBUZI IWE MAMUNA WAKO AKUPEREKA MIMBA KWAZIMA OSIYANA SIYANA NDIWE CHITSILU NGATI MAMUNA WAKO CHAKWERA

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya 3 дні тому

    A chakwera please dziko li ndi latonse
    Palibe chosatha moyo ndi zina zimatha mukulola izi zidzichitika chifukwa chofuna kulamulirirabe woti moyo wa chilima udapita banja lake ndi abale akuvutika
    Pomwe inuyo mukuti muli nokha
    Yet malawians are suffering like gehena

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga 3 дні тому +1

    A utm nawoso mitu singwira

  • @Saeed-r3z
    @Saeed-r3z 3 дні тому

    Utm zinatha pamenepo chilima Ana joina KU gwirizano wa tonse

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 3 дні тому

    Misewu yake iti......very poor constructed roads yayamba kale kuphwasuka coz of such thieves and liers in power

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 3 дні тому +1

    Akumpoto akakhale ndi anthu akumwela aulesi saziwa kulima lfe kumpoto tikhale potokha not anthu akumwela alomwe maboza kwambiri koma kulima ai

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 3 дні тому

      Ndiwe chistilu chachikazi akubwela amadya kwanu?

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 3 дні тому

      Mulungu akukhululukire pena pake zoyankhulazi ndizimene mukuputa nawo ukali wa Mulungu mama ndani anabwera kudzapempha kwanu kuyankhula ngt sindiwe mzimai bwanji iiii Mulungu akuoneno komwe muliko

    • @Debbie2004-x9q
      @Debbie2004-x9q День тому

      Ndale za mtundu nde zopusazo. Not only are the politicians stupid but also the country’s people

  • @DanielDoctor-t3p
    @DanielDoctor-t3p 3 дні тому +3

    Chakwela amalimbana ddp malo mokhoza dziko garu iwe

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon 3 дні тому +1

      @@DanielDoctor-t3p CHAKWERA simunthu oti angakonze dziko ndiolephera uja chomwe AKUDZIWA ndi kumanga anthu komaso kupha basi,

  • @blessingschirwa7292
    @blessingschirwa7292 3 дні тому

    Are you sure what you're saying about cost amount per kilometre MK2billion that's a lie there's no such, which company charges you that much.

  • @chimwemwedulla6760
    @chimwemwedulla6760 3 дні тому

    Olo chipani cha usi chingapite kuti?😊

  • @emmanuelchimusi8844
    @emmanuelchimusi8844 3 дні тому

    Sanawayitane anabwela okha

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 3 дні тому

    Anapanga conventional momphwanya malamulo achipani cha utm panthawi yomwe anali pa u president tsopano don't complain because you started when Usi was talking about breaking rules of the party. Nkhonya yobwezera yimaeawa kuposa yoyamba 😂😂😂my favorite Vice president USI, i love you don't listen to those stupid people. We are behind you man my vote my ❤️💝😘

    • @MacfelsonMunthali
      @MacfelsonMunthali 3 дні тому

      You have spoken my mind, they were suppose to follow the party constitution,instead they chose to take shortcuts. Receive the out come in name of devil

  • @DanielGanizani-h8r
    @DanielGanizani-h8r 3 дні тому

    Opposition yathu ndi yomwe ikuonongesa Malawi,Kaya kukalambadi?anzao sakusata malamulo koma iwo akumakakamizidwa kutero iwo ndikumavomeladi,pankhondo mumasata malamulo?pano tisakhazikise dpp kuti tiifere ayi koma Malawi tifela iye amene ati aonese mtima ofela Malawi,osati ena akufukizidwa ndi usi wina akudya ma nyivwinyovwi kunyumba kwake ati kudikilila ku state house,Dr Kabambe tikukuonani Malawi sali mtulo.

  • @DavidNdozi
    @DavidNdozi 3 дні тому

    Umbuli