I like the song powerful message
Zamphamvu
Nyimbo izimveka mogwira mtima ngat iy pitilizan pasta
Good job
Mchewa woganiza uyu uime u mp tizakuvotera
Nyimbo yopatsa chiyembekezo,, zoonadi posachedwa tinyamuka kupita kwathu komwe kulibe moyo osalira
Imandiwaza bwanji ❤
Ulemu wanu Akalumba kwaya
Koma mumakwana msamame kalimba woee
Amen ❤
❤❤❤Congratulations ladies and gentlemen
Wooo glory to God
At chinkhoma in kasungu
❤❤❤❤
Proud to be Sena . Koma ndkufunambo nyimbo zidaimbemwe na Davie Mkhutche ndkuzisaka kwabasi plz plz .
Zilibwino
Keep it up God must be Glory 🙏🙏🙏
I love this song so much yooo 🎶🎶dancing
Amen
Good. Song
Well organised choir, koma sizikufunika munthu wa mulungu ku ma tinta tsitsi.
Well organised choir
Zikuchita kubebatu
Well done
🙏🙏🙏🙏🙏🙏Amen ambuye timakunyadilan kwmbli
Nyimbozi mutumize zose zimatisuthila kozama
Mumatitsitsimutsa amen
Nyimbo yabwino keambiri❤❤
❤❤❤❤❤ amen
Nice one❤❤❤❤
Komatu kunali ma danko kkkkkk ambuye alemekezeke
I love this song
Mwandiimbila bwino Ambuye akudalisen in nonse munatengapo mbali zikomo
Mbambande
Ndavwera nyimboyi 3 days panu koma ndukanika kukhutisudwa nayo, zulo ndagona past 12 kumangomvera nyomboyi ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤❤ guys you touched my heart, ndipo ambuye akudaliseni kwambiri
Kuimba uku nkwakupulumusa miyoyo yanthu ndithu, ambuye azipitiliza kukudalisani guys ❤❤❤
Ineee kumtima myaaaaaaa kumavwa nyimbo zanu akalumba, ndipo ambuye azikudalisani kwambiri ❤❤❤
Ziri bwino koma kuvina kwinaku si Kwa yesu
Amazing 😍, glory to God 🙏
Nice songs where I can find kalumba
AMEN
maphwanga apa ndiye mwabweratu,,,,respect mkaziyo a choirmaster inunso mmatha inuyo ine choirmaster mnzanu ndatero,, moni kwaya yonse kuchokera kuno ku Blantyre
Ilove this song from Area 36❤❤
My favorite song
) 😊
Keep the fire burning guys am blessed
Voice yabwino