MAFUNSO OMWE ANAFUNSIDWA A MOSES KUNKUYU NDI ATOLANKHANI |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 57

  • @AllanJentala-g6h
    @AllanJentala-g6h 10 годин тому +2

    Kupatula za ndale ineyo Moses Kunkuyu amandiyankhulira mwa mzeru kwambri❤❤❤❤❤

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms 6 годин тому

      Zelu zake ziti nenani

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 5 годин тому +1

    I think atola nkhani ali pamenepa nd a mcp

  • @memorychimpesa198
    @memorychimpesa198 10 годин тому +1

    Za commission of inquiry ya ndege komanso zachi machine ku MEC simukuyankhulapo bwanji? Mxiiiew!!

  • @ShaibuMbwana-wv9nj
    @ShaibuMbwana-wv9nj 12 годин тому +1

    Uwu akuyankhula mwauchisiru ndale zokhazokha he's not speaking as a minister of Malawi but as MCP minister and that's foolish.Panopa things are worse kaya

  • @MarkMasangwa
    @MarkMasangwa 10 годин тому

    Plane crash inquiry bwanji sakufotokoza 😂😂😂😂

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 6 годин тому

    Chikangawa aaaaaaa aiiiiiiiii Bingu si inuyo mupha 123 kupatikiza chilima

  • @munyenyembe
    @munyenyembe 8 годин тому

    Kodi nkhani ya wittika ija mukuti nayo bwanji poti akunkuyu munamupha chifukwa cha hule 😢😢😢😢

  • @emmanuelchedab760
    @emmanuelchedab760 10 годин тому

    Hahaha nde zikukanika bwanji kuli fotokozera dziko kugwa kwa ndege ija ku chikangawa komaso kuti a president anatinamiza

  • @TumaleChiona
    @TumaleChiona 10 годин тому

    Palibe fundo apa uyu ndikapetu ndipo dpp my vote

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 10 годин тому

    aaaaaa palibe chamzelu apa zachimachini sakuyankhapo zandege sakuyankhapo kuthamangila zaziiiii

  • @dicksonhangiwa7847
    @dicksonhangiwa7847 9 годин тому

    Koma mafunso ake ndiye odzidzira, atolankhani ake amenewa bwanji

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman 3 години тому

    Musamanamizile amalawi ayi kod mukuti Madina akubwelerao kwa one ndili kumudzi pindu ndi chani panopa

  • @PriscillaKhumbanyiwa-i1d
    @PriscillaKhumbanyiwa-i1d 10 годин тому

    Makhulupila kukambilana lelo akukuyu inalipo nthawi yomwe sauli ama ntchingila njila Davide kupangila chiwembu chosiyana siyana koma mapeto wake Davide anakhala mfumu

  • @RajaAlicky
    @RajaAlicky 15 годин тому

    Where is commissional of inquiry

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 7 годин тому

    Pangani fundo fundoless galuwe amene utm inachoka manganya si president wa utm aiiiiiiiii choka

  • @LastonMmanga-r2u
    @LastonMmanga-r2u 7 годин тому

    Amalawi sadikira wina kuwawuza zochita lero, maso athu siakhungu chilichonse tikuwona and tikudziwa, kodi mudapha ku chikangawa tikuwona aja plus witika tikudziwa, agalu anthu oyipa.

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman 3 години тому

    Ine ndingofusa nao kod mfumu angaweluze mulandu was mwana wake kapena amfumuo kuweluza mulandu was chemwali ao chikuvuta chani ngat palibe vuto kwachosa anthuo chikuvuta chani kwa achosa mmayesa muli okhozeka ikaniponi Ena mutamangisane pa ground

  • @ThialingsonChiphwanya
    @ThialingsonChiphwanya 16 годин тому

    Bwanji mwalankhura zomveka zomwe ineso ndimafuna kuriuza dziko la Malawi 🎉

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 15 годин тому

    Chakwela mushona ndi buzi,
    So president Chakwela ndi phwala mu zonse.
    Let's exercise our democracy speak ur mind sangakunjateni mutukwaneni president chakwela kuti Pantumbo pake enjoy ur democracy. Ndatha ine Ben Longwe chikuni chautsi delela nyani

  • @CarolyneGunda
    @CarolyneGunda 6 годин тому

    Iwe paja ulisotu ndimulandu wakupha pano sukuzengedwa chifukwa uli muboma tikumana 2025

  • @DanielDoctor-t3p
    @DanielDoctor-t3p 19 годин тому +1

    Sizimenezo akunku tikuti ife tilibe ma I'd tikavote inuyo muchoke bomali sitikulivuna chitukuko chake chiti zautsiru basi anthu akupha inu

  • @dicksonmakawa
    @dicksonmakawa 11 годин тому

    Bwanji osawasiya a mec kuti aziyankhile okha? Kusiyana ndi uyu m'neneli wa boma yu

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 15 годин тому

    Mesa sipika wan uja samalongosoka,,,koma guys ngat mudalila ndalama mwabazo ndithu muzuzisa makolo anu

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 15 годин тому

    Anapha phwitika ndi ndan ? Koma akulu ngat mukulitenga ngat zikoli ndi lamaja mwan, ayi wina achimina

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 6 годин тому

    Boma la mcp linalowa ndi mademo inu mukukaniza mademo pali zelu

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman 3 години тому

    Amalawi tikudzindikila sopano olo inuyo zonse mukulakulazo siza amalawi ayi ndi zanu kod kulolelana kuli kuti ngati mumapanga zithu zanu pambalambanda aloleni amzanu zomwe akufuna na ngatidi palibe cholinga mmayesa zithu zanu za pambalambanda

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh 11 годин тому

    Onama ndiwe. Tikuona zalero

  • @Johndimechikonda
    @Johndimechikonda 7 годин тому

    machende ako konkuyu unapha alani witika

  • @RobertFretcher
    @RobertFretcher 18 годин тому +1

    Khan ya witika ilipat

  • @Zanele1978
    @Zanele1978 17 годин тому

    Aaaa machende wakho iwe konkuyu ndigulu lako

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 6 годин тому

    WITIKA ARI KUTI MCP YATIKWANA KUKUYU KOMA INUYO CHILIMA ORDER FROM ABOVE TO KILL 8 PEOPLE

  • @ElliotNdanga
    @ElliotNdanga 8 годин тому

    Mwambiwo nde mwatinamiza vuto munamupha mwachangu nzanu uja mukanaphunzira miyambi. Komaso inu bwanji mukulandila anthu omwe amatukwana MCP yo, fundo zakuthelani

  • @HiltonZaone
    @HiltonZaone 10 годин тому

    Boma lanu ndi loipa silisatira malamulo

  • @SamuelKamwana-r4w
    @SamuelKamwana-r4w 15 годин тому

    Nanga mulandu wanu bwanji

  • @ShaibuMbwana-wv9nj
    @ShaibuMbwana-wv9nj 12 годин тому

    Chete kulipakula bodza ngat z nzn 😂

  • @SuzgoMkandawire-ss4kh
    @SuzgoMkandawire-ss4kh 7 годин тому

    Atola nkhani opusa inu osafusa mafuso anzeru

  • @LazarousBanda-q8g
    @LazarousBanda-q8g 11 годин тому

    Boma nilomweli zoonadi.osusa anjenjemela

  • @RajaAlicky
    @RajaAlicky 15 годин тому

    Mbuz yamunthu iwe kwanu ndkupha ndkuba mxim

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga 18 годин тому

    Dpp musaiware anapha apwitika paja munaiwalaso beana

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 15 годин тому

    Waziziwa relo zot madem ndi achabe? 2020 iwe ndizako chakwera sunayende paseu? Mmm ukunama siife Ana uziwaso

  • @RobertGoliat-gt2qh
    @RobertGoliat-gt2qh 15 годин тому

    Nonse ndi zitsiru nanu atolankhani Mesa mmene mujanso munali nkhani ya enquiry bwanj simunakambeponso mxwee

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 18 годин тому

    Iwe moses nkuyu manyi ako palibe chomwe unganene apa inu ofunika kuzamangidwa inu mwazuza mizimu ya amalawi osalakwa mbolo yanu

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh 11 годин тому

    Kwanu kwatha man

  • @samsonmtumbati4855
    @samsonmtumbati4855 14 годин тому

    Ankukuyu inu lero mukuona chitsotso chili mmasso mwazanu mwayiwala kuti zanu zitsoso zili mbweee mmaso mwanu mwayiwala boma lanu kuti nslo nachululka zolakwika kwambiri ndibola dpp koma inu fundo mulibe dikirani mutuluke mmenemo ndipamene midzaone kuwawa dziko

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 19 годин тому +1

    awa akuona ngati ndi amuyaya akunkuyu chimwendo chothyola zikhale ng'oma koma afunse kamuzu ali kuti nawonso kuzati ziiiiii 1day

  • @miguels.steenberg6708
    @miguels.steenberg6708 18 годин тому

    Osafusako za equary yachilima

  • @MustafaEdward-bp2ip
    @MustafaEdward-bp2ip 17 годин тому

    Unapha witika iwe

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 6 годин тому

    Utm sili mu mgwilizano ndi usi yekhayo basi

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga 18 годин тому

    Moto sufuka popanda moto tiziona marume tazisiyani paja kulikose mumarowa mukufuna kuononga MCp mukamariza kuononga muthawira kt akukuyu

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 7 годин тому

    Mmm anthu apha albino why mkulephera kuwamanga, mcp anali kupanga zimene zija kuyipitsa mbiri ya azawo

  • @Edward-y3v
    @Edward-y3v 18 годин тому

    Nkhope zakuba izi kkkk

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh 11 годин тому

    Iwe ukutani

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 9 годин тому

    Chokupha ichi

  • @RobertNyaude
    @RobertNyaude 5 годин тому

    Mose

  • @CharlesMbewe-g2o
    @CharlesMbewe-g2o 19 годин тому

  • @stevenchirwa5028
    @stevenchirwa5028 19 годин тому

    Mcp