It’s very sad to learn about the passing of Mr chibiliti, you played a very big role in this episode, my condolences to the entire clue of Tonde Wadula and his family……may his soul Rest In Peace
Rest in peace mr chibiliti mzimu wanu uwuse mumtendele. Farao mawa tambala oyamba ali kale kuti chipatala and devie katundu akamuona kuti asang'alule game. Thank you guys pitilizani ndithu
It’s very sad to learn about the passing of Mr chibiliti, you played a very big role in this episode, my condolences to the entire clue of Tonde Wadula and his family……may his soul Rest In Peace
Zomwe wayamba Dave ndi zomwe zikupangitsa kuti Edzi izipilirabe ,zikuchitika , achinyamata uwu si mwayi koma pothera....thank you Tonde....
AKUTI WAKONZEKA DAV BWANA KKKKK
Awesome 💥
GAGA N NAZOMBE Mwaipanilira this ep
Kkk😂gaga ati mnyamata ameneuja Ali ndi ndalama zonyasa😂😂😂
Gaga ndi number one love you bro
Ilibwino kwambiri, Asiyatu adyetsa katundu uku😂😂😂😂😂😂
I appreciate you all. Rest well brother Chibiliti we shall remember you in prayers munkatichotsa nkhawa.
David blackmail imeneyo kkkkkkk wadya ngini bass😂😂
Rest well chibiliti, km all in all this comedy is nothing without king gaga😂😂😂😂😂😂
Kufunsir kw na legend,#Gaga.
Nazombe iyiso waiphura mosavuta
Nice one and rest in peace Mr chibiliti😢😢😢
Kodi ndizoonadi kuti achibiliti anamwalila
@@TwaibuMustaph yes zoona boss malilo akeso anatumiza ku UA-cam ya nkhalango multimedia mutha kukaonera
@@Bikyzgaming guys be serious here
@@Bikyzgaming where is the video?
Falao waiphura 😂😂😂 congrats
Gaga anakonza zatheka bas
Farao ndi chiso mumandiwaza. Asuyatu mwayamba uhuletu mpaka zibwezi zitatu umu ndi momwe zikuchitikila m,mabanja
Koma Gaga u made my day
Rest in peace Mr chibiliti 😭😭😭 tizakusowani ndiluso lanu farao zatheka sopano kma eeee umalimbikila ❤❤❤
Davie naye aying'alula kuno😂😂😂😂
Kkkk Gaga wapanga ngati munthu wamfundotu zigulire malo basi
Komatu episode imeneyi ya koma zedi 😂😂😂.keep it up and rest in peace Mr Chibiliti
Gaga sazatheka guys ❤
Gaga kuzigulira Malo koma patuma ndiwe stunning beautiful I like you
But gaga 😂😂😂😂😂eish gaga ndi galu wachabe😂
😂😂😂 ndiye Mr Devi mkuoanga blackmail asiyatu koma sibwino
Komatu Farawo😂😂 mawa ku sikelo eeeti😅
Gaga its too much, mamina osamba??? Rest in peace Mr Chibiliti
Welcome back guys. Sorry for the loss. May his soul rest in peace
Pharaoh wawina chigayo😂😂😂😂😂❤
Welcome back guys koma rest in peace Mr chibiliti until we meet again
Kkkkkk chefalawo sopano kkk ,muthawi yowawisa pomwe taluza muthu wachikulire mr chibiliti
Nice commedy
Afarawo kuvuta kosekuja lero mwai wapezeka mwayamba chidodo😂😂
Big up family kutuma gaga sunatume kape
Faraoh man of the moment 😂😂 mawa tambala akangolira wakusikelo welcome back guys and mr Chibiliti continue to rest inpeace
anangumbo pepani mr chibiriti😂😂😂
Gaga suzatheka😂😂😂
Big up to Gaga and keep rest in peace Mr chibiliti
Last born rest well chibiliti😢😊
Achibiliti kumeneko kunali kuyang'ana kwanyumba kkk Komabe sorry kubanja loferedwa, rest in peace bambo chibiliti
Mr chibiliti dzimuwanu U usemutendela
Will indeed miss mr chibiliti.... Amatha hvy
Koma Devi ndi Gaga mumakwana pepani akubanja lachibiliti mulungu akutoNthozeni
Gaga haha aye
Koma Dave, ungondidyesa katundu😂😂😂😂katundu wake utiyo anenedwayo.
Rest in peace mr chibiliti mzimu wanu uwuse mumtendele. Farao mawa tambala oyamba ali kale kuti chipatala and devie katundu akamuona kuti asang'alule game. Thank you guys pitilizani ndithu
Eish guys Mr Chibiliti amwalira litilo?
Gaga ati alindi ndlama zonyasatu
Rest in peace Mr chibiliti
Gaga ndee wangoyika mfundo mbambande cholinga amvane ndi mlamu?
Kodi munali mutaisunga seweloi. Naga mesa chibiliti watisiya😢
Gaga ndi Nazombe ndi madolo achabe😂😂😂
Gaga zikatheka umuuze mulamu wako kt akupase dimba😂😂
Achibiliti asiya nkaz wanyowan kwa achemwal awo kaya amukwatle nkaz uja ndan😢😢😢
Faraoh akuona kuchedwa tsiku lopita kusikelo
RIP 💔 Achibiriti 😭 anagumbo munawakonda hvy
Banja tsopano achisomo rest well achibiriti😢
Rest in peace Mr chibiliti
Farao chikondi chako chapamwqmba
Gaga munachenjeretsa kkkkkkk
Davie kkkkkkkk
Ife ndi amulungu ndipo kwa mulungu tikobwelerako
Achibiliti tilisowa luso lanu😭😭mzimu wanu wuutse mutendere🙏
Achibilit tikusowani mzimu wanu use mtendere
Rip Mr chibiliti koma Davie, Mr zimveka and gaga eeee makhuluku 😂😂😂
RIP mr chibiriti m'zimu wanu uuse m'ntendere
May the soul of Vinicent Lester , rest well
Waying'alura Gaga ❤😂
KOMA DAV KKKKK KULHA KATUNDU OSALIPIRA KKKK CHIPWANHA AKU PWANHAPWANHA DAV
Gaga ndi more😂😂😂
Take it or leave it Gaga amatha
Koma gaga eee ndi dolo uyu mpaseni plot, rest in peace Mr chibiliti, we will remember you as best comedian of the time
Koma anthuwaaa
Farao mmawa wakuskelo😂😂😂😂❤❤❤big up guys,
Rest in peace mr chibiliti mwawasiya anagumbo manja alikhosi
His last move may u soul rest in internal peace Mr Chibiliti😢😢😢 we will mis ur part and acting
Chibiliti mene wakalambila iwemo uziti mwana last Born 😅
I will miss Mr Chibiriti 😢
Gaga umakwana basi big up sorry Ku family ya chibiliti 😭😭 madala mulungu akufungatileni
Koma chonde ngat kuli kotheka chifuniro abwereso please, kayà abwera ngat m'bale wake wa chifuniro,bola abwere , by the way rest in peace a chibirit
Ase Mundey musiye zlivekayo lndi 1.6 yakeyo ine Baby Rasta ndikupasa 2.9 kashe ndimakhala pasinja pa Mondiwapa kuyandikira kuchifumu asakupusise
🎉🎉🎉🎉Gaga adakonza all in all rest in peace Mr chibiliti
Patuma wanga patuma wanga kkkkk yakwamwire
Sizawayiwala Mr chibiliti rest in peace my king I can't forget you all the time
Kamtu izayambire popotu chonde abale ndi alongo timakunyadire from south africa pumalanga ❤❤❤❤❤❤
Anagumbo ndiwomwe apha achibiliti Mr last born
Tikusowani bambo chibiliti,gaga umantha
Tchimo likati lizunze ochita, eeee umalakalaka kusamuka koma ulibe zokuyeneleza.
Chikobility Allah ☝️ bless him 😢
Ndy KT chifuniro uja adamwaliradi kpn nzamusewero?
Keep on resting in peace, Mr chibiliti
Rest in peace achibiliti, 😢😢 mumatisangalasa kwambili mu seweroli, luso lanu tilisowa ife 😢😢😢
Mulungu awachitile chisoni ndi chifundo Mr Chibiliti RIP
Welcome back
Ndinakusowana anthu anga rest in peace Mr Vincent
Falao watenga basi rest in peace mr chibiliti tikusowani baba mulungu atothoze akubanja lonse la A chibiliti
Welcome back guys zachisoni Mr chibiriti mulungu akawe nanu
Rest in peace mr chibiriti 😢😢😢😢😢 we miss u forever
RIP. Mr chibiliti😢😢😢😢tikusowani
Pokhapa gaga wandisewelela yabwino koopsa ndipo waitha simasewela eishiiii
Asiyatu adyesa katundu wa chipwanya kkkk
Mzimu wa a Chibiliti uwuse mumtendere
Gaga uyambise chipani 😂😂😂kpt up
Mr chibiliti we gonna miss u for ever mumatisangalasa Koma ifa eish samasamkha ur soul rest in power
😮😮😮 mwatikhomelela mwatisiya malele kkkk 🤣🤣
Gaga ndiwe dolo
Asiyatu wagwidwa kunoooo😂😂😂😂😂
Inna lillah wainna ilayh rajiouna father lester😢
RIP Mr chibiliti
Gaga , Azimveka
Ndinu akamuna basi
Welcome back guys and rest in peace mr Chibiliti😢