Ndipo chilembwe kodi amavala makala a mcp? Siku ili ndi la John chirembwe ndipo ndi siku la a Malawi ose sisiku la chipani cha mcp nose mavala mcp mwe azerereza ukongwa simukusiyanisa musonkhano wa chipani ndi musonkhano wa amalawi
Koma ine Chimwendo amandinyasa kwambili Malawi akutenga ngati banja lake akututumuka kwambili azitengera ngat za MCP eish kwinaku nditukwana koma nkhani ndiyoti MCP september pack and go ndinu zitsilu kwambili
Kodi azimayi atatuwa sakuchita manyazi pamene akukuwa kuchikamwa kwaoko pamene sinsonkhano wadare azimai opusa kwambiri mmmmhu my question is inuyo a leg leg muli ndi ma digress angati chifukwa mukuoneka kuti yanu ndi ya from 4tu
😪😪😪😪😪 When I see this man ine mtima wanga umawawa kwambili eish who told you kut ndege yadzadza? chitsilu kwambili ichi ndipo akutenga ngat Malawi ndi yake..... Chakwera kukamwa ngati somba ya chambo
Achimwendo simunabwere pa msonkhano wa ndale
Chimwendo Banda Mbuzi, uwu si mnsonkhano wandale u chitsiru umenewu
Kulowesa ndale galu iwe Your days are numbered.....✍️
Chimwendo woyeee😂😂😂😂
Nyengo zinasithadi anthu amangomangidwa osalakwa
Uyuyo ndiamenedi akumuononga chikangawa
Kodi Chimwendo uku sikopangira kampenitu nachimimba iwe
Mwautenga ngat msonkhano wa ndale achimwendo
Speech iyi ikugwilizana bwanji ndi mwambou kkkk koma abale
Chimwendo usapange zandsle kumeneko panga za chilembwe basi basi wanva Muthu uyipa iwe
For the first time ndagwirizana ndi chimwendo
Chibwendo ndi amene akulamulila chakwela
A chimwendo ndikuyamikireni mkuyankhula ngati nduna koma msinthe chabe kuntchula pafupipafupi president, mwayankhula Banda pitilizani
Chimwendo mutuwo wangokula ulibe nzeru kumalo amapephelo ukupitisako ndale chitsilu
Iwe nde ukhodzekele Kumangidwa BOMA likudzali bwanji mwalowetsa Ndale Aaaaaaaa zachisoni
Chimwendo galu kobazi ukulalika kuchipani kapena kuchilembe mukuchoka popano boma ndipo muzamangidwa noze😂😂😂😂😂
This party must end
Tathokoza kuti moyo wa malemu koma akulephera kuyamika zamoyo wake.
Nanga chilima munamuphelanji
Ngati mukuona bwino ampingowo sizikuwasangalasa
Inu zandale muziwona ndimalo ake
Mulandeni mike ameneyo sikumusonkhano wandale kumeneko ndikumarilo chonde asatinyase chonde mulandeni atumbukafe mumatikonda ? Mesa mumatisankha
Uyuso ndiye wandinyasa ndi kachisilu kachikangawa nkhope ngati galu
Kodi ndimayesa kuti mutiudza mbiri ya chilebwe abale mm koma ndale
Nanga chilima munapha bwanji mwayamba ndale apapa
Hahaha azimayi atatu analipidwa mwina kkkkkk
Mcp Muziona 2025
Ali pandale uyu
Mbava iyi imandinyansa bwanji
Komatu ma handshake renewable bwino nawo umakangofikira kukomoka kunyumba khayaaa😂
Kod ndisokhano wandale zovesa chison kwambili 😢😢
iwe ngalu chakwera ngalu nyani
Mwayamba ndale akulu tikudikila chaka chamawa ndenge sidzadza ndi anthu eight
Kodi black box yilikuti iwe chimwendo
Kod chimwendoyi amakhala pasogolo why
Ukuyankhula zandale kapena zokumbukira John chilembwe nawe kusowa zochita uzakomoka mcp ikazaluza
Kod amenei chisilu et
Kodi za ndale kapena chilembwe day iwe chimeendo ndiye katundu ochipayo ali kuti koma mutu wako umatogwira
Achimwendo yomweyo 2025 mcp ndi boma kale
Kodi ndi mwambo oyamikira Chakwera kapena okumbukira John Chilembwe?? No sense Chimwendo Bandaa.
Wakuuza ndani kt 5 years ikubwerayi mudzapitanso
Akweni kusekelera kuyiwala kuti anagona muchitokosi chifukwa cha anthu omwewa
Apakire bas tatopa alowe ena tione dzina
Ndipo chilembwe kodi amavala makala a mcp? Siku ili ndi la John chirembwe ndipo ndi siku la a Malawi ose sisiku la chipani cha mcp nose mavala mcp mwe azerereza ukongwa simukusiyanisa musonkhano wa chipani ndi musonkhano wa amalawi
Lero ukapolo uja akutipanga ndi mmalawi mzathu: Chakwera watitopesa pokweza maphunziro kuti osauka asaphunzire, kubweresa njala, devaluation nthawi ndi nthawi
Chimimba ndi uputsa kwambiri chilichonse ndale bas ngati ukunva kukoma iweyo dziko la nyasalande usaone ngati tonsefe mbuzi iwe
Koma ulaliki uja anaumva bwino? Sakwanisa kuwasokoneza anthu
Sanayanjane munthu suyanja ndi wamisala ndiye kut iweso ngwamisala
Ndale ndale amalawi kunyada ndi misonkho yathu..shame...
Msokhano wa chipani eti??
😁😁😁😁😁
Chimwendo nachimimba iwe usatenge mwambowo ngat wa ndale usamutame mnzakoyo Kuti adzakhalanso akubwera kumeneko Zaka Zina 5 ndiwe ozitukumula, ndiwe kape kwambiri ndipo umandibowa
Chimwendo mulungu adzakulanga mochititsa chison kwambiri
Koma ine Chimwendo amandinyasa kwambili Malawi akutenga ngati banja lake akututumuka kwambili azitengera ngat za MCP eish kwinaku nditukwana koma nkhani ndiyoti MCP september pack and go ndinu zitsilu kwambili
Mutu waking sumagwila iwe Chakwela ndi chipani chako Abusawo alalika zaiwe galu
It's not sonkhano wandale
Kodi azimayi atatuwa sakuchita manyazi pamene akukuwa kuchikamwa kwaoko pamene sinsonkhano wadare azimai opusa kwambiri mmmmhu my question is inuyo a leg leg muli ndi ma digress angati chifukwa mukuoneka kuti yanu ndi ya from 4tu
koma kuyankhula kosameza malovuku amathawa chani
Chimunthu chopanda zeru ichi bwanji timadya Tala ife timadya nsima mafuta akukanikan agalu inu zipangizo zaulim kudula tigulitse chimanga kut tigule fertilization ife tilibe chimanga munapha chilima inu agalu inu
Matama ndi bodza Chimwendo
Iwe ndi mbuzi 5yrs yake ITI yomwe mupitilizeyo nthawi yakutherani vomerezani
Mamuna onyenga mbalume🥱
Kodi nditsokhano wa ndale
Tazioneleni nkhope zikuchita kuoneka kuti ziafiti
Mukukhala makola pa moza mukutukilanachi pala muli kwayekha kwayekha?
Chimwendo kuputsa sikuzakuthela pamenepo ndiye ukuti chani
Mmm koma awa maboza abale
Iwe chimwendo usaipise mpingo wa pim ukuona ngt uli ku ndale ND chakwela wakoyo agalu Inu
Koma zandale ndi Mapemphero tidzisiyanitsa
Iwe chimwendo unangokula chimutu zeru mwaiwe mulibe
Machende ako
Chakwera and waboza kwambere
Zimenezi mumafuna azikutamani ndani?Kodi mumaziwa kuti winawake anafa kuti ife tinkhale pa ufulu?shame on your chimwendo
Chimwendo mutu wake sumagwila ndithu
Mmmm koma chimwendo umasokosa zinthu zopanda ntchito bwanji olo zako ukumutamanrirayo ukamuyang'ana akuvadi zakozo munthu kumagoyankhula gati wadzidzimutsidwa kutulo?aaaaa zachibwana
😪😪😪😪😪 When I see this man ine mtima wanga umawawa kwambili eish who told you kut ndege yadzadza? chitsilu kwambili ichi ndipo akutenga ngat Malawi ndi yake.....
Chakwera kukamwa ngati somba ya chambo
Inenso mtima umandiwawa kwambiri hmm😢
Chimwendo umphawi sumatha umangochepa zonse ukunenapa nzabodza njanje Ili kuti ? Fodya mwapinyulisa kale
Koma anakuuza ndani kuti ndege yazaza iweyo chimwendo tanena
Kodi iwe chimwendo ulipamwabombo wachilembwe kapena ulipolalikira va chikangawa wakoyo ndiwe wopusa kwambiri galu iwe )
Mbuzi yamunthu iyi nizolankhula izi galu wachabechabe