Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
I love the way sangie and piksy act.
Ntebede adzathera mmanja mwa Albert ndinthu 😂😂😂 coz yhoooo! 😂
😂😂😂
Sangie is my favorite usauver character
I love sangie and pikxy the way they act
Sangie ndi Piksy my fav 🔥 🔥 🔥 Ganizani eish 👌Ati mng'aluriii eeeh😂😂😂😂😂
Ganizani game mbolatu apa 😂 Mr n Mrs Ngozo mmabebesa, Albert nde sizikumuendera 😂 Edo umandiwaza hvy suchedwa kuing'alura 😂😂 mmakwana guys 🔥🔥🔥
Anthu onse oshota let's gather here , lero ayitulutsa😂
Best actor sengie and piksy love u guys makometsa koma arbat ndi m,busayu azaphana ndithu kkkkk
I like most the way this guy called gani acts😂 eeee ichichi chimatha🙌🙌🙌 receive your flowers gee🌹🌺
Sangie and piksy the way you acting mandichotsa nkhawa....l love you guys❤
Ngati isathetu🔥🔥banja la a ngauzo ndi one❤
Edoo pakamwa osatsekaaa,kumangolankhula lankhula....ndiwo zagulu zibudukaa
😂😂😂😂 this is more than international
My favorite is amanthuuuu I like her voice
Touchy ❤
Ainake
Ine koma Gani😂
As if it should not end, very very nice
Eddo Mng'aluri😂😂😂😂
Gani🤣🤣🤣🙌Kodi Albert umangopeza ma type a Ntebe??😂😂😂
❤❤❤...to be honest guy's really like this comedy...keep it up guy's...mumakwana angauza
Albert zikuwoneka kuti zakazizi sizinamuyanjetu usamare nawonso abusawo 😂😂😂😂❤❤❤
😂😂 sizimuyanjadi
Gani is everything amwene ati nanga mmene ndililimu size 8
Nde ndizioneka ngati L tu 😂
Ndalama zako ndi zanga Mesa I love that kind of talk❤️😂😂😂 basi tiyeni kwa Eddo akandiuze mabodza🤣🤣🤣🤣 I can't wait for this week's episode 🥳🥳🥳🥳🥳🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Ngozo is a good family man in this movie❤❤ I love the way he is being there for patricias pple
Koma guys to be honest mwaiponyera kwakuya nowadays keep the fire burning 🔥
Angozo, Gani n Patricia inuyo guys ai zikomo🙌 keep the fire burning 🔥
Zikandizeraso Albert ndikhoza kumuwza😂😂😂😂
It's Ngozo and sangie for me ❤️❤️❤️
😂😂😂 Albert Sali safe ndi Mashas
Barman 😂😂 wopepelapepela mwadodongosolo ngat uyu sinamuoneko😂😂❤❤
Good work usauver 🎉🎉🎉
Choyamba, Gani amatha nego🤣🤣🤣🤣 Naye patilisha ndikutchingila🙌🙌🤣🤣 lastly Ntebe zina azitha kumwela madzi eeeh🤣🤣
Mtebe azaphedwa
I always look forward to Usouver. You guys mumatha
I feel sorry for Albert,Poor Albert 😂😂😂
Me too iìiiish
Big up ganizan and the camera men trip ino munabwerad de camera is good u have improved alot
Waiting for next episode 🎉
Sangie ndi Piksy amabebetsa 🎉🎉🎉
kwabac🎉
@@RabeccaChafulumira akapanda kupezekamo simmamva bwino
Iyi nde yaphikidwa kuyamba mpaka kumaliza kkk koma mtebe ulendo uno asaziyambe aphedwa 😂
😂😂😂😂😂 komatu Ntebede sazatheka kumushoshatu Albert😂😂😂 can't wait next episode
The bar man my favourite
Amanthu ndi dolo amwene😂😂😂
Mtebe chomwe umafuna ukazachipeza uzanena sure 😃😃 koma Albert azakuswa
Sangie n angozo ur the best 🙏
Keep it up guys we're really enjoying it in Pietermaritzburg SA
I think Albert ndi abusa amakonda zofanana🤣🤣🤣🤣
🎉piksy and sangie my favourites keep up the gud work ❤
Munthu sungakhale okwiya nthawi zonse...pamazabwera usauver
But the song at the end🔥🔥. You are sitting on gold. Release it and let us abuse it here
Komatu zithuz zikukoma😂😂😂🔥🔥🔥🔥
Koma Usauver I can't stop laughing 😂😂😂😂
ine ndi timu gan koma na iyi yokha m'busayi wandionjeza, kumeneko nde kumulonda mmapazi arbat😀😍
🤣 🤣 🤣 🤣 🤣 Ndipo mkazi Albert waonjezatu naye
Aah 😂😂😂 akuti mukuoneka kuti munaiyesatu imeneyi 😂😂😂😂😂😂
Eshiiii so fantastic eee....I really enjoyed it....buuuuut u r taking time guys aaaa inu
Albert zachikondi ingozisiya simbal yanu dzadzy😂😂😂 nanga kumangodyeledwa
Ilibho guyz..eagerly waiting for the next part😊
Tonde kukhala neba wa Abusa sichifukwa, uzipanga zako😂😂😂😂 love u guys mwainu tikondwera
Dis is wow🔥🔥I can smell nxt episode kwachema
Piksy wayamba kuoneka ngat MDee manager wa Jetu 🤣🤣🤣
Iyiyi nde ka m'busa kachinyengo kaipha😂 😂
😂😂😂😂 alarm ngati ikudzutsa munthu wakufa 😂😂😂 kma Ngozo 🙌🙌🙌
I love you guys ❤❤❤ 🔥🔥🔥🔥🔥
Banja la ngauzo palibeso🔥 kma guys machedwetsa Kaa
Am a big fan of Usauver🤗
That's true Maguy you take long time musanapange release episds mpaka ka attention kakumathawa kuti tinasiyira pat
Amathu mmmmmm ndi shasha kkkkk big up
Piksy favorite ati mesa size 4 ndi ya azimayi nanga palinso azibambo a size imeneyo
Ganizani ndi more 🔥🔥🔥🔥
Great acting in here🔥
Mathu ukubweratu ndiyakoyako tsono as if siukumudziwa Ngozo bwanji 😊
You are taking longer to realise epsode guys
It was released earlier kungoti we had to pay to watch it thru Ulinzinga mode
Pano is for sale kkkkk
Fact
Release or realize😂🙌
@@cathbertpamenepo 😂😂
Ati ndizioneka ngat L 😂😂😂😂 Gani is a vibe koma 😂
Albert angosiya zama love azingomwa bawa
Wow gys mukutenga nthawi kwambiri pls
where can I download this movie ? this movie is so so amazing
Obviously piksy your number one ❤❤
Like sangie and ngozo ka nice family
Mtebe wagwa nayo 😂😂😂😂😂Edoo muudzeni albert
mtebe kkkkkkkkk
Kodi nyimbo ikuseweredwa ku mapetoyo ndingayipeze bwanji?
Usauver more blessing💥💥
Kkkkk 4n yamamuna ndiyovuta😂😂😂😂
kkkkkk
Mwana wabwera chifukwa cha pephero yo 🤣🙆🙆
Kkkk 😂😂 km guys wowo Mwana wabwela chifukwa chapephelolo
Kkkkkk koma ntebe akhuzumuke ndithu akugulira bwanji mowa nkaz oti samudziwa
Mmm guys episode mwaisithatu iyi .. episode 8 inathera ku food .. ❤spicing ngat rajah 😂
Mmene ndikuonera Albert zachikondi alibe mwayi kkkkkkkkk
We can be streaming pa ulinzinga po but please ka fair price nanga tigule bundle then kulipilasoo eeh ....atleast if app ija could work like Netflix app
Mng'aluri Eddo😂😂
Patricia and ngozo 👌🏼Amathu and Eddo 🥹Beautiful combination😅
Apa nde mwabwera kwina kuja sitikanakwanitsa ma 1sau pompo 1sau ina bundle 🔥
I love pisky n sangie the way act❤
Patricia and Ngozo litakhala banja lenileni lingakhale bwino
Nde ndichamwano!Imene ija alarm chilira ngt ukufuna kudzutsa Muthu wakufa
Love this from ndirande side❤
Patricia ndi ngauzo😅 Patricia yamulakwila phone wakanizidwa😂 Albert pepani matius watengaso madam ndiye abusa amugulilanso mowa😂😂😂kaya zitha bwanji?
Nde mpaka ngozo kumvomeleza kuti ndi wamwano kkkkk
The work suit man
Angoz mumakwana inuyo is my favorite
Nawenso Duntu ziyankhula ngat mwamna kaya 🤣🤣
1 week ndiyokwana for another episode mumachedwa mmm
Good guys ❤ especially to my guy pkcy
Awatu ubusa uzawatheratu sure 🤣🤣🤣🤣
Mutatulusa Cha 1hr simungalakwiseso
I love the way sangie and piksy act.
Ntebede adzathera mmanja mwa Albert ndinthu 😂😂😂 coz yhoooo! 😂
😂😂😂
Sangie is my favorite usauver character
I love sangie and pikxy the way they act
Sangie ndi Piksy my fav 🔥 🔥 🔥
Ganizani eish 👌
Ati mng'aluriii eeeh😂😂😂😂😂
Ganizani game mbolatu apa 😂 Mr n Mrs Ngozo mmabebesa, Albert nde sizikumuendera 😂 Edo umandiwaza hvy suchedwa kuing'alura 😂😂 mmakwana guys 🔥🔥🔥
Anthu onse oshota let's gather here , lero ayitulutsa😂
Best actor sengie and piksy love u guys makometsa koma arbat ndi m,busayu azaphana ndithu kkkkk
I like most the way this guy called gani acts😂 eeee ichichi chimatha🙌🙌🙌 receive your flowers gee🌹🌺
Sangie and piksy the way you acting mandichotsa nkhawa....l love you guys❤
Ngati isathetu🔥🔥banja la a ngauzo ndi one❤
Edoo pakamwa osatsekaaa,kumangolankhula lankhula....ndiwo zagulu zibudukaa
😂😂😂😂 this is more than international
My favorite is amanthuuuu I like her voice
Touchy ❤
Ainake
Ine koma Gani😂
As if it should not end, very very nice
Eddo Mng'aluri😂😂😂😂
Gani🤣🤣🤣🙌
Kodi Albert umangopeza ma type a Ntebe??😂😂😂
❤❤❤...to be honest guy's really like this comedy...keep it up guy's...mumakwana angauza
Albert zikuwoneka kuti zakazizi sizinamuyanjetu usamare nawonso abusawo 😂😂😂😂❤❤❤
😂😂 sizimuyanjadi
Gani is everything amwene ati nanga mmene ndililimu size 8
Nde ndizioneka ngati L tu 😂
Ndalama zako ndi zanga Mesa I love that kind of talk❤️😂😂😂 basi tiyeni kwa Eddo akandiuze mabodza🤣🤣🤣🤣 I can't wait for this week's episode 🥳🥳🥳🥳🥳🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Ngozo is a good family man in this movie❤❤ I love the way he is being there for patricias pple
Koma guys to be honest mwaiponyera kwakuya nowadays keep the fire burning 🔥
Angozo, Gani n Patricia inuyo guys ai zikomo🙌 keep the fire burning 🔥
Zikandizeraso Albert ndikhoza kumuwza😂😂😂😂
It's Ngozo and sangie for me ❤️❤️❤️
😂😂😂 Albert Sali safe ndi Mashas
Barman 😂😂 wopepelapepela mwadodongosolo ngat uyu sinamuoneko😂😂❤❤
Good work usauver 🎉🎉🎉
Choyamba, Gani amatha nego🤣🤣🤣🤣 Naye patilisha ndikutchingila🙌🙌🤣🤣 lastly Ntebe zina azitha kumwela madzi eeeh🤣🤣
Mtebe azaphedwa
I always look forward to Usouver. You guys mumatha
I feel sorry for Albert,
Poor Albert 😂😂😂
Me too iìiiish
Big up ganizan and the camera men trip ino munabwerad de camera is good u have improved alot
Waiting for next episode 🎉
Sangie ndi Piksy amabebetsa 🎉🎉🎉
kwabac🎉
@@RabeccaChafulumira akapanda kupezekamo simmamva bwino
Iyi nde yaphikidwa kuyamba mpaka kumaliza kkk koma mtebe ulendo uno asaziyambe aphedwa 😂
😂😂😂😂😂 komatu Ntebede sazatheka kumushoshatu Albert😂😂😂 can't wait next episode
The bar man my favourite
Amanthu ndi dolo amwene😂😂😂
Mtebe chomwe umafuna ukazachipeza uzanena sure 😃😃 koma Albert azakuswa
Sangie n angozo ur the best 🙏
Keep it up guys we're really enjoying it in Pietermaritzburg SA
I think Albert ndi abusa amakonda zofanana🤣🤣🤣🤣
🎉piksy and sangie my favourites keep up the gud work ❤
Munthu sungakhale okwiya nthawi zonse...pamazabwera usauver
But the song at the end🔥🔥. You are sitting on gold. Release it and let us abuse it here
Komatu zithuz zikukoma😂😂😂🔥🔥🔥🔥
Koma Usauver I can't stop laughing 😂😂😂😂
ine ndi timu gan koma na iyi yokha m'busayi wandionjeza, kumeneko nde kumulonda mmapazi arbat😀😍
🤣 🤣 🤣 🤣 🤣 Ndipo mkazi Albert waonjezatu naye
Aah 😂😂😂 akuti mukuoneka kuti munaiyesatu imeneyi 😂😂😂😂😂😂
Eshiiii so fantastic eee....I really enjoyed it....buuuuut u r taking time guys aaaa inu
Albert zachikondi ingozisiya simbal yanu dzadzy😂😂😂 nanga kumangodyeledwa
Ilibho guyz..eagerly waiting for the next part😊
Tonde kukhala neba wa Abusa sichifukwa, uzipanga zako😂😂😂😂 love u guys mwainu tikondwera
Dis is wow🔥🔥I can smell nxt episode kwachema
Piksy wayamba kuoneka ngat MDee manager wa Jetu 🤣🤣🤣
Iyiyi nde ka m'busa kachinyengo kaipha😂 😂
😂😂😂😂 alarm ngati ikudzutsa munthu wakufa 😂😂😂 kma Ngozo 🙌🙌🙌
I love you guys ❤❤❤ 🔥🔥🔥🔥🔥
Banja la ngauzo palibeso🔥 kma guys machedwetsa Kaa
Am a big fan of Usauver🤗
That's true Maguy you take long time musanapange release episds mpaka ka attention kakumathawa kuti tinasiyira pat
Amathu mmmmmm ndi shasha kkkkk big up
Piksy favorite ati mesa size 4 ndi ya azimayi nanga palinso azibambo a size imeneyo
Ganizani ndi more 🔥🔥🔥🔥
Great acting in here🔥
Mathu ukubweratu ndiyakoyako tsono as if siukumudziwa Ngozo bwanji 😊
You are taking longer to realise epsode guys
It was released earlier kungoti we had to pay to watch it thru Ulinzinga mode
Pano is for sale kkkkk
Fact
Release or realize😂🙌
@@cathbertpamenepo 😂😂
Ati ndizioneka ngat L 😂😂😂😂 Gani is a vibe koma 😂
Albert angosiya zama love azingomwa bawa
Wow gys mukutenga nthawi kwambiri pls
where can I download this movie ? this movie is so so amazing
Obviously piksy your number one ❤❤
Like sangie and ngozo ka nice family
Mtebe wagwa nayo 😂😂😂😂😂
Edoo muudzeni albert
mtebe kkkkkkkkk
Kodi nyimbo ikuseweredwa ku mapetoyo ndingayipeze bwanji?
Usauver more blessing💥💥
Kkkkk 4n yamamuna ndiyovuta😂😂😂😂
kkkkkk
Mwana wabwera chifukwa cha pephero yo 🤣🙆🙆
Kkkk 😂😂 km guys wowo Mwana wabwela chifukwa chapephelolo
Kkkkkk koma ntebe akhuzumuke ndithu akugulira bwanji mowa nkaz oti samudziwa
Mmm guys episode mwaisithatu iyi .. episode 8 inathera ku food .. ❤spicing ngat rajah 😂
Mmene ndikuonera Albert zachikondi alibe mwayi kkkkkkkkk
We can be streaming pa ulinzinga po but please ka fair price nanga tigule bundle then kulipilasoo eeh ....atleast if app ija could work like Netflix app
Mng'aluri Eddo😂😂
Patricia and ngozo 👌🏼
Amathu and Eddo 🥹
Beautiful combination😅
Apa nde mwabwera kwina kuja sitikanakwanitsa ma 1sau pompo 1sau ina bundle 🔥
I love pisky n sangie the way act❤
Patricia and Ngozo litakhala banja lenileni lingakhale bwino
Nde ndichamwano!
Imene ija alarm chilira ngt ukufuna kudzutsa Muthu wakufa