Kodi ku ungaku united nations meetings amakonda kulodza ma president athu à.kumalawi..Ndiye pano akamdzapitanso adzikakhala ku visitors lodge where they will be cooking and eating.and bathing alone..by theor own malawi cooks.amen.but not the wicked azungus doing or hosting them.
Komatu ku UNGA uku anthu amapangako zinthutu,si amutharika a Peter nawonso zanja lakumazele lidafa that time amachokelanso ku UNGA komwekoso. Nde katemela wake nde waukalitu yomwe amalandila kumeneko.
Rest in peace 😂ngati zili Zowona, ife timawona ngati ndiwoposa Mulungu tu, amuyaya
I dont wait msg say lessen that ...Any way rest in peace chikangawa go well ❤❤🙌🙌
Ndipo ther is no peace for the weaked ndipo sindingamvere chisoni munthu oipisisa Malawi muno uyu!..apite kumene olo ntamva kuti zatero ndizangoti “rip skc and 8pipo”..justice shall be served..Mulingo umene umamulinga nawo nzako naweso uzalingidwa omweo..ndipo munthu sungakhale ndimtendere dziko lonse kumakamba zoipa za iweyo never..mxiew
Ngat ndichoncho ai akapume watidyesa chiteze 😂😂😂😂
Dziko ndila yehova
😂😂😂😂my people ✋ @kullu nafs malikul kitaba kkkk ayi xikomo washiyao wangalusa yakuona eee.
CHEERS CHIKANGAWAAAA AMBUYE KUMWAMBAKO CHONDE DULANI MOYO WA LAZARUS CHAKWERA PLZ GOD IN HEAVEN
Amen
Why mcp is hiding this store
Limpompo yonama makape😅😅😅😅
Asafe koma azingozuzika nd kudwala mesa amat Peter wathu ndi wokalamba😂😂😂😂MULUNGU mwini moyo wapanga zoziwa yekha😂😂😂😂😂
Zoona kod nanga Dan lu apanga bwanji kkkk
Amwelile ndigaluuyu
Ndayamba kukaika zokamba zanu a Ntanyiwa including Bakali Muluzi tv. Nanga munthu kudwala choncho angapange ma press ups chonchija
Ndizoonadi chilimawamwalira ine ndimaona ngatiiye ndimulungu😂😂 8:31
Komano ngati wamwarira zitisangarasa chifukwa athu amazuzika 😂😂😂😂😂
Ngat Sanafe ine ndituma Anthu Kt Akamaleze Mission Kuzinga Ngati Mbuzi
Dziko ndi la yehova ndi zozala zake zomwe. Kwa iye ku khale ulemerelo lero ndi nthawi zonse
Amen
Chimwalire bas chimunthu choipa mtima 😢
Muyeso umene umamuyesa mzako mulungu amakuyesa oposa msikhu wake yense okumbila dzenje mzake adzagwelamo yekha
Azaweluza akha mlungu
Yawina 😂😂😂😂😂 watizuza kokwana
Yawina kkkkk
Kkkkkkkkkkllkkkkk tiziona ndi ntanyiwa
😂😂😂 athu angundika akuti 20 30 wooo 😮
Akhala President wakumalawi, oyamba kuchira ku Garden city
Tsitsani mbendera chikangawa watisiya🕺🕺🕺🕺chisangalalo chake kuposa chapa 1 january😂😂
😅😅😅😅😅
Tasisa kale apite uyu galu
Ntanyiwa, ntanyiwa, ntanyiwa ndakuitana kangat ndi maboza ako kuyipa nkhope ndi mau omwe chitsiru Cha munthu
President or kaya ndindani akadwala asamapite kunja koma adzipita kuchipatala cha m'Malawi mommuno.
Zosatira zakuchingawa zayamba kufika 😊
Akanamugoneka kuzipatala zakwathu konko kumene sakugurirako mankhwala iye waba ndalama zamalawi nanga anthu akumuzi akadwala apanga bwa
Iwe ndiwausilu umatinamiza
Ambuye chonde malidzan 100%😂😂
Zonama zonse mwalankhula umu.
Chepetsani kutalitsa nkhani zonama.
Mawa President akupita kukamenya Golf.
Mwanya nayo mwakhaula
My country is not going well
Yes! We can confirm that here report from galden city tilimbe mtima basi Mikel usi has to appoint his vice president 😢
Achakwera awona zokhoma kwambili chifukwa cha nkhanza zawo ndipo chakwera atafa lelo ineyo ndiye ndisangalala koopsa
Malawi ndimaziwa ine ameneyo 😂🤣
Achipatala chonde yesetsani kuno sitikumufunanso tikamupeza komweko watizumza munthu ameneyi kwakwana anthu 9 osalakwa ajaa mizimu yawo myokwiya anasiya anthu omwe amawathandiza Yesu ndi ambuyedi
😂😂😂 yomweo chikangawa satanic
Ayende ndithu watikwana
Dan lu waigwetsa mcp ndinyimbo
Kodi ku ungaku united nations meetings amakonda kulodza ma president athu à.kumalawi..Ndiye pano akamdzapitanso adzikakhala ku visitors lodge where they will be cooking and eating.and bathing alone..by theor own malawi cooks.amen.but not the wicked azungus doing or hosting them.
Yawa asaname ,,, pretoria ndi jozi ndika mtundatu komanso akulankhulamo angadziwe chani or ku Garden City ko angayandikire 🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂😂 ndudikila apeleke report aboma ndipomwe ndi comment ok
Komatu ku UNGA uku anthu amapangako zinthutu,si amutharika a Peter nawonso zanja lakumazele lidafa that time amachokelanso ku UNGA komwekoso. Nde katemela wake nde waukalitu yomwe amalandila kumeneko.
Kodi anthu openga Inu Kodi munakhalabwanji?
Dzanja LA agogo ako ndilo ladwala mxa
Kod chitedzechi chabwela bwanji ndi chakwela tiyeni tizidzilimbikila osamaloza chala munthu masiku omaliza ano kudzakhala njala basiiiii
Mzukwa umeneu watitopesa
RIP Mr Chakwela 😮😮😮
Pathako panu nonse a dpp, amene wamwalila ndi Peter mathanyula
KUMENYA KUGWETSAAAAAAA MUNYERAAAAA MUNYAAAA MA CADET AMAGAZIIII
Akufa nd m"bale wakoyo
Chafwa ichoo iwe😂😂😂
RIP chakwera 😂😂😂😂😂😂😂😂
Bola next life asakakhaleso president 😭
Koma ngati wafad kumwamba kidyele nyama
Iiiiiii
😂@@handsomenkonde2552
⚰️⚰️💉⚱️⚱️🤲🤲
Makolo apita chkangawa woyeeeeeeee kkkkkkkkkkk
😂😂😂 chikangawa
AKAPUME CHAKWELA WANAMA NTHAWI YAITALI LA 10 LAFIKA 😂😂😂😂😂😂😂RSP
🎉RIP CHIKANGAWA
Chikangawa woyeee
Ayi zicomo zabwino soze😂😂😂😂
Ma Cadet mukhalabe choncho mpaka YESU adzabwela osapeza mtendele, mudazolowela kudya zodzipenta
🙆
Utsi subuka popanda Moto HA lero ndachedwa ku NTCHITO,kodi kumudziko zikuti bwanji?😢
Pita yomweyo abwelele olo bakhili abwelele
Anakomoko bwanji sanamwalile amwalile
😢
Geyezi ndidzoona
Tiyeni tizikondana
Galu anadya nsima yanga,pano amwalira achita bwino amwalira.galuwe mzimu wako usawuse mmtendere.hehede ulu
😢😢😢
Alimoyo chikangawa koma kukumununkhula kusabwera
Akause mu mtendere tikampeza 2099
Akuchedwa kufa nyani hule chigawenga ameneyo mbuzi
Kkkkkkkk
Wailesi yabodza kwambili
Mwagwa nayotu ma cadet apa. Bodza lija balalaa. Manyazi bwaa?
Km akachedza ndichilima bwino bwino?? 😂😂😂😂
Ngati ndizoonad ambuye tengeni bas
Ngati chilima anafa iye kulibwanji? Tikasake ku chikangawa naye
Achile asathawe zisankho
Ine sindingalile aaaaa
Chimwalire basi chimunthu choipa
Koma Makomenti mbweeeeee kukunena kut oipa,, enaaaa pamaliro po mukamva anali wabwino ayi abwino sakhalitsa chabwino.......
Km ineso zothela data dzina aaaa za ziiii afe ndilibe naye mission
Ngati wafa chikangawa akause muntendere chifukwa watinzuza a Malawi
Aganyu ama 2000 ndiomwe angadandaule
Ngati wamwalila akaphume sitimufuna galuameneyo
Kkkkkk km ndye yaaa mwayankhulatu man ohool olila akhale a MCP okha
Okumba dzenje agweramo Linda madzi kuti adutse umazisempha iwe mtanyura
Oh zonse nthawi kaya ali moyo kaya wafa akudziwa ndi mulungu
Apite watikwana
Koma tisayembekeze kuti atalowa wina kuti zinthu zingayende even atalamula abambo anu sangasinthe dziko ngati ulesi wake ukhale omapemphetsawu ayi
Choyipa chitsata mwini
, Mabodza awa pano ai.
Apitebwino
Amwarire nde bwino amene adati phera chirima
Igwe Basi mbendela
Tiyamike mulungu
Alipo ndipo akharapobe mpaka wina achita manyazi 2025.
Mbole yache afe basi
Koma zilibwino kwambiri iiii ambuye ayakha pephero lamawi
Wasala Gesebelo ndi azilongo ache Chimwendo Banda ndi Kamajekete
Kumenya kugwesadi😅
Bambo asikono mwai wanu ndiumeneo
Ndiye tsopano poti zinali zabodza ndiye iwe amene ukuwerenga ma comment we summarisation yako nd8yotani
Ndipo ngati sakumwalila m,sanga chilima ndi athu ena anawapha kuchikangawa aja asamusiye amukoke sangamulephele kumuko amwalile changu asatinyase ife
Zoonazake are basi