- 9
- 238 900
Toptik🦁
South Africa
Приєднався 13 жов 2023
Am afro dancehall artist from Malawi
Based in Ntchisi 🦁
Based in Ntchisi 🦁
TopTik - Kamba (Official Audio)
KAMBA LYRICS
Ndanyamula kamba
Ulendo wawutali ndawuyamba
Kopita sindinena
Ndukana kutsatidwa
Ndachifwamba
Mwina nditalikire
Muupeze mtendere
Ndimatchuli zimayina
Ndimasowa
Mtendere
Ooow one day(one day)
Idzakhara one day(one day)
One day(one day)
Idzakhara one day(one day
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah prisoner
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah beggar man
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah prisoner
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah beggar man
No matter
Ngakhale ndilibe makolo onse ineee
But am still pushing
Kuzikumbira chitsime cha moyo wonse ineee
Amasintha abare ako
Chimakhara Chimwemwe
Misozi yako
Bola kusuntha upange zako
Mu nthawi yako
Panga Chimwemwe chakoo
Nyengo zimasintha mama
Zomwe timafuna tizipeza pa mawa
Kulimba mtima kupepusa nkhawa
No worry
Pali zonse zabwino
Ndipomwe ndimafuna ndidzikhara ine
Amandidziwa bwino
Ndiyemwe analenga inee
Amasintha abare ako
Chimakhara Chimwemwe
Misozi yako
Bola kusuntha upange zako
Mu nthawi yake
Udzipangire mtendere
Amasintha abare ako
Chimakhara Chimwemwe
Misozi yako
Bola kusuntha upange zako
Mu nthawi yako
Udzipangire mtendere
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah prisoner
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah beggar man
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah prisoner
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah beggar man
No matter
Ngakhale ndilibe makolo onse ineee
But am still pushing
Kuzikumbira chitsime cha moyo wonse ineee
Amasintha abare ako
Chimakhara Chimwemwe
Misozi yako
Bola kusuntha upange zako
Mu nthawi yako
Panga chimwemwe chakooo
Ndanyamula kamba
Ulendo wawutali ndawuyamba
Kopita sindinena
Ndukana kutsatidwa
Ndachifwamba
Mwina nditalikire
Muupeze mtendere
Ndimatchuli zimayina
Ndimasowa
Mtendere
Ooow one day(one day)
Idzakhara one day(one day)
One day(one day)
Idzakhara one day(one day
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah prisoner
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah beggar man
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah prisoner
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah beggar man
No matter
Ngakhale ndilibe makolo onse ineee
But am still pushing
Kuzikumbira chitsime cha moyo wonse ineee
Amasintha abare ako
Chimakhara Chimwemwe
Misozi yako
Bola kusuntha upange zako
Mu nthawi yako
Panga Chimwemwe chakoo
Nyengo zimasintha mama
Zomwe timafuna tizipeza pa mawa
Kulimba mtima kupepusa nkhawa
No worry
Pali zonse zabwino
Ndipomwe ndimafuna ndidzikhara ine
Amandidziwa bwino
Ndiyemwe analenga inee
Amasintha abare ako
Chimakhara Chimwemwe
Misozi yako
Bola kusuntha upange zako
Mu nthawi yake
Udzipangire mtendere
Amasintha abare ako
Chimakhara Chimwemwe
Misozi yako
Bola kusuntha upange zako
Mu nthawi yako
Udzipangire mtendere
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah prisoner
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah beggar man
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah prisoner
I know God will sort it
I'll no longer leave in life like ah beggar man
No matter
Ngakhale ndilibe makolo onse ineee
But am still pushing
Kuzikumbira chitsime cha moyo wonse ineee
Amasintha abare ako
Chimakhara Chimwemwe
Misozi yako
Bola kusuntha upange zako
Mu nthawi yako
Panga chimwemwe chakooo
Переглядів: 9 518
Відео
Toptik - Chizindikiro (Official Music Video)
Переглядів 36 тис.4 місяці тому
Music Video by Toptik. Chizindikiro (sign ) is a sweet sound created by an amazing Artist. We all know that this was long awaited and it didn’t disappoint. The best Malawian vocalist Toptik. This song is for the lovers and for the ones who can’t keep their hands off each other. Video shot and Directed by Dir Kpaul. Listen to TopTik on Digital Streaming: Apple Music:music.apple.com/us/album/ndat...
Toptik - Ndatopa (Official Music Video) Dir by Kpaul
Переглядів 168 тис.6 місяців тому
#music #lovesongs #malawi #zambia #ndatopa #vegamedia #framecity
Toptik - Sizoona (Official Music Video)
Переглядів 4 тис.6 місяців тому
#duet #live #duo #music #love #malawi #zambia
Toptik - Attention (Official Music Video ideo)
Переглядів 19 тис.10 місяців тому
Toptik_ATTENTION(Official music video) Viacksy magnificent dir #malawimusic #zambianmusic @takticmwofficial4151 @NyandahMw @viacksymagnificentdirector
dolo 🤝❤️🔥
Nice one my artist to ntchisi
Malume awa😎😎
Chinyimbo mbambande
this guy is hot 🔥🔥🔥
Ntchisi to di welod 🔥
Umakwana ngt LA 40
❤❤❤❤❤❤
Nice song bra🎉❤
❤❤❤in love with this tune🎉
Big up muphushen mzanu😂😂
So touching 😢
Iyi ndiye timenyedwa saname
Zaka zichulukilenji kidikilira kudzalira
I know it's one day
Nyimbo yabwino iyi,it's hits patsen mikozi akuthamangisiren ma file
pure talent yosakakamiza,you deserve a trophy 🎉
kom ndkufuna nyimbo yako ija umati,dziwa ukumalira ndmalira nawe,ukamakondwa ndmakondwa nawe ndmangofuna mzikuona ukusekelera ndngaipeze bwanj
you deserve a gold medal 😮
Toptic umakwana ans
Fire 🔥🔥 team toptik where ar u
Fada 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nice one ❤
Nice songs bro
Even here in Nigeria we have all agreed to listen to Malawian music. Even though we don't understand the Language koma eee toptik amatha heavy.
😂😂😂😂
Powerful song
Unaza💪
This is nice my bru keep burning 🔥🔥🔥🔥🔥
🎉🎉🎉🎉
Respect
Nice🎉🎉
Wayipweteka
Is she jst a model or ndi mkazi wake was artists?
Nice 🎉
Breda 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Shasha umatha
Well composed 🎉
Bro taponyani audio yakunjanja nkamabo it's December tiikoke man please kuno ku Livingstonia pat
Nice song
Nice song
Umatha 🔥
Mesa unabwera ngat coming kkk🔥🔥🔥🔥❤️❤️❤️🤝🤝
big up ✨
Keep it up 🥰 you are the best ✨
Nyanda iweyo asee umatha
Ase nyimbo iyiyi eeeee 😢😢😢 ndakhuzika nayo fire 🔥🔥
Zanyimbo
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
❤mwaphatu iyiyi ❤❤
Video ili kuti