KODI MWAMVA? PAMENE ANTHU ANALI BUSY MTOWN KUPANGA ZA MA DEMO... KWINAKU CHAKWERA WATOKOTA IZI....
Вставка
- Опубліковано 28 лис 2024
- KODI MWAMVA? PAMENE ANTHU ANALI BUSY MTOWN KUPANGA ZA MA DEMO... KWINAKU CHAKWERA WATOKOTA IZI....
Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
#MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika
Chaona Mzako Chapita mawa chilipawe your friends failures are Bright than Yours A President amalalikira Mtendere nanga Bwanji mdziko muno anthu akupangana maupandu osiyanasiyana mpakana zikwanje koma President sanadzudzureko So what kind of peace you Preach Mr. President
Ngalu ameneyi chikangawa
😊😊😊😊😊😊😊
Olalikila mtendereyo ndani??? Zaziiiii
❤ my words
Do we have President in Malawi? Or is it Nyawu government . Under the leadership of Makanja
Muchira Abwana, ndiye ngati we don't have a president mufunilanji kuthandizidwa?
Lazy aphweteka guru
muzazindikira bwino patsogolo
This is not Mulhakho wa a Lohmwe DPP government,this is the only party in Malawi that represents the whole nation not these Mickey mouse family,tribal parties like AFORD,UDF and DPP.
Chilima ndi xipan 9 zinatiyika mavuto 😮😮 malawi agwire mtengo wanji
Maka Chilima 😭😭😭
Akuti amalalikila mtendele .zisenga Zija kukhapa anthu NDI mtendele Kodi?
Your speech is very positive to.all Malawians but on your ground opposite direction
Tilibe president ku Malawi
Ndisamangoononga madata ine zikumaniipiladi panya pamako unapha chilima iwe chitsiru
Ngati president zoona azisegulira powerbank? Kkkk malawi uphawi weniweni eeee koma !!😂😂😂😂
Kkkk kkkk
Kkkkkk ndipo uchitsiru wake
Chigalu iwe mtendere ndi wumenewu woyenda ndi zikwanje fumu yawa yuda iwe fiti
We were deceived by the devil no wonder Satan is smiling and laughing at us,may God see us through,soon or later light Wil shine on this nation again and this darkness will go forever
What came first, President going to open escom energy power or seeking contacting demonstrations? Let's forget that we fight for our country to be out from personal interests of our leaders mostly presidents because we have not achieved our goals fought for in 2020 since we are in uncountable problems across the country.
Iweyo wakanika kuyendetsa malawi sizoona mpaka anthu aziyenda ndi zikwanje president uli mudziko momo ndi chifukwa chani sukuyankhurapo ngati umafuna umodzi mu dziko muno sibwino kumakhala chete pamene anthu ambiri akudandauza mudziko lino ubwino wanu amakudziwani ndi anthu amene adakuzungulirani enafe sitinganene koma choti mudziwe ndi chakuti muli pa bwino chifukwa cha anthu amene akuvutikawa mulungu akuyendereni mwapadera ndi nduna zanu zonse
😯🤨🙆🙆😭😭😭 Lord have mercy on Malawi. Save the people of Malawi.
Sinavepo nfundo mwina ndiine ndekha
Alibe fundo uyu yoti munthu nkutolapo
Ninathamini sana juhudi zako! Nina swali la haraka: Nina mkoba wa SafePal na USDT, na nina seed phrase. (alarm fetch churn bridge exercise tape speak race clerk couch crater letter). Ninawezaje kuzihamisha kwenda Binance?
Koma ngati chilima unali yankho kwa malawi mulungu ukuyang,anire chifukwa unayika athu mu ukapolo ndithu kudya katatu kulikuti
Mfana oganiza bhoo ujatu paja adanena kuti wapa keliyala sayimba belu muganiza kuti amkatanthauza chani inuyo???
kodi........ka chakwera ndi anzawo ndi chitsiru zaku malawi...kumangu pempha ndalama kunja.kodi chakwera wo chita chiyani ndi ndalama zobadwira ku malawi...wo kuba ameneyu....
Inu mtenderewo mukuuziwa lero achakwera,ngat mudasindika kukhetsa mwazi ,umenewo ndi mtendere
Ulape chakwela chonde lapa ambuye akuyendele please apa palibe chomwe mwanenapo phiri tatsegulilani majulatawo bsi zatha zinazo zitayeni muonongapo zambili
Ayambe amako kulapa usanalapitse bambo azako
@@josephphiri7161kumeneko nde kulankhura kopunsa
Kunja ndkumeneku kwa Mvura Mvura kma fertilizer kuli ziiii😂
Pita kushop alipo ndiwe mnyamata uzigwila maganyu kulibe zamanja lende
Akulu timacende tanu mwamva
@@JaiLamu-dk8wdiwe ndi chitsilu kwambiri
Preaching peace but behind scenes Devil where is SKC?
Indeed 😢
Also we pray to the same God your praying but God knows the best for us
Chabodza ichi chimalalikira zikwanje.Bwanji sichokupanga condemn zikwanje za nyau zake zikupilikitsa anthu amademo
Inuyo muganize kachwiri anzanu abwerepo ziko lakukanikani sometimes kuvomereza kugonja nkwabwino .
Mavuto alipo ndithu koma inuyo chaka chamawa musalamulirenso ndithu kwakwana ndithu 😩😩😩😩
Chitsiru ukuwalemekeza malamulowo iweyo? Pansana pako angakhulupilile iwe ndani?
Oyipa iwe Kadett
Mpaka kukatsegurira ma mbatire Ayi dzikomo misokho ya Malawi yaphwwka
Wakuliramo kutsekulira ma battery😂😂😂😂😂
It is lavish President.
Iwe chakwera unawonongq zinthu zingati iwe 2019 2020?!!!
Muno mulibe president ayi president opanda nzeru Ngati uyu sindinamuonpo ayi
He is a wise president
Much love
Kupusa kumeneko
The most stupid guy on earth
Kutchinga kokhako nde kulimbana ndi anzanuko,, ubusa winawu very questionable!!
You sacrifice our vs president Dr chilima s life chifukwa Cha udindo uku zikwanje mtawunimu mtendele wake wakuti
Kodi iwowa akuti amalalikira mtendele kodi mu 2019 kodi ma demo amapanga aja amalalikira chani😂😂😂😂
Chakwera my vote
Kwanga ndikuwapepha abwanawa kuti dziko la Malawi ndilantendele koma zitengela iwo kut awauza bwanji anthu amene akuwalamulila zantendele muziko muno
Zikwanje zili ku Lilongwe iweyo chakwela siwukuziziwa?nanga chilima uja ku chikangawa ndi ntendele pantumbo pako chakwela
Nzaziiii kulikonse mupiteko kusowa zochita
Mhule akuchemelera basi ,kuonengetsa Dxiko basi .malamulo ukuswa ndiweoooo!!!!!!
Kodi akuti nchani,kumalawi tilibe president munadzitembelera nokha popha chilima. Ndi anzake
Achakwera ndinu oyipa kwambiri ukuyakhula apazi thawi ya dpp umazisusa iweyo ase amalawi unawalakwira kwambiri uchose smatimatic
Koma abale akamayankhula ngati wabwino ngati sakuziwapo kanthu za zikwanje mulilongwe. Akanakhala a opposition bwez mutawagwira kale. Komabe pangatalike tsku lina malawi adzayankhula
Very nervous lady, take your breath
Kd walezela chakwelai sizikuveka kmso azimai ndi zisilu kwambiri
Poor government
Mavuto alipo,and chilima uja ndmamudandaula Kwambili popanga ubale ndi chilombo ichi
Yinagwa bwanj ndege k chikangawa??? Blackbox yolikut??? Komanso wapereka mimba ku aria something
Tiuzeni kaye kuti maluziwa tithana nawo bwanji? Musanapitenso kwina BWANA.🙏🙏🙏
Zofuna zachilima mtambo chihana zosatilazake izi chilima anachitabwino kufa
President amatluka kukatswgulira nsewu, battery lamagetsi, izizi sizofunika even nduna, mayiko a anzathu President kapema samatuluka kukapanga msonkhano pa zinthu zazing'ono ngati izi.
Ah za zii kkkk chitukuko Mr chikangawa 😂😂😂
Kodi Achakwera nyau zanuzi ndi azikwanjewa akuounetsa chikondi kwa anzao?Osamatinyasa ndi mabodza anuwo tinatopa nawo
Ngat mukunena kut muchosa MCP mu BOMA mophweka ndiye mukuzinamiza guys
Mwatailila palibe chomwe tinganene kuti tili ndimsogoleri malamulo kulibe bwana apolice nfi a mcp basi feterizer wa 4500 alikuti
President wina aliyense ku Malawi akakhala pa mpando ndi woyipa wabwino mumupeza kuti mulindiumboni wanji kuti Chakwela anapha Chilima tikutengeleni kachipindakomata mutiuzainu
Kodi bwanawa bwanji pamisonkhano yawo sanenako zakukwera kwa fertilizer kapena zinthu zina"akuona ngat zawo zilipabwino??
Tiyeni Malawi tilimbikire kulipempherera dziko lathu chifukwa achakwera sanabwere kuzatumikira dziko ayi koma kuzatizunza ife tinamuyika pampando fe,komaso abusawa umunthu alibe ali ntima wa fisi
Zoona tikamaononga kuganiza kuti ndiwachakwela tilimmadzi gyz
Akulu akulu a mcp ndi amene adagula zikwanje kwagulila anyamata akwansundwe,ayiwala kuti a mcp wo ankachitanso ma dem.lelo akuletsa madem komatu Malawi ndi dziko laling'ono kwambiri ndiye komabe zidzatheka tigawane akumpoto ali ndi president wao ,achigawo Cha pakati alinso ndi mtsogoleli wao kumweranso chimodzimodzi .Zimenezo ayambitsa ndi atsogoleli a mcp
Koma guyz mukupeleka ndemanga zabwino,komas KT amenayi achoke tiyeni tikalembese mkaundula wavote kut tizachose nyauyi .
Uyuyu akanachoka before mavote. Useless, akuononga dziko.
Mukachose nyasi kuzabweresa nyasiles
Tinayesela kupanga Za AZUNGU zonyambitanazi lero sabata Ziwiri ndikutsekula mimba" Shakila iwe
We have no leader my poor malawi.
Mulungu azikudalitseni mau omanga umodzi kuti Malawi apite patsogolo
Ine mayanga atamuombela M’manja uyuyu tingakhale tadana 😂 Koma stress nde yamuswa eeeh
Koma Chakwera ali pa Chibwana cha n'chombo lende
Dziko lipita patsogolo bwanj has no fuel, no passport, forex?? Tonsefe simburi
Ngakhale anthuso amene Ali apowa sasakukufuna Koma akupilira mmtimamo Kuti poti ndi ntchito nakoso akukuopaso Kuti uwapha akakuyandikira komaso adziwa Kuti ulibe nzeru wakupha
Mutiyakhule zatsogolo osati zanuzo ,,,,ife tikuvutika,,,,, rest in peace p chilima
Olo manyazi mulibe, tsono munthu Ngati alibe chisoni manyazi ndiye simunthunso ameneyo
Zantiiiiii....
Where is the black box?
Akanakhala bambo anga nkanauza kuti adadi tulani pasi udindo chifkwa anthu sakukufnani, 80% ya anthu sitikuwafna achakwela
Kodi nawoso kuziwa kuti kuli mademo nawoso ndikumakhala akuchita zawona dera lomwero cholinga ndi chani? 2 kodi chifukwa chiyani chili c hose amafuna prezideti akasegulile sizingatheke project kuyambika atangolamula kuti apa ndikufuna mutchite ichi athukuyamba kugwila tchito ndalama zingati zimenezo zimawonongeka Kuyend kwa prezideti? Zina muzingotuma mp kapena ngavinala chitoyo ikatheka athu azalozabe inu chonde ndife athu olakwisa ndalama zononga inuyo siku limozi pawulendo mungathandize athu Angati? Amenewo sangavotele wina chifukwa mwawoneka chikondi zikomo
Koma awawa ndimanyaka zoona anthu akuyenda nzukwanje osalankulapo nkumati ndimalalikila mtendele ?komaso akuiwala kuti Iwo ndiamene amatsogolera mademo aja kuti akhalepamenepa.musaiwale kuti nkwidzi mwayamba ndinu kuononga Malawi paliponse ,koma uyudi ngalu sure
Munyela apo mungosamuk ku malawi kuno iyaa km tizikalimbanas ndiwalitata uja kt zimveke bwanji aaa dpp yopanda chitukuko km kulemeletsa chisale 😢
Koma anthu ena kumvetsa chisoni kumasekela zimenezo ndithu mmakomo mulibe chokudya kugundika mzopepelazi 😮😮😮😮otembeleledwa uyu
Malomote zamafuto mukunenazina zauzilubazi 2025 mukupita makape noze mcp
Iweyo umakonda azako chakwela 😮😮😮😮
Chitsiru wa chabe
Malawi wanga ukupita kuti ambuye yang'anirani Malawi akuvutika
Mulungu akuona,ndipo akumenya yekha nkhondo Ife tili chete,Moti sangalore aMalawi tizunzike mopitilira muyeso kupitilira 2025. Olo mukanize mademo, Mulungu akutimenyera nkhondo Moti athana Nanu pangachedwe mwakuti chilichonco mudziyetsetsa kupanga sichidzitheka mpaka mugonja nokha.Ambuye sachokera kumudzi kwanu mudziwe ichi.
Chakwera pamtumbo Pako mwana wa mfiti iwe anthu onse akukuombera manjawo ukuona ngati Ali mbali yako chitsilu chamunthu
Mulungu akuoneni achakwera kod ayenda zikwanje anja ndiosusa boma km Mulungu simunthu
Zina zilizose akutbkusegulila misokhano yopusayi ndi yomwe ikupangisa kut malawi azibgovutukilabe alibe nthawi yokhala pasi ndikusokhanisa ndalama ndikupanga zinthu zooneka
Iwe 2019 unawononga zinthu zambili mbiri
Wa mcp aliyese asapedze mpata opanga msonkhano adzithamangitsidwa nkhondo yakwana apa kwatsala ndikuvomereza
Mtendere wake uti? wanyamata azikwanje shame on you Mr president opanda mzeru ngt uyu sindinawonepo pa dziko lonse lapansi mumudziwe Mulungu apresident
Wises president mbutuma ndizomwe zimalimbana naye
Mawu anga Kwa MEC sangandikanize kut ndilembese coz akut ndine wanyuwani nkumalimbana ndi akale eeeeeeee km katangale asazathedi
Ndala woputsa iweyo akuyambananawe ndi ndani wasaukitsa dziko la Malawi iwe
Uwule basi chitukuko chapatipo azimayi inu zinveleni chisoi
Akupuma molefukatu ....mizimu ya anthu nine simasewelatu
Kumwela kwanuko simunalembetse busy ku maminda kwathu kuno kwa chewa ntchito yolima ndiye mukutinyozas aaaa ngati kuli anthu ovutika mkumwelako
mwadziwa lelo ndi achitsilu😊
Mukayankhula dziwani kuti 2025 vote yanga simuyilawa paja 2020 nchifukwa Cha chilima pokuvoterani
Mulandile ulemu a chakwela ndindani anati dzitsilu zisamalandile ulemu😂😂
Akuipisa zinthu ndi azimayi mthungululu zawo zikupwetekesa amalawi😅😅😅
Munthu uyu ndi crook kwabas, Kaya azibusa assemblies of God onse Ali chonchi
Mwat power Bank????
Kazerezq iwe mumutu umo muli ma mphinya yekha!! Kutindeka nakusqnga mafuta mchalo?!! Kachiswaswa akaa!! Kumangogwetsa ndalama yathu basi ulibe ndi mfundo or nzeru zomwee!!!!!
Kkkkkk a zimai ndameneo akuvina mofuna banjawo😂😂😂