- 4
- 324 417
Joel Suzi
Приєднався 14 жов 2007
Thomas Chibade_MUKANDITAYIRE KUNYANJA (AUDIO)
"Mukanditayire ku Nyanja" is a solid local reggae jive song released in 2005 by one of Malawi's popular musicians, THOMAS CHIBADE presents a vivid picture of domestic violence and advocates an end to it. LYRICS (ChiNyanja) (Chichewa):
Abambowa 'samaone chonchi
Akavala bwino ulemu poyenda
Koma akaledzera mkazi ndi kapolo wawo
Kumenya mkazi ngati mwina apha munthu
Akaledzera amafuna nsima, ya ndiwo zankhulu komanso sanagule
Akamabwera mkati mwa usiku, amayi amangolira: "zibhakera zikubwera"
Ana kulira momvetsa chisoni, amayi akutuluka magazi mphuno ndi mkamwa
Akumalira momvetsa chisoni mayi modandaula, kuganizira kwao
"Amuna anga chonde!"
Mukanditayire kunyanja
Ndatopa, ndikapume
Ndikamakufunsani chilungamo, mumandiyankha mwano, ndalakwanji ine?
Anthu akwathuwa akundidabwa oh! chifukwa ndanyozeka
Poti mwandivula ufumu wanga
Banja ndikupilira koma ayi zina zinyanya
Amayi asakachedwe kuchigayo, ku msika kapenanso ku mjigo
Kothyola mnkhwani ngakhale kudondo
Abambo amawatsatira konko
Kuwachititsa manyazi pagulu
Ngati nkuchigayo ufa onse kutaya pansi
Kodi bambo mukamachita choncho, mumamva bwanji muli ndi mulongo wanu
Mwamuna wake akumuchita choncho, inu okhala ankhoswe mungaweruze bwanji
Kodi siuja kale munkangolira amayi anu akutibulidwa ndi mwamuna wao oh!
Koma ngati ndi nkhanza zoyamwira, bambo adamwa tameki nanga mukaniranji?
Musamatero choncho
Bambo kutangwanidwa ndi wana kuntchito
Tiwana take tosayenera kutero
Kunama: "It's my office" mwina "Don't worry woman"
But second see kuti ako ndi mwana
Tiwana take small in appearance, teenager genuine but danger in actions
Tikuchitira mwano mwini mwamuna, kulankhula motumbwa: "Nafenso tidya mommo"
Mwanawe tamadzimvera chisoni, mDala uli nayo is same size with your father
Akazi am'banja sizidole ngati akukwanani atayireni ena, akasiyanitse....

Ndi mwayi wanu bambo mwakwatira
Musungane likhale banja la mtendere
Anzanu afuna banja salipeza, awo!
Angokwatira akazi aziwewe kale
Othamanga, amwano, opanda mwambo
Bambo ndipemphe chimodzi muleke nkhanza
Amayi wanga musafere banja
Kutchena ndi kukhwasula, mumtima ndi kapolo
Nyimbo yanga siyothetsa mabanja
Ine ndikungoimba nanunso mayi mumve poti...
Akazi ena mumayerekedwa, mukaona mwamuma akukhalira pakwanu oh!
Kusamva, makani ndi chisembwere, kusanduka mwamuna:
"Kasake deya tidye", kulepheranso
Zimakhala choncho, dziko lake lomweli
Awo adali ndi mkazi wao, wa ulemu, womvetsa, wosunga mwambo
Adawathawa chifukwa cha nkhanza zawo
Zimakhala choncho, dziko lake lomweli
Amayiwa adali ndi mwamuna wao, wolera, woveka, wodyetsa, womvetsa
Adawathawa kaamba ka chisembwere

Переглядів: 102 357
Відео
"Tidzingocheza" (AUDIO) The Black Missionaries (KUYIMBA 10_promotional track)
Переглядів 221 тис.9 років тому
a signature Chileka_lovers_rock tune by the great Black Missionaries. Part of promo releases ahead of KUYIMBA 10. WE LOVE MaBlacks!
Soul Raiders CHIKHALIDWE
Переглядів 46010 років тому
Chikhalidwe is taken from Reggae Revolution the second album from the Soul Raiders. This reggae "ballad" provokes reflection on moral degradation in the society.
Crazy Market Fight - Thekerani Malawi (by joel.suzi).3gp
Переглядів 1,1 тис.13 років тому
two guys exchange blows (and beverage bottles too) after the other trespassed and was drinking liquor on his friend's grocery shop. I captured it on my phonecam on my work travel sometime in 2010
Eeee nyimboyi imandikumbusa zambili Rest & peace chibade
Rest in peace Legend
Dolo kwa ma Dolo onse
one of the best band in the country MW the best
❤❤❤❤❤
Luther vandloseuth
Akangondimenya ndimaiphulitsa iyi😂😂😂
😂😂😂
This song made my day,, continue resting in peace gee
Enjoying the. Music
2024 tiyeni tiyeni tiyeni eishhh
2024 and still listening to the one of the legends in the business
Rest well my brother thomasi chibade i will remain your fan paka kale
He was genuine legend
If youve ever been taken for granted this song hits different when that moment comes.
May his soul rest in peace
Mbambande black missionary palibeso
May your soul rest peace...
You are one of my legends 😢😢
Those days when l was ristening to this song on my way to Mzuzu from Byrantyre with dad esh rest well bro
God bless you all
Iyi imandikumbusa mai anga akupangidwa nkhaza ndi bambo angaondipeza😭😭😭Rest in peace Legend
Rest in peace
Rest in peace
Rest well Legend
Rest in peace
Rest in peace
Rip genuine legend
Legend rest in peace
Good muzic
P❤
Strong voice and Strong message Achibade..love your music from Zimbabwe
Master piece of a song!
Nice
Never give up Thom chigoba.
My favorite song
NYC nyc bro
Ooh yès 2022 end am here for Tizingocheza😋 who else remember this song🔥🔥🔥🔥🔥
Say less my brother 🤌🏾
Siyabonga
Good song man
Back then....Chibade iweyo ndi dolo adha...
Zilibwino kwambili
je écoute encore et encore 🇲🇼🇬🇳🇬🇳🇬🇳🇲🇼🥰🥰🇯🇲🇯🇲🇯🇲
From guinée Conakry 🇬🇳🇬🇳🇲🇼🇲🇼🇲🇼 on lov
Ndimakukonda inu, Malawi! Ine ndi mzungu koma basi 🤷🏾♂️🇲🇼💃
The best band!
ur alwys gys
Kale langa Eish nice songs
mumatha ma guy salute
Keep the fire burning we love you guys
Nice song Mablacks
Keep it up
I feel that song,so much!