Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Nice one Mr,like u a lot
Kkkk abudul wabudula mpunga wa gulu big up bro nice one
Che mandota that's good!😂
I like you my brother 😂😂😂Khemge heavy man keep fire burning my brother
Mandota ur perfect
Abdu wapangitsa kt akita afe😂😂😂😂😂😂 wabwera ndi moto🔥 welcome 👏👏
Kkkkkkkk utambwali watenga Bambo ake ka kkkk Che mandota mmatha
Nice che Mendota zili bho
You're great comedian
Kkkk umandisangaratsa. Mandota.
Nice one mandota
Maitha che Mandota keep it up
Sibwino kumayenda ndi mwana kuchibwezi akakunenerani❤
Abdul utambwali watengela bambo ake😂😂😂
Great drama! Glory to God in Jesus Christ name!
❤❤❤mumakwana guyz big up
Mandota mkuchikweza
Nice mamaili
Fire mesa👌👌👌
Your number 1 Mr Mandota keep it up
Ma children amasiku ano ndi ma B A kkkk😂😂😂😂😂 akudyela bambo ake
More fire 👌👌👌👌👌👌👌kkkķkkk from capetown
❤❤❤
Kkkkkkk koma abud umakwa❤❤❤❤❤❤❤
You think as l think 😂Mind you sitivundika masiku ndiwana😊😊
Kkkkkk amayili lero ndawaona
Perfect koma ndisanasamuke ndiye kae mpungawo kkkk
Kkk Abdul uja wabudula m'meno😂😂
Mandota umatha 😂😂😂
Marvis watching from Durban kķkkķ chemandota love you
Iwe nd Actor 😂😂😂 umata kuchesa abdul waulula chinzinzi
Mwini nyumba kupakira wow big up bro
Wafadi chifukwa cha mwana wake yemwe, been blackmailed by his own child 😂😂😂 big up
apa wayamba kundifikapo aysey 🤣🤣🤣🤣🤣(ndikanena kwa mama) 🤣🤣🤣🤣
Next bro, it's good movie❤
Mama Abdul mumandiwaza musasiye kupanga ma comedy ndi chemandota
Jefule black
Mulaka maillo
So far so good so nice ❤❤❤❤
Big up mandota
Yili Bo keep it up
Mwana aatipweteka uyu...punishment yantundu wanji imeneyi😂
😂😂😂 che mandota inuyo ndi one🔥🔥
🤣🤣🤣🤣Iweyo ndidolo🔥🔥
I love it
Abdul utambwali watengera bambo ake kkk 🤣
Mamaili ndi chemandota ndinu patali, mumaitha kwambiri, banja lamaphokoso😂😅😅
❤❤❤❤big up bro
🤣 🤣 mwana akufunika mbama
Is very very good comedy
Salute brother
Dad nd mwana 😂 mandota wakumana nazo 😃
Ndine Anastasia waku SA.... timango seka ndi a Wariya 😂😂
Mumakwana Che Mandota ❤
Abdull wabwera ndi moto😂😂😂
😂😂😂😂 actor wafa chifukwa cha mwana
Kkkkk che mandota kankhani alikuti ndakwiyatu mwandinyasatu
Mumatimvetsa kukoma Che Mandota
Abudul amakwana 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Koma abdu ndikatundu 😊😅 chilichonse ndikanena kwa mayi koma alemera
Zilibwino chemandota🙌🙌
Umatha
Kkkkk actor wagwa nayo, phunzilo labwino Kwa amunafe okonda kuzuza mkazi ndi ana athu
You are so good
Amaili ndiye sakukulatu😅😅
Hahahahahahahaha koma ndaseka kwabasi eeeeee mandota ndi dolo
Keep fire burning
Wadyera bambo no worries 😂😂😂😂
This is nice
Love it
Amen Ali aaaa tengani spoon tidye mpunga unachenjera iwe
Abdul wabwera ndi moto🤣🤣🤣🤣🤣. Kodi Morogeni alikuti?
Abudu mwana washabe sedi sasiwa kutseka pakamwa🤣🤣🤣🤣🤣
Bro it's nice
😂😂😂Utambwali watenga adad ake
Koma iyi yandipeza ulendo uno wapezana ndimwana odziwa zithu 🤣🤣😹🤣
Kkkkk utabwali watengera inuyo kaya
Nice video
Kodi ndi abudu inetu ndimaona ngati amayili kkkkkkk keep it up
Abdul ndi mbambande 🤣🤣🤣🤣 ngat akita wafa chfukwa cha abdul
Moto unandi 🔥🔥🔥
Zilibwino pitilizani amandota ndi mayi amaili😂😂
Mwana uyu siwanu 😅😅😅kulephela kumuuza kut iwe mamuna ineso mamuna koma koma osasiyabe 😂😂😂changamu pa town
Respect brother mandota
Abud wawulura game 😂😂😂😂
Bola abdu tamuwona km sikono paka pan citinamuwonepo
😂😂😂😂😂😂😂umakwana mandota ilovuzi yuu
Ntchimo limazuza🤣🤣🤣
😂😂😂😂❤️❤️❤️❤️ Mwana ziopanga naye chizizi mundu wamkulu
Pano kuli Abdul, kaya mayili alikuti🤣🤣🤣
Ndipo apa pokha ndaphunzira palibe kulongeza kuti ndikupita kwathu, ma maili muli bho osamuka ndi olakwayo
Kkkk😂 number one
Abuduyo ndimaona ngt ndi mailitu😅😅😅
Mumakwana Mr Ndoxy (mandota)
😂😂😂😂😂😂😂😂 chenandota bribe yamupweteketsa
Mphuzitso labwino kwambiri😅
Ase umayionesa
Mandota Malowo ndi mawafuna ndiye ndigapange bwanji ndili kuno ku south Africa durben
Imbani ma number tapelekao
Kkkkkk abudu wavuta
Kumwa madzi ndi kugona 😂😂😂😂
Kkkkk Koma yaah a Chee mumandisagalasa kkk chiseka pakamwa kumwana kkk
Che Mandota mumatha inuyo. Kkkkkk
Che mandota on fire 😢😢😢😢
Nice one Mr,like u a lot
Kkkk abudul wabudula mpunga wa gulu big up bro nice one
Che mandota that's good!😂
I like you my brother 😂😂😂Khemge heavy man keep fire burning my brother
Mandota ur perfect
Abdu wapangitsa kt akita afe😂😂😂😂😂😂 wabwera ndi moto🔥 welcome 👏👏
Kkkkkkkk utambwali watenga Bambo ake ka kkkk Che mandota mmatha
Nice che Mendota zili bho
You're great comedian
Kkkk umandisangaratsa. Mandota.
Nice one mandota
Maitha che Mandota keep it up
Sibwino kumayenda ndi mwana kuchibwezi akakunenerani❤
Abdul utambwali watengela bambo ake😂😂😂
Great drama! Glory to God in Jesus Christ name!
❤❤❤mumakwana guyz big up
Mandota mkuchikweza
Nice mamaili
Fire mesa👌👌👌
Your number 1 Mr Mandota keep it up
Ma children amasiku ano ndi ma B A kkkk😂😂😂😂😂 akudyela bambo ake
More fire 👌👌👌👌👌👌👌kkkķkkk from capetown
❤❤❤
Kkkkkkk koma abud umakwa❤❤❤❤❤❤❤
You think as l think 😂
Mind you sitivundika masiku ndiwana😊😊
Kkkkkk amayili lero ndawaona
Perfect koma ndisanasamuke ndiye kae mpungawo kkkk
Kkk Abdul uja wabudula m'meno😂😂
Mandota umatha 😂😂😂
Marvis watching from Durban kķkkķ chemandota love you
Iwe nd Actor 😂😂😂 umata kuchesa abdul waulula chinzinzi
Mwini nyumba kupakira wow big up bro
Wafadi chifukwa cha mwana wake yemwe, been blackmailed by his own child 😂😂😂 big up
apa wayamba kundifikapo aysey 🤣🤣🤣🤣🤣
(ndikanena kwa mama) 🤣🤣🤣🤣