MDYANGU | 3 JANUARY 2025

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 20 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 64

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363
    @dhaoudhiabedinegomaseko2363 12 днів тому +1

    Kkkkkk uyo wamfupiyu tamulumikizitseni ndi Pawpaw sure coz wabweratu

  • @HamidaDaud-p6z
    @HamidaDaud-p6z 16 днів тому +4

    English nd chizungu zizisiyana😂kmatu mkazi wa shoko shoko waza nd fire🔥gani madhala azakuswatu awa😂😂😂

  • @BashilDaud
    @BashilDaud 16 днів тому +2

    Queen mwana wakulazatu ndaonera kuwala diso❤
    Welcome mdyangu actors and actresses to another annum(2025) lv u all❤

  • @EsteryHassan
    @EsteryHassan 16 днів тому +1

    Kkkkkkk kma mercy suzatheka mpaka kuishosha ya shokoshoko kuti qeen amumenye treesha 😂😂😂😂😂ayi ndithu

  • @hamiltonlemilton7322
    @hamiltonlemilton7322 10 днів тому

    One nyekhu one taya

  • @DeborahMkwezalamba
    @DeborahMkwezalamba 16 днів тому

    Queen yakumapetoyo yandiwaza🤣🤣🤣🤣🤣

  • @EnerstMwachande-yt5sj
    @EnerstMwachande-yt5sj 16 днів тому +1

    A queen ndinu Hule kumene

  • @ethelkamwendo702
    @ethelkamwendo702 16 днів тому

    Koma mlelemba tsitsilo eeeee ayi zikomo 😂😂😂😂😂😂

  • @BridgetGunde-w9c
    @BridgetGunde-w9c 15 днів тому

    Prosper ndi munyanyiwa apezana eish😂

  • @StanleyKalavina
    @StanleyKalavina 16 днів тому

    Kkkkkkkkk Queen anakonza... Ingovomerezani kut ndinu galimoto yongothira mafuta garage iliyonse kkkkkkkk

  • @RosetNkhoma
    @RosetNkhoma 16 днів тому

    Km Queen iweo ndi 1 kumapetoko ndabwelez pak ka 4 😂😂😂😂😂

  • @luciapita
    @luciapita 16 днів тому

    Ndimakukondani nonse fans ya mdyangu ❤

  • @AntonyWaFasten
    @AntonyWaFasten 12 днів тому

    Koma kwini mmmm zalelo bas

  • @BernardoDonocianoHonório-h3r
    @BernardoDonocianoHonório-h3r 16 днів тому

    Muli nkhati galimoto yotha mafuta sisankha filngstation, kkkk

  • @fwanya
    @fwanya 17 днів тому

    Mwana wa mkango suseka bwino😂😂

  • @LytonChirwa-i8s
    @LytonChirwa-i8s 16 днів тому

    Kandege Kanji komangobwera month end yokha yokha kkkkk lero kagwidwa

  • @IsaacChisambi
    @IsaacChisambi 16 днів тому

    Ndimakunyadirani nosenu❤❤❤❤❤🎉

  • @ChiccoKadza-u4m
    @ChiccoKadza-u4m 17 днів тому

    Ifeso tiri ndi athu achina popo😂😂😂

  • @SafirahwaBanda
    @SafirahwaBanda 16 днів тому

    😅😅😅😅😅kom ashokoshok ai zikom 😊

  • @rashiddeula5715
    @rashiddeula5715 17 днів тому +2

    Prosper kulimba mtima kwabwanji kufuna kugwetsa njovu? Hahahaha. Koma Ali bho kusiyana ndi Junior. His acting is much better than Junior. Sopano mtumiki wa Mulungu tsitsili akufuna kupota dread?

  • @MaritaChapola
    @MaritaChapola 16 днів тому

    Ineyo ka fula uyo amandinyasa bwanji aaaa

  • @Harrychokanda
    @Harrychokanda 12 днів тому

    Munyanyiwa 😂😂😂

  • @storytambala6088
    @storytambala6088 16 днів тому

    M'dyangu comedy, nkhani zake zambiri zongokambirana zichigololo basi.

  • @Selina-n1o
    @Selina-n1o 14 днів тому

    Koma mercy ulindimtopola

  • @NancyNyirenda-v9o
    @NancyNyirenda-v9o 17 днів тому

    😂😂😂😂😂 koma anthu inuyo 🎉

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 17 днів тому

    Kodi chuma alikut ❤❤❤❤❤❤

  • @AbrahamsMlelemba
    @AbrahamsMlelemba 16 днів тому

    Popanda chiphwanya ndi sasoka sizikukoma izi aaaa mwasala aximai okha okha

  • @InnocentShumba-c3h
    @InnocentShumba-c3h 16 днів тому

    Inu chiphwanya ndi satsoka ati ziiiitu

  • @AubreyMukhwapa-k1t
    @AubreyMukhwapa-k1t 16 днів тому

    Zoona Gani kumupanga chipongwe m'dala mdyangu

  • @MariamTwanky
    @MariamTwanky 16 днів тому

    Nepman alikt wasowato❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

    • @RajabMwhite
      @RajabMwhite 16 днів тому

      Wachita bwino kusowa amanditopesa kwambili😹

  • @IssahHussain-pe4ue
    @IssahHussain-pe4ue 16 днів тому +1

    Abatwa wayak

  • @PeterBendeka
    @PeterBendeka 17 днів тому

    Queen umakwana linens chilungamo

  • @mayathemba
    @mayathemba 15 днів тому

    Kodi popoyu bwanji nanga

  • @jackbello2170
    @jackbello2170 16 днів тому

    Kandege kagwidwatu uku kkkkkk

  • @MalumboMndala
    @MalumboMndala 16 днів тому

    Kodi short wina uja sakuoneka bwa?

  • @SharonJalamu-d7l
    @SharonJalamu-d7l 16 днів тому

    I miss nepman plz where is he

  • @LuckyMkwanda-m8i
    @LuckyMkwanda-m8i 17 днів тому +1

    Km mercy nawe mmmmmm mtopola km nde wakupanikizatu

  • @dalitsoghocho3048
    @dalitsoghocho3048 16 днів тому

    Sasoka ndi chiphwanya vumbulukani azikazi anu azingwa kuno

  • @SamuelChaoloka
    @SamuelChaoloka 16 днів тому

    Chiphwanya ndi mnzake Sasoka awonekereko abale?😢😢😢😢

    • @kesterkaunda
      @kesterkaunda 16 днів тому

      Hope anasiya coz Ku mfumukadzi kujaso anaika anyamata ena

  • @PatriciaBanda-e3v
    @PatriciaBanda-e3v 17 днів тому

    😂😂😂😅😂😂Shokoshoko

  • @PatricioAntonioDaniel
    @PatricioAntonioDaniel 16 днів тому

    Oi kkkkkkkkkkkkk😂😂😂😂😂

  • @PrinceGodfrey-kw2yu
    @PrinceGodfrey-kw2yu 16 днів тому

    Drama iyi ndiye ndi 3D lalowaso ku MFUMUKAZi

  • @MikeZiotche
    @MikeZiotche 16 днів тому

    Nice one

  • @HassanJulius-xt8ih
    @HassanJulius-xt8ih 16 днів тому

    Kodi sasoka ndi chimpwanya analakwisa chani

  • @OscarSolomoni
    @OscarSolomoni 16 днів тому

    Mulelemba ali kt

  • @ConnexSwerveOfficial
    @ConnexSwerveOfficial 17 днів тому

    Koma kunoko 😂

  • @NkhomaFungo
    @NkhomaFungo 16 днів тому

    Yea neh

  • @AllieMajidu
    @AllieMajidu 16 днів тому

  • @PeatryNdanga
    @PeatryNdanga 17 днів тому

    Koma ndazionayo mwamuona kumbuyoko?

  • @PeterBendeka
    @PeterBendeka 17 днів тому

    Guys iyi yokha sinapindule nayo

  • @FrancisShumba
    @FrancisShumba 17 днів тому

    Koma munyanyiwa English ndi chizungu ndizosiyana?

  • @MercyHalison-m2i
    @MercyHalison-m2i 17 днів тому

    Jkkkk kma gyz

  • @CorneliousMwalure
    @CorneliousMwalure 16 днів тому

    Chi shirt cha shokoooooooo

  • @JoelKacheche-e5r
    @JoelKacheche-e5r 16 днів тому

    Woza 2025 moto kut buuuu

  • @mussasamuel774
    @mussasamuel774 17 днів тому

    Half man anadalitsika😂

  • @EricRutuku
    @EricRutuku 17 днів тому

    Never stop

    • @brifamichael5117
      @brifamichael5117 17 днів тому

      Ngati galimoto yotha mafuta, akuti sisankha filling station Kkkkkk musatikomolepoapaaaa

  • @davidjoemalungah6338
    @davidjoemalungah6338 17 днів тому +3

    CDM YOUR RELIABLE CAR DEALER

  • @PrinceGodfrey-kw2yu
    @PrinceGodfrey-kw2yu 16 днів тому

    Drama iyi ndiye ndi 3D lalowaso ku MFUMUKAZi